Ngati sanaphe bwanji anthu akalankhula akwamanga ife tikudabwa tizifufuza chani this crear aloud chakwara kill chilima all maiko akunja akudziwa
@EnerstManessСағат бұрын
Munasowatu big man inu mumalankhula zaphavu
@AbudulJohnСағат бұрын
Kodi malamulo amagwila ntchito kwa osawuka okha? Kapena malamulowa munapangila ife osawukafe a police officer? Kodi mesa mumati tawamanga chifukwa aluganizilidwa kuti anapha nanga awa bwanji mukukanika kumanga kusonyeza kuti sali mugulu loganizilidwa a police? Kapena mukufuna anthu ayambe then muzati tawamanga chifukwa amayambisa zipolowe mu dziko? Nanga nkhani iyi ikukanini pati a police kutenga anthu amenewa kuwafusa mafutso kuti anthu timve chowonadi Cha nkhaniyi a police kapena inuso muli ku ngwapa kwa bomali? A police ndi Asikali ziwani kuti chilungamo chikukukanikani koma boma likazasinda ambili muzaliza ntchito zanu chifukwa Cha chibwana chanu ntchito yanu ambili mwayiwala Mai chilima kundawula inu mumawawopsezaso ndiye zichani zimenezo munthu adawula mamuna wake muzawona ngati dziko ndi lokondela pasogolo nthawi ikubwela
@isaaczuzeСағат бұрын
Mayi wopusa iwe kwambili .....wadya ndalama iwe ngakhale kunyumba ya malamulo palibe chimene amapanga
@peterlowole7841Сағат бұрын
The truth shall make us free, amangidwe and Tilande misonkhoyathu yonse aba within 48hrs, and re, build our country with it. Palibeso zoyang'ana khope .
@DanfordMkalimbaBandaСағат бұрын
The hands of MCP government are not clean, their ship is sinking never to rise again
@esaMoha-dm4kjСағат бұрын
Ndine Malawi apha ndili ku sautha Africa ndimakusidwa sosho media yonse simene ankushitar ashankwela indedi amangidwe ngat tilindi macoti nkumalawi please 😅
@zimmekapachika6784Сағат бұрын
Afiti okupha amangidwe onse akanyimbi aku Chikangawa