A Lyton Mangochi Awawuze A Malawi Chilungamo - Bon Kalindo

  Рет қаралды 22,405

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

Ай бұрын

On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo comments on what Lyton Mangochi said in praise of the President. He discusses alleged rigging schemes being prepared by MCP ahaed of the 2025 Election.
Ku Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo apereka ndemanga pa zomwe Lyton Mangochi adanena poyamikira Purezidenti. Iyenso akamba za mmene zipani zikukonzekela zisankho mu 2025.
#malawi

Пікірлер: 71
@user-qq4ks5mf2s
@user-qq4ks5mf2s Ай бұрын
Iwe Henry umuti Bon Kalindo president wa afiti?Ngati nzika ya Malawi kumayankhula zinthu zothandidza dziko.Ukuonetsa kuti wadzadza mafinyera mu ubongo mwako.
@HastingsShaba
@HastingsShaba Ай бұрын
Henry ndi manyi
@robertrichman9376
@robertrichman9376 Ай бұрын
Muuzeso kuti pathako pake
@WakuMalawi
@WakuMalawi Ай бұрын
This guy is the real first President of Malawi. Zikomo Mr. Kalindo. Mtima wanu ndi mtima woopsya kwambiri. I admire you.
@victorbanda9039
@victorbanda9039 Ай бұрын
Winiko asatukwane mangochi zoona zake winiko ndimangochi aliyese analongolola pa social media Kuti apeze ndalama koma angosiyana kodyera
@charleslimbani8590
@charleslimbani8590 Ай бұрын
Ndiye kuti kalindo amalandira ndalama ku Dpp
@user-vu5gy8wf8y
@user-vu5gy8wf8y 28 күн бұрын
Mr Bon Kalindo indeed a president for poor Malawians ...Mumakwanila🔥🔥🔥
@stanbanda
@stanbanda Ай бұрын
Mukuziwana
@AafiyaMalek-pt7di
@AafiyaMalek-pt7di Ай бұрын
Big man
@user-wf6on9xb3r
@user-wf6on9xb3r Ай бұрын
Idzi zipangisa kuti tisamakhulupilile ma artist zomwe wachita raiton mangochi mwana wa hule ameneyu .aaa ndithokoze inu a bon kalindo pokhala mbali yathu ife if
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m Ай бұрын
Opposition ikugona konzani zinthu zisanafike povuta
@user-wf6on9xb3r
@user-wf6on9xb3r Ай бұрын
Aaaaa bon kalindo ndiwe mamuna wantanda usatisiye ine ndili ku Capetown south Africa koma ndilinso kumalawi nkonko koma iwe ase bon ayi ndithu ndiwe jontroman BOOOONIIIII KALINDO
@JosephMlungu
@JosephMlungu Ай бұрын
Wodala munthuyo wosayenda mu uphungu wa oipa kapena wosaimirira m njira ya ochimwa kapena wosakhala pansi pa bwalo la onyoza :masalimo 1 :1
@EstherPeter-cf1vf
@EstherPeter-cf1vf Ай бұрын
Fire mabomba bon kalindo auze zoona 🔥🔥
@KhizohMdala
@KhizohMdala Ай бұрын
Mmatiimilira Mr DC
@robertrichman9376
@robertrichman9376 Ай бұрын
You the best
@Moses51
@Moses51 Ай бұрын
The DC bon kalindo
@alimalawi2661
@alimalawi2661 Ай бұрын
Ngat akufuna ngotndo a MCP asabele nde ndipane asaone Kut kod tsiko Muno muli ankapolo okwiya
@mariezorgen7735
@mariezorgen7735 Ай бұрын
Please where are trusted passports also??
@ShadreckNgozo-ng6ll
@ShadreckNgozo-ng6ll Ай бұрын
Kodi ndekuti abomawa amadana ndiwowadzudzula?
@homeremedys3748
@homeremedys3748 Ай бұрын
Amangochi tawapatsa 3 million inu mukuchedwa pati akalindo? Tabwerani ku Emisipiii
@promixphotography8056
@promixphotography8056 Ай бұрын
😢😢😢😢😢😢
@user-nc4vi1jt5g
@user-nc4vi1jt5g Ай бұрын
Kodi munthu safuna ndupelezident azitinamiza kuti akutimenyela nkhondo mabodza takuonani mulongolola mufuna ndalama laitoni mangochi waitha udyendiwanawako mmene umalankhulila
@AlisenMatola
@AlisenMatola Ай бұрын
Komanso ndikudabwa amalawi akupangisa ma I'd akumozambiq akut akavote muokotobala Koma boma likupeleka nkhwimbi la anthu I'd ikutuluka pompopompo zikumachitika usiku
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq Ай бұрын
Pepani ndikhala ngati ndikutsakha mitundu koma sidzili motele akulu akulu alomwe ndi anthu opanga dziyengo mwadziwonela nokha watsala bon kalido yekha basi
@GrecianWyson
@GrecianWyson Ай бұрын
Bon kalindo umakwana.a DPP kuli ziii osatithandiza Ife ovutika .mulilatu atakuberani azanuwo uphungu osewu Koma osachitako Kathu
@mellipherjohn7158
@mellipherjohn7158 Ай бұрын
The DC chilungamo 💪
@JamesKamtedza
@JamesKamtedza Ай бұрын
Layton mangochi ndmene amaonekera munj or kupasa 1 million sangakane athu uphaw unakanda akapexa ka 4n bas kuyamba ma audio cholinga adye ndalama
@ChikondiKammaluwa
@ChikondiKammaluwa Ай бұрын
Wanthu wamuna mukukwana mwava
@successm-vt3dx
@successm-vt3dx Ай бұрын
mwana owopsa kwambiri
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r Ай бұрын
Kkkk kalindo unakwana
@LukaThawe
@LukaThawe Ай бұрын
Zaziiiii
@JosephAlfred-bu7ic
@JosephAlfred-bu7ic Ай бұрын
The Dc
@ChimmsRichardOrden
@ChimmsRichardOrden Ай бұрын
Lyton Mangochi ndi mbuzi wandiradi ndalama ndipo wayamba kulankhula ma VN otamilira Chakwera
@AlickChiumia-zk6id
@AlickChiumia-zk6id Ай бұрын
Kupanga chinthu chabwino kapena choipa kumangobwebweta 😂😂😂eish
@atusayeMtalama
@atusayeMtalama Ай бұрын
Ndindani angakane ndalama, lyton Ndindani, kodi amagwira ntchito kuti?
@user-wu8kp7ui5j
@user-wu8kp7ui5j Ай бұрын
The DC 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w Ай бұрын
Auze zoona zokhazokha ndipo opposition ili ndi tulo kwambiri
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx Ай бұрын
Analandira ndalama asamatiuzeso chili chonse
@JosephJosab
@JosephJosab Ай бұрын
2025 thithithiiiiiiii kumenya kugwetsa
@user-dk4he8zr7m
@user-dk4he8zr7m Ай бұрын
Ku Mangochi sugar ali pa 5 pin zachisoni ku Malawi
@karlchingapa6193
@karlchingapa6193 Ай бұрын
Kalindo akangopemphanso naye! Kalindo alibe njira yeni yeni yopezera living and livity!! This noise he is making won't sustain his livelihood!! Kusauka ndi mbola!!
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq Ай бұрын
Mwalawi yatha basi tdza bwela ikadzachoka mcp kumalawiko chifukwa dzikungo wonetsa kuti olo tita bwela kudza vota dzikungofana
@user-nx7yz4qo8f
@user-nx7yz4qo8f Ай бұрын
A Mangochi analandira ndalama zochuluka kwambiri MOTi PANO ndi millionaire tikutero chifukwa Cha malnkhulidwe awo
@user-lf6qf2tw5o
@user-lf6qf2tw5o Ай бұрын
Mangoch ndi wamasila akufuna chithqndizo kwa chakwela
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Ай бұрын
Akukalonga anakukanilani zobelazo ndiwe kambwe ndiwe waboza
@dontreybanda278
@dontreybanda278 Ай бұрын
A lytoni, analandila ndalama finish.
@stevejizaremu3396
@stevejizaremu3396 Ай бұрын
The DC
@stanleymollen7273
@stanleymollen7273 Ай бұрын
2025 chaka cha mademo...
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete Ай бұрын
Mangochiyo wagulidwapo😂😂😂 basi
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz Ай бұрын
Mangochi wadya banzi
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m Ай бұрын
A mangochi adya chibanzi finish
@uchizJoelMumba
@uchizJoelMumba Ай бұрын
Boni kalindo musamubvele ndiwamisala uyu chisakho sichingabeledwe akungofuna ndalama
@KassimmwSteven-og8ny
@KassimmwSteven-og8ny Ай бұрын
Iwe ndi agogo Ako nose ndinu zisilu osat bon kalindo never
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Ай бұрын
Wamisala ndi iweyo
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Ай бұрын
Ufiti waboni kalindo wasukuluka mulungu simunthu uzalangidwa ndi ufiti wako umati sangandimange koma umangidwa chisilu chamunthu
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Ай бұрын
Umangoziwilati ojiya wa ku state house
@user-dy5bj9ck5e
@user-dy5bj9ck5e Ай бұрын
Chisilu ndi agogo Ako mpwanga Kodi ndiwe ndani pa mnyapako
@user-dy5bj9ck5e
@user-dy5bj9ck5e Ай бұрын
Chisilu ndi agogo Ako mpwanga Kodi ndiwe ndani pa mnyapako
@AlickChiumia-zk6id
@AlickChiumia-zk6id Ай бұрын
E koma akulu inu simutopa nkuyankhula
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Ай бұрын
Iwenso sutopa kumvera ma audior ake
@user-fv8ey8hx6w
@user-fv8ey8hx6w Ай бұрын
Iweyo wadziwa bwanji kuti satopa born kalindo iwenso sutopa nawe kumvera
@johnkambala692
@johnkambala692 Ай бұрын
MCP because of good policies have aleardy won the 2025. So don't waste your time on us.
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd Ай бұрын
ur time not for everyone
@TiyanjaneKapalamula
@TiyanjaneKapalamula Ай бұрын
Panyelo pako
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Ай бұрын
Mwalandila chibanzi chitsiru chamu thu, anapita kumamanjira wangochoka kumeneku a basitu amupatsa ndalama activist zopusa kwambiri....
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Ай бұрын
Iiiiii koma ndiwe omvetsa chisoni
@charleslimbani8590
@charleslimbani8590 Ай бұрын
Bon kalindo waona kuti Boma Lili ndi kuthekera koti lizawina zisankho.....ndiye wabwera ndi yoti boma likufuna kuzabera zisankho
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Ай бұрын
Maganizo amunthu sangafanane ndi zochichita zkambwe bon kalindo daily kunyoza boma ayi iweso ndiye kuti unalandila ndalama ku dpp
@henryhenry6632
@henryhenry6632 Ай бұрын
Bon mathanyula president wa amfiti Malawi
@levymalikebu1813
@levymalikebu1813 Ай бұрын
The problem Malawian politicians is that they act angelic when in opposition. Once in government they change the tune. This guy Bon Kalindo, can say so much. Unfortunately, even the current president is extremely corrupt so much that Malawians are for lack of basic necessities like food. Mr. Chakra promised paradise to Malawians during campaign and ironically he is the pastor who knows what it means to play with God. But see what he is doing, he is so pathetic as far as running the government is concerned. We don't have democracy in in Malawi. I hope one day we'll have a military government. These clowns are coming killing us. To survive in Malawi is a serious challenge. God knows when we will be free from these freaks.
Ma Passport Akuchita Kuyanika Pa Dzuwa Kuti Ituluke  - Bon Kalindo
14:41
A Malawi Lyton Mangochi Musamukhulupilileso - Bon Kalindo
19:43
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 12 М.
ONE MORE SUBSCRIBER FOR 6 MILLION!
00:38
Horror Skunx
Рет қаралды 11 МЛН
Indian sharing by Secret Vlog #shorts
00:13
Secret Vlog
Рет қаралды 49 МЛН
1❤️
00:20
すしらーめん《りく》
Рет қаралды 32 МЛН
If I Was Chakwera I Would Not Have Gone To USA   Bon Kalindo
12:24
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 7 М.
The Confession of Charles Ben Longwe (Part 1)
33:13
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 2,6 М.
Confessions of Charles Ben Longwe (Part 3)
32:42
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 419
UTM Musapusitse A Malawi Lero   Bon Kalindo
17:09
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 36 М.
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51
Jomo wamukana Bon Kalindo
4:20
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 49 М.
MOSES KUNKUYU EXCLUSIVE INTERVIEW
56:13
Zodiak Malawi
Рет қаралды 24 М.
Confessions of Charles Ben Longwe (Part 2)
33:07
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 852