Boma ndilomweli Koma tikufuna kusintha mtsigoleli nde musatikwanepo apa,
@tasmania52718 күн бұрын
@@patriciajangaza675Mtsogoleri ndi yemweyu palibe kusintha kkkkk
@JoelKacheche-x6i17 күн бұрын
Dr Lazarus maccarthy chakwera ndi mcp kulamulira mpaka 2030 wooooo!!!!,dpp sizalamuliranso ziko la malawi kunatha basi; mutha kugwilisa njira zanu zonse zowoneka ngakhale zakumidima,koma palibe mwayi wolowanso mmboma,izi mulungu okhala kumwamba ana sayinila kale kuti Dr Lazarus maccarthy chakwera akuyenda nayo ndodo ya ufumu mpaka 2030,ndipo palibe osusa kapena kulesa ndondomeko yimeneyi,munthu ndani kususana ndi chomwe mulungu wanena ndikuvomereza? Inu nokha simungawone president Dr Lazarus maccarthy chakwera sacheuka, kunthunthumira kapena kuyankhapo zama propaganda ndi zonse zomwe osusa boma akumunyoza,chimenechi ndiye chikhalidwe cha munthu wowina mnjila ya mulungu,akuziwa chimene ali ndi mulungu wamoyo.Enanu muli busy kugwilisa ntchito mphamvu ndi nzeru zanu,with flesh no man prevails but only by the spirit of the lord, watch out!!
@ShamimuBisani18 күн бұрын
Olamulanso ndye 1 opoira olamula madolo akutukula maiko awo pomwe olamul walero chil chonse 0 fertilizer manyaka znthu kudula ndye tonse tikukandra limodzi akakupasa2000kwacha yosowa chogula ndye usiye kulimban ndi opposition garu iwe
@mayesojameskatete18 күн бұрын
Tikuyipasa matama MCP bwanji
@tasmania52718 күн бұрын
Si choncho koma vuto la inu a DPP mukuganiza kuti mungapange intimidate eni ake amu Lilongwe kapena kuwopsyeza MCP, mwachepa kwambiri ndipo muwuzane ndi Namalombayo pamodzi ndi Chisale.