Eya zimafunika choncho,muthu azimva malangizo kwa ena mwapepesabe,bolaniko.
@user-jm8kw9gw2d19 күн бұрын
There's hope, afford party is going to rule this country
@YellowmanMalawi-qe8zh22 күн бұрын
Mwa inu nokha simungawine,pangani alliance
@ManganiStanley22 күн бұрын
Onsewa ndi akuba
@user-nf3ik3ff6y22 күн бұрын
❤❤❤ number one moto buu
@user-nf3ik3ff6y22 күн бұрын
Good message
@princessyvonnesinoya657122 күн бұрын
Chilungamo chiyende ngatu madzi chihana
@stalickkafera345423 күн бұрын
Kusowa zo sapoter
@KassimmwStevenetc21 күн бұрын
Sitingataye thawi kuba 'fundo za ntambo Tambo ndiwa boza owukira amakamba zithu akawina kut wavutika korowera Bora komawonera TV osat zakhutu kuve iyi
@stanleykaludzu-bm4pm23 күн бұрын
More fire Aford
@AndrewChimwaza-rf7hw23 күн бұрын
Timothy ntambo ndinu opepela munaononga kale ziko la malawi ndipo tikudziwa kt mwatumidwa ndi chakwera musokoneze DPP nkhanga zaona. APM my vote
@user-fl7br3dw4h23 күн бұрын
What ever koma walakhula za dzelu antambo tiyeni nadzo tilimbane nawo mpaka tikafike
@GeeGuu-zy4oi23 күн бұрын
@@user-fl7br3dw4h u r right
@user-jn9tz3li3v23 күн бұрын
@@user-fl7br3dw4hThe devil 👿 also knows the bible, do not be blinded
@Kasawalah22 күн бұрын
Yes it's true make alliance kuti muphe chakwela mbava
@ibrahmdoka748623 күн бұрын
Apology received We take neither side in receiving Still we feel pain because of those whom you put in power
@user-he4jv1sb1m23 күн бұрын
Kuzaononga chipani
@JonesChingaya-yf4gg23 күн бұрын
Mtambo ndiwe oseketsa kwabasi, posachedwapa pa zodiak unanenetsa kut sungapepese chifukwa palibe chifukwa chopepesera, ndie lero uzikat ndikukupepesani amalawi zoona????? Koma anthu mukamafuna ma votii, ayi zikomo.
@AUSTENBUSHIRI22 күн бұрын
Amtambo azindikila liti kuti amalakwisa kkkk my malawi
@OwenMajoni-qv3eg22 күн бұрын
Sindi sapota zipani zotsogozedwa ndi banja limodzi.
@user-vw7tj2ss3l21 күн бұрын
Nonse ndin mbala
@KanyozaMatope23 күн бұрын
Ndinkafuna ndigale ndichidwe.. koma chifukwa Cha Mtambo... Aaaaaaa.. bsi
@user-oc9vl9xz8e22 күн бұрын
Freedom fighter
@mcsellahntv689623 күн бұрын
Popanda nfundo, tingonva za akamuzu apa.
@user-dp7bc7yy6s23 күн бұрын
Or mutabwaza bwanji km chikhulupiliro chikataika zimakhala povuta kut uchibwezeletse
@jameshuwanzulu23 күн бұрын
Ayi man peter munthalika anthu anataya naye chikhulupirilo lero bwanji anthu abwezeletsaso chikhulupiro mwa iye
@user-vl5on2lj8b22 күн бұрын
Chikapanda kukuthamangisa ku m c p ukanakapepesera kutu ? Tikudziwa kuti ukupepesa chifukwa anakuthamangisa ku m c p
@AllanChabwela22 күн бұрын
Mtambo,wabudula nmemo wagulu
@vytwistthelion9822 күн бұрын
A Ntambo kutha ma plani kanamizeni ena
@josephykapichi364723 күн бұрын
Following
@giftbanda769023 күн бұрын
Or pa chikondi mukhale mwasiyana ndee muzbwerelaneso mmmh Love imasiyana amwene than the past nde awawa asatipepeleseso😅😅
@eliffagondewe821423 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥
@user-dv6rt6vb6e23 күн бұрын
After kuchotsedwa unduna
@user-zv3cy2xj5p22 күн бұрын
Mwana wathu wathu, osaopa
@GraceLimani-zw7dx22 күн бұрын
Wa hit a bwino kupepesa mtambo ku mtundu wa Malawi unazitenga for granted kuli konse ukupita uwapepesedi a Malawi inawononga Malawi ndi iweyo kuwaphuzitsa ma demo achimata amaononga katundu wa anthu ndiye mupepesedi amtambo
Ndiye lero ukupepesa ku mtundu wa Malawi lero mesa pa zodiak unka kana kupepesa ku mtundu wa Malawi lero wapepesa bwa?
@user-zk7jw9up6m23 күн бұрын
Komaso mwachita bwino kupepesa zikomo
@PrinceKachimanga23 күн бұрын
iwe...ife tikufuna ADADIE.....APM
@spargomw22 күн бұрын
Nganganga kumbuyo kwa Adad❤❤❤
@ChikondiChauma-ib9pg22 күн бұрын
Asilikali or a security 🤔 😅
@user-ln3zx6wo4w23 күн бұрын
Chakachamawa ikupita mcp
@BlessingsTembenu22 күн бұрын
Nsilikali amakhumata? Aaaa
@user-vl8uw8mc3u22 күн бұрын
Dpp boma Apm boma basi
@ashadokhomzy578123 күн бұрын
A Ntambo sopano tinamizeninso tilipano kumvesela
@petermsamariamapira893323 күн бұрын
Kodi atinamize kkkkkk
@JonesChingaya-yf4gg23 күн бұрын
Kkkkkkkkkk
@assankamwendo85222 күн бұрын
Mr Mtambo Thanks for help Malawian to remove APM anatikwana makamaka ndi Chisale wake uja Thanks for giving us good government ever. Better you stop here otherwise you can't manage to remove our almighty Dr Lazarus MacCathy Chakwela. Viva MCP,Viva Malawi MCP Upto 2050 wooooh
@dondamissonchdziwe395823 күн бұрын
Koma Enoch,ndiwe waukali pitiriza Chakwera Ndi khakhakha mzake wa katumbu amangonya nkhanu zokhazokha, Koma heee zirrikoooo
@user-ux9ik4zr5x22 күн бұрын
Can't support this nonsense,he's doing this because of his dismissal from Cabinet,he's just greedy & selfish trying to take Malawians for granted.
@GulliverTower21 күн бұрын
Afford is just useless . T. Mtambo is a desperate man ,hz no direction 😂
@RobertDJambo21 күн бұрын
Mtambo nd opepera uyu
@SamsonMokowa22 күн бұрын
This guy has no interest to human being
@PatriciaTikhiwa22 күн бұрын
Koma mulungu amasadamuzadi zithu. Ndaonera Timothy