ALEX NKALO-ANANSI (OFFICIAL VISUAL) DIR VJ KEN

  Рет қаралды 126,180

AUTO FOCUS

AUTO FOCUS

Күн бұрын

Пікірлер: 462
@MaggieMangani-uj8we
@MaggieMangani-uj8we Ай бұрын
Mwaimbansotu Nyimbo ndinakusungitsani ija 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂this is beautiful Papa and mumve kuti mwatitumikira kwambiri, Ambuye akudalitseni nakulitse malire Anu.
@BatisonKalonga
@BatisonKalonga Ай бұрын
Za serious koma?
@janezimba6960
@janezimba6960 Ай бұрын
Ooh ooh😮
@janetnavaya
@janetnavaya Ай бұрын
kkkkk masten
@TawinaMachowa
@TawinaMachowa Ай бұрын
Powerful song brooo
@comesee-p2ds653
@comesee-p2ds653 Ай бұрын
Ndipo song of the year ndiyiyi.... Be Blessed Mr Nkalo
@HenryMikithayo
@HenryMikithayo Ай бұрын
Nyimbo iyi inabwera kudzakhala sure Keep on fire anampereka ndi anansi
@giftbanda244
@giftbanda244 29 күн бұрын
very true
@EliPhiri-s2j
@EliPhiri-s2j Ай бұрын
Congratulations my brother go deeper l blessed with your songs 🙏
@BrendaChifutwa
@BrendaChifutwa Ай бұрын
Amen n Amen 🙏🙏 eishhhh straight talk, Ambuye aonjezere ma vumbulutso mwainuyo❤❤❤
@janetnavaya
@janetnavaya Ай бұрын
samakhala adera ayi ndithu 🙌🙌🙌anansi omwewa congratulations my bro 😊🙌 tisamaledi ndi anansiwa
@ceciliamponda476
@ceciliamponda476 Ай бұрын
Nyimbo yayankhulira ambiri ophinjika, song of the moment
@preciousnyali2746
@preciousnyali2746 6 күн бұрын
True 😢
@Monicaligomeka
@Monicaligomeka Ай бұрын
Waiswatu dear zokongola and keept up glory to Jesus yeah neh anasi kuti boom🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤❤❤
@Allieukachasize
@Allieukachasize Ай бұрын
Song filled with wisdom. Beautiful melody. Well done
@ThokoPeace
@ThokoPeace Ай бұрын
Am in love with this song muli uthenga ❤your songs Alex keep it up
@MarthaMponda-h4k
@MarthaMponda-h4k Ай бұрын
Goosebumps pomwe ndikumvera😢😢 tidzipemphera ndithu
@EmmaMakonokaya
@EmmaMakonokaya Ай бұрын
This is powerful, bravo ma Zion
@BonifaceChitsamvu
@BonifaceChitsamvu 17 күн бұрын
Ine ndikungofunako nkanjowo koma ikhale mikanjo iwiri ine ndi akazanga❤❤😂😂😂 Love you bro
@AndrewChimphonda-ly2lp
@AndrewChimphonda-ly2lp Ай бұрын
Bomba la uzimu Ulemu kumapatsana mwakunga broo zapamwamba
@WatsonmMarkomkwezah
@WatsonmMarkomkwezah Ай бұрын
LUSO LOBADWA NALO ALEX BIG UP nyimbo yabwino kwambili utha kumanvera every time muli massage ya mphanvu
@BonifaceChitsamvu
@BonifaceChitsamvu 17 күн бұрын
So powerful song nd I po mulungu apitilize kukuonetselani ma vumbulutso ochuluka ndithu
@SydneyDivaison
@SydneyDivaison Ай бұрын
Alemekezeke wakumwambayo ndipo nyimbo iyiyi eeee muli uthenga .
@innocentchimkukuzi4818
@innocentchimkukuzi4818 Ай бұрын
On repeat, this song has made day, what a coincidence , this is what has exactly happened this morning.Aaamen
@EuniceNkalo
@EuniceNkalo Ай бұрын
So proud of you Alex, well done 👏
@GeoffreyChakhaza
@GeoffreyChakhaza 7 күн бұрын
Culturally responsive. As a Malawian.Nyimboi ikuonetsa komwe ikuchokera. your Show can make a good combination with Doc Ethel Kamwendo Banda. keep in touch with her
@LawdAlfandika
@LawdAlfandika Ай бұрын
Kumwamba kuzingolandila ndi malemekezo ake omwe❤❤
@NaamanMtika
@NaamanMtika 13 күн бұрын
A very great piece! Talent 🙌
@danielnamwini3735
@danielnamwini3735 Ай бұрын
Bomba bomba bro Iyiyiiii iyiyiiiii mwaphaaaaa bro Zoona zake Ndanasi omwewa ndithu
@NaoMakah-gh3td
@NaoMakah-gh3td Ай бұрын
Ndipo ikuveredwa tsiku lonse ili pa repeat god bless u bro anas🙌🙌
@roselynchanika8189
@roselynchanika8189 Ай бұрын
Nice song with a powerful msg Bravo Mr Mkalo 👏👏👏
@LovenessVinthenga
@LovenessVinthenga Күн бұрын
Zili mu nyimbo mu ndendende nyengo zomwe ndikudusa ine 😢 anansi andimvesa kuwawa mbali yakuno
@janezimba6960
@janezimba6960 Ай бұрын
Officially declared hit🔥🔥 brother Alex iyiyi mwakungaso, national anthem
@EllatonMoyenda-ye9zd
@EllatonMoyenda-ye9zd Ай бұрын
Nyimboyi utha kunvera mwez onse pa repeat muli uthenga waukulu kwambili
@RobertChikawonda
@RobertChikawonda Ай бұрын
Yaaaa zoonadi
@collinschipala611
@collinschipala611 Ай бұрын
Exactly 🎉
@EmmaKaguwa
@EmmaKaguwa Ай бұрын
Dis z really true
@mantetwa9038
@mantetwa9038 Ай бұрын
Olo ingokhala national anthem koma
@TraverMbewe
@TraverMbewe Ай бұрын
Fact
@FaithKamende-y2u
@FaithKamende-y2u Ай бұрын
U have nailed it brother🔥🔥
@MacferesonElias
@MacferesonElias Ай бұрын
Thas is golden voice bro gd job❤❤❤
@harrietpangani
@harrietpangani Ай бұрын
on repeat.. anansi .... will make sure mudzaimbe kwathu kuja.. mwana wakwathu God shud continue using you..
@alicekamwendo4271
@alicekamwendo4271 Ай бұрын
Same here on repeat🔥🔥🔥
@WisdomGondwe-c9e
@WisdomGondwe-c9e Ай бұрын
Amen Powerful song keep it up Glory be to God almighty
@NdakondwaMatchado-je3ro
@NdakondwaMatchado-je3ro Ай бұрын
A great message eeeh. On repeat
@EmilyKanyimbi
@EmilyKanyimbi Ай бұрын
This is more than beautiful,bro iyiyi mwabandula muli mvumbulutso umumu,nice song,nice video 🔥🔥🔥
@MayamikoChiwiya-wl3pr
@MayamikoChiwiya-wl3pr Ай бұрын
Powerful message! May GOD bless the talent ❤❤❤
@mercysilia
@mercysilia Ай бұрын
Uthenga wamphamvu, ndipo nyimbo yalalikira moyo wanga ndipo ili parepeat mbali yakuno🔥🔥
@alicekamwendo4271
@alicekamwendo4271 Ай бұрын
1.2 million views within 5hrs ehh ehhh ehh 🙌🙌🙌 well deserved Alex.. congratulations
@emmiewaselinah219
@emmiewaselinah219 Ай бұрын
Kkkkkk onani bwino it's 1k not million
@emmiewaselinah219
@emmiewaselinah219 Ай бұрын
It's 1k not million
@chifundokanyemba2305
@chifundokanyemba2305 Ай бұрын
Uyu wadza ngati coming Nice song nkhondo ndi anansi
@naomiewiscot8458
@naomiewiscot8458 Ай бұрын
Nyimboyi tayikonda gulu❤❤
@lazaruspias86
@lazaruspias86 Ай бұрын
Wow! Yaphedwa, very nice ♥️💕🇲🇼🤝💪.
@MaidaLuhanga-pt9uk
@MaidaLuhanga-pt9uk Ай бұрын
Wow!!!! Zili bwino keep it up
@shadrickmuseu8523
@shadrickmuseu8523 Ай бұрын
Powerful massage ❤❤let me repeat this one 10×
@NaomieTheu
@NaomieTheu Ай бұрын
I like this song Alex keep the fire burning
@PeterChisomba
@PeterChisomba 14 күн бұрын
🔥🔥
@BonfaceGeorge-t8d
@BonfaceGeorge-t8d 2 күн бұрын
Komatu zitipangitse kuti tidane ndi anasi athu izi kumbukilani kuti Yesu adati tikonde adani athu. Komabe nyimboyi ingotichenjeze .
@DorothyMass-u9y
@DorothyMass-u9y Ай бұрын
Ndipo iweyo Alex wausokola moyo wanga eish
@mikechisale8209
@mikechisale8209 Ай бұрын
Powerful song . Keep up the fight. Zion
@ThokozaniChikanguya-l5x
@ThokozaniChikanguya-l5x 20 күн бұрын
Mmmm nice brother nyinbo yokhudza
@GladsonMwale
@GladsonMwale 15 күн бұрын
Let us be watchful with our relatives.I am really touched with the the song
@GoodsonChandawira
@GoodsonChandawira Ай бұрын
Kumwamba kulemekezeke it's a nice song that will motivate the majorities Amen
@AgnessChirwa-q9o
@AgnessChirwa-q9o Ай бұрын
Vumbulutso ili ngakhale wakuba akamabwera pakhomo pamakhala mnasi ali pafupi mwamwanya ndithu
@LastbornCharles-xd5hf
@LastbornCharles-xd5hf 23 күн бұрын
Kungoti dziko lapansi ndi loyipa, tiyeni tizipemphera. tikasangalala ku mwamba.
@magchifunga-u4s
@magchifunga-u4s Ай бұрын
Nyimbo z Ilibwino heavy, akutiononga ndianadi
@PriscaNdereman
@PriscaNdereman Ай бұрын
Ineyo nyimboyi ndakumana nayo dzuro koma kuyambila dzuro mpaka pano ndikungomvera yomweyi nyimbo yachilungamo ndendende ndizimene ndudutsamo ine
@NyashaNyalugwe-su9sb
@NyashaNyalugwe-su9sb 26 күн бұрын
😢😢 nyimbo iyi muli chilungamo chopweteka 🙌🙌🙌😔😔😔😔
@ChimwemweBakali-ws4sv
@ChimwemweBakali-ws4sv Ай бұрын
Powerful nyimbo ili bwino kwambiri exactly mmene zikukhalira moyo uno
@GilbertSatoh-pi2ux
@GilbertSatoh-pi2ux Ай бұрын
Taoneranso konkuno misoziyi ompeleka Ndi anansi . Nyimbo yabweradi mu nthawi yake iyi
@ShanThengo
@ShanThengo Ай бұрын
Mwapha 😂 on repeat samalilanii!! Samalilanii!!,🎉🎉❤
@BraveChigumu
@BraveChigumu Ай бұрын
Umatha big ups God continue blessing you Amen ❤
@wilsondickson1727
@wilsondickson1727 Ай бұрын
What a hit......🎉 ..... yakungidwa nyimboyi
@KathieMapulanga
@KathieMapulanga Ай бұрын
Tigona mochedwa ... repeat mbali mchakuno❤❤❤
@luciousmalizani8884
@luciousmalizani8884 Ай бұрын
Apa nde Mwabwera Alex Nkalo 😍😍😍😍😍
@EddaMakileni
@EddaMakileni Ай бұрын
On repeat ❤❤ every morning God bless you
@NicolasChinyama-l6l
@NicolasChinyama-l6l Ай бұрын
Nice song. You have killed it❤
@mnazirifestonmussa
@mnazirifestonmussa Ай бұрын
Beautiful message worthy applause 👏
@VeronicaYohane
@VeronicaYohane 28 күн бұрын
Koma nyimbo iyiii yandinkjudza ine ndzoona pakunthetsa banja anasiya iiii ♥️♥️♥️♥️♥️♥️♥️🤣🤣
@charlesbickton5578
@charlesbickton5578 Ай бұрын
Nyimbo iyi ili mwala kwanthu kuno or alendo akumaipepha🔥🔥
@MoureenMkute
@MoureenMkute Ай бұрын
Inde ndi anansi,,nyimbo yabwino iyi🔥🔥🔥
@anniewphiri4555
@anniewphiri4555 Ай бұрын
Wabaya mwana wakwathu.... nkhondo ndi anansi omwewa sure
@alicekamwendo4271
@alicekamwendo4271 Ай бұрын
Nice song🙏 Also the message in this song ehh🙌
@LucyChilala
@LucyChilala 3 күн бұрын
Nkhondo ndi anansiwa awa timati azathuwa........Amen
@GraceGundampanda
@GraceGundampanda Ай бұрын
Gospel koma iyi osati zija mukumati gospel amapiano
@ChimwalaAlex-oh5ww
@ChimwalaAlex-oh5ww Ай бұрын
Amazing song .. well done 👏 l saw akhwakaa
@ApatsaKaliati-tv1rp
@ApatsaKaliati-tv1rp Ай бұрын
Muli uthenga wachilimbikitso kwambiri 🙏🙏🙏🙏🙏
@BrendaMatemba
@BrendaMatemba Ай бұрын
Kwambiri 🔥🔥🔥ndi anansi zoona 😢
@mercyalufandika3158
@mercyalufandika3158 Ай бұрын
Chi hit kawawa🔥🔥🔥
@ClementJohnLion
@ClementJohnLion Ай бұрын
Nice song bro keep it up
@TelezaChirwa-x8r
@TelezaChirwa-x8r 9 күн бұрын
Number wani❤🎉
@MephyCourtney
@MephyCourtney Ай бұрын
Wow🎉🎉 nyimbo ndaikonda iyiyi
@fantesher
@fantesher Ай бұрын
Kd model ndi akhwaka 😅😅 nice song
@CostanceManda-h1f
@CostanceManda-h1f Ай бұрын
Muli uthenga umu 💥💥
@blessmax5148
@blessmax5148 Ай бұрын
Beautiful ndayikonda sure wabwera bho
@RuthChalengama
@RuthChalengama Ай бұрын
🔥🔥🔥 yabwera mu nthawi yake 🤸🤸
@belnardsompho5617
@belnardsompho5617 Ай бұрын
Motooooo ochuluka
@sandersonmuwawamw
@sandersonmuwawamw 25 күн бұрын
Mbambande mbambande broooi
@HappyHarry-qt7ik
@HappyHarry-qt7ik Ай бұрын
This can be the best song of the month
@GraceBethelAngel
@GraceBethelAngel Ай бұрын
Pena ukamaimvela, ngati ulire, nyimboy muli anointing
@JoyceBanda-v3i
@JoyceBanda-v3i Ай бұрын
May good lord bless you my brother Alex Nkalo where ever youre
@hellenbitto7416
@hellenbitto7416 Ай бұрын
Anansi kungoyikumbusa kuti dzinazi zikuchitikazi mnasi akukoledzera moto penapake
@victoriamtseka831
@victoriamtseka831 Ай бұрын
On repeat 🙏🙏 nice song dea
@jimmyjagaidah9441
@jimmyjagaidah9441 Ай бұрын
keep it up mtumiki wa mulungu.🗣
@dumisannhlema7494
@dumisannhlema7494 Ай бұрын
This is a good piece Alex.
@AndrewChiomba
@AndrewChiomba Ай бұрын
Extraordinary one... Big up
@miriammvula9797
@miriammvula9797 Ай бұрын
Zoona ndithu. Kanyimbo koyimbidwa ndi mau anthetemia😊
@PaulMunukwa
@PaulMunukwa Ай бұрын
Nice song u brother keep up good l live from south Africa
@RejoiGama
@RejoiGama 21 күн бұрын
This is true and ndikumayimvera daily
@SmartKamangaMusic
@SmartKamangaMusic Ай бұрын
Katundu my Internal Brother❤️‍🔥❤️‍🔥
@StonardPhiri-z2d
@StonardPhiri-z2d Ай бұрын
Muli ulaliki wa ukali mu nyimbo iyi Amen Amen ❤❤❤❤
@omegabanda364
@omegabanda364 2 күн бұрын
Ndanansii omwewa akumatinyela amunathu ndakazi athu😢😢😢
@MemoryKacheche-te3tp
@MemoryKacheche-te3tp Ай бұрын
Amen powerful message ❤
@GloriaVeraIssah-gq1qb
@GloriaVeraIssah-gq1qb Ай бұрын
Zikuchitika ndithu....nice song
Alex Nkalo - Odala ndi Onsewo
5:45
Alex Nkalo
Рет қаралды 78 М.
Evance Meleka -Yashuta
5:10
Evance Meleka
Рет қаралды 247 М.
Real Man relocate to Remote Controlled Car 👨🏻➡️🚙🕹️ #builderc
00:24
Mia Boyka х Карен Акопян | ЧТО БЫЛО ДАЛЬШЕ?
1:21:14
Что было дальше?
Рет қаралды 9 МЛН
Elza love to eat chiken🍗⚡ #dog #pets
00:17
ElzaDog
Рет қаралды 21 МЛН
Kasungu C.C.A.P Praise and Worship Team-Ndimitima Yokondwera
7:10
kasungu_ccap_praise_and_worship_team
Рет қаралды 528 М.
Taimon Tipa_SIWE WEKHA (official Visualizer)
3:53
Taimon Tipa
Рет қаралды 586 М.
Driver wevana vechikoro ofumurwa pamberi pechurch naProphet Miracle Paul
21:56
Alex Nkalo ____ Anasi 😍
4:48
Malawi wake up 👁️👂.
Рет қаралды 746
NDIMTA - THOM KACHIMANGA (OFFICIAL VISUAL) - DIR VJ KEN
4:14
Thom Kachimanga
Рет қаралды 129 М.
JOSHUA _ SINDIGWEDEZEKA... OFFICIAL VIDEO {Terabyte studios}
5:31
TERABYTE STUDIOS
Рет қаралды 800 М.
Real Man relocate to Remote Controlled Car 👨🏻➡️🚙🕹️ #builderc
00:24