ZIKOMO KWAMBIRI INU ABAMBO NDI AMAYI MU CHOIR IMENEYI YA MTHAWIRA SPIRITUAL MELODIES CHIFUKWA CHA MAYIMBIDWE ANU WOKOMA WOTERE KUCHOKERA UKO KU MUDZI MACHINJIRI BLANTYRE (MALAWI) INE KUNO KU DZIKO LA CHILENDO LA SOUTH AFRICA MU MZINDA WA CAPE TOWN - WESTERN CAPE PROVINCE NDIRIBWINO NDITHU NDIPO MU ZINTHU ZINA ZONSE ZOMWE ZIKUNDICHIKIRA MU NTHAWI IMENEYI YOMWE NDIRI MOYO... NDIKULEMEKEZA YEHOVA MLENGI WATHU CHIFUKWA CHA CHIKONDI CHAKE KUTI : AKUTISUNGABE IFE TONSE ANA AKE PANO PA DZIKO LA PANSI KUKHALA NDI MOYO KUCHOKERA NTHAWI YOMWE TINABADWA MPAKANA LERO LINO!!! NDIDZAPITIRIZA KUMVERA NYIMBO ZANU NTHAWI ZONSE... YEHOVA MLENGI WATHU AKUYANG'ANIRENI USANA NDI USIKU, AKUTSOGOLERENI MU MAGANIZO, NZERU, MACHITIDWE ANU A MASIKU ONSE, AKUDALITSENI NTHAWI ZONSE ❤❤❤AMEN.