AMENE ALOWE M'MALO MWA ACHILIMA KU UTM/ NKHANI

  Рет қаралды 31,164

HOT 265

HOT 265

14 күн бұрын

Пікірлер: 58
@BestonMakochera-qk4sz
@BestonMakochera-qk4sz 12 күн бұрын
UTM president Tikufuna brian banda wisy man
@user-mh7cc8up4i
@user-mh7cc8up4i 12 күн бұрын
Chakwela asowe fiti yothelatu UTM ganizani mofasa musakonde ndalama kumbukani tsogoleli wanu chilima upangili omwe analinawo sitikufuna kuti kupita kwachilima ndizinalake lithe ayi mukuziwabwino zomwe amafuna chilima still I remember S K C ambuye sungani mizimuyawo 😭😭😭💔💔💔
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 12 күн бұрын
Chakwera pamtumbo pakę anaba ndalama za fertilizer asamatipusitse azipusitsa zitsiru zake zomwezo
@user-uv5rf4zt5q
@user-uv5rf4zt5q 12 күн бұрын
Malawi is lacking good leadership that's why is the poorest country in the world.
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 9 күн бұрын
Chakwela satana wohipa ziko lamu nyeraaa
@user-xu9rh1lm8o
@user-xu9rh1lm8o 12 күн бұрын
Asamango namidzila covid19
@WestonGawaza
@WestonGawaza 12 күн бұрын
UTM,mapulezident awa mayi chirima, mwana wachilima , Brayani Banda UTM awa ndi mapulesident a malawi, mukawasiya awa chipani chapita ndimazi, kongo kabira analowa ali ndi 31 years mundinkhulupirire , yeremiya, davidi, anali ana kaliyati ankhale muzati wa UTM, BY BY
@saadisadie3125
@saadisadie3125 12 күн бұрын
Ayi kabira analowa Ali ndi28
@DanielVictor-pi5fj
@DanielVictor-pi5fj 12 күн бұрын
Tikufuna Timothy mtambo
@sharifujoe7633
@sharifujoe7633 11 күн бұрын
Fredo yomweyo
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 12 күн бұрын
Am still worried about Chilima, Chakwela Anapaga Zolakwa Kwambili, Sangamuphe Munthu Chonchija
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o 12 күн бұрын
Kwambiri ndipo ine zimandiwawa mpaka lero pano bwenzi chilima atatiyankhula zokhuza comvension imeneyi hmm😢
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 9 күн бұрын
Chakwela mbuzi yamuthu
@kubengovender6996
@kubengovender6996 12 күн бұрын
Big up brother man!!
@TiyanjaneLuka-e2l
@TiyanjaneLuka-e2l 9 күн бұрын
😢😢😢😢Hey
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 12 күн бұрын
chakwera asanamizire zimenezo chakwera ndi chitsiru chamunthu chigawenga
@user-jn2oc3cn3q
@user-jn2oc3cn3q 11 күн бұрын
Mwakweza ferteleza tsopano mukuti tizigwilitsa ntchito manyowa ayi zikomo Bola la chakwera
@goodwilljeza8419
@goodwilljeza8419 12 күн бұрын
Adah iweyo Bass limenero bwanji Koma?????
@user-ii2sh1mz3r
@user-ii2sh1mz3r 12 күн бұрын
President Chakwera akanabwera ndi chipani china osati MCP , nichifukwa chake mbiri yakale ya MCP ikumukhuza, but instead of kutukwana a president let us pray for our country, kutukwana sikusintha zinthu guys,
@MisheckNtanbalika
@MisheckNtanbalika 12 күн бұрын
Mukufuna kt azaimile chifukwa mukuziwa kt Ali ndi mphavu xokupha aliyese odana ndichipanichi
@brainsmkumbwa6267
@brainsmkumbwa6267 12 күн бұрын
Wathamanga kukasiya ma pepela opikisana nawo pa udindo wapulezidenti chifukwa akudziwa kuti munthu yekhayo amene akanalimba mtima kuti apikisane naye wamupha kale (Chilima)changucho sichina koma kusangalala
@user-sd3cl2dq7v
@user-sd3cl2dq7v 11 күн бұрын
Mwalephera kuyendetsa boma osanyengezela COVID 19
@marryphili5419
@marryphili5419 12 күн бұрын
Covid 19 mupaka liti bwanji simukufuna kuvomereza kuti mwalemphera
@user-sd3cl2dq7v
@user-sd3cl2dq7v 11 күн бұрын
Mwalephera osanyeng ezela COVID 19
@user-co3wr3rn4h
@user-co3wr3rn4h 11 күн бұрын
Chakwela akangokhala pamupando basi mcp yathela pomwepo ndithu galu uyo wakupha achoke
@MisheckNtanbalika
@MisheckNtanbalika 12 күн бұрын
Komas osamanena kt covid 19 wasokoneza kd matendawo anagwela ife tokha komwe zinayambilako zithu zikuyenda bwanji
@MkandawireKennedye
@MkandawireKennedye 12 күн бұрын
Zaboza zimenezo kugwa kwa kwacha nanga. Zautsilu bas
@allansili-rc9gc
@allansili-rc9gc 12 күн бұрын
Covid 19 mpaka liti kod akuba inu
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 11 күн бұрын
Hahaha covid
@user-kg5lf6bd1g
@user-kg5lf6bd1g 12 күн бұрын
Patumbo pake chakweyo nyelo wake
@user-ti8ds7iq8z
@user-ti8ds7iq8z 12 күн бұрын
Mmene anayambila za covid Muja mpaka liti
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 12 күн бұрын
Pongopha Chilima uja basi, Chakwera waluza, Chakwera must go
@user-em1qi8kj9h
@user-em1qi8kj9h 12 күн бұрын
Inu mudzikhala ndi manyazi ponena za covid....palibe anthu opasa manyazi ngati inu every statement of economics development....koma mukafuna Kuba ndalamazo Palibe za covid anthu onyansa mitima
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 12 күн бұрын
MCP ndiyakupha
@user-nb8wg3fh4u
@user-nb8wg3fh4u 12 күн бұрын
Patumbo pako chakwela
@user-yq1mc3nm1f
@user-yq1mc3nm1f 12 күн бұрын
Utm uchitsiru mmmm
@HarryKandani
@HarryKandani 12 күн бұрын
Blaming covid 19 mpaka pano? Abusa aku bagamoyo alibe nzeru za usogoleri
@phillipphiri2119
@phillipphiri2119 9 күн бұрын
Next time go straight to the point,Tizionera Zama parish Mmalo mwa za UTM
@WestonGawaza
@WestonGawaza 12 күн бұрын
UTM BALIBE MUGWILIZANO MAONA NONKHA AYIMASO AZANU AJA MAYI CHIRIMA KAPENA MWANA WACHIRIMA AYIME AMENE AGWILE NCHITO NDINU MAMUZUNGULILA KABILA 31 ANALOWA UPULESIDENT MUWINO MUSAKAYIKE MUKAPHONYA APO BRAYANI BANDA, MUKASIYA AWA CHIPANI MALUZA.
@user-ti9yk4eg2l
@user-ti9yk4eg2l 11 күн бұрын
Mayi chilima ayime basi atha kuwina
@JohnAsendi
@JohnAsendi 12 күн бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@user-kg5lf6bd1g
@user-kg5lf6bd1g 12 күн бұрын
Mapwala abambo ake chakwelayo
@user-fh3dn8kt2j
@user-fh3dn8kt2j 12 күн бұрын
MCP moto kuti buu patsogolo ndi Chakwera olo mutukwane zopanda phindu izo mutopa nokha
@user-ww9rj2wx8d
@user-ww9rj2wx8d 12 күн бұрын
Za ziiiii basi
@user-vh3gq2tp2l
@user-vh3gq2tp2l 12 күн бұрын
Misala etiii
@user-fh3dn8kt2j
@user-fh3dn8kt2j 12 күн бұрын
Mukhaulatu inuyo ndipo simunatiii MCP mpakampaka
@vinceynyone6693
@vinceynyone6693 12 күн бұрын
I wish Timothy Ntambo alowe UTM party to mlowamumalo a later president SCK
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 12 күн бұрын
Kkkkkk koma MCP kovid Wake uti shame on you anthu adayamba bwino kuvala buluku ndiye abwelerenso kupampaz 😂😂 you are not serious bullshit
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q 12 күн бұрын
A MCP chimene chikwalimbitsa mtima ndichani?
@brainsmkumbwa6267
@brainsmkumbwa6267 12 күн бұрын
M.C.P kudzungulira mutu ndikuzabela ma vote ndi zimene zikuwalimbitsa mtima
@user-xx4jb9se3z
@user-xx4jb9se3z 12 күн бұрын
Kkķkk kupha kuba ndi nkhaza bro zomwe zikuwalimbitsa kulimba mtima ndipo mcp sidzawinanso
@user-xx4jb9se3z
@user-xx4jb9se3z 12 күн бұрын
Kkķkk kupha kuba ndi nkhaza bro zomwe zikuwalimbitsa kulimba mtima ndipo mcp sidzawinanso
@EllahChikwatu
@EllahChikwatu 12 күн бұрын
Ndpo inu zikudabwisatu
@user-xx4jb9se3z
@user-xx4jb9se3z 12 күн бұрын
2025 ambuye MULUNGU akukasesa ku state house
@GodisoneNoel
@GodisoneNoel 12 күн бұрын
Kovidi inali ku malawi kokha katangale ndi amenewakura mboma
Mwana Mudoko chaiye anogona kukwira mu Chikuva iwe munhu mukuru uripo
23:49
Karanganda Tv (Waiyepo ere ?)
Рет қаралды 1,3 М.
New model rc bird unboxing and testing
00:10
Ruhul Shorts
Рет қаралды 23 МЛН
Я нашел кто меня пранкует!
00:51
Аришнев
Рет қаралды 5 МЛН
Cat Corn?! 🙀 #cat #cute #catlover
00:54
Stocat
Рет қаралды 15 МЛН
Donald Trump speaks for the 1st time on the assassination attempt
14:17
FOX 9 Minneapolis-St. Paul
Рет қаралды 7 МЛН
'I Stand By My Statement,' Ndume Breaks Silence After Sack As Chief Whip
11:10
Channels Television
Рет қаралды 139 М.
Nightly News Full Broadcast - July 19
18:15
NBC News
Рет қаралды 602 М.
New model rc bird unboxing and testing
00:10
Ruhul Shorts
Рет қаралды 23 МЛН