Kodi video imeneyi mumajambulila foni ya tilili kapena ayi
@LoveNatala3 ай бұрын
Zamatsiku osiliza owerenga khala maso
@user-ws2xi7ch7z2 ай бұрын
Inu nkhope take mwaiwala ya munthu?
@EvansKatambo-hi3sr2 ай бұрын
M'bale wako oti wamwalira angabwere akuoneka ngati munthu wina mkumati ndameneyo zoona?guys come on come on,these so called prophets asokoneza anthu Kwambiri,
@user-tj2vx2xf7e2 ай бұрын
Koma muzionetsako akulankhulayo ndinso munthu omwalirayo
@DauglassNkhoma-dj9lpАй бұрын
Mukuti pano alikutoti ifeso kuno tili
@livemonkaposka37143 ай бұрын
Number ya prophet please
@mercyphiri68673 ай бұрын
Timve zosatira plz
@rashidadan25333 ай бұрын
Zamasiku akumapeto
@Jermah51kennias2 ай бұрын
Sanabwelebe
@user-iq3iv8tp8t3 ай бұрын
Don't stress your self please,munthu àmene mukunenayo ndi scammer amango panga pretend ngati wa asma nditambwali ameneyo he used Kuma panga zakeko ku Lilongwe around kanengo komanso area 43 titamuzindikira maplan ake adathawa
@SurprisedDriftwood-ef3lc3 ай бұрын
Bodza mukufuna ma comment 5:25
@SaidiMbawa-st6bj3 ай бұрын
Zabodza izi munthuyo ndi wina
@slatielchipeni-zy3wb2 ай бұрын
Ziwanda iziiii
@lasmoboko59893 ай бұрын
Zabodza zeni zeni kulibe zimenezo
@osbornleman25002 ай бұрын
mmmmm profit wanama apa
@augustMag3 ай бұрын
Funso langa ndi Ili kunena kuti koyamba kunabwera mnyamata amene amaonesa kuti Ali ndithenda yomwe amadwala m bale wanu asma eti? Ndipo abusa anakuyimbirani phone munthu mukamufuna uja anabwera simunamusama pamene wanu yemwe anamwalira ndi mkazi sichoncho tinene kuti athufe tikamwalira timakasitha matupi anthu? Muthu oti anali mzibambo kudziko lapansi pano ndiye bambo uja mwalira pozauka Kwa akufa azauka ndinthupi la mzimai? Koma anthu amene munakhala busy ndi azibusa musamale inutu ameneyo simunthu amene mumamuyembekezera ai ndichiwanda chimenecho chochokera Kwa busa pofuna kuti atchuke ku dziko kuno
@user-ky4nh4wg7y2 ай бұрын
Koma zikoli
@EmmaRichard-hr7jj2 ай бұрын
😭😭
@ShiraSaidi-oz5mx3 ай бұрын
Tionetseni munthuyo
@andrewmwachande76122 ай бұрын
😂😂😂
@DolineDalison-br1etАй бұрын
😂😂😂😂
@user-ju3kj9vy9e3 ай бұрын
Za ziii
@mwale11543 ай бұрын
Last day
@user-kn3ym1zf3m2 ай бұрын
Zabodza
@paulchilola54623 ай бұрын
Aaaa
@user-dk8ey5pu5w2 ай бұрын
Munthu amene anabwera kunamizira ku wa esthma uja ndi mmene ndi amene anadzafufuza maina anu