ANTHU ADABWA NDI ZOMWE TRUMP WAYANKHULA KUTI AKHALA AKUTENGA DELA LINA LA GAZA KUTI LIKHALE AMERICA

  Рет қаралды 5,379

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер
@JamesLeonardhowa
@JamesLeonardhowa 5 күн бұрын
Ndipulani yotamangisira asiramu zopusa😂😂😂
@MarkManyowa
@MarkManyowa Күн бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@BerthaKasambala-y5k
@BerthaKasambala-y5k 4 күн бұрын
Amene arindi maso auzimu akutha kuwona kt zikori rikupita kt komanso baibo rimati chani zamasiku osiriza
@MercyChisanya
@MercyChisanya Күн бұрын
End of World
@GraceShaibu-i9d
@GraceShaibu-i9d 2 күн бұрын
Atenge Malawi bwanji zinthu sizibwino ayiiii
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 5 күн бұрын
MA AMERICANS ONSE NDI AMODZI NDI ISRAEL.CHIFUKWA MA AMERICANS ONSE NDI ANA A ABRAHAM.+ ISAAC + JACOB.NDIPO MALO ATACHEPA ENA ANAPITA KU AMERICA .KUKAPEZA MALO OWAKWANA.KUTI ADZIKALIMAKO..KOMA ISRAELNDI AMERICA NDI AMODZI.MA JEWS.KUPATULA MA RED INDIANS ONWE ALI AENI AKE A KU AMERICA KO
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 5 күн бұрын
Zoonadi bola America itenge Malawi popedza talephera kuzilamulira tokha
@GoodsonMtambo-e9g
@GoodsonMtambo-e9g 4 күн бұрын
Ndipo love atenge maliwiyi bs
@kennedybanda
@kennedybanda 5 күн бұрын
Koma ndiye
@MelvinShawa
@MelvinShawa 5 күн бұрын
Mmmm a Malawi kutengeka basi
@YassimineRasheed
@YassimineRasheed Күн бұрын
Bora atengenso malawi, chonde tikufuna tikhare ma mericans
@EsnartNkhoma-i1r
@EsnartNkhoma-i1r 4 күн бұрын
Mutengen Malawi tikutsatilan mwna kumeneko zithu ndzotsika
@issahmakunganya9675
@issahmakunganya9675 5 күн бұрын
Tikukutsatila koma koma zazigawenga za palesitina ndikulakwitsa please
@noahkalima5294
@noahkalima5294 Күн бұрын
Kod iweyo suziwa kuti asilam nd gulu lankhondo,,chisilam ndnkhondo
@noahkalima5294
@noahkalima5294 Күн бұрын
Asilam ndmagulu azigawenga
@PatricaTchuwa
@PatricaTchuwa 5 күн бұрын
Abwana titengen ndinthu chakwera watikanika kkkkkk
@DanielShaba-z6s
@DanielShaba-z6s 5 күн бұрын
Malawi yati kwana 😂😂😂😂
@AdamBoston-s6q
@AdamBoston-s6q 4 күн бұрын
Azatenge malawi
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 5 күн бұрын
Kkkkkkkk😂😂😂😂😂😂😂
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 5 күн бұрын
Atenge Malawi ndipo chakwera akalowe Ku ndende ndi nduna zake
@SalimuDelekena
@SalimuDelekena 5 күн бұрын
Zikanatero Bora chifukwa mamvuto achepa mudzikorino komatu zimenezo zitheka chifukwa tirikare under Britain Eeeetuuu!!!!!.
@marryphili5419
@marryphili5419 5 күн бұрын
😂😂😂😂 mulungu alowelelepo ndithu atitengeso ife amalawi tikuzuzika anyamata oganiza boo akuti zuza
@harrymicah6140
@harrymicah6140 5 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 Malawi nde zatengeni bs
@FlynessWinga
@FlynessWinga 5 күн бұрын
Tenganiko Malawi plz
@BwanaGD
@BwanaGD 5 күн бұрын
Aaa wachedwa ameneyo ife achakwera yatipeleka kale ku tadzaniya apa gati tatsogoza nyanja tatsala patiso
@shukurajaaffarie-cr2nm
@shukurajaaffarie-cr2nm 5 күн бұрын
Mmesa iwowo ndi amodzi. Ine sindikulola mawo ndipangapo kanthu...
@Felista-m4q
@Felista-m4q 5 күн бұрын
Tikunzunzika atitenge
@ERNESTONANSONGOLE-m5p
@ERNESTONANSONGOLE-m5p Күн бұрын
😂😂😂😂
@JulietLizziePhiri
@JulietLizziePhiri 4 күн бұрын
Eya ifenso please
@AchinaKellz
@AchinaKellz 5 күн бұрын
Yes 😂
@ChikuMega
@ChikuMega 5 күн бұрын
Atitenga pokhapokha chakwela akachoka pa mpando
@PempheloAmoni
@PempheloAmoni 5 күн бұрын
Fuso langa nali athuwo akawachotsa kutengedwa ndimayiko ena kenako akamaliza kumanga adzawabwelezetsaso mmalo mwawo kapena ayikamo athu aku America???
@FahzKananji
@FahzKananji 5 күн бұрын
Welcome to Malawi Trump
@DanielShaba-z6s
@DanielShaba-z6s 5 күн бұрын
🎉
@AlwayneH
@AlwayneH 5 күн бұрын
Atengedi Ineyoso ndavomeleza mmmm malawi is not a country only but also a though prison
@rashidadan2533
@rashidadan2533 5 күн бұрын
Not allowed America to invade GAZA , let palestinian's to have their state , let them be free , Ku malawi kunonso azabwele , zinthu ziyamba kuyenda bwino Professor Peter muthalika akayambanso kulamulila
@VitumbikoKaunga
@VitumbikoKaunga 5 күн бұрын
Mmmmmmmmm guys osaziyika mumavuto please
@CardoJustin-l7m
@CardoJustin-l7m 5 күн бұрын
Zachamba zimenezo
@LesterNtolilo
@LesterNtolilo 4 күн бұрын
Trump na pamenepo magnanimous abwino
@MichaelStaford
@MichaelStaford 5 күн бұрын
Zoonadi abwere adzatitenge chakwera akutinzunza.
@EnallaMsiska
@EnallaMsiska 5 күн бұрын
Ndipo tikupepha kuti angotenga Malawi ngati akana Malawi yonse azatenge kumpoto kuno
@MosesMzembe-z7s
@MosesMzembe-z7s 2 күн бұрын
Malawi atengeso basi
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 5 күн бұрын
Vitumbiko Mumba ayendeleko kupolisi, apolice akuvala ma uniform achigamba pathako komanso nsapato alibe akuvala ma slippers
@JohnWame-u3l
@JohnWame-u3l 5 күн бұрын
Zilibwino zikatero Koma asaiwale Malawi,tatopa ndi vilombodzi
@AbisalomJackson
@AbisalomJackson Күн бұрын
ziri bwn
@MphatsoKakole
@MphatsoKakole 5 күн бұрын
Atengedi Iiìiii tatopa
@IvyKanyenje-d1c
@IvyKanyenje-d1c 5 күн бұрын
Kkkkkkkkkkkk
@MangulenjePaulo-j3n
@MangulenjePaulo-j3n 5 күн бұрын
Ineso ndamupereka marawiyu ndimanja awili
@RichardKathumba-q8c
@RichardKathumba-q8c 2 күн бұрын
😂😂😂😂
@JohnBamusi-o8l
@JohnBamusi-o8l Күн бұрын
Trump came to malawi
@BurunoMbewu
@BurunoMbewu 5 күн бұрын
Sono kudikilaso chn Apapa ititenge bs
@LukaSamson-w5h
@LukaSamson-w5h 5 күн бұрын
Chonde bola Malawi atengedwe abale
@JohnMazera-jn9cm
@JohnMazera-jn9cm 13 сағат бұрын
H0
@HanifuAnussah
@HanifuAnussah Күн бұрын
Mukhunama.galu.iwe.mangochi.boma.news.yakhoyo
@AlwayneH
@AlwayneH 5 күн бұрын
Atengedi Ineyoso ndavomeleza mmmm malawi is not a country only but also a though prison
The evil clown plays a prank on the angel
00:39
超人夫妇
Рет қаралды 53 МЛН
Quando A Diferença De Altura É Muito Grande 😲😂
00:12
Mari Maria
Рет қаралды 45 МЛН
NGATI SASAMALA NKHONDO IYIYI IKHALA YOOPSA __RUSSIA ILI MBALI YA DRC
7:38
The evil clown plays a prank on the angel
00:39
超人夫妇
Рет қаралды 53 МЛН