Mukamava kuti mtopola ndiumenewu , ndimayembekeza kuti a usi ndiwokonda mtendele koma apapa mmmm siwamtendeleso, koma ndimati ndikukumbuseni kuti pambuyo pa moyo uno kulinso moyo wina . nde inu andale samalani makamaka muziwopa ma court amoyo ulimkuza zikomo
@MathewsDyson-z6z17 сағат бұрын
Iyi ndiye UTM yeniyen osati yakaliyat ija ay
@JeremiahPhiri-j8p17 сағат бұрын
Yotsatira constitution
@symoldicky15 сағат бұрын
Mavuto multi nawo
@MandalaChaona11 сағат бұрын
Yokumwa magazi Ku Chikangawa . God is watching tiye nazoni
@ChapwetekaChauluka13 сағат бұрын
Manganya ndi chitsiru akanafuna kukhala president wa UTM akanapikisana ndi anzake ku convention koma pano president ndi Dalitso Kabambe basi
@wendaemily317914 сағат бұрын
Manganya moto umapita kwatsala tchire. God is watching you. Kufa kwa Chilima Inu siamuyaya.
@laalendodziko90993 сағат бұрын
To all UTM family what Mr Usi is doing ndinjira imodzi yofuna kuwononga chipanichi but he doesn't belong to UTM at all.Zimenezi nde ndale.Anthuwa angovala makaka a utm koma ndi achipani cha Malawi congress Party.This is one strategy that these people have organise to confuse the people of Malawi.UTM members don't worry, the spirit of Saulos Claus Chilima is watching.UTM family you are bigger than this go on the ground mobilise your supporters to vote for the party come 2025 general Remember oipa amathawa yekha.God bless UTM and God bless Malawi.
@dominicadamsonphiri744016 сағат бұрын
Umenewu ndiye mtopola. Ngati a Michael usi amafuna mpando wa u president wa utm, bwanji sanapikisane nawo ku convention. Kumeneko timati kuderera komanso kunyozera. A Michael usi akuyenera aganizetso kachikena, chifukwa akubweretsa chisokonezo mmalawi
@EthelKubalasa16 сағат бұрын
Zikomo ussi ndi chakwela poyipangila khapeni UTM powapatsa azimayi uniform ya UTM/ mupitilize kuwapatsa moto a Kabambe.
@MollenMponya12 сағат бұрын
Usi ndye wa UTM weni weni that's why Anja abetsa dzina lachilima kwa alendo muyelusalemu
@chrischigoma585411 сағат бұрын
Munthu sakhala mulendo Ku dziko lakwawo bwana, akuluwa akuwatuma akuwanamidza
@EllenKapinga-rm9zm14 сағат бұрын
Usi ndi vice president wabdziko lino emwenso analowa mmalo mwa malemu Dr Saulos Chilima Ndipo palibe angamuchose mu chipani cha UTM, Choyambitsa okha ndi malemu, Chilima, mphanje ya chipanichi amenya nawo, uyo wobwerayo ndi emwe akuyenera kuchoka not Dr Michael Usi Never
@MandalaChaona11 сағат бұрын
Usi God is watching you Afirisiti omweo ukuwalambirawo iwe mkumazitenga ngati odzindikira mawa adzakupanga Kanyenya.
@FosterPhandama17 сағат бұрын
i love michael usi than zinazazo
@JeremiahPhiri-j8p17 сағат бұрын
Boma ndilomweli
@FrancisNyayi14 сағат бұрын
Eya iwe sunama aliyese ali zokomda zake ine wadenis mahata
@LangMalone10 сағат бұрын
Osangonena you love MCP bwa
@kingsleymsampha226016 сағат бұрын
MCP iyo....old xul move iyo,, Ife ma gen Z mwachepa nafe kwambiri.
Ndale za umbuli komanso usi akuwonetsa Moyo wa mabodza ntopola ngati nkazi a kuchita I zosayenela mamuna komanso azimaiwa ndi longosoka ndithu? A kuchoka kumabanja ndithu?
@FidesChandama17 сағат бұрын
Angonyela ameneyo aliyese adamutuluka kwatsala ndi ku mcp nthawi iliyose amuthamangitsako nthawi yamuthela mmalo mopanga za odya zake alibe mulandu
@BannetMwale15 сағат бұрын
O
@MebleNgulinga-hi6rg16 сағат бұрын
If you are vice presdent ku MCP ndikomweko koma ku UTM u are a member only The Presdent is DALITSO KABAMBE
@StevenGJohn17 сағат бұрын
Manganya Ngati akufuna akuti azimayi azimusata angiyambisa Chipani chake basi
@priscillamangata402317 сағат бұрын
Koma kunja kuno kuliathu oipa Ndithu
@ChifundoZimba-jh7dh3 сағат бұрын
Mwangodana naye Usi bwanji nankhumwa sanapite ku court kuletsa Muthalika kupanga za DPP atasakhidwa ku Lilongwe secretary general ali popo koma court linati zinali zosazelezeka coz president panalibepo Muthalika
@samchibenene4458Сағат бұрын
Correct
@robsontyg39286 сағат бұрын
Bwana wanga Michael usi ❤
@BOSTONMALISAWO5515 сағат бұрын
Amanganya mumuona mwa wa chilima momwe akung'ambileni SEAN
@BlessingsSungani11 сағат бұрын
Manganya ndi kape plus MCP yonse 💔💔a Usi dekhani mufanso kangati kape easy ndi dziko ili 🙌🙌
@masoyaonamunkhondya907455 минут бұрын
Some people said usi has a good reasoning but look now he doesn't know what goes wrong at moment. He remains a person who can cause riots here in our country. Sorry usi think before you do
@smartpetermusic783817 сағат бұрын
Ife UTM tikuidziwa
@MaryJuwa11 сағат бұрын
❤❤❤
@SamuelChimangeni-e9m18 сағат бұрын
Usi chipani watenga basi
@JeremiahPhiri-j8p17 сағат бұрын
Kwabasiiii
@ronaldkalimandanda871812 сағат бұрын
Musapusisike@@JeremiahPhiri-j8p
@JackMvura5 сағат бұрын
UTM ya chilima ndi imeneyi sadachoke mpaka zofuna amalawi akwanitsa zidangovuta RIP wherever you are Mr kaliat wabetsa zinthu ku DPP mwai usi walanditsako mwazina kaliat ngoononga zediii wapsa wa 2025 apa zili bwino
@jeremiahmalikebu239317 сағат бұрын
Manganya mutu sukugwira. Azimai a MCP akugwiritsidwa ntchito kumavala uniform ya UTM wo angopangira poti akudziwa kuti pochoka pamenepo ti ma 50 pin tikulowa. Chosangalatsa zafikapa or munthu wakumudzi akudziwa kuti Manganya ku UTM kulibeko chake😂😂😂
@HARRYSABBATEEN17 сағат бұрын
kkkkkkk guyz musapusisike onsewa awa awa ndi a mcp inuyo simukuona kuti anthuwa zalowa? bolani asamakhaletu ma 2 pin aziyambila 50 pin zidyedwe kumene ndi mnthawi yake 😂😂😂😂😂
@@HannahTulizohkkkkk kuteloko inu mukut mwabaya nfundo yanzeru kod si MCP yomweyi imati sili pagwilizano ndi wina aliyese ? So y kumpopa usi mopusa ndi modzesa chisokonezi chonchi
@FefieTenisha-du7ge17 сағат бұрын
Kicks of a dying 🐎
@JanetNyamayalo-f4r12 сағат бұрын
UTM anakonza, mpaka kukakamira uniform ya chilima, munthu mutamukonza nokha, shame on u
@ChifundoZimba-jh7dh3 сағат бұрын
Convention simachita popanda president mwayiwala thawi yomweyi kuti nankhumwa anasakhidwa as DPP president popanda Muthalika koma court linapanga cancel
@Giftvictoryambani17 сағат бұрын
Agaluso ndi awa akumusatilawa mbuzi zenizeni kufuna kusokoneza bas
@Blessings-td4cr14 сағат бұрын
MCP ndi maganya akhoza kukhala kuti imfa ya chilima akuidziwa inu a inquiry pitani kwa MG 1ndi MG 2.
@CharlesWitness-vp6dw13 сағат бұрын
Kkkkk akuderera nchifukwa chake MALAWI ANTHU Aku bvutika, Anthu Ali ndimipando amaderera , kunyodza, komanso Ku dzimva kapena Ku dzikhwedza
@JamesChimera-x8c16 сағат бұрын
Mukuti adamutuluka pamene mudamutuluka ndinu nokha ena alinaye 1milion vote ija muzidziwakuti ndiyogawana ndi ussi
@KinziWindasoni-h4b4 сағат бұрын
Awa pakufunika kuwaitana ku displinary comitee .then kuwachosa ku chipani
@Biath-m4b12 сағат бұрын
Usi uziona kt utani president wa UTM siiwe kod ukukakamila udindo?
Koma Mulungu wanga kumwamba ko chonde chilitsani Malawi wanga
@HasheemManzymanyozo16 сағат бұрын
Ngakgale mavinidwewo akuchita kuwoneka kuti ndi mcp imeneyo , angovala chikopa cha utm koma ndi mcp
@BrunoChakukuma15 сағат бұрын
Usi machende Ako panga nsalu Yako osati ya president wathu chilima ulibe manyazi kodi
@DavidPhiri-o6w15 сағат бұрын
He is UTM, when did he resigned from UTM
@johnntilah473515 сағат бұрын
Agreed with u 100%, n he knows his position
@FrancisSakasa13 сағат бұрын
Koma anthu nde akukupepelesa usi ndthu!!! Ukamapanga zakozo uzichotsera makusi azopusa zakozo
@usumanidaudi12 сағат бұрын
Inu mukamati manyanya ndi ntsogoreri wa utm tisiya kukusata usi ndi chisiru muwuzeni kuti machende ake ameneyo
@MwanaWachawutaСағат бұрын
Usi ndi mfiti yayikuru kwambiri koma adziwe ichi mwamba mulibe nthaka chowuluka chizatera
@FrancisSakasa13 сағат бұрын
Ma guys a UTM musiyeni ali pa nkhate avuta kupheka.koma akangochoka nayeni ku mabwalo.
@NosiphoMazibuko-e9z18 сағат бұрын
Ndi anthu amcp awa akuvala makaka utm kufuna kusokonesa utm ausi adakana kukaima nawo lidali vuto lake palibe yemwe adamukaniza koma nazikayikila ndeno akamapanga izi wasowa pogwira mcp yamisokonenza uyo tawonani lero akusowa kopita akavela mcp akauzidwa chochita ndi mcp zomwe zimunonga tsongolo lake
@ShabaniBashir-o8g13 сағат бұрын
Akuluwa ndinkawakonda koma apa ndawatuluka ndiobweletsa chisokonezo mdziko. Munazipeza muzazisiya
@MichaelMakoka-g7y17 сағат бұрын
Munthu wadyera amatero opusa ndi Chakwera chifukwa akudziwa kuti UTM President ndi Dr Kabambe olo nyimbozo zokonza ndi ma 5pin. Agovala ndi a MCP okha okha basi kkkkkk 😃😃😃
@RichardSeven-x7p10 сағат бұрын
😢
@GiftKmoyani-bb7ut4 сағат бұрын
Kodi a Usi asanduka a plan maker?
@WatsonMsukwa-y5i13 сағат бұрын
OK
@HopeMakoka13 сағат бұрын
Manganya ndinkamuona ngati ndi ozindikira Koma wakomdwa kwambiri Pali chomwe chikumutsata
@idenmkumba-q8j15 сағат бұрын
Azimai awa ndi afiti a mcp mpaka kuvala makaka a UTM zoona koma izi bambo asikono zoona izi