I have been defending MCP but the way they have handled this fuel crisis, they have completely lost me
@AtupereSadikiСағат бұрын
Kkkkkk
@SamisonLevison-z5pСағат бұрын
Pakhale lamulo loti,amene akupikisana pa mpando wa u president azikayesedwa ku mento.Kutsogoku wamisala adzakhala msogoleli wa dziko.Muwaonetsetse akuluwa yankho mulipeza.
@IsmaelGift-d3mСағат бұрын
Km programme iyi ay ndthu Keep going,...... Mukusekula mmaso amalaw
@KatengezayobuСағат бұрын
It's only this program I love from Malawi radio stations
@AlhadjDouglasСағат бұрын
😂😂😂😂😂 nde mwat achakwera anaika m'botolo. Watching from kk
@FelixMachika2 сағат бұрын
Bodza NDILOMWELI la mafuta ngambwingambwi, akudwala manyazi pano. 😊😊😊😊😊😁😁😁😁😁😁😁😀😀😀😀😀☺️☺️☺️☺️☺️😃😃😃🤗🤗🤗🤗🤗🤗🤗🤗🤗🤗
@HanifaAdam-tm9yv2 сағат бұрын
Jessie Kabwira 😂😂😂😂😂kuli ziiii
@GiftKamwaza2 сағат бұрын
Wabakili muluzi uja osazamudela
@Yungjoe7862 сағат бұрын
Telling the truth without fear,keep it up gents
@IvyMkhuraСағат бұрын
The spirit of negligence is flowing in this country and it was started on the death of Dr Saulos Chilima
@DigleDafter3 сағат бұрын
Times radio n tv siopa ndipo ilindichilungamo polakhula ❤ osati awa zikachitika muvera kwa ife arikuti zoti ziko laora saziwa pano ndi mcp radio etti zachisoni
@DesmondKelly-x6x57 минут бұрын
Good job guyz
@EricChilumphaСағат бұрын
a boma akusowa anthu odziwa timati stock controllers, timakhazikitsa timati ma stock levels. andilembe ndiwaphunzitse zimenezo and its on a serious note
@AARONBOSTERKAPAMAMAKWAKWA2 сағат бұрын
Wonderful program and great atola nkhani a times
@StaffordNgalande3 сағат бұрын
kodi mr Chikangawa kuti Bwanji pakhani ya Mafutai? and you Remember adalakhulapo kuti sakuziwa kathu Ziko liochedwatu ili
@AnthoniohMazengeraСағат бұрын
Gayez inuo nd more
@BenjaminFriday-h4nСағат бұрын
Mbambande program
@ChikobdilityEdwardСағат бұрын
A bakili muluzi aja akuomeka ngati ndi awawa bwanji tagwirani Kaye ndevu zamwaiyu Kaye akuomeka kt ndiameneu wa bakili muluzi
@SamuelThanganyika2 сағат бұрын
Mbambande guys,mukuimililadi anthu a kumudzi Shure,big up.
@Dellingsmunthali2 сағат бұрын
Chizukulu chananja I can confirm ndindani zilingat akamat kamajekete😆😆😆
@PeaceNkhoma2 сағат бұрын
Brian ndiwe pangolini, when you are with these guys amayankhula fundo kamba ka mafunso anu Mr Brian!😅
Ayi guys abomawatu chilipo ndichakuti akusowetsa dara mafuta chifukwa kalembela wa chisankho wayambirila ku mwera akangoyamba ku kulembetsa achigawo cha pakati mudzaonanso mafuta ngabwingabwi zimenezo amalawi ndiye musunge
@ErtyvhkСағат бұрын
Madoras amatha ndimaulendo a president osati kugura magalimoto kokha ai komansotu magalimoto ndi amene akubweresa ndalama ku M R A coz galimoto imozi imatha kulipira custom 30 million koma ndalamazi sizikugwirisidwa ntchito bwino bwanji osafusa anzowo kuti amaziyendesa bwanji zinthuzi.
@MizzyWasiliСағат бұрын
U Guys munabwera kudzakhala Ku Malawi Ulemu Wanu Mumayitha
@PeterMakaika2 сағат бұрын
Dziko likulamulidwa ndi makawadi zitsiru akuziwa zomwe akuchita
@MathewKalinkhuСағат бұрын
Akulu akulu inu mukwana pa Times tv. Chakwera ndi munthu olephera ndipo mulibe utsogoleri. Mbuzi yeniyeni.
@LameckGamah2 сағат бұрын
Ulamuliro opanda matso phenya, ulamuliro wongoziwa kulakhula pa ground bas 😢
@patesnkajenda4258Сағат бұрын
Abusa alemedwa akusowa madola kom alinazo zopitila kunja zilipo 😂😂😂
@GribetaBongisСағат бұрын
Kkkkkkk l can confirm oh yes Malawi wafika pa mwana wakana phala
@AndrewjemesJemesСағат бұрын
Ndiye echina boma nilomweri mkumati wa bakili muluzi tv amanama mzimenezi ma guys inuyo pitilizani mmatsekula mmanso amalawi
Boma losamva chisoni ndi anthu Ake omwe tinawaika pampando. Zafika posauzana. Kukhala pa filling station ngati tiri Kukalandira zakudya pa que
@Tiongetv-o9w3 сағат бұрын
very bad indeed
@WhyteSmart3 сағат бұрын
Mulungu anawachotsera mzeru anthu amenewa
@BonomaliRajabu3 сағат бұрын
Together with wedson Chiwoko It's me Rajab Bonomali Watching from south africa Eastern Cape❤
@corretabanda768556 минут бұрын
Koma people you can talk...indeed chilungamo chimachotsa mantha
@AsaniFelix55 минут бұрын
Is not like neglegence is arrogance thinking that they r on top forgetting that that nobody's seperior than the community
@AsaniFelix59 минут бұрын
Y the top dont knw hw to blame those behind him? If he doesn't knw hw can he lead?
@lloydkondowe262Сағат бұрын
Network sabwerekana.😊
@peterbyson6269Сағат бұрын
Simukulakwa a brian
@GraciamChopih2 сағат бұрын
Kachaje and kumkuyu akanaima kaye pa ntchito zawo coz ananamiza a malawi pa za mafuta a galimoto
@MAGOLELEVISONMWALEСағат бұрын
Koma zinthu sizilibwino adindo plz chitaponi kanthu
@BrianMulekeСағат бұрын
A MBTS alephera kubwera ku xool kwathu kuzatenga magaz ati disel alibe zoona izi ?
@CliffMoyo-n7dСағат бұрын
Kodi ku ministry of energy ku kuli PS??
@ELLENKANJEREСағат бұрын
Waoh kukamba mosambisa zizitero amalawi
@TonyMhone2 сағат бұрын
Chikangawayu kupha kugwetsa sakuonapo bvuto koma. Za mafutadzi ndie kupha kutani???? Ndiudzeniko a Kachaje
@LewesadiasСағат бұрын
Ku dedza tikumatha 3days tili podikira mafuta
@ChrisantKapandansalu-o6vСағат бұрын
Anthuwa atipha because kuli njala maluzi mafuta kulibe
@JeremiahThaulofromMalawiСағат бұрын
Kodi ku UNGA KUJA ANA ONONGA MA US DOLLARS NANGA SAMKADZIWA KUTI KULI NGONGOLE YAMAFUTA ASANAPITE KU UNGA.NAGA MA US DOLLAR AKU OPITANA KU UGA ANAWATENGA KUTI? KODI MALAWI YAPONDULAKO NDIUNGA KULEKANA NDI MAFUTA
Kodi president ngati ali wakuba angakhwimitse bwanji malamulo chakwera ndi idiot ndipo since I was born sindinawone chidzete chamunthu ngati chakwera
@VincentMapira-h1f2 сағат бұрын
Uku ndikuwapangira campaign a opposition
@JerePosiano-tc9nu2 сағат бұрын
Ndiko kudyako Mr nsima
@Dauson-j5iСағат бұрын
Bvuto la bomali zimene amalangizidwa amazitaya asanazimvesese and mubaibulo muli mawu onena kuti ena saziwa kuti saziwa mzeru za yekha anaviika msima m, mazi
@AbrahamLLoyd-xb2xc2 сағат бұрын
Powerful gays
@DumisanMkandawreСағат бұрын
Koma ngambwingabwi alikuti
@LaissoneAmosseСағат бұрын
Zikafika apa President amasiya pansi usinado akakhala Olikonda dziko kake