ANTHU OTHAWA ZISOKONEZO KWA ANEBA AYAMBATU KUFIKA KU MALWI KUNO KOMA MWATI SIYIFIKA KUNO

  Рет қаралды 48,690

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 138
@SelemanChimtolo
@SelemanChimtolo 18 күн бұрын
Moto umapita kwatsala Ncthile,let's wait and see
@EvanceMaster-v5o
@EvanceMaster-v5o 22 күн бұрын
So sad, malawiso akupita komweko koma tipempha mulungu atithandizile kuti chakwela asakwanitse kubela tikufuna dziko lino alamulile wina?
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi 22 күн бұрын
No smartmatic here in Malawi
@jenipherbanda3303
@jenipherbanda3303 11 күн бұрын
Of course ndima lastday km mulungu ananena kuti sazalola kuti mwana wake akumane ndizomvuta iye alipo ndipo azankhala munthawi zonse amen
@JustinChinombo-dy6tp
@JustinChinombo-dy6tp 21 күн бұрын
Izi Anabel mtalimanja atengelepo phuzi ndipo kumalawi zikubwela zimenezi
@InnocentMtafya-c6b
@InnocentMtafya-c6b 18 күн бұрын
Poti mukuzifuna zizakupezani kudela lanu komweko..
@ahmedmsume1489
@ahmedmsume1489 21 күн бұрын
Chakwera ndizomwe akufuna next year, let's wait and see 🙈
@InnocentMtafya-c6b
@InnocentMtafya-c6b 18 күн бұрын
Muzaisova nokha...
@MathaNamanja
@MathaNamanja 18 күн бұрын
Anthu oipa awa,kuli kwao muganiza angalore? zisekelerani chon'cho
@EliseAndrew-v4x
@EliseAndrew-v4x 18 күн бұрын
Anthu oipa awa ife kwawo sitingathawileko
@CiprianoBindissone
@CiprianoBindissone 9 күн бұрын
Kuli amalawi ambili kunoko iwe akukhala bwinoso, komaso othawayo ndiwaphuma Mantha ndikufa adzafabe
@jamessheki4293
@jamessheki4293 19 күн бұрын
Koma awa amangoona kuthawira kuno Kwawo amatizunza!
@FrancisPhiri-x6l
@FrancisPhiri-x6l 19 күн бұрын
True
@FrancisPhiri-x6l
@FrancisPhiri-x6l 19 күн бұрын
Imagine
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 22 күн бұрын
Alandileni ndiabale anthu amenewo Africa were one 😢😢
@HarryMsudzula
@HarryMsudzula 22 күн бұрын
Vuto akumozambiki amaiwala kuti akamenyana amathawira Kuno kwathu komatikapita kwao amatizunza kwambiri khalidwe alibe
@DouglasDazuKamwendo
@DouglasDazuKamwendo 21 күн бұрын
Ndizoonadi Africa is one thing Julius Malema adatero koma ma guy aku Moshicco ndi anthu oipa mtima kwambiri adatizuza ife kufuna kutipha kwawo.
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 21 күн бұрын
Akumatigawanitsa ndi anthu andalewa ,
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 21 күн бұрын
Anthu opanda umunthu abale athuwa .
@IbrahimJackson-i8h
@IbrahimJackson-i8h 21 күн бұрын
We are one Africa, koma Mozambique siyimaona zimenezo nkhanza zake kwachitila azawo Maka ife Amalawi yooh satifuna anthu amenewa
@DaudBonomali
@DaudBonomali 22 күн бұрын
Ndiye zikayambika ku Malawi amalawiwo azathawila kuti?? Chakwela atule pasi udindo
@MaxwellSinoya-e1m
@MaxwellSinoya-e1m 10 күн бұрын
Tiwapepherere anzathu
@Pr.LaitonMbalame
@Pr.LaitonMbalame 12 күн бұрын
I am in the city of Beira, the second capital of Mozambique. What is happening here is a peaceful demonstration. If you don't know, you should find out more. You Malawians really like to stir things up.
@MedusaMhango
@MedusaMhango 18 күн бұрын
sanabere nayeso nthawi musavutise anthu ayi
@mcdonaldchimwala
@mcdonaldchimwala 12 күн бұрын
Aaaa ! Awathandiza chani ngati akulephera kuthandiza Malawi akuvutikakunoko?
@StoreNkhoma-ii2lo
@StoreNkhoma-ii2lo 12 күн бұрын
Iwe wa Trends TV ndiwe wa DPP sungamachemerere zopusazi aliyense amene amakonda nkhondo simMalawi komanso Mchewa ayi koma anthu amitundu inanu agogo aja ndiwofowoka sindiwe wa MEC! mbuli iweyo
@StarchJonas
@StarchJonas 21 күн бұрын
Smartmatic must go.
@RadiantmmPhiri
@RadiantmmPhiri 14 күн бұрын
Zizachitikaso kuno kumalawi zimenezoso
@Pr.LaitonMbalame
@Pr.LaitonMbalame 12 күн бұрын
The funniest thing is that this gentleman over there has no shame to the point of telling such false lies?
@Mahamudu-q6b
@Mahamudu-q6b 22 күн бұрын
Yes😢😢
@JonasChicuni
@JonasChicuni 9 күн бұрын
Chilungamo anawina ndi venaçio mondlane
@IbrahimJackson-i8h
@IbrahimJackson-i8h 21 күн бұрын
Smartmatic ai normally election we want
@damiaograciano9101
@damiaograciano9101 22 күн бұрын
Sizoona zimenezo Kuti FRELIMO yawina muchonadi vuto makhoti athu Kuno sioyima paokha. Amalamulidwa ndi FRELIMO
@johnmwase676
@johnmwase676 17 күн бұрын
Asiyeni abwere anthuwa si olakwa zinthu sizilibwino kwawoko
@JulieNdekha
@JulieNdekha 17 күн бұрын
Inuyo chisoni kwambiri eti!!! Chisoni chamanyi
@johnmwase676
@johnmwase676 16 күн бұрын
@JulieNdekha Ganizani bwino dziko la pansi lino,sikoyamba anthu a ku Mozambique kuthawira ku Malawi.Atsogoleri awo ndi amene akuyambitsa zimenezi,kuzunzitsa anthu osalakwa
@MosesMwengo-ku1lv
@MosesMwengo-ku1lv 22 күн бұрын
Welcome Africa is one
@PatrickChilombo-l2s
@PatrickChilombo-l2s 10 күн бұрын
Zoona zake makina obelawa a choke ziko lathuli timalikonda,munthu sanganene kuti mkodzo ndi wanga koma tudzi sindine
@ibrahimjafali
@ibrahimjafali 16 күн бұрын
Zowona koma eee Malawi
@MarthaGama-q1o
@MarthaGama-q1o 21 күн бұрын
We don't want smartmatic here 😢
@SamsonMukhawa
@SamsonMukhawa 16 күн бұрын
Nkhani ndiyoti mavoti azawelwngeledwe pa ground osati pa machine ayi
@chimwemwechiundira6002
@chimwemwechiundira6002 17 күн бұрын
Asabwere anthu oyipa osayamika awa.
@EsetaGerate
@EsetaGerate 22 күн бұрын
😂😂😂😂😂 chikangawa uwona zimenezo 2025
@InnocentMtafya-c6b
@InnocentMtafya-c6b 18 күн бұрын
Muzaziona nokha, kumaganiza. Mukamaganiza ngati nkhuku muzaisova.
@MathewsDaliken
@MathewsDaliken 11 күн бұрын
Aboma asakakamile makina akubawokuno ku malawi
@PolinaPhetera
@PolinaPhetera 14 күн бұрын
Komatu kwao salandila munthu awo ndi anthu oyipa
@ChristianfChinyamajunor
@ChristianfChinyamajunor 18 күн бұрын
@anabel Talimanja tembo 😢
@EnrikesJoaqim
@EnrikesJoaqim 13 күн бұрын
Abwerera kwawo wenanawo ndi amarawi kare inu
@AnnieChitsonga
@AnnieChitsonga 17 күн бұрын
Kunonso dzulo abwera kwambiri akumozambique kwambenje kumalaka
@YahayaJawadu
@YahayaJawadu 17 күн бұрын
Azipita kwawo zi anthu za khaza izi
@LucksonChipofya
@LucksonChipofya 20 күн бұрын
Ndizomwe akufuna achakwera chonde anthu sakukufunani achakwera mukuyambayo ndinkhondo
@lotchilembo
@lotchilembo 18 күн бұрын
Mukanangoyakhura za kumozambiqu osati zopandapake izo ayi owina ndiamene azaiwine kumakhala ndiulemu .muzikapanga zanu
@JulioChiwalo-t4f
@JulioChiwalo-t4f 18 күн бұрын
Anabel Chakwera ndi Mcp yaoyo aziona zimenezi
@MaxwellChiwaya-i8q
@MaxwellChiwaya-i8q 21 күн бұрын
Smartmatic sikufunika please amalawi
@BaxterKachelenga-mb7wx
@BaxterKachelenga-mb7wx 18 күн бұрын
System iyi ntchito yake NDI kubera,NDI chifukwa chani winawake akuikakamira.A Mozambique amathawira Ku Malawi and amalandilidwa Koma Malawi azasowa kothawira .
@namondwejohn9354
@namondwejohn9354 14 күн бұрын
Ambuye atichitile chifundo
@YusufAlidi
@YusufAlidi 20 күн бұрын
We don't want smart matic
@RichardGoodson-f5x
@RichardGoodson-f5x 11 сағат бұрын
Nani mukozekele kubeledwa kuchokera ku mantchine amenewa kunoku sizinayende bwino
@chiipiramtsamira1444
@chiipiramtsamira1444 17 күн бұрын
apolo Anabela kunafuna kuyambilaso kuvota
@HevenChiwaya
@HevenChiwaya 21 күн бұрын
Smatimatic ndiyomwe ikubwelesa nkhomdo ku Mozambiki ndizomwe akufuna hule anabelo kuti zizachitikense ku Malawi kuno
@Mda5-kq8fq8gs7q
@Mda5-kq8fq8gs7q 11 күн бұрын
Anadyapo zachinyengo
@crytoniegrantliffa2431
@crytoniegrantliffa2431 22 күн бұрын
Chaka cha mawa ndi malawi
@FrankMakulumiza
@FrankMakulumiza 21 күн бұрын
Kunonso ku Malawi tionesana
@Bizymalw
@Bizymalw 10 күн бұрын
phamvu zachakwera zimenenzo
@ErickTym-u2m
@ErickTym-u2m 18 күн бұрын
Nafeso next yr tipanga zomwezo chikangawa ungoti pheee mcp izathawira ku Tanzania
@OssmanAbubaker-v7t
@OssmanAbubaker-v7t 21 күн бұрын
Zoonadi wa wina ndi wa opposition ku Mozambique 🇲🇿 asalole komaso ma judges alowesa katangale
@JimmyGattuso-w5z
@JimmyGattuso-w5z 14 күн бұрын
Very sorry indeed
@salekhalizha
@salekhalizha 22 күн бұрын
Bambo mukunama Ife ndi amene tili Muno m'mozambique anawia Venancio osat chapo
@MalawiTrendsTV
@MalawiTrendsTV 22 күн бұрын
Ife sitimangoyankhula timachita kafufuku bwino bwino welengani report la aljezeera www.aljazeera.com/news/2024/12/23/mozambique-top-court-confirms-ruling-partys-win-in-disputed-election
@geraldtuwaga-iz6ll
@geraldtuwaga-iz6ll 22 күн бұрын
Ndiye mukuthawa chani , osakutetezani a boma anuwo, ngati mukuti anawina wa bomayo, smart matic ndiyachabe
@VeronicaTime-jn7fp
@VeronicaTime-jn7fp 21 күн бұрын
.ndizimene akufuna chakwela
@MihiretuYohannis-c3j
@MihiretuYohannis-c3j 14 күн бұрын
@LawrenceMsango
@LawrenceMsango 22 күн бұрын
Akufunaso kuthamangisa ambassador wa kuZimbabwe ndi amane akukolezela ziwawe sadc chair personal munangangwe he is a feller
@DouglasDazuKamwendo
@DouglasDazuKamwendo 21 күн бұрын
Mwasokonekeratu inu
@alicksango9878
@alicksango9878 10 күн бұрын
Word war ilipafupi zosezi zinanenedwa kare
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma 21 күн бұрын
Kuno kumozambiuq atopa ndiulamulilo umodzi chifukwa zafika apa olo atawina koma athu akufuna kusitha zakazachuluka zolamula afelalim
@MaxwellChiwaya-i8q
@MaxwellChiwaya-i8q 21 күн бұрын
Amenewo avotenso chifukwa ngati anaonjezera ndiye kuti anabera
@AnessChisemphele
@AnessChisemphele 17 күн бұрын
E ndiye zovutatu zomenezi
@Ellard-e2f
@Ellard-e2f 19 күн бұрын
Escape from Sobibor
@lastonmasoatenganji-bs5gf
@lastonmasoatenganji-bs5gf 21 күн бұрын
Iye amene aumitsa khosi atadzudzulidwa kwambiri, adzasweka modzidzimutsa palibe chonchiritsa.
@LenadChelute
@LenadChelute 10 күн бұрын
Kumarawi ngondo yiyi murungu anatifungatira tasiyani enawo azimenyana Ife Jaja amatifungatira
@MacxwellStuarts-h9r
@MacxwellStuarts-h9r 19 күн бұрын
Nchoona ndi chakuti abera avotenso koma asagwilise machine akubawo
@MariaDandazaraJSDmoio2024e
@MariaDandazaraJSDmoio2024e 22 күн бұрын
Chimene chinachita ndi chamashini aja akabela mashakho pogwilitsa ntchito ya mashini
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 22 күн бұрын
Kuno ku Malawi Machine amenwo asagwire ntchito kuno Amalawi tidzavutikatu
@omarejussa8703
@omarejussa8703 21 күн бұрын
Mulungu wabwino ndipo satisiya tikuvutika Choncho mpakana kale kale. Iye ndi wamphavu ndi nzeru pachìli chonse cholengedwa
@danielmakala-p6i
@danielmakala-p6i 18 күн бұрын
Tiziwona
@IsaiasIsaias-yq7zg
@IsaiasIsaias-yq7zg 21 күн бұрын
Bomala flelimu ndiyakuba koma athu akwiya kunoku nde manhumba akuwonchedwadi ndi anthuwamba
@JaytuSaisi
@JaytuSaisi 17 күн бұрын
Sukudziwaso iweyo zaziiii
@AchinaKellz
@AchinaKellz 22 күн бұрын
Ife timadalira ku Mozambique komweko tikayamba kuthamangisana kuno chaka chamawa
@HawaHussein-o5k
@HawaHussein-o5k 22 күн бұрын
Vuto ku malawi kulibe ma court ndi ma judge a chikungamo kuti alowelele pa nkhani kuchotsa smart matic mpakana ku nethu adzapitilize kuluza miyoyo akungoyangana ambuye akhale loya wa amalawi mpaka chilungamo chochotsa smsrtmatic chitatheka
@McdonaldChimwala-w9z
@McdonaldChimwala-w9z 22 күн бұрын
Kumalawiso zichitika
@MaryChavula-jz3di
@MaryChavula-jz3di 19 күн бұрын
Ife amalawi tikukana chimashin chimenecho bwanji amec akutikakamiza sakutiphwanyila ufulu pamenepo?
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 21 күн бұрын
Ma judge amaiko athuwa amakhala nthawi zonse ku kumbuyo kwa chipani cholamula chifukwa cha makobidi ndikufuna kugula kukoma ku boma likubweralo .
@mcphersonngwira7467
@mcphersonngwira7467 21 күн бұрын
Tipewe
@HassanJabali-r5x
@HassanJabali-r5x 17 күн бұрын
Ife ndy tizathawila kut Mozambique pot inatizugulila
@JorgeMiguelPofu
@JorgeMiguelPofu 14 күн бұрын
Kuno kulibe nkhondo,alesi amenewo
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 17 күн бұрын
Inu tisiya kukupangani follow ngati mukuwonetsa mbali yomwe muli machende ako
@MascotAnderson
@MascotAnderson 10 күн бұрын
Wakutuma ndani kt upange follow osangopanga unfollow bwanji
@StewartGoma
@StewartGoma 22 күн бұрын
Muuzeni chakwela amathandizira kubela mavoti ndi machine smartnstic
@BashiruAdamus-l2b
@BashiruAdamus-l2b 21 күн бұрын
Zikubwera kuno kumalawi
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 9 күн бұрын
ndisave,winna,akunena,kt,chakela,sawina,ngati,sukamuvotela,km,ifetikamuvotela,
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 22 күн бұрын
ZEDZE PANO NZATONSE CHAKWERA ANATHANDIZIRA KUBERA ZISANKHO KU MOZAMBIQUE NDI SMARTEMETIC MACHINE .NDIYE CHIKANGAWAYU AZIONERE YEKHA
@Rasheedissa-f3q
@Rasheedissa-f3q 19 күн бұрын
allandilleni manebasi amenewo
@MosesDicostar
@MosesDicostar 22 күн бұрын
Nafe tisake kozathawira chaka chamawa
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i 22 күн бұрын
Are you watching ??
@BennettNjedza
@BennettNjedza 22 күн бұрын
Mcp ndiyoipa singamve opanda kududuluzidwa
@AchinaKellz
@AchinaKellz 22 күн бұрын
Tiduduluza Black or white
@HusseinMoffatt-mi1fl
@HusseinMoffatt-mi1fl 22 күн бұрын
Takunyadila aise potidziwisa
@alexsumani6823
@alexsumani6823 22 күн бұрын
NKHANI YABWINO KACHIPANDE KATHELERE KAKOMA NKUYENDERANA IFENSO CHAKA CHA MAWACHI AZATISAMALA eeetu
@GoldenNamanguya-b1f
@GoldenNamanguya-b1f 22 күн бұрын
Alandileni ndi abale athu
@ErickTym-u2m
@ErickTym-u2m 18 күн бұрын
Povo No podemos
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 9 күн бұрын
chakwela,boma,2030,woooooo
@MarkoSimon-q3b
@MarkoSimon-q3b 22 күн бұрын
Chakwera. Ndi osokoneza a turepansi. Udindo. Adzatiyambitsila. Nkhondo. Ku malawi.
@BwanaGD
@BwanaGD 22 күн бұрын
Iii amelika ndi dziko la zungu zinthu zawoso amapaga mwachizugu sizanthuzi zachitsamundazi munthu kugwira ntchito yokodweletsa anthu ako kokuvuta koma kakaka gati bilimakhwe kukakamira mpando hede ulu kuchita kunthawiwa ku ubusa kusankha ndale koma ziliko Chocho dziko ligayende gati tikufika pomukana mulungu ha mh
@JosephGabriel-y7w
@JosephGabriel-y7w 17 күн бұрын
Asazangwilise nchito manchin
@RichardThera-i1p
@RichardThera-i1p 18 күн бұрын
Abale athu amenewo, asiyeni akhale. Zikakhala bwino kwawoko, abwelera!
@damiaograciano9101
@damiaograciano9101 22 күн бұрын
Zosatila za mmasenta amasogola anali oSusa koma zitafika kulikulu zinasitnhindwa.
@SmilingFishingRod-zc4wx
@SmilingFishingRod-zc4wx 21 күн бұрын
Alandireni ndi abale amenewo. Ifenso 2025 tithawanso ndiye sitiziwa tizathawira kt?
@FrancisPhiri-x6l
@FrancisPhiri-x6l 19 күн бұрын
Kwawoko?
@FrancisPhiri-x6l
@FrancisPhiri-x6l 19 күн бұрын
In Mozambique are cruel same as Angola they are Killer's, tret you badly my friend they don't joke in their countries
@FrancisPhiri-x6l
@FrancisPhiri-x6l 18 күн бұрын
Believe me or not
Living U.S. presidents arrive for Jimmy Carter funeral at Washington Cathedral
12:00
Milwaukee Journal Sentinel
Рет қаралды 1,2 МЛН
Леон киллер и Оля Полякова 😹
00:42
Канал Смеха
Рет қаралды 4,7 МЛН
Cheerleader Transformation That Left Everyone Speechless! #shorts
00:27
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 16 МЛН
Hoe Elon Musk de satellietmarkt domineert
15:53
BNR
Рет қаралды 4,1 М.
Klimaatcrisis & extreem weer: wat staat ons te wachten?
46:05