Yes madala mukukwana pa commission of enquiry ya Malemu SKC.
@GiftChilanga-u3c18 күн бұрын
Tisataye nthawi abale chakwera ndiye owner of this mission tatiyeni satanayu timuchose pampando mphamvu ku anthu imagine tisathe Mawu komaso t isagone abaleanga talira mokwana ndi imfa za abale athu😢😢😢😢😢
@AiwaMedia-sh6vx17 күн бұрын
Nkhani iliyonse ya Chakwera imangondipsesa mtima ndipo ndine wankwiyo
@edsongeorge80326 күн бұрын
kwabasi inenso imandioyysetsa ntima
@MartinKapito2 күн бұрын
Ine ndiye amandinyansa
@MchachaGoodson8 күн бұрын
Chakwela he is got case to answer.why Malawians are just quiet we must take him to court and he must step down.he is not fit to stand for next election.
@yohanekanjana49256 күн бұрын
I totally agree with you, he must resign from the office. he's something we can not imagine. he's blaming anyone who's talking about the death of vice president. I don't even know why he's still in office. Izi zikuchita kuonetselatu kuti chakwelayo ndi emwe adapha chilima. Ndiye chakwelayo asaone ngati ndi 1940 ino yoopsezana, adapha vice president basi, zomalankhula zabodza chilungamo chilipo ine sundupanga nawo.
@TrizaGeorge-q8w18 күн бұрын
Inu chikangawa ndi satanic ngati akuvotela khondo kuti izipitilila ndi muthu ameneo
@JonathanMtambo-w6e3 күн бұрын
What you are saying up to now we all do not believe that young hand some man is gone because of greedy people
@EdwardBotha-h1i4 күн бұрын
Achakwera akuziwapo kathu paifa ya achilima
@KondwaniBanda-ul8sj21 күн бұрын
Amene Ali ndimaso auzimu awone nyengo tiliyi nyengo yakumapeto tili matsiku otsiliza tisiye kuyika chikhulupililo chathu pa athu koma tidalile mulungu wamoyo kusiyana nalo tchimo ndipo yesu akufuna tilape
@Musa1828-l5d21 күн бұрын
Iwe palibeso zamasiku omaliza apa galu iwe Chakwera anapha Chilima basi
Chakwera thought malawians are stupid and will not ask him and his blood party
@Musa1828-l5d21 күн бұрын
Chakwera ndimunthu oipa mtima kwambri
@SteveKaphamtengo-gf2mp7 күн бұрын
Akudziwa po kathu ameneyo
@BlessingsGama-j3r13 күн бұрын
Onse omwe anaanamiza a president pa 10 paja achotsedwe ntchito 😢
@ericmakunganya473015 күн бұрын
Asatana mcp, history is the best teacher,we all know they are murders, but we put them into power ,why my fellow Malawians?
@PaulPhiri-c5u9 күн бұрын
Koma zoona mwane brother zoona apa apule akuoneka kuti akuziwapo kanthu ngati sichochi lakhulanipo kanthu
@SoniaPolokera11 күн бұрын
Amaziwapo kanthu chakwerayo
@PhiripChinkango-k5p6 күн бұрын
Chilungamo chidziwika ndithu eeee boma la chakwela ndi nduna zawo afotokoze bwino bwino basi
@LouisAndrew-jr1yj17 күн бұрын
Mulungu mwatisiiranji ife 😭😭🙌
@EssauChimpango6 күн бұрын
Choipa chisata mwini
@StewartGoma8 күн бұрын
Good morning Amalawi nonse Kodi singatheke strike the whole country to pressurized chakwela to step down it hurt alot of Malawian what is happening to malawi What makes the opposition not to act what Mr chakwela n his government is stupidly childish even a little boy knows that there is justice Since the plan crashed no one has been fired coz of different statement The government knows everything
Zonsezo chifukwa anthu sakuchitapo kanthu pa khani ya Chilima ndi ena onse amene anafa pa ndege akuona kuti akupambana because there's no action we are just talking that's why so now we're very worried of what's happening in this country ,
Mmalawi muno mulibe president ....ichichi ndisilu kwambili
@FysonMkuzura9 күн бұрын
Sitidzavotera oimba or nyimbo yachipani koma kusintha atsogoleri aboma !!
@TelezaManyela7 күн бұрын
mawu a mphamvu brother
@robsonmapeto1911Сағат бұрын
Anthu ankamuuza Chilima kuti adzichepetse lero womwewo ma banzi ali kukamwa ali duu zitsiru zawanthu dyera ndilo lakula
@JamesALLi-m8i14 күн бұрын
That is true my big brother be strong 💪 my guy 👦
@yohanekanjana49256 күн бұрын
Ifetu chomwe tikufuna angonena chomwe adamuphela Chilima, mwati kuipa mtima kwanji kungoposa satana. Moti zoona kupha mnzake chifukwa chofuna mpando? koma ngati ndi umfitiyo ayi chakwela mudadziwadi. koma dziwani kuti aliyense adzamka kumanda komko. Umfiti wanuwo sudzakupulumutsani kaya ndi ndalama sizidzakupulumutsa mphwanga. No one overstayed forever.
@MartinKapito2 күн бұрын
Malawi sitikusowa umboni yemwe anapha achilima ndi ladzaro cakwera ndi MCP
@FelixChikaondagama21 күн бұрын
Kkkkkkk Chakwela nayeso ndi munthu chere wa anapuna wamulowa kamwa ndiye si boza lakelo mmmm zikukanika kuti amubakile pongonena kuti ndege sinafike ku mzuZu basi zose zose ndizaboza munthu atatu atule pass udindo kuti afufuzidwe please
@chimwemweshadrick59729 күн бұрын
As a civil servant, he has failed us big times, negligence at its best, ma civil servant amapatsana handover kuti ntchito ipitilile , now why lying about all the precedings . Ndipo asilikali amakadikila ma civilian ku drc koma VP kukanika kukamusaka VP wa dziko, kukuzizila , kokaika maliro nde ma bus ma bus kudikila maliro .Mulungu odziwa kubvumbulutsa zinsinsi adzabvumbulutsa, ndipo Mulungu yekha ndi amene tili naye limodzi koma ,anthuwa salinafe .
@DawoodIssah-mp1yi4 күн бұрын
Achakweratu sakudandaula chirichonse ayi olo pang'ono angochita pretend ngati akudandaula koma ayi angowapusitsa amalawi kuwaona ngati opusa, Ine chikangawayu ndinamustada ndi chigawenga choopsa mMalawi.
@RigementMshanga2 күн бұрын
Apa tinganene Kuti a Chakwera anaphanao kapena amamuopa Chimwendo.
@samdiverson973321 күн бұрын
Pamenepotu zikudabwitsa akatelo adzitinamiza kuti mu ndege munalibemo ma connect device
Uyu chakwera adatiuza kuti ndege inakafika ku mzuzu ndi kubwelela atiuseso kuti adamuuza ndani kuchokera pamenepo nde tione kuti tiyambile pamenepo
@lyiemanganjira970821 күн бұрын
Kodi impeachment inatha mudziko la Malawi???? Ifetu tatopa ndikungomva zokambakamba zanuzo.. Take the action asativutitse ku mtundu wa Malawi
@JoyceBanda-k8t13 күн бұрын
Khaniyi ndi ya straight kuti chakwera anapha chilima bwanji nhati sanaphe safufuz mdi ndani yemwe anavula chilima zovala chifukwa chani anthu amapedzela ndi zipolopolo ndi ndani anawaletsa chimwendo Banda kukwera ndege ndi chifukwa chani okupha allan witika amanena kuti ndenge yagwera kovuta anthu sangafikeko lodi ladzalo ndi mchimwene wako chimwendo komaso mozes okupha Allan witika mukuona nhati ife ana mukhonza kumatinamidza
@mathewssiliya57421 күн бұрын
koma ziliko chalachanga chinandilakwisa koma ndikoza
@aphilichimangaКүн бұрын
Ndipo nkhani ya chakwera si momwe zimandinyasira
@DalitsoMatope10 күн бұрын
2025 ngat mbiri ya andale za malawi sinayambe yamanga ndi kuphedwa president ndi nduna zake tiyambira pachakwera ndikondanso azakhale pa makako
Very sad position yau president njokomadi et? Mpana kuphana😢😢
@WarriorKB-u3k9 күн бұрын
Palibe cha mzeru chomwe akulankhula,chikangawa ndi amene anapha anthu onse aja asatipusise. Iyeyi ndi mbuzi ya munthu koma amalawi tisadandaule 2025 onsewa akupita APM boma
@Mwenda-sr9ro13 күн бұрын
Mwatimphera chilima amcp koma amene anakuika pampando
@RuthChilobwe2 күн бұрын
Talira ife a malawi.a chilima kutikokera kwa ng'ona yakupha mcp..party in tonse Alliance .@ Yet my question is. This tonse Alliance led by chakwera and chikima and the other 7 political parties of Malawi nation including pp" of Joyce Banda ; DPP of APM;Afford of chihana ; Udf of Bakili Muluzi .and the kumbawaku party etc did these not notice the mission of the Alliance that it was to Shed malawians blood ..and cause frastratration and turmoil to all us malawians ? Tiuzen zeni zeni amangwetu
@MariaGatoma19 күн бұрын
Kodi ndinu amalawi first,,,omwenyela ufulu amalawi,,,kodi mukudikila chani mukufuna anthu amidzi anene kuti ife takozeka,,komaso nokha simunaone ku chikwawa kuti anthu atopa,,,kodi amalawi first mukudikila chani???ife takozeka tangolengezani za mademo,,,timenye tokha nkhondoyi,,,opposition yonse ikukhuta ali ndi ndalama,,,pomwe amalawi tikuzuzika zedi tiyeni mademo
@edwinearlkachiwala307018 күн бұрын
Vuto ndi lakuti posachedwa mulandila ndalama ife anthu wamba mutisiya opanda Maya nkho pa knhani iyi
@KaumaNtora3 күн бұрын
Zovuta kwambili kumalawi😢
@FlorencePhiri-p1t14 күн бұрын
Kodi ndikoyamba kuva ngozi yandege chakuti mudziwe munthu aliyense adzafa ndipopangoziyi sanafe ndi chilima yekha
@AtupeleChitenje9 күн бұрын
Ngozi yochita kupangayo nanunso
@DennisTobias-b4r7 күн бұрын
Zoona ngozi zimachitika koma boza linachuluka, mkulu wa asilikali anati inagwa popita, president inagwa pobwera, aliyese azafa chifukwa chani ifayi ikudabwisa anthu?
@YammsyZebron5 күн бұрын
Munapha nzanu kufuna ma udindo mbuzi
@mohamedriazshreef86979 күн бұрын
Ather Wise timumphenso naye
@AyandaJanga-fe7wp18 күн бұрын
Pofunika ma videos adzipositidwa because enafe tinavutika kwambiri ndi mcp kuyambila nthawi ya kamuza banda timagona kutchire enafe kuopa mulibwino amene munabadwa ma 2000 koma enafe ama 1980 timagona timathawa ndimakolo wathu kukagona kutchile chifukwa chaumphawi bambo wanga amalephera kulipila nsonkho wapachaka. Mpaka sukulu ndinayamba nawo atawina a chair nditakula kale. Madala wanga anamangidwapo kukakhala kundende kwamiyezi 6 osaonako abambo wanga amakagwila ntchito yakalavula gaga this true story sindichita manyazi zammene ndinavutikila chifukwa mutandiona panopa mukhoza kumaona ngati takulila moyera. So guys ngati ma vedeo alipo postani chifukwa kubweraku mmene mcp yafikila, ikulamulila lamulo lachikalekale lowopseza anthu akuphedwadi next time muvi oyang'anira sumachedwa kulowa mmaso
Zangozi yandege idatha kale palibeso zochedwa Mmalo mopanga chitukuko chonekelatu
@DalitsoMatope10 күн бұрын
Iwe
@DalitsoMatope10 күн бұрын
Iwe
@robsonmapeto1911Сағат бұрын
Ndigalu ameneyu mfiti
@frankcassim20 күн бұрын
Zosakhala bwino awadi ndiazimfwambadi
@juliochiwalo20 күн бұрын
Pomwe palibe chilungamo ali yense amanena zosiyana ndi mzake ndi zomwe zikuchitikazi
@FelixTsabolaNamaya18 күн бұрын
Ife nde tafika potopatu khani yomweyomwe ngati inu simudzafa
@doreenkaliati316620 күн бұрын
And lipoti lidabwera ndi chakwera Iye amakataniko pa thakopo pake akusewera ndi iyeyu
@JafaliAkimu-ll1bf14 күн бұрын
boma la zitsiru zokha zokha zigawenga izi zonse
@LusiyaGoliath5 күн бұрын
zisilu izo zokupha za zesamkwiyo kumalawi
@kingsleyhopematchaya518418 күн бұрын
Kod iweyo chilima unacheza nayeko?nanga mnkazi wake wamuthandizako chiyani? Kod kubanja iweyo akudziwa? Maliro akachitika tikayika basi amoyo amafunika awone chitsogolo iweyo unkhala ngati kt amakudziwa chilima za ziiiiiii
@DamianoYohane14 күн бұрын
Maganizo anuwa amayenera kumaperekedwa nthawi ya kamuzu kulibe social media koma pano mmm ma plan amene anapangidwa apa anafoira nawo
@BethsiderTavares-ug4sv21 күн бұрын
😭
@kingsleymsampha226018 күн бұрын
Many doubts to this pastor mmmm..... Christians let's show fake pastors that there is a true God.
@edwinearlkachiwala307018 күн бұрын
Akulu akulu ndufuna anthu odziwa za malamulo andithandize za mafunso ena
@Semuwandawanda-b2n10 күн бұрын
Mukuchedwa nikusokosa ni za chikangawa ulesi mulibe Mmalo moti muzitsitsa mfundo zoti mlowe m boma lomwe ife report lomveka bwino lomwe inu ngati nikudziwa Zina fotokozani muli wee wee wee wee sosamveka mbuli inu ife boma nomweli dziwani kuti chakwela ni mtsogoleli wanga komaso iweyo ni mtsogoleli wako
@christophergibson7221 күн бұрын
Mukakhuta basi kumangosokosa apa malo mokamanyera uko
@MadalitsoChinkhonyo20 күн бұрын
Udyatu ntsono
@robsonmapeto1911Сағат бұрын
Munyeratu simunati agalu Inu paziphwisi panu
@berlz12k8 күн бұрын
2025 awa onse akukaseva kumaula anthu oipa kwambiri anthakati,zitsiru zaanthu..anapha anthu aja and zinthuzi sizofunikaso kufunsa kapena kuganiza it’s so obvious guys..google “how can i hire a sniper pa jon and how much can it cost?😡🦧
@Mwenda-sr9ro13 күн бұрын
Mwatimphera chilima amcp koma amene anakuika pampando