Apapa Mwano omwe Hot Current yachita mmmh Uwuwu ndi mtopola 😂😂😂😂 Mcp aiphweketsa kwambiri 😂😂😂

  Рет қаралды 7,347

Malawian Cameras

Malawian Cameras

Күн бұрын

Пікірлер: 90
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 6 күн бұрын
Ayi simwano koma Chakwera zofuna. Tangoganizani, 1) Simplex Chithyola akhala bwanji Mr. of Finance? Mbuli imene imadziwa kuba ndalama ndikumakagawa njinga ndi fetereza kwa mafumu. 2) Chimwendo amene amadziwa kugawa ndalama kwa oyimba angapange chani. Chimwendo amene olo MSCE alibe. 3) Kunkuyu imene ili mbuli yeniyeni. Amene amadziwa kupha Witika. Anagtan. 4) Henry Kachaje amene ali ndi master's degree ya fake. ☝️Mbuzi za kudabwe izizi zongatani?
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
😂
@PeterLemani-jk3mw
@PeterLemani-jk3mw 6 күн бұрын
You're the best tv in the world
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 6 күн бұрын
It's kwagwanji my brother but thanks for always giving us updated ❤❤❤❤
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
Thanks brother 🎉❤
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 6 күн бұрын
@@MalawianCamera keep on doing that coz eee malawi wafikapo
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
@PrinceBlessings-bv5bs Thank you brother 🎉🙏😂 Malawi wanunkha
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 6 күн бұрын
@MalawianCamera 🤣🤣🤣🤣 eeesh kwachema
@austinjune379
@austinjune379 6 күн бұрын
Look how Malawi as a country voted in the united nation general assembly, Malawi has never had friends around us. Network is to communicate with friends or people who are around you.
@fannyzimba149
@fannyzimba149 6 күн бұрын
Network yathawa ku Mcp kkkk apa zavuta basi mmmm angochoka
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
😂😂 Vuto lake Network sabwerekana😂
@jangiamsume7248
@jangiamsume7248 5 күн бұрын
That's very nice and beautiful
@CustomHetre
@CustomHetre 5 күн бұрын
Boma ilili nde Kaya tiziti vuto ndi chan 😢😢
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 5 күн бұрын
Kkkkk Boma ndilomweli kkkkk no petrol no diesel mboma ndilomweli kape chakwela
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 6 күн бұрын
Uyu ndi mwano wachilungamo 😂😂
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
😂😂😂😂Eeeee
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 3 күн бұрын
Aaa kulephela kwa boma lelo paka mayi banda kumawoneka ngati dolo nayetse ali owononga kķk koma MCP ndi chakwela wanuyi kumafunatso kubela ma vote iiiii adzathelatu Malawi bolani pano anthu opanda chitsoni koma mvuto loti awononga dzedi nde akudziwa kuti akachoka adzalowa mu ndende motsakayika
@hassammaulana4529
@hassammaulana4529 6 күн бұрын
Iyi kwangwanji special bro king brain banda ..J pakuku and w musishaa
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
Thanks broh
@FlynessWinga
@FlynessWinga 5 күн бұрын
😂😂😂😂 behaviour matters more.......athu omwe Ali ndi network ndi awo anawaphawo😢😢😢
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 3 күн бұрын
Simwano koma zikuwoneselathu kuti nthawi yoopa inapita
@MphatsogiftJerejr
@MphatsogiftJerejr 5 күн бұрын
My second favourite channel, Malawian cameras, just a point of correction this programme is called kwangwanji Hot currents it's only on Sundays from 06pm
@PeterLemani-jk3mw
@PeterLemani-jk3mw 6 күн бұрын
You're number one guys
@NovemberMmangathayo
@NovemberMmangathayo 6 күн бұрын
Mpomwe atamuganizilile chilima no apapa anthuomwe munawapha ndiwomwe alindi network pomwe achina chinthyola alibe network network yako koma ndikuwagule
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 5 күн бұрын
Nde achimwendo ndi alazaro ali ndi network koma
@NovemberMmangathayo
@NovemberMmangathayo 6 күн бұрын
Chilungamo chimawawa ayendakangati achakwela azungu amamupusitsa gwetsa kwacha zinthuzikhalabwino right now akungomuyang'ana chakwela kusamva amadzimva kuti afikapo lelo siizi mwezewatha palibe tsogololo palimwambi suluma chala chopisila mphuno chikatupa udzapisamo ndichani
@OssmanAbubaker-v7t
@OssmanAbubaker-v7t 6 күн бұрын
Eya sakunama
@AlexBeluka
@AlexBeluka 4 күн бұрын
Network ku MCP ndipacibale njopoyila 😅
@Edward-y3v
@Edward-y3v 6 күн бұрын
Ma network ose akuthawa ku mcp
@Lizzie-h1k
@Lizzie-h1k 6 күн бұрын
Anyamatawa amalikonda dziko lawo..ndipo amatha!
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 6 күн бұрын
She was better
@Lushaka
@Lushaka 6 күн бұрын
😂😂😂😂😂ngani ndi achimwene anu achakwela😂😂😂plus network 😢😢😢😅
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 6 күн бұрын
Achakwera avekedwa skirt ndi mzimayitu apa kupusilatu 😂😂😂😂
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
😂😂😂😂😂 Eeeeee mbolatu
@JamesChiphwanya-m4v
@JamesChiphwanya-m4v 6 күн бұрын
Koma abambo inuyo ayi ine pheee ma stand kumvera inuyo ulemu wanu boma ili palibe zathapo iziii
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂
@PatrickLuciano-bq3ww
@PatrickLuciano-bq3ww 6 күн бұрын
Koma kwagwanji 😂😂😂😂😂
@NovemberMmangathayo
@NovemberMmangathayo 6 күн бұрын
Chakwela anzake ndiagule mafuta awapezakuti pakanakhala pakufunika nkhuku kapena agule 1000 anakathakupezeka
@Jumatv1370
@Jumatv1370 5 күн бұрын
Sangavotere kuti nkhondo izipitirira lero ndi izoo
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 6 күн бұрын
Vuto chakwera safuna kumvera zanzake ndiopungwa
@NovemberMmangathayo
@NovemberMmangathayo 6 күн бұрын
Mesa usi amati amatha kupempha apapa zatani akapemphe mesa amadzitama
@NovemberMmangathayo
@NovemberMmangathayo 6 күн бұрын
Akukagwilizana ndi Israel akupatsachani ma Israel ubulutuwu ayi ndithu osamagwilizana ndimayiko oti athakukuthandiza nthawingati iyiyi
@RaffickAllie
@RaffickAllie 6 күн бұрын
Kodi chakwera nkhadza zake zimenezi angapedze network
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 5 күн бұрын
Choka nawe (what about cash gate
@ImulanJafali
@ImulanJafali 6 күн бұрын
Nitiweki sabwekana 🤣🤣🤣🤣
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 6 күн бұрын
Dzandikonda🔥🔥🔥🔥🔥
@LaufuJames
@LaufuJames 6 күн бұрын
Chakwera ayimbireko lsreal kut awabwere ndrama dat z best way
@ChifundoNinje
@ChifundoNinje 5 күн бұрын
Ndipo ndiye mwano weni weni zoonadi
@samsonyuda674
@samsonyuda674 4 күн бұрын
😂😂😂😂😂kwasabwaza
@thomasbotha9790
@thomasbotha9790 4 күн бұрын
Vuto ndinu guys, ndife amalawi chifukwa dziko ndirobwereka, ndicho chifukwa chake timakanika kupanga mademo,, kuti chakwera achoke,, kukanakhala ku mayiko ena akanayichotsa kale MCP, koma vuto mantha kukonda zoyankhura zokha koma zinthu sizikusintha,, tiyeni tipange mademo iiiiìiiiì? Koma mantha amalawi, palibe dziko lamantha ngati malawi?
@thomasbotha9790
@thomasbotha9790 4 күн бұрын
Zowona kukhala ngati dziko anakubwelekani kukanika kupanga mademo
@wisdomchilanga723
@wisdomchilanga723 6 күн бұрын
This is real hot 🔥
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
Kwambiri
@JamesSaiti-h1l
@JamesSaiti-h1l 6 күн бұрын
Mumakwana 😂😂😂😂
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
😂😂
@GeoffreyBAyatuKazembe-q7u
@GeoffreyBAyatuKazembe-q7u 4 күн бұрын
Network yomwe mcp ikuyendera ndi ya Zain mw 🥱🥱🥱
@memorychirambo4869
@memorychirambo4869 6 күн бұрын
Life eish
@billymhoni9527
@billymhoni9527 5 күн бұрын
Kwagwanji iyiii tinaiooneraso live Dzana
@YasinterKapinga
@YasinterKapinga 6 күн бұрын
Kwagwanji special brother wanga
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
😂🎉 Hot Current ili hot😂
@YasinterKapinga
@YasinterKapinga 6 күн бұрын
@@MalawianCamera kkkkkk
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
Oooh yes Kwagwanji thanks for correction nanga si anyamata ake ndomwewa nde nabalalika😂😂 thanks my Cc
@YasinterKapinga
@YasinterKapinga 6 күн бұрын
@@MalawianCamera zikomo brother pitilizani kutibweletsa zabwino bwino nkhani ndi ka network kkkkk
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
@@YasinterKapinga Nkhani zizibwera koma network sitibwerekana😂😂😂😂😂😂
@Jumatv1370
@Jumatv1370 5 күн бұрын
Amayi amenewo amatha koma
@Edward-y3v
@Edward-y3v 6 күн бұрын
Kkkkkk koma iiiiiiii
@edwinnyasulu2088
@edwinnyasulu2088 6 күн бұрын
Akutitu network sabwelekana😂😂😂😂
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 6 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@SeleKanthyole
@SeleKanthyole 5 күн бұрын
Mudagulitsa dege bosa inu amayi
@MalawianCamera
@MalawianCamera 5 күн бұрын
@@Alice-z7t4z 😂
@Mobilot2android
@Mobilot2android 6 күн бұрын
Koma Yah😂
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
😂😂 Akut alipo angatibwerekeko 15 mita? 😂😂
@KondwaniNkhoma-q2k
@KondwaniNkhoma-q2k 6 күн бұрын
This is kwagwanji not hot current
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
Thanks broh for correction 😂❤
@kennethkaunda3636
@kennethkaunda3636 2 күн бұрын
Kkkkkkk malawi
@AlieNkalapwagaNkalapwaga
@AlieNkalapwagaNkalapwaga 6 күн бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣
@MalizaniHarlod
@MalizaniHarlod 6 күн бұрын
Kkkkk
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
😂😂
@ShukuraniTonex
@ShukuraniTonex 6 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
😂😂😂😂 Ati ka ka network ko atibwerekeko😂😂
@YasinterKapinga
@YasinterKapinga 6 күн бұрын
​@@MalawianCamera network sabwelekana kkkkkkkk
@MalawianCamera
@MalawianCamera 6 күн бұрын
@@YasinterKapinga 😂😂😂 Akuti apange yao 😂😂
@eunicesaiti
@eunicesaiti 6 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂
@GeoffreyMaulana-rh5rx
@GeoffreyMaulana-rh5rx 6 күн бұрын
😂😂😂😂😂
@AdamMakala
@AdamMakala 6 күн бұрын
Kkkkk
Ebya Gravity ne Sheebah bibi 😃👌
1:03:40
Kasuku Live
Рет қаралды 6 М.
Elza love to eat chiken🍗⚡ #dog #pets
00:17
ElzaDog
Рет қаралды 21 МЛН
Trick-or-Treating in a Rush. Part 2
00:37
Daniel LaBelle
Рет қаралды 35 МЛН
Donald Trump's full victory speech
26:31
FOX 9 Minneapolis-St. Paul
Рет қаралды 6 МЛН
ZAULULIKA ZA IMFA YA CHILIMA-KOMA ANTHU AMALIMBA MTIMA
27:18
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 19 М.
LAPD in pursuit of vehicle
FOX 11 Los Angeles
Рет қаралды 14 М.
US Elections 2024 special coverage
1:43:59
SABC News
Рет қаралды 6 М.
Elza love to eat chiken🍗⚡ #dog #pets
00:17
ElzaDog
Рет қаралды 21 МЛН