Umatiyimilira Brother MTANYIWA keep it up don't stop by keeping up dating us tidziwe zoona tilikomweko ju nchewu MADEMO basi
@GivesonBanda2 ай бұрын
Mbuz yamuthu chakwela kuphamuthu chifukwa cha ndalama? Chifukwa cha mpando is it true? 😢
@PhillspicJere2 ай бұрын
Koma Ku opposition nkumavuto kwabasi zoona munthu kumasankha kukhala Ku opposition ma stress ndi daily kuyesesa kukamba zinthu zopusa, iwe osatulusa report lo bwanji Mesa munkati mukuziwa zomwe zinachitika,? Koma uchisiru wa amalawi ena ndithu munthu ungamamvere izi ndikumazidyesa ndizoona?😂😂😂😂😂😂😂 Koma Ndinu zitsiru nonse Amene mumakhulupilira zokamba za chisiru mzanuyu sure, Mufa ndi ma BP
@rodglae66572 ай бұрын
Ili ndi bodza lapoyera. It's surprising ena mukukhulupirira bodza limeneli. If it were kufuna kukakumana ndi anthu amene akuchita kafukufuku ndiyekuti report lisanatuluke ndiye yemweyu akuti Chakwera atulutse report! Kafukufuku opanga anthu a ku Germany report lake silingabisike because leven before kulipereka ku boma amakhala kuti aponya kale pa website yao. Nobody can tamper with it. And Chakwera akadakhala ndi any sinister motive sakadayenda on a state visit coz that way president amakhala pa public on anything he does, otherwise akadapita.on a private visit or ku holiday. Bodza ili simunaliganizire mofatsa
Yea, mostly some of malawians are very confused due to loose 8 peoples plus vice president chilima on plane crash. Plz plz this is not Good here in malawi and We can said from late Dr H kamuzu Banda up to peter mutharika and why chakwera?
@berlz12k2 ай бұрын
Kodi kumalawi kuno kulibe sniper ochokera pa joni? Uyu munakangompanga za Trump cheteee palibe angagwidwe,kushuta nkumapita jonz...watikwana scariot mxiew!
@ClydeNyasulu-tk6fj2 ай бұрын
🎉🎉🎉good job
@AlexPhiri-in1re2 ай бұрын
Well done mr Ntanyiwa
@CassimMbalaka2 ай бұрын
Mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pokuyikani nose wokhudxiwa pa ifa ya chilima
@WillianBanda-p7d2 ай бұрын
That very brilliant decision not to meet chakwera
@ThivadoartistDyson2 ай бұрын
Even ine akabwela panja pa nyumba yanga sindingatuluke
@Rose-wu5ef2 ай бұрын
Pa chichewa timati mbuli ya muthu
@FrancisBanda-q2w2 ай бұрын
Achita bwino a Malawi aku Italy kukana kukumana ndi mfiti yokupha Chilima.
Kudzitenga ngati iye ndi wamuyaya mwini chilengwe chonse ndi Mulungu
@DumisanPhiri2 ай бұрын
Happy to hear that
@MercyHassan-p4e2 ай бұрын
Ife a malawi tikumva kuwawa pa imfa ya maremu A Vice president Saulos chilima dzimu wao uziusa mumtendere
@GrinTemboh2 ай бұрын
Tipange ngati zinapangidwa Ku kenya xhakwera anye Kuti nyi
@LawrenceBelson2 ай бұрын
Alibe mtendere mr chikangawa asowe mtendere chikangawa party alliance
@ThokozaniBondo-em9fr2 ай бұрын
Well done 😂😂😂😂😂😂😂😂
@karimshaik44852 ай бұрын
Timakunyadilani atanyiwa mudzitipasa moni from Capetown
@juliochiwalo2 ай бұрын
Chakwera ndi MCP akuzunza amalawi kwambiri akuononga ndalama pamene anthu omwe anapum antchito pano mpaka zaka zitatu ena akumwalira kusiya ndalama zawo
@IshmaelNgeyani2 ай бұрын
Machende ako ukuikira kumbuyo chakwera
@AchinaKellz2 ай бұрын
Chilima tidayika limodzi ndi mcp, koma popanda manganya kudali komvuta raph nod chilies sadakafa history is a teacher same udasi
@corretabanda76852 ай бұрын
Zilibwino Mulungu sagona tulo. Ndinthawi yoti a Malawi tipemphe Mulungu kuti atitsegule Maso ndipo atisogolere ndikutipatsa mtsogoleri woyenera.
@ShorayChimera2 ай бұрын
A Catholic amakondana koopsa❤🎉🎉
@dagaphiri18672 ай бұрын
Munya mukutuluka basi . Mutu sikugwira. Ulendo wa ku Mozambique ndi Zimbabwe kusochera kukafika ku Italy. Koma mizimu ya anthu opemphera imazunza. Sanati.