ATUPELE MULUZI ANALOTA KUYANKHULA IZI - TINASANKHA AZITSOGOLERI A NKWIYO

  Рет қаралды 10,104

MPUNGWE-PUNGWE MW

MPUNGWE-PUNGWE MW

Күн бұрын

Пікірлер: 25
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i 4 сағат бұрын
That is true Apm is coming soon to be president of this country that is serious 👏 😳 dpp is my vote 🗳 2025 boma for sure 😀 😉 😄 Adad woyeeeeee
@MchachaGoodson
@MchachaGoodson 4 сағат бұрын
That's what is happening with MCP now.we must expose them while there are sitting comfortable life.
@MichaelBefore
@MichaelBefore Сағат бұрын
Apm ....my vote
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 6 сағат бұрын
Atupele uja osazamuphwekesa ❤❤
@Mobilot2android
@Mobilot2android 4 сағат бұрын
Zaliti iziii atupele lero angayankhule zimenez?
@ENOCKSEVISON
@ENOCKSEVISON 5 сағат бұрын
Tiyeni tivotere atupere, add akhare vice president, kodi mu lora kapena ayi?
@MonalisaMwale-c5k
@MonalisaMwale-c5k 5 сағат бұрын
Eya tilola or atupele atakhala vc add plsdnt ndkt athat kudzamusiyila udindo add akungofuna kutichotsa paizi bsi
@RelaxCool-dp9jn
@RelaxCool-dp9jn 4 сағат бұрын
Chilungamo
@ThomasSawati
@ThomasSawati 4 сағат бұрын
Ine sindingavotele nchawa
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i 5 сағат бұрын
Chakwera wachepa nzedi walephera kuyendedza dziko la Malawi 🇲🇼 and we don't need 💯 this government again 💯 🙄
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 2 сағат бұрын
Ine Bora nkhalamba yomwe ija
@MkandawileLloyd
@MkandawileLloyd 5 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂atupere ndi one ♥
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 5 сағат бұрын
Ai bola ngt zil zoona bolako koma ada qwawa amakaikisa aaaaaaaa
@User_n6-8n
@User_n6-8n 4 сағат бұрын
Nanu a UDF mumabwera kunja kutacha kale bwanji mbuyo monsenu kunali ziii Dpp ndi utm ndiyomwe imamveka koma Inu mumatulukira mukaona kuti zisakho zawandikira mtima wadyera kufuna kudzangomphura nao mphika omphuka ena kale
@Mobilot2android
@Mobilot2android 3 сағат бұрын
@@User_n6-8n zakalekaleizi
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 4 сағат бұрын
Kkkk ulemu wanu tupere 2025 boma tupere 🎉 pamosi dpp adadi
@GreyBanda-v3u
@GreyBanda-v3u 6 сағат бұрын
M umanena zoona big
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 3 сағат бұрын
Zakale kale izi tinambvera kale pano atupere sangayankhule chonchi
@NicksonKotokwa
@NicksonKotokwa 3 сағат бұрын
Bola ngati akunenadi pansi pa mtima
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 5 сағат бұрын
Wekha sukudziwa kuti ku Malawi kulibe president komas mau awa wayankhula liti zisakhale zakaletu izi mmm Atupere kukaikisa 3much
@ThoccoChimbali-h6g
@ThoccoChimbali-h6g 4 сағат бұрын
Atupele chitsilu cha munthu mesa ali limodzi ndi mcp
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 5 сағат бұрын
Zoonad
@RelaxCool-dp9jn
@RelaxCool-dp9jn 4 сағат бұрын
Timakunyadilani
@FRANCEHunga
@FRANCEHunga 5 сағат бұрын
Kkkkk yes panepo
@Lushaka
@Lushaka 5 сағат бұрын
Ndiwe munthu opanda zelu ndiziko lakho kale kale bwezi uli president pano mvuto umakhonda ndalama ndi family yakho iwe Anthu akumachinga anakhulakwila chani pamozi ndi muluzi wanuyo palibe boma likuvutika like machinga koma iweyo atupele ndi muluzi mumachokela koko mwatipangitsa manyazi ku machinga ndipo za manyazi
REAL 3D brush can draw grass Life Hack #shorts #lifehacks
00:42
MrMaximus
Рет қаралды 12 МЛН
This dad wins Halloween! 🎃💀
01:00
Justin Flom
Рет қаралды 43 МЛН
2 MAGIC SECRETS @denismagicshow @roman_magic
00:32
MasomkaMagic
Рет қаралды 23 МЛН
How Strong is Tin Foil? 💪
00:25
Brianna
Рет қаралды 39 МЛН
WAIYALUSA MEC UYU BLESSINGS LAZALIO - ANTHU AKUFUKULA ZOBISIKA.
8:43
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 4,6 М.
COMRADE NTANYIWA PA LIMPOMPO FM - 1.2 BILLION YAPITA
22:58
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 21 М.
BROTHER SALLO  MAYANKHULIDWE OMANGA AWA?  MPAKA NKHONDO?
20:17
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 6 М.
AKUKAKHALA KU NDENDE ZA 53 CHIFUKWA CHOKUPHA AMUNA AWO PROF. MUMBA.
11:04
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 1,9 М.
BON KALINDO *THE DC* - 31/10/2024
15:36
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 22 М.
AMUPANIKIZA NDIMAFUNSO UYU ANABEL NTALIMANJA TEMBO
30:00
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 6 М.
REAL 3D brush can draw grass Life Hack #shorts #lifehacks
00:42
MrMaximus
Рет қаралды 12 МЛН