Palibe chimene akuyankhula uyu angozinyenga......amalawi ndiomwe atazaweluze pa tsiku lovota
@CyprianoSandalamu4 ай бұрын
Chakwera adzawina, pali zifukwa zingapo,Inu adpp mukadagwilizana ndi Nakhumwa uja osachotsa adausi,ajefrey,auladi mussa,asonda ndi ena, chifukwa anthu amenewa atenga masupporters so ndye kuonetsa kuti number yomwe idali ku DPP idachepetsedwa ndi anthu amenewa, amene onse apts ku mcp ndye DPP sidzawina ndipo mudziwe zimenezi
@MACFARLANEMULENGA4 ай бұрын
Osati a Malawi, uziti iweyo wava. Nanga ine ngati mMalawi zikundikhudza?
@Slyvia-uu3wc4 ай бұрын
Munthu amene akumuyikila kumbuyo chakwera ameneyo ndi watsala pang'ono kufa
@Slyvia-uu3wc4 ай бұрын
Anawopsa ndi kamudzu banda achakwera ndindaninso bavayo balukundu pa achakwera
@LuciusPatrick-f2c4 ай бұрын
Chakwera ndi wakuba ndi mec. zayeseren kubera kt muzaone kt zizatha bwanj chakwera ndi galu komaso chitsiru chamunthu chomwe akuziwa ndi kubas
@AndersonBishop-i2t4 ай бұрын
Amenewo awineso mukufuna kupha amalawi chani mutulukamo boma inuo muonaso ngat fetelezer ali pa 100pin ndie kuti muwineso zazafika pa 200,000 sugar 10pin Kaye kusamva za munthu chakwera, boma losangalala nduna zokha ndi family ya chakwera komas ndi nduna zawo mcp yawonjeza kudula zinthu
@DjshukulanGift4 ай бұрын
.mulungu wazatheka bwaji akuchosa oamenepo apo ayi uzachoka mowawa
@SheenahMwalabu-iz3pr4 ай бұрын
Ineyo kugona osamvera program yi ndekuti sindilota 😅😅 komatu kudzngowinanso mcp 2025 ndeyosagwira cz ndendinaituruka ndikusailotakonso. Ambuye atithandize anthu awa achoke basi
@rashidadan25334 ай бұрын
Inshort , MCP under tonse alliance has done nothing to Malawi since they won , Chakwela is out of nonsense and not allowed to procide . Chakwela is the fuiliar and coward.
@usumanidaudi4 ай бұрын
ACB ndi yokuba yakumarawi zawusiru matha chizuma ndi chisiru bwanji chito yanji yimene akugwira
@martinnyirongo28924 ай бұрын
Amalawi kuvotera mcp eeee feteleza azafika pa 300,000 and mzadya nyika mpaka 2030
@AleksaWilliams-qc6cn4 ай бұрын
Mulungu wathu ndiwamoyo ndipo sazalora mazanamzana a anthu azivutika kamba ka anthu 10 no