Indeed the Vice President, you are a brilliant, humble and wise person. As you help our President in governing Malawi, may the Almighty God help you and give you all the desires of your heart.
@tiflo20125 ай бұрын
One wise statement that caught my attention " ine ndinalowa mmalo mwa a Chilima...when he died, was he out or inside Alliance? " Wakumva wamva...yankho la straight 🔥 👌 💯
@UchizieFMtemela4 ай бұрын
Brilliant Usi 🔥🔥🔥🔥🔥
@AbwinoBanda2 ай бұрын
Msiska interview yakukulira iyi....bravo Dr usi
@WistedFole5 ай бұрын
Very familiar with people, may god bless you Dr usi
@elizabethbalalasdp7215 ай бұрын
Of course I don't underate Wonder Msiska in this interview! He is also very challenging and well composed!! Bravo Mr Msiska!
@KhaliluGiftMasala5 ай бұрын
I have learned something from Michael usi akuti ukakhala tsogoleri don't rush kuyankhula because as being a leader you need kukonza ma speech olakwakika kwa okutsatira
@obrienalfkarmaysir93725 ай бұрын
Facts
@SHABILUKAZEMBE5 ай бұрын
Ngat yudasi adapheleka yesu kulibwanji Dr usi
@MustaphaChimangeni5 ай бұрын
Wonder you should have given this interview Brian banda
@elizabethbalalasdp7215 ай бұрын
I loved so much Usi when he was abambo a Sikono in ADRA Koma pano mmmmmmm ayi, I can't take him on board as the VP of Malawi! Zinthuzi aliyense amakhala ndi malo ake choondeee!
@WahiedaWadie5 ай бұрын
Young talent vp i salute you kuyankha mopanda mantha komanso chimene mukudziwa odya zake alibe mulandu
@StevenMjMbama5 ай бұрын
Now I love this guy he is doing anything for malawians achakwela aziyamiza ma vp awoo ndi a nzelu koma achakwela musamavele mafana anu akuchipani kwanu plz ma members aku mcp ndi nsanje kwambili komanso amadalila kwambili zaufiti but good job Mr usi under the president chakwela
@frankiechasokoneza58025 ай бұрын
@@StevenMjMbama bwana opoila ndi Chakwerayo he don't have leadership
@assankamwendo8525 ай бұрын
DR Michael Usi is a man with wisdom and a philosopher.proud of you VP
@SiphamandlaNcaphayi3 ай бұрын
Good interview and we learnt a lot
@yotamumkandawire-k8j4 ай бұрын
Wise and humble leader. God bless you.
@Prianka5675 ай бұрын
Woow Manga you are blessed ,wishing to learn more from you.very good answers with examples without any complications
@stevemtambalika5 ай бұрын
Uyu amafunika Brain banda sanyengerela mafunso.usi adamupeleka skc.wamagazi mmanja iwe
@SaulosiPhiri-e9f5 ай бұрын
Bravo wander msisha olive you big
@frankiechasokoneza58025 ай бұрын
Exclusive iyi imafunika Bryan Banda uyu akanaithawa interview imeneyi ndithu
@dennissawamba29395 ай бұрын
Anakanika kale adamawa nda nzeru osat masewela
@KUCHEKATULI5 ай бұрын
Brian Banda ake aja adalephela kwa fusa ma a m'sonda........ Amwene kwa onse panopa amene akumafusa ma funso omvekandiwa nkazi uja amene amampanga interview Winiko uja
@StewartMustafa5 ай бұрын
Wonder sangamukwanitse Dr Usi. Olo Brian Banda amanama koma Britain banda amayesesa
@dennissawamba29395 ай бұрын
Uyuyu simbuli chomwe amapanga amachidziwa 🙌
@fabianochimenya72315 ай бұрын
Brilliant Dr Usi, am encouraged with your sentments
@PhilomenaChikabadwa-dt6vy5 ай бұрын
Keep it up sir.Mulungu amadziwa zonse,
@ManeyBen5 ай бұрын
Thanks Mr VP for your clarification
@ChifuniroKalanu2 ай бұрын
rsz
@peterchiutsi5 ай бұрын
Vuto la a Malawi ndiloti when it comes to Presidency, we always miss the right person to be the President guys Micheal Usi hes has the characters of a right president and he can deliver the gest kungoti a Malawi timangomuona pa angle yolakwika munthuyi sinthila kuwili guys ndimunthu oyenela uyuyu Lets believe him and give him a chance
Awa ndebolaso kalindo straight to the point osati kulambalalaso apa.
@obrienalfkarmaysir93725 ай бұрын
Watching from Rosenberg Germany
@CliveWhitman-rr9ew5 ай бұрын
Politician is not a person that will give u a direct response in most cases...
@sandersonmayuni75575 ай бұрын
Dr Usi is unifying leader who don't want to injure the divided party. His agenda is to bring unity In the party. UTM should nurture the wisdom in their Leader.
Michael Usi. you are number 1,ndiwe ochenjera kwambiri
@innocentchiuja5 ай бұрын
Akatundu
@FatimaSande-lb1hd5 ай бұрын
Am getting your points mr vp and you are a wise person big up mr usi❤❤❤❤❤
@DeliaKaduya5 ай бұрын
Chilima anakukondani a Usi ndi mtima wake onse, koma inuyo chikondi chanu chinali cha mitala, that's why nzanu uja atafa mumapanga ma celebration ndi Chakwera wanuyo ku state house, olakwa ndi Chilima mwina pokukondani 😢 still in our heart SKC 😭😭😭😭😭
@DanielKaombe-im3pr5 ай бұрын
Two mistakes made by chilima 1. Making alliance with MCP 2. Trusting Michael Usi
@DeliaKaduya5 ай бұрын
@@DanielKaombe-im3pr ndipo that's a big mistake
@KarongaDiocese5 ай бұрын
Ur seeing this in a small minded point of view
@JuvenileDebwe-bv8ow5 ай бұрын
Ndipo udindowu ankausakasaka ndipo zikuoneka kuti njira ayisaka kuti afikepo basi ndipo panopo is happy
@happychavula44695 ай бұрын
Mwanena chilungamo
@PrinceMittochi5 ай бұрын
Watching from Vietnam ..Ooh my beloved Malawi
@EdwardZuze-r7w3 ай бұрын
how are you there bra
@MabvutoMichaelPanagona5 ай бұрын
Watching from south Africa
@hopesato5 ай бұрын
Leading between the lines, and ofcoarse without forgetting about the plane crush... Usi is with MCP
@AnnieNkhata-q9j5 ай бұрын
Dr Usi is wise lets give him support 🙏
@MustaphaChimangeni5 ай бұрын
Wander wachepa nayotchitiyi Brian banda is very capable
@OdalaaSifa-wj3vw5 ай бұрын
This guy is in Very Serious Situation. If he won't reveal his Intentions avutika Mumtima hvy
@LouisMisha4 ай бұрын
Bwana vice president pempho langa lakuti pitirizani kupanga zabwino ndi maganizo okonda anthu osati wina akusokonezeni kaamba ka udindo wanu please try to do good things koma moopa Mulungu poti iye ndiye mwini zonse. ❤ Love your country ❤❤❤❤ monga tonse ndife anthu amodzi posayang'ana mbali kapena mtundu wa anthu kuti uyu ndiwakumpoto kapena chigawo chapakati kapenaso uyu ndiwakumwera ai, inu ndinu kholo la a Malawi wonse ndipo mukhale ngati m'mayi amene adabala ana amapasa amagona pakati chagada kuti mwana wina akafuna kuyamwa ayamwe osagonera mbali imodzimodzi ai kumbukirani kuti odyetsa anthu wonse ndinu ndipo tikunena panopa Thiko ulindiinu.
@JuvenileDebwe-bv8ow5 ай бұрын
Don't forget that UTM wants to be independent
@JohnWyson-z3x4 ай бұрын
High time to hear that
@stelladolizyi5 ай бұрын
Izi akadakhala Brian ❤
@SiphamandlaNcaphayi3 ай бұрын
Bravo hon usi
@MustafaAbdullah-pb5zv5 ай бұрын
Genius Michael usi bravo
@goldenbanda67575 ай бұрын
God bless Mr Vp
@MargaretLindaChikapa-Phiri4 ай бұрын
I repeat, Dr Usi ndakunyadirani, ufulu tilinawo koma tsopano what remains now - is the battle against disease, poverty and discipline.
@MarthaTwisaSelemani4 ай бұрын
Or ka minute of silence in honour of Chief odya naye mtedza, taaaa!
@DonsondouglasKim5 ай бұрын
Munapereka bwana wanu Dr utsi, nkulakwa kodi kutero, akanakhala Brian Banda tu akanafutsa limenelo
@RobertChimenya5 ай бұрын
Usi Ali ngati Judahs skaliyoti adamupereka SKC koma anva ululu owopsa
@innocentmagaleta4925 ай бұрын
I think it is you bra uli judahs
@GiftKumbweza5 ай бұрын
Komatu mmayankhula ngati muli ndi umboni.Just guessing but kuyankhula as of you have concrete evidence
@Rometcma5 ай бұрын
Concrete evidence iposele SKC adamwalila😂😂😂😂
@jnrsibonelo94445 ай бұрын
But this guy is trying to cover himself in terms of answering questions.😢 My point of view this Usi is an Mcp member not Utm🤞powers can make people completely change. Let's meet next year bwana Usi mulungu akuona chilichose atimenyera nkhondo🙏 muzaululika.....
@modestamhango77375 ай бұрын
Amen. Zoona.
@kondwanimwafulirwa-jh4hj5 ай бұрын
Genius Usi
@CosmasMaluwah-mh4ji5 ай бұрын
Dr Usi mukumubalalisa Wonder
@quincyswart18845 ай бұрын
Ndipo nde wabalalikiratu😂
@ThoccoPearson5 ай бұрын
@@quincyswart1884wabalarika kale koyambilirako ine zandimvekera mokolana kolana 🙌🏻🙌🏻🙌🏻😳
@quincyswart18845 ай бұрын
Aliyese mayankho aziwapeza yekha apo sanamvetse 🤣🤣
@georgezaya10715 ай бұрын
Usi just do your job but don't forget where you come from
@elizabethbalalasdp7215 ай бұрын
Brian Banda would have been the best host in this Times Exclusive interview!
@unfortunatelyfoikencharles60925 ай бұрын
Ndalamazo zikupelekedwa lelo nthawi yonseyi mmene Malawi wakhala aku kulukutika ndi umphawi zidali kuti Don't play with our mind,we need serious leaders and leadership So Michael wayamba bwino do not change,please we recognize you
@CeciliaNthenda5 ай бұрын
Ife talandira kale
@nicholasshema90165 ай бұрын
I would feel gud if Wander ask him about v investigation about v crash of Airplane VT MW we ready to hear
@LawrencePhiri-tt9zq5 ай бұрын
Watching form Lusaka Zambia 🇿🇲 big up vp of Malawi 🇲🇼
@yasitafuphiri-nw2he5 ай бұрын
Wonder wachepa nazo Usi si size yako
@AbelBlack-f9q5 ай бұрын
I thought you will help the Nation bwana
@tamalangoma27655 ай бұрын
My VP
@simeonwilliamsbanda31324 ай бұрын
This man has very clear points and feelings before towards his country. He has points step by step well analysised
@carlossadimba5955 ай бұрын
❤❤ our new virce president Dr micheal Usi......😊😊
@jamiel-gr9ny5 ай бұрын
Kma ndfe anthu anu bwana mukanamatiyankha kut tidxiwe
@OsmanMailosi5 ай бұрын
He should not confuse utm people he is mcp member for long time. People will meet him at utm convetion leave him adzatha ngati curtain
@Chipilirosafalaoh-hl4vz5 ай бұрын
Usi ur brilliant but don't be deceived with this so called position..... build ur own party aise
@Al-BaakirBoysSecondarySchool5 ай бұрын
Very Interesting. Sitinati
@MicyThobve3 ай бұрын
U r true veep in mw
@isabelmartin75675 ай бұрын
Udasi miss Usi Munthu Oipa zedi 😢😢😢
@MargaretLindaChikapa-Phiri4 ай бұрын
Ndakunyadirani a Vice President. Mwanena zowona.. Mudziko muno anthu ndawona kuti zowonadi wanthu akuvutika ndiposo so ma schools Mudziko muno achepa ndiposo atalikirana kwambili. Tinthandizenipo.
@StanleyMayenda5 ай бұрын
Inuyo Amalawi ndinu mbuzi ..Kodi ndale NDI uzimu zikugwizana bwanji .mfiti Za wathu inu
@aggiemlotha12085 ай бұрын
Onaa nzeruu 🎉!!
@brightbwanali25095 ай бұрын
Bwana Usi mukuyankha bwino. And apapa musamukakamize kuti ayankhe zopanda umboni. Usi sakugwira ntchito ngati wa MCP. Michael Usi ndi m'malawi, akuyenela kugwira ntchito paliponse. Let's not mixup things guys. MCP ndi chipani, UTM ndi chipansinso. Amalawi tiyeni tikule mu zochitika zathu. MCP si malawi. Let' him work for malawian's sakugwirila ntchito MCP
@iangondwe68575 ай бұрын
mr vice president and mr president himself all the best God help you
@NumbDee5 ай бұрын
Koma nzeru zilimo APM my vote
@FrancisDominic-w1s5 ай бұрын
Chief emweyo sizikumveka akurankhurazo
@GloriaWalawala5 ай бұрын
Ndinu 1 , munthu wa mzeru our VP🎉
@MakuLuni-si1wd4 ай бұрын
VIVA USSI
@ClementChimombo5 ай бұрын
Big up bwana vp
@madalitsomakawa97085 ай бұрын
Atsogo ka background music ko sikali bwino
@StewartMustafa5 ай бұрын
Usi u r the best if u don't interact with MCP Party. Coz MCP no matter what MCP can do. Prease be wise
@EthelKubalasa5 ай бұрын
This man is indecisive, wadziika pa mpani sakudziwa kuti aliku UTM or MCP .
@CharityMhone-uk9ym5 ай бұрын
Kopenga anga nanga ngati chilima amakukonda bwanji osamulira anzako...chitsiro iwe chilima wagona kuchikangawa iwe busy kusangalala ndi mr chifunga...wait you wl follow chilima osachenjerapo apa😮😮
@BehindThecamera-xo1qg5 ай бұрын
Akulephera kuyakha mafunso uyu
@Janet-y5j5 ай бұрын
Usi mulungu akuone😭😭😭😭😭😭
@BeynoMike5 ай бұрын
Michael your number one, mupitilize because anthu ena akumakudelerani dada
@realsu78165 ай бұрын
You may have full support if you just play ur cards well Mr VP....
@AzaliahEvessDakahDakahChangach4 ай бұрын
Eeeeh km tinva zithu kumalawi tilipano tidziwe which is truth about this issue
@mccarthykonyani98665 ай бұрын
He is wise
@PatrickMbewe-pf5fp5 ай бұрын
Never judge a book by its cover
@IshumaelPhiri-v7d4 ай бұрын
Bwana chilungamo ch anu chikutsogololeni inu a Presidentmunthuyu akuthandizani
@unfortunatelyfoikencharles60925 ай бұрын
You deserve Michael,let's hold hands malawians let's support Michael