AZIBUSA A CCAP ANAKAKUMANA NDI CHAKWERA KU STATE HOUSE AJA A NKHOMA SYNOD NDIPO AKAMBILANAKO IZI

  Рет қаралды 1,752

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 32
@DawoodPongolan
@DawoodPongolan Күн бұрын
Funso mkumati kodi inuyo achakwela Mutu wanu wamagwira bwino bwino? Umenewo ndi mkuluwiko Tikuziwa chomwe mukutanthauza Mchakuti ifeyo tipiliza kukhala akapolo anu,koma siyani kulota Mulungu wake siyemwe tikumupembedza ifeyu ayi Iwalani ndinthu. Mulungu wanthu ndiwamoyo ndipo sagona, ndiposo sangayankhe mapephelo anu inu
@Khadija-q9r
@Khadija-q9r Күн бұрын
Ameen
@bensonmanda235
@bensonmanda235 Күн бұрын
Blantyre Synod - Kumwera; Nkhoma Synod - Pakati Livingstonia Synod - Ku Mpoto
@MalawiTrendsTV
@MalawiTrendsTV Күн бұрын
Noted with thanks
@WilliamNhlane-fd9hi
@WilliamNhlane-fd9hi Күн бұрын
Nkhoma synod ndi Livingston , sakuthandiza a Malawi koma mcp ,koma Bantyre Synod sikugawa ma sweet koma kuimilira amalawi .
@EliasLungo
@EliasLungo Күн бұрын
Inusotu mukutichitisa manyazi azibusa athu a CCAP ankhoma synod mwanva, m'malo moti mumuwuze zoona m'tsogoleri wadziko pamene pasakuyenda bwinopo, inu basi mukungoti zilibwino.
@IgnacioChibwana-n1v
@IgnacioChibwana-n1v Күн бұрын
Azibusa okhutitsa mimba zao anthu osakonda anthu ao,panopa katundu akukwera chakudya kulibe ndalama ikusowa azibusa oipa kwambiri Mulungu amene amamutumikirayo awankhululukire
@FexonSwamboko
@FexonSwamboko Күн бұрын
Mbuzi za anthu azibusa malawi alitengera pa ging, o komatu lero si mawa azakhumudwa akapamba amenewa
@YusufMaulidi-b2c
@YusufMaulidi-b2c Күн бұрын
Ngati akunenadi zoona zakatangale ayambe iyeyo kukazipereka ku police
@AmosJere-ir4zr
@AmosJere-ir4zr Күн бұрын
Onse makape azibusa ndi chakwera wawoyo ndipo mitu yawo sikugwira
@YusufMaulidi-b2c
@YusufMaulidi-b2c Күн бұрын
Pano azibusa mudziwe izi ,ife amalawi sitikufuna mapemphero tikufuna ife ndi utsogoleri wabwino kuti miyoyo yathu isinthe
@shepherdkingston
@shepherdkingston Күн бұрын
azibusa nonse mutuwawo kukonda ndalama
@AdamJames-x7x
@AdamJames-x7x Күн бұрын
😂😂😂😂😂😂Nzeru alibe anthu awa anapita kukatapako basi kkkkk
@isaaczuze
@isaaczuze Күн бұрын
Azibusa adyera
@MalizeniOliviaBridan
@MalizeniOliviaBridan Күн бұрын
Ankhoma sinodi ndadyera amakapepha ndalama misonkho yamalawi,mphingo umeneu sukunva chisoni ndikulila kwamalawi kumalimbikitsa chakwerayo kunzunza amalawi koma zoona mpingo mkukhalapasi mkumapangana zokayamikila mbava imene
@alexsumani6823
@alexsumani6823 Күн бұрын
azibusa awawa kutheka kuti Sali mu gulu lija amati adzozedwa
@marypatriciamakuru226
@marypatriciamakuru226 Күн бұрын
Nkhoma synod ndi ya dyeta
@ChrissyBenito
@ChrissyBenito Күн бұрын
Ayi imeneyo ndiye mfundo ya igwe yosagwila apitilizeso kachikena zaka five tikhala moyo??????
@KelvnGrin
@KelvnGrin Күн бұрын
Kkkk Jesus is about to come chilungamo akuchiziwa mulungu ngati kumwamba kukukondwera ndi utsogoleri wawo apitilila pasept koma I don't believe
@AngolaChinga
@AngolaChinga Күн бұрын
Bro kumenek nde kuyankhula kwa zelu kwa zelu
@crytoniegrantliffa2431
@crytoniegrantliffa2431 Күн бұрын
Bwana chakwera ndinu munthu wosadziwa ndithu mukanakhala kuti mumadziwa mukanadziwa mmene ife tikuvera
@YusufMaulidi-b2c
@YusufMaulidi-b2c Күн бұрын
Nanga munaziona kuti watchito akumumanga bwana wake ,mukunamiza zizukulu zanu ?
@isaaczuze
@isaaczuze Күн бұрын
Chisilu cha munthu ichi ....galu ameneyi achoke azipita kwawo Kwa akabudula .....mbuzi imeneyi
@LuwizaChika
@LuwizaChika Күн бұрын
Akunena ifeyo kuti akapolo galu ameneyi
@mercymalenga1884
@mercymalenga1884 Күн бұрын
Livingston synod ndi Ku North
@JTUPHIRI
@JTUPHIRI Күн бұрын
Mwini wake chakwerayo ananena ekha kuti term ikuthayi yandilaka, ndimafinya zithupsa, ndiye mutnhu wina ayamikila bwanjiiiiii?
@Jafari-s3c
@Jafari-s3c Күн бұрын
Iwe usamaname ma Synod alipo atatu, nkhoma synod, livingstonia synod komaso Blantyre synod, livingstonia ndiya ku kumpoto pls
@alexsumani6823
@alexsumani6823 Күн бұрын
mhuuuu ayi zikomo
@Noel-y6t
@Noel-y6t Күн бұрын
Zako izo udzionera
@FexonSwamboko
@FexonSwamboko Күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@YusufMaulidi-b2c
@YusufMaulidi-b2c Күн бұрын
Pano azibusa mudziwe izi ,ife amalawi sitikufuna mapemphero tikufuna ife ndi utsogoleri wabwino kuti miyoyo yathu isinthe
小丑教训坏蛋 #小丑 #天使 #shorts
00:49
好人小丑
Рет қаралды 54 МЛН
Support each other🤝
00:31
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 81 МЛН
The Best Band 😅 #toshleh #viralshort
00:11
Toshleh
Рет қаралды 22 МЛН
小丑教训坏蛋 #小丑 #天使 #shorts
00:49
好人小丑
Рет қаралды 54 МЛН