Bwerani bwerani bwerani!!!! Best ever Tv in Malawi
@cossaphyxo2 күн бұрын
Bakili muluzi TV fans let's gather here 🎉🎉🎉
@KarimTapyMshanga-kd1vzКүн бұрын
Noted bigg man
@MikeLodziКүн бұрын
we are together
@ChimwemweRajab23 сағат бұрын
Mumuuze kachaje asatitengere kukatiyesa boss
@PeaceNkhomaКүн бұрын
You are awesome, zangovuta kut anthu samakumvesesani komanso popeza mukupanganso HISTORY. yah kusongoloku muzakhala BEST TEACHER to them pano kwaife tikuphunzira😊
@MdalaJuma-w4jКүн бұрын
Bakili muluzi TV 📺 telling ase everything you're my best teacher
@YasinterKapinga2 күн бұрын
Ndalawilila gululu ndi bakili tv history is the best teacher indeed brother 🎉🎉🎉🎉
@FavourGodfreyMw2 күн бұрын
Best video ndii mbali yanu bwana zikuyenela kutelo kumene
@kelvinchola739Күн бұрын
Mmmmm my best TV channel in the world thas Bakili Muluzi TV, is also the one tells me about President's who rule Zambia 🇿🇲. Malawi yasochela tsopano pomanganso munthu woyamba kupanga phone payekha dziko lonse lapansi mmalawian. Bakili Muluzi TV am watching from Zambia 🇿🇲🇿🇲
@DominicNantowa-t4d2 күн бұрын
Uwu ndi nkango ukangotuluka nduna zonse zimapinda michila❤❤❤Bakili muluzi TV
@Mervic-vm8eoКүн бұрын
Ndipo or chakwerayo amapinda Kaye muchira wake😂😂😂😂😂
@MandalaChaonaКүн бұрын
😂😂😂😂😂 Zoona zake kupindiradi michira
@MandalaChaonaКүн бұрын
Koma Chakwera eeeeee man mwasakaza . Ndipo zakukanikani. Bwanji osangotula pansi Udindowo mukufunanso Chani?? Eeeeee Ng'ona ndi Ng'ona 🐊🐊🐊🐊. Weldone Brother from BAKILI MULUZI TV the best teacher ever ✍️❤️ Sta safe ✊✊ Stay blessed 🙏🙏 Be protected 🙏🙏✊ You are Loved ❤❤ever
My KZbin channel I believe in malawi !! Keep on updating us brother man, I'm here to stay brother man!!
@MuhammadSamson-yz1klКүн бұрын
Thank you my brother ❤❤ koma lero nde kachepa umandisangalatsa ukamalakhura
@actuarialscience22832 күн бұрын
John Tembo ndi banja lawo (Kadzamira Cecilia) Akhala akuyesesa kupha democracy ku Malawi. Leroli tili ndi umboni kuti mbewu ya John Tembo, Anabel Mtalimanja, ikuyesetsa kuti ifufute democracy. A Malawi musamale ndi mbewu yoipa ya John Tembo.
@user-Grant2602 күн бұрын
Watching from Venezuela in Caracas 🇻🇪
@IdrisahChumaКүн бұрын
Za 50 million munatiuza chisilu chamelachi chisanayankhule apa chakambaso zomwezo nde enanu simukumvesa pati?? Bakili muluzi tv the best TV in Malawi never give up
@ChristinaMdezaКүн бұрын
Kom ndiye nkhani tu yathera pa njira ❤❤
@EmmanuelGordon-q9sКүн бұрын
Bakili Muluzi Tv we love you so much coz mumatiunikila koma awaso a opposition osawatenga kut iwo ngolondola Nawo azasintha..
@MonicaBvumbweКүн бұрын
Bakili muluzi tv number one🎉🎉
@GodfreyGraciano2 күн бұрын
Proud of you bro ❤❤❤🎉 continue 👏👏👏👏
@MaulanaIriyasaКүн бұрын
History is the best teacher boma longodzadza ndi an thu onama McP sindidzayiyiwala
@GiftMhone-b6g2 күн бұрын
History is indeed a best teacher
@Mwaiphiri-v3dКүн бұрын
Here we are, Bakili muluzi tv's fans
@LETUSCHIPHUPHUКүн бұрын
Much appreciated brother tikavota ndth molondola ❤ tichose nyansizi
@DawoodIssah-mp1yiКүн бұрын
Zitsiru zosadziwa kuyendetsa dziko ngongole basi mpaka liti zimenezi abale, Inu ndi phumpani basi onyadira ngongole demet 😢😢😢
@JohnstonNyirenda-zw6jdКүн бұрын
Ine kachaje ndiniawona ngati ndi munthu wanzeru kalero koma ndimbuli yophunzira 😢fuseki
@SafariBvumbweКүн бұрын
Bwerani zamveni kuno, best tv ever
@JosephIsaac-s1cКүн бұрын
I will follow BM TV entire life ❤❤❤❤❤❤❤❤
@AbdulNyambiКүн бұрын
U are number one bakili muluzi tv mumatiyimilila God bless you
@ernestsanjira7859Күн бұрын
Mukazaona nd Kumva Bambo kuudza Banja Lake Kuti Wayenda Wapenga pa Chakudya plus Kunenana kut madibwe azichitka kamodzi pa day Mmalo mwa katatu muzangodziwa kuti Bambo ameneyu ndi OPEPERA Ndiposo Walephera Udindo wake. Zikomo Kumpando.
@GiftNorton-s3gКүн бұрын
Long live mfumu yathu bakili muluzi TV history is a best teacher
@AdamKay-q1lКүн бұрын
Bakili muluzi TV ❤❤❤❤ truth come out don't give up we are with you God bless you 💖🙏🙏🙏
@DennisSokoKozentani-w1kКүн бұрын
Akuluakulu! Munthu ngati sudziwa history ndiwe wamisala.
@webstermbewe83952 күн бұрын
We have been waiting for this continue to give us the best analysis of what is happening around the world
Bakili Tv keep on updating us for what this useless government is doing,,aMalawi tatopa naloboma iri
@SkeffaKaifa123Күн бұрын
Best TV bakili muluzi ❤
@LeyvanSamuel-c2lКүн бұрын
Live from South Africa Johannesburg
@ASEDIRABSONКүн бұрын
Watching from Eastern cape south africa
@HenryManda-c4iКүн бұрын
The only true TV in Malawi 🔥🔥🔥
@MillieMalakam11 сағат бұрын
God ahead u my brother I love you so much my brother
@MikeLodziКүн бұрын
history is the best teacher komatu kenaka tizangomva anthu nonse achigawo chapakati samukilani kumpoto coz central religion tabweza ngongole kwa azungu mmmmmmm kapinjonjo area we are watching
@christophermkhize1991Күн бұрын
Our best TV bakili muluzi TV home of history
@Mohammed-sk1fy2 күн бұрын
Km Chaka Chino ayaluka akanganya amenewa,,..... The Home Of History Bakili Muluz tv ❤❤❤❤❤
@franciskameko2586Күн бұрын
Zomwe zupanga MCP akuvutika nd Kachaje pa ma press briefing😂😂😂 munthuyi ngosalakwa
@ELIJAHNgambi12 сағат бұрын
Inuyo ndi akamuna bakili muluz tv🎉🎉🎉
@LETUSCHIPHUPHUКүн бұрын
I would love you shall be awarded for the great job to say mosaphyatila muli nd mzeru zakuya ndthu Mulungu apitilize kukhala nano nthaw zonse amen
@ChiccoJaliКүн бұрын
All their best Bakili Muluzi TV
@AngolanChingaКүн бұрын
Yhooo ndachedwa kuona lelo bakili muludzi tv
@ThokoKamasulaКүн бұрын
History is the best teacher 😅😅
@ShasimiyaRajabu2 күн бұрын
Inuyo munabwera kuzakhala BG mny💪🤜🤜🤜
@AdamMakalaКүн бұрын
Bas sipitilizano abakili muluzi tv❤❤❤❤
@ChikhaondIssahКүн бұрын
Bakili muluzi tv number one
@OretarbadrBwanaliКүн бұрын
❤❤❤❤❤❤ Uyu akuyankhula yu nd osangalatsq
@JeanBanda-zy6wuКүн бұрын
Am.here my best TV ever ❤❤❤❤
@GodfreyKamphiripiriКүн бұрын
❤❤❤❤❤Best TV bakili muluzi
@IshmaelDenzoКүн бұрын
History is best teacher 🎉🎉
@Moses51Күн бұрын
only best TV bakili muluzi TV chulungamo poyela osawopa until chikangawa chibwele poyela
@YamikaniPhiri-f1tКүн бұрын
Watching from Lusaka Zambia
@KimuWasi2 күн бұрын
Ndinu maso athu boss owonera pa taaaaali kwambir🎉
@JamesImranКүн бұрын
History is best teacher 😊😅😅
@daudsagonaКүн бұрын
brother ndinu akatundu mumatha wallah mulungu zikudalitsni mpak kale kale
@EmmanuelGasiten-fo5drКүн бұрын
My best TV ever. BMTV
@HopefulCoralReef-tx4vx2 күн бұрын
Ulemu wanu big God bless you ❤❤❤
@ChimwemweSaukaКүн бұрын
Welcome brother BMTV
@Augustinoblessings2 күн бұрын
Big welcome back ❤❤❤❤❤ Bakili muluzi tv izooooo umakwana iweyo
@Dee-h7c13 сағат бұрын
LONG LIVE BAKILI MULUZI TV 🎉🎉🎉🎉
@hanifahmponda8711Күн бұрын
Aaa ulemu wanu otsakhulipilila BM TV chetsilu cha MCP inefe olo potsankhidwa anthu ofufudza za ndege ife kut tidziwe anthuwo ndinani tinamvela bm TV ndipamene tidadziwa kuti ndi anthu a mcp ndiabwedzi achakwela thas why NAMIWA NDEYETSO ATAMVA ANTHU ALI KATIMU NAYETSO WADZITAYA ASAFELE FUNGO NDALAMA AKUDYA CHIMWENDO God bless you and family's