Michael Ussi the traitor Komabe manyazi akukwapule
@InnocentBanda-ze8de2 сағат бұрын
Kumenko ndiyekuyakhura brother ❤UTM 🤝
@MandalaChaonaСағат бұрын
May His Soul Rest In Eternal Peace ✝️✝️✝️✝️. Mulungu wathu wamoyo tiululireni zonse zili zobisika pa imfa ya Anthu Onse anafera Ku Chikangawa.
@TriciaMalikebuСағат бұрын
Zoonadi, well spoken. Ndipo osati kungolembatu m’bukhu basi kuthera pompo. Malawi needs action
@BLUR-p6c2 сағат бұрын
Kwanga ndikumulila skc
@abgi.doctor.august2 сағат бұрын
Mulungu oziwa Chilungamo Kwa anthu amene amaziona kuti ndi ochenjera Kwa anthu anzao Chauta Mulungu wamphamvuzonse pitilizani kuulura anthu amene anapha Dr Saulos Chilima Ndi Anthu 8 kuchikangawa history is the best tikudikirabe kuti mu 2025 onse muzawayike poyera tikudziwa kuti mukuzera mwa munthu wina wake amene akutengedwa ngati ndi olakwa koma chili chinsisi Cha Inu yehova kuti anthu oipawo abwere poyera anene okha kuti ndife tinampha anthu aja zikomo Chauta pitilizani kuwapasa chiusiro chositha mizimu ya abalewa iunse mumtendere 🙏🙏
@frankmanda63954 минут бұрын
Nkhunda osauluka mizimu yqkwiya
@omarlux3434Сағат бұрын
Kuyakhula kwazelu uku anakhalapo nose mungoti ine ine muli zi musiyeni manganya anamusakha ekha
Wa camera wanuyi mumuphumzitse kagwilidwe Ka camera Koma so m’mene timajambulira 😂
@kingsolo696339 минут бұрын
Koma camera yatipwetekesa maso, kaya camera man amavina kaya
@corretabanda768559 минут бұрын
Usi kukhala pafupi ndi Mary yikhale nkhani?? Ukanasankha title yabwino not this one. We don't care about Usi. Sindimvelanso to the end
@LucyThambo9 минут бұрын
Mau ogwira mtima
@AchinaKellz2 сағат бұрын
Usi amakatani bwezi lachakwera
@DoreenSankhoСағат бұрын
Koma chikangawa anapita kumwambou
@MadalitsoMaungu-z7sСағат бұрын
😭😭😭😭😭😭
@chikamandala7436Сағат бұрын
Eeeh Kuli ntchito
@P.BilaliСағат бұрын
Koma yeah
@GeshoMwakitwile2 сағат бұрын
Mayi kaliat ngati Ali ndi chison pomwe ayi akuziwapo kanthu pa infa ya saulosi mayi woipa uyu
@EsnartGirivin2 сағат бұрын
Kodi anthu mukukhulupilila zandalezo A mcp aziyalutsatu okha kumunamizila kaliat ine siwachipani koma nkhaniyi ndiyongofuns kumuipitsila mbiri koma Mulungu sanalole ai mcp yangodziyalutsa kuti inapha chilimadi
@quoniemagalasi91232 сағат бұрын
The time u will understand Malawian politics, that will be the beginning of understanding that all what people are saying against Mai Kaliati are just fake (fubricated)
@MlecheFatchСағат бұрын
Nanu inu aaa😂😂😂
@SimonJesimaniСағат бұрын
A MCP bwanji kuganiza ngati nkhuku. Propaganda yomwe mukuchita will bring lightening to strike you all