Рет қаралды 8,497
On Nyasa VoiceBox, Mr. Abdull says that a good father never leaves the house to play games when there is no food at home. Similarly, a good leader should not go on a foreign trip for leisure while the country is facing numerous challenges.
Pa Nyasa VoiceBox, a Abdull akuti bambo wabwino samachoka panyumba kukasewera pomwe kulibe chakudya. Mtsogoleri wabwino sayenera kupita kudziko lina kukasangalala pamene dziko likukumana ndi mavuto ambiri.
#malawi