BLANTYRE NDILANDE A DR MICHAEL USI ATOKOTA🙌🙌🙌

  Рет қаралды 16,088

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 82
@JaphetSakala-pq4fl
@JaphetSakala-pq4fl Ай бұрын
Chilima samamupasa mpata omayenda motero
@MichaelNkhandwe
@MichaelNkhandwe Ай бұрын
Aziyenda ngati ndani? Mesa vice president wa dziko anali chilima uja
@MosesTangwe
@MosesTangwe Ай бұрын
Naweso jomo ameneyu ukuona ngati angakupangireni
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj Ай бұрын
Ressall wonkytwa nkuwilli ndi amanganya mulinkut mballi yanji mulli iweyyo bwanj sandege simunkamba awussi
@CatherineDesire
@CatherineDesire Ай бұрын
Ka Usi kakubwera ndi manfestaltu Hospel nkati🤸🤸🤸🤸
@ChisomoMsiska-oi2vg
@ChisomoMsiska-oi2vg Ай бұрын
Usi atha kuyendesa ziko bwino kwambiri muli nzeru president amafunika asanyengelere anthu ogwira nchito mu boma ndi amene amawononga zitukuko
@CharityChirwa-t1e
@CharityChirwa-t1e Ай бұрын
Ausi mukamapanga zanuzo muchepese kutchula Zina lachakwela chifukwa enafe tikamava zaazanuwo timaboweka and athu akudanananu chifukwa Mr chikangawa mukuntenga ngati mulungu gwilani tchito yamalawi osati ya MCP konsekotu nkufuna muwapangile kampeni kumwelako samalani zochitazanu
@AnitaLikado
@AnitaLikado Ай бұрын
Koma ndipo
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Ай бұрын
@@CharityChirwa-t1e ndi bwana ake inu mumati msanje bwanji
@WallyMsiska
@WallyMsiska Ай бұрын
USI saziwa kt MCP ikufuna kumugwirisa ntchito mawa azalira
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Ай бұрын
@@WallyMsiska ntchito yanji iye ali pa ntchito ya Boma ndiye Mcp ndi chipani chipani chimugwirisa ntchito bwanji muzisiyani ndale ndi dziko
@MemoryMbepula
@MemoryMbepula Ай бұрын
Anthu a MCP ndioyipa. Chilima olo tsiku limodzi kumupatsa mpata umenewo amvekere apule akuberani shine. Ambuye kumwambako expose what happened on that accident day
@ChikondiChauma-ib9pg
@ChikondiChauma-ib9pg Ай бұрын
Awa alibe fundo man zeruzo nza papepara degree and masters ndizao koma PA ground mamina
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 Ай бұрын
Ukamuuze chakwera Mr chikangawa kuti atiuze kuti za chilima zili pati mukatifusile
@CatherineDesire
@CatherineDesire Ай бұрын
🤣🤣🤣🤣 Ndrama iyo ndrama iyo yatengamalo pa Yudas
@JohnsonMaulana
@JohnsonMaulana Ай бұрын
Inu mubwelesa chitukuko ngt akulephera chakwera chikangawa😅
@FrancoKaunga-rq2ki
@FrancoKaunga-rq2ki Ай бұрын
Iweyo ndi chakwera munapha chilima! Wait you will leap what you saw.
@alexmkolongo3089
@alexmkolongo3089 Ай бұрын
Kodi ku immigration akuopako bwanji
@BornfaceMakamu
@BornfaceMakamu Ай бұрын
Chikangawa
@CatherineDesire
@CatherineDesire Ай бұрын
Wavala reflector Manganya?kodi ngongore paja yakwana season yake njomweyi?Usi ukukhara ngati ukubwera bho if you really mean it
@AmosScott-z9x
@AmosScott-z9x Ай бұрын
Pitani chigawo china mwatitopesa ku mwera kuno
@chisomotaika4479
@chisomotaika4479 Ай бұрын
U r making too much promises. Beware of tomorrow 👌
@yasitafuphiri-nw2he
@yasitafuphiri-nw2he Ай бұрын
Good clarification a VP on kupempha. Mmakwana
@patassonelucaszovuta3431
@patassonelucaszovuta3431 Ай бұрын
Tikufelanji
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift Ай бұрын
Pa 28 pan mukuchoka papando
@WakuMalawi
@WakuMalawi Ай бұрын
Imagine, your Father always speaking about borrowing to improve, and you still live in the Ghetto with no signs of improvement.
@ChikondiBanda-k5z
@ChikondiBanda-k5z Ай бұрын
Kumangot bwana😂
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift Ай бұрын
Son bwaji chilima uja sanapase chasi chomayenda yenda chochi?
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb Ай бұрын
Bambo asikono muwuzane ndi mr fit chikangawa Kut eti ndife zitsiru amalawi atidyera alibe nafe ntchito agalu lnu kupha chilima chosecho anakuyikani mipandoyo ndi lyeyo amanganya yudasi wafikapo mzayankha tsiku likubwera
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon Ай бұрын
UYU NDICHIFUKWA AMUSWA NDI MIYALA KU MPOTO, KOMASO A MALAWI MUSANYENGEKE NDI GALU MANGANYA UYU NGONGOLE SANGAKUPASENI ,MAKA KUMWERA IWALANI NGONGOLE NDI YA CHIGAWO CHA PAKATI, BOMA LASANKHO ILI ANGOFUNA KUKUGWIRITSANI NTCHITO AMALAWI MULIBE NZERU SIMUCHEDWA KUIWALA AKUFUNANI LERO ZAKA FOLO ANALI KUTI ? AMALAWI MUDZAKHALA OSAUKA MPAKA KALE CHIFUKWA CHOPANDA NZERU
@AllanJentala-g6h
@AllanJentala-g6h Ай бұрын
Boma ndilomweri basi ❤
@JasonMailos
@JasonMailos Ай бұрын
Choyamba mukanasitsa zithu , osati kugawandalama cholinga anthu azakuvotelenij , chuma Cha ziko NDI chakudya , feteleza momwe wadulilamo
@SamuelMthengo
@SamuelMthengo Ай бұрын
Umakolora chomwe wadzala, ngati wadzala kupempha udzakolora kupempha.
@CatherineKalumbi
@CatherineKalumbi Ай бұрын
ATI wapeza koyendera ndiye ndix angofuna akudyere
@CatherineKalumbi
@CatherineKalumbi Ай бұрын
Kkkkkk wakutolatu awadyere awa idyani guyz osasiya
@ChristMaunde
@ChristMaunde Ай бұрын
Kma yaah,more to penya
@MisheckAselo
@MisheckAselo Ай бұрын
Mukandifunsire kwa chakwera kuti bwanji sakudzatiyenderako kuno angopita kumpoto ndichigao chapakati 😮
@MisheckAselo
@MisheckAselo Ай бұрын
Kodi akanganya inu tikuvutika Pano mukukakamila 2063 bwanji mukuona inu 2063 agalu kwabasi 😊
@ClementKhomba
@ClementKhomba Ай бұрын
Akupanga kampeni wa mcp uyuyu is skelem
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg Ай бұрын
Chakwera camp ndinu anthu oyipa, Chilima uja samayenda chonchi, munkafuna muzizaoneka ngat oziwa ntchito atamwalira???
@GermotMicah
@GermotMicah Ай бұрын
😂😂koma
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb Ай бұрын
Manganya fiti yudasi maliro achilima unasankha kukhara chete mubare wakoso Lazaro akubisaso report Kd ndichani km mwangosankha Kuba ndi kugawa ndalama ndichikangawa munapha chilima muliphe Zanu zikuyenda mulungu akukantheni
@imraanJafal
@imraanJafal Ай бұрын
Koma mukanakba za ku chikangawa vice president
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of Ай бұрын
abwana tithandizeni ife tikufuna ndalama enawa zawo zomenezo
@victorkachepa3515
@victorkachepa3515 Ай бұрын
Adaferanji series.
@AlexSymon-he1vt
@AlexSymon-he1vt Ай бұрын
Mkugawana nokhanokha kumwela kumpoto ndife oima patokha no vote you
@jomochirwa
@jomochirwa Ай бұрын
Koma usiyo akuyigwilatu ntchito ine mkoyamba kuwona munthu wa straight ngati uyu .kunena chilungamo posatengela chipani munthu uyu atithandizadi .
@DennisBvumbwe-ft7hf
@DennisBvumbwe-ft7hf Ай бұрын
Mukanangong'alula kuti makadeti amadya ndalama za Malawi posamanga zinthu zosalimba komaso kuzembetsa ndalama
@omarlux3434
@omarlux3434 Ай бұрын
Vp mumakwana anawa alila sa ati
@AngungaThatcherNgoma
@AngungaThatcherNgoma Ай бұрын
Kwa Chinsewu not ku chinsewu😅
@yusufbreak905
@yusufbreak905 Ай бұрын
Muuuzen asamatchule dzina la chakwela plz
@ChikuMatemba
@ChikuMatemba Ай бұрын
Ndinaiwala Kodi Panja Dr Chilima ndi anthu ena 8 munawapha eti eishi!!!!
@tamalangoma2765
@tamalangoma2765 Ай бұрын
Cheap politics
@MussaZimba
@MussaZimba Ай бұрын
Galu iwe kungokhalila zomangopemba bc koma ndalama mukungosakaza agalu inu
@MussaZimba
@MussaZimba Ай бұрын
Ungatani iweyo manganya ulilipo ndimalilo kale udamupeleka chilima kwa falawo uzamwalilabe naweso mbuzi yamunthu
@yohanenene
@yohanenene Ай бұрын
Akuwakonza a Pulezidenti
@BrightZionga
@BrightZionga Ай бұрын
Mukuyankhula bwino a VP pitilizani
@BlessMnyenyembe
@BlessMnyenyembe Ай бұрын
Ndiye mwafikapo
@lacksonsiyadi943
@lacksonsiyadi943 Ай бұрын
Ziyanamizani anthuwo kumeneko
@ChristianChibwe
@ChristianChibwe Ай бұрын
Koma madziwa kuti zinthuzi timawoneraso ma TV , ngakhel ma official pages live zikamachitika?? Mawona ngati sitimawona?🙄🙄🙄🙄🙄
@RobertManyesa-s5d
@RobertManyesa-s5d Ай бұрын
Kkkkkkkkkkk
@TitusGoba
@TitusGoba Ай бұрын
Kod akumakwela pa stood?
@HostixNdalakwanji
@HostixNdalakwanji Ай бұрын
😂😂😂Comment ayi
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c Ай бұрын
Uyu alibe mfundo ndimkamufila ku tikuferanji kundaleku 0 pa 10
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Ай бұрын
Fundo zilibe ntchito koma ntchito ya bwino basi inuyo mukafuna Fundo ziyakhulani
@tamalangoma2765
@tamalangoma2765 Ай бұрын
😂😂😂😂😂
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c Ай бұрын
@@SaidiMbawa-st6bj iweyo zimvetsera bambo asikono akowo chikangawa crew
@louisgolden
@louisgolden Ай бұрын
Kodi mzunguyo watchito yanji
@Dickies-mk8cd
@Dickies-mk8cd Ай бұрын
Galu iwe kamasewelo
@lacksonsiyadi943
@lacksonsiyadi943 Ай бұрын
Ali pa contract ya mcp kut apeze ma vote ku mwera
@user-kr1tf2tu7s
@user-kr1tf2tu7s Ай бұрын
Sukuzifuna ndi iweyo cadet iwe uchedwa ayise ndale ndipagiround osa fb
@BrightZionga
@BrightZionga Ай бұрын
Kkkkkk njala ikuphani
@danielmagwaya1074
@danielmagwaya1074 Ай бұрын
Michael usi mutu wako sukukoka idiot nd Chakwera mimtengo wakoyo, mukutitenga life anthu ngat baby's mitu yo panda nthakayo
@SamuelMthengo
@SamuelMthengo Ай бұрын
Iwe ndiopemphapempha
@LoyceMhango
@LoyceMhango Ай бұрын
Mu office akukhalamo koma
@CharlesTambala-zn2bd
@CharlesTambala-zn2bd Ай бұрын
Eya..chifukwa..sakugendedwa... ...ku LILONGWE pajatu..a mcp..
@LeviChakwira
@LeviChakwira Ай бұрын
Zomatchula chakwera izo anthu sakuzifuna. Mwina suukudziwa
@JamesKhudze
@JamesKhudze Ай бұрын
Kma ku Blantyre wakukondakotu
@JosephKumwenda-o7m
@JosephKumwenda-o7m Ай бұрын
Ndikuti kumene sanawakonde koma mzisamala poyankhula2 mmmmmm enanu mkuyankhula zosamveka kwambr
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 Ай бұрын
​@JosephKumwenda-o7m Inu zinthu zikuchita kuoneka , nanga miyala wathilidwa nayo ku Lilongwe ija?. Tangolandilani ndalama za magazizo nzaulere, zikatha muyambilanso kuvutika
@LindaKaombe
@LindaKaombe Ай бұрын
Mfundo alibe awa
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt Ай бұрын
Tayangula lipot yandege lero usi
Is peace possible with Netanyahu in Israel and Hamas in Gaza?
17:17
Channel 4 News
Рет қаралды 174 М.
Girl, dig gently, or it will leak out soon.#funny #cute #comedy
00:17
Funny daughter's daily life
Рет қаралды 14 МЛН
Brawl Stars Edit😈📕
00:15
Kan Andrey
Рет қаралды 44 МЛН
Teaching a Toddler Household Habits: Diaper Disposal & Potty Training #shorts
00:16
KWACHEMERATU KUSERIKU- KEN NSONDA.17 September 2024
48:50
HOT 265
Рет қаралды 2,4 М.
Houthis Long Range Ballistic Missile Hits Israel!
15:16
CBN News
Рет қаралды 183 М.
última hora: DISPARAR4M GÁS LACRIMOGÉNEO CONTRA O VENÂNCIO NA MARCHA
3:19
Paul Osiris Chanel
Рет қаралды 1,3 М.
Ip Man 2 | The Boxing Competition
15:57
Cinewatch
Рет қаралды 8 МЛН
Will the 'Assassination Attempt' on Donald Trump Affect the Election?
22:58
Good Morning Britain
Рет қаралды 32 М.
Girl, dig gently, or it will leak out soon.#funny #cute #comedy
00:17
Funny daughter's daily life
Рет қаралды 14 МЛН