BASITU OKHAOKHA KUMASUKA KUMAULURA KUTI MACHINEAJA ANAWAKONZA KUTI IKAKWANA NTHAWIYO AZIPANGA IZI

  Рет қаралды 47,100

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 106
@Chikwawa
@Chikwawa 23 күн бұрын
Machine amene sakuyenera kugwiritsidwa ntchito. Tiyendere yakale basi. Asatipangire chochita ife.
@JimmyWChibwe
@JimmyWChibwe 14 күн бұрын
Twe mwana twe smatmatic woyee! Chakwera moto kuti buu 🔥 wolira samugwira pa kamwa woo!
@GeorgeDamiyano
@GeorgeDamiyano 19 күн бұрын
Smart matic maggic bwanji sitilola anabero mtamanja ali mbali ya chakwera
@jamesmtukula3062
@jamesmtukula3062 20 күн бұрын
Watching from klecksdorp north west dolingkruin south Africa
@MacdonaldMajohn
@MacdonaldMajohn 20 күн бұрын
Machine achoke dzikoli laonongeka owina awinire kuvoteredwa ndi anthu osati dzochera makinadzo
@RobertCosmas-bo1uo
@RobertCosmas-bo1uo 19 күн бұрын
Amalawi timakonda kuchita zinthu zongona machine amenewa agwire ntchto ndithu mwina tipunthukula demeti
@ThabaniZuma-d7u
@ThabaniZuma-d7u 20 күн бұрын
NRB & MEC, YOU SHOULD KNOW KUTI; Action speaks louder than word's. Inuyo ndimomwe mukumayankhulira dzikumachita kuwonetsa kuti ; dzolinga zanu mukufuna kuthandiza MCP kuti idzawine chisankho ndinso yipitilirebe kupha/kuzunza anthu mdziko muno, Ndimomwe awonongera a MCP dziko LA MALAWI. " Pangavute Maka bwanji iyoyo siyingawine chisankho. Ndiye chonde zolinga zanuzo mudziwe kuti anthu akuziziwa ,
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 15 күн бұрын
Machine amenewa sagwila ntchito never ayiwale
@GodfreyMzembe-b3n
@GodfreyMzembe-b3n 23 күн бұрын
NRB ndi MEC ili ndi dziko lanu ndi bwino kusatila maganizo a Malawi kusiyana ndi a ndare poti a ndare ambiri amakhala ndi maganizo ongofuna mphavu ndi chuma posaganizila abaleofe
@StenChirwa
@StenChirwa 23 күн бұрын
Maudindo kwa mthumwi zili pa line pa ndi achewa okha okha boma ili lilibe chilungamo ,sizikuoneka kuti pa chisankho chikubwelachi pazakhala chilungamo ayi
@LucyManda-y2l
@LucyManda-y2l 17 күн бұрын
Machine ayi chonde-chonde abale tagwira mwendo.
@steveduwa6856
@steveduwa6856 23 күн бұрын
As long as NRB failed to operate side by side with Mec as per the high court judgement of 25 Oct,NRB is held in contempt of the court
@LeonardLuka-y5n
@LeonardLuka-y5n 18 күн бұрын
Am live from India am Malawian it's not true MCP it's not agorvement to rule people in our country
@daviechannel8603
@daviechannel8603 23 күн бұрын
Yesu anati nthawi iyii ndiyanu poti ndiyadima muzaziona
@BrotherLester
@BrotherLester 12 күн бұрын
Matchini amenewa siwoyenela kugwilitsidwa ntchito mmalawi muno chifukwa mmatchinimo muli mayina kale omwe anayikamo ndipo muli figure imene yayikidwa kuti ikazafika mwa automatic matchin adyayime apa mchifukwa akuyika mthawi yofulumila kuti azasiye kugwila mtchito, ndiye sikoyenelela kugwilisa ntchito matchiniwa
@MayamikoJeke-d5m
@MayamikoJeke-d5m 23 күн бұрын
Zanziiiiii
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v 22 күн бұрын
Inu a mec musazitengere ku ntoso dzikoli si la chakwera muzamva kuwawa
@rashidadan2533
@rashidadan2533 16 күн бұрын
His exllence professor Peter muthalika The last man president of the republic of MALAWl 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 🌹The winner of 2025 general election 🌹 Everyone keep in mind , not any mistake allowed this year
@WilsonFelix-j9n
@WilsonFelix-j9n 23 күн бұрын
Tieni a Malawi tigulepo zikwanje zokwanira zayambikazi ndi chibwana tizingokhapanapo basi
@YunusuMaulidi
@YunusuMaulidi 23 күн бұрын
Mukamati nthawi kungokwana 16:00 machine a smart matic izakhala ikusiya kugwira ntchito, funso mkumati simunaisetanso kuti izakhala itamaliza kuwathandiza anthu ovotawo chifukwa simungabweretse machine ochita kufuna kwa iwo koma mubweretse machine ochita kufuna kwa anthu apo ndiye timvana bwinobwino
@HendrixChaputa
@HendrixChaputa 23 күн бұрын
Tikapanga Pa Demo....koma ine can't wait kufika September...akazangoti Chakwera wa wina ndizavula ku Bathroom mpaka ku Area 44 Kamuzu palace/State house...akazandiombela bas Ndizakhala mu history yaku Malawi I HATE THIS LEADERSHIP...Achakwela bola akanakhala Sir wa Bible Knowledge 🇿🇲🇲🇼
@LottiAffati
@LottiAffati 23 күн бұрын
kodi manyaka a smartmatic anuwo azagwira Ntchito mmalawi momuno, komatu guys zankhondo ife sitikufuna
@laurentbutao4084
@laurentbutao4084 23 күн бұрын
Nde chovutikira mkukavota ndichani
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 23 күн бұрын
mufune,olo,musafune,npiklsano,ndi,anthu,awili,wekha,suchita,npikisano
@ElemuAllam
@ElemuAllam 22 күн бұрын
0
@RaladyeTambala
@RaladyeTambala 9 күн бұрын
Panyapako anabell
@diliyaniimulani
@diliyaniimulani 15 күн бұрын
Kokatu mukamashula maina anuoowoo tikusungu shifukwa mukalunza tizakumangan
@juliussamson6212
@juliussamson6212 19 күн бұрын
DZIKO LILILOSE LIMENE ADZATHAWILE TILIKO AMALAWIAN ANTHU AMEKI MUDZATENGEREPO PHUZILO KUTI KUKHARA MBALI YACHIPANI SIBWINO AI AMENE AWONA ZOWAWA CHIFUKWA AKUTI NDIGOLO LA CHAKWERA
@AnyamataExecutive
@AnyamataExecutive 22 күн бұрын
Live from Botswana Kodi inu a mec monga mmene anthu ambili akudandaula pa khani ya smartmatic system potengela maiko angapo kuphatikiza mozambique omwe Ali pa mpungwepungwe pakali pano komaso ku malawi ko zipani zotsutsa sizikukhulupilira njira imeneyi simukuonapo vuto pa zotsatila zachisankho zikubwelazi chifukwatu tsogolo lathu Lili mmanja mwanu.?
@juliussamson6212
@juliussamson6212 19 күн бұрын
NTHAWI IKUBWERA NTHAWI YOMWE TIDZADULA MALISECHE ANABEL
@charlesmuwanya7845
@charlesmuwanya7845 19 күн бұрын
Munthu wa NRB akunena zosamveka. Court lidanena kuti NRB ilembe aliiyense oyenela kulembetsa.Koma NRB ikuika zikomo kuti anthu ena alephele kulembetsa.
@CharlieChirwa
@CharlieChirwa 19 күн бұрын
Smartmatic ikagwira ntchito nyumba mwa kwamtere
@JanetMphenzi-t2v
@JanetMphenzi-t2v 16 күн бұрын
Koma anthu awa ndi abodza kwambiri ndipo ndi anthu awa angasokonetse chisankho
@ShareefKalima
@ShareefKalima 18 күн бұрын
Chakwela Ndi zipan 9 anawinila Manuel ndichifukwa chiyan akukakamila machine omwe maiko ena akuzensa nkhondo ine ndi jk 2025 Manuel continue not smart matick machine nooooo tikufuna Manuel osat zakubazo ayi
@DicksonSquare-y2m
@DicksonSquare-y2m 23 күн бұрын
Chifukwa chani akufuna anthu amene alindi chaunzika chakalekal asalembese mugawo laonjezera
@JulioChiwalo-t4f
@JulioChiwalo-t4f 20 күн бұрын
A Malawi takana za Smartmatic machine a Anabel ndi Mec ya Mcp
@JemaxChibwanazulu
@JemaxChibwanazulu 13 күн бұрын
Iwe Anabero usatitokosore pamtumbo wamva, kanyini kako shupit
@PhiriVictor-e9l
@PhiriVictor-e9l 22 күн бұрын
Mwawononga mbiri yamasankho kumalawi.sizikukoma mpang'ono pomwe. Muzalanditse ndeu kutsogoloku
@RichardNkumbira
@RichardNkumbira 23 күн бұрын
Mudzawona tikasitha BOMA mudzayaluka chifukwa mukukondera MCP
@SiphamandlaNcaphayi
@SiphamandlaNcaphayi 23 күн бұрын
Udzalisinthabkuti
@omegasheibamussa3900
@omegasheibamussa3900 19 күн бұрын
Zoopanda cheere ziiii
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 23 күн бұрын
Koma a MEC musayambitse nkhondo ku malawi ok
@RobertCosmas-bo1uo
@RobertCosmas-bo1uo 19 күн бұрын
Nthawi ndiyofunika km mukachiona china chikafika 4:00pm nthawi yotsekera akt akukavota kukonda milandu olakwa uli iwe.
@SydneyNyasuli
@SydneyNyasuli 23 күн бұрын
Digital time is not a problem
@steveduwa6856
@steveduwa6856 23 күн бұрын
In fairness NRB should explain why unique identifier number delayed in the light of court judgement?
@FelixLivison-mk2cf
@FelixLivison-mk2cf 23 күн бұрын
Akuziyalusa okha basi
@isaacimmantambala5294
@isaacimmantambala5294 22 күн бұрын
Just like Brian Banda
@samdiverson9733
@samdiverson9733 19 күн бұрын
Machine amenewa achoke nkhani ndi ya manual basi
@GeorgeDamiyano
@GeorgeDamiyano 19 күн бұрын
Bwanji aka nthawi mu somatic ndiye ndira yofu kubayo mayiwa achoke bola manyo anthawi zonse ifukwa chani akuwumira akukana kuvota monga timavotera za zonse 1892
@laurentbutao4084
@laurentbutao4084 23 күн бұрын
Nde pamenepo tikuvota? Zaugalu basi
@JasonMailos
@JasonMailos 23 күн бұрын
Zausile basi
@MartinKapanga
@MartinKapanga 23 күн бұрын
apa khani ndi yakuti machine achoke pakhale chilungamo basi
@marryphili5419
@marryphili5419 19 күн бұрын
MCP mumumanye yesu palije ku vota apa chinyengo chokhachokha chiti
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 21 күн бұрын
Tivota mene timavotera osatipusisa ife
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 19 күн бұрын
Inu a N R ndi aMEC malankhuludwe anu okhudza za Chisankho mukutibalalitsa.koma anthu kudzafika be4 4:00 pm mwati sadzavota Koma zoona mudzabweze anthu atafika kale? Koma inu mukufuna mudzayambitse chisokonezo eti?
@EdwardChibaya
@EdwardChibaya 16 күн бұрын
NRB and MEC pantundu wambweyanu mukangobela chisankho muona polekana miendo agalu
@MphatsoSalima-z9b
@MphatsoSalima-z9b 22 күн бұрын
Mukabera zisankho Malawi adzaotchedwa dzulo chifukwa amalawi ndipita kwambili chakwera sakukufunani Kaya mwamva.
@madakabichi2251
@madakabichi2251 15 күн бұрын
Ana a Balaba chakwera awa
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 19 күн бұрын
Kodi m,Mesa machine anu samagwira ntchito Abale tapangani zothandiza anthu.kunali NRB mbuyomu zonsezitu kunalibe.Aliyense akuyenela kulembetsa .Ndipo kulembetsa kwa zaka zino Mavuto ndiochuluka.N.R.B muli ndi Vuto mukutisokoneza.Kodi mavuto anu ndi angati.Bungwe losathandiza .Vuto akumvela wina wake nkuika ma Control measures Obowa ngati amenewa.Shame on you A N R .B
@JanetMphenzi-t2v
@JanetMphenzi-t2v 16 күн бұрын
Koma inu anzathu mukuyendetsa za chisankho muziyendetse bwino mwamva
@MussaWilliam-q3l
@MussaWilliam-q3l 23 күн бұрын
Komatu guys mukawonetsetsa anthu awa akutitengela ku ntoso anthu awawa dzomwe dzikuchitika ku Mozambique akudziwona akuganidza dzochedza ndichifukwa chani akunena kuti amachini akanena kuti basi kungakhale anthu atadzadza basi palibe kupitilidza wy kungoti dziko lakwathu kwayambika khondo anthu monga ngati awa kukufunika kuwapanga tageti ndikudzimenya
@TrebuMalunga-sr2rz
@TrebuMalunga-sr2rz 19 күн бұрын
Zawuchitsilu tiyendela zakale basi
@JohnmjigoMalinda
@JohnmjigoMalinda 19 күн бұрын
Komatu anthu inu kaya mukuchita chibwana kwambiri mcp ikupwetekesani soon zikuvutani,smartmatic yanuyo mukaone kogwilisira tchito not kumalawi
@MariaNkhata-i9q
@MariaNkhata-i9q 23 күн бұрын
Zacbwana muzaphesa aana anu
@LomosiKanzingeni
@LomosiKanzingeni 19 күн бұрын
Kodi a NRB ndi MEC ndi a Malawidi?. Nanga akukonda Ndalama kusiyana ndikukonda aMalawi, powagulitsa kudZera munjira ya Smartimatic bwanji?bwanji?. Kodi mmene Malawi wawonongekeramu sizikuwakhudza?
@Sosten-x4e
@Sosten-x4e 22 күн бұрын
Kodi chigamulo Cha khothi chitha liti ndikufuna ndiziwe please ndiine mbuli
@ClementWanja
@ClementWanja 18 күн бұрын
😅 23:57 mbava 40
@TapiwaKalira-b1r
@TapiwaKalira-b1r 22 күн бұрын
Sizoona zimenezi machine ku malamula nthawi ?
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 23 күн бұрын
kumangoti,kudzakhala,nkhondo,chakwela,akadzawina,ifeyo,tikuti,mudzayesele,dala,kudzyiyambitsa,tidzasangalala,kwambili,
@BrightZionga
@BrightZionga 23 күн бұрын
Iweyo kwanu nkuti osatha kulemba mbuli ngati iwe 😂😂😂 osamango recorder bwanji
@OmarFPMchawa
@OmarFPMchawa 23 күн бұрын
Sitikufuna machine tiyendere njira zomwe timaziziwa
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 23 күн бұрын
amalawi,ngati,sanagwila,zikwanje,ataona,tipekisi,sadzichitaso,ziwawa,chifukwa,tipekisi,inali,njila,yowawitsa,kwambili,
@JackieMugawa
@JackieMugawa 23 күн бұрын
Izi sixon
@ChuzyBoy-u1c
@ChuzyBoy-u1c 20 күн бұрын
Ndiposo amayi inu ndiachitsiru
@patricksinyala1345
@patricksinyala1345 23 күн бұрын
Funso lakuti Kodi omwe amanena kuti akumalemba ana ali Ndi Umboni wanji ilo ndi funso lopusa, chifukwa funso lomwelo inuyo mumakhala ndi umboni wanji kuti mwana aliyense oyambirira 16 years iyeyo mwanayo alidi ndi zaka 16??
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 23 күн бұрын
mukakamba,zankhondo,amamenyana,ndi,olamula,ndi,otsutsa,palibe,amene,amalolela,kumenyedwa,
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 23 күн бұрын
nafeso,tidaona,mashini,okhoza,kubela,2019,km,sitimalila,,tinadikila,kuponya,voti,kenako,ndipamene,timadabwa,kt,tipekisi,amapaka,ndi,amai,aja,kapena,chimapaka,ndi,chimashini,chija,
@bisweckchimphamba8497
@bisweckchimphamba8497 22 күн бұрын
Kodi nanga mukukakamila bwanji machine amenewa pamene mukudziwa kuti anzathu pa Mozambique pompa apeza nawo mavuto!mbava za mcp izi
@MaryShumba-ob4to
@MaryShumba-ob4to 13 күн бұрын
Mwina sakuona zomwe zikuchitika Ku Mozambique zija
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 23 күн бұрын
musamatichititse,mantha,pankhondo,olamula,otsutsa,,aliyese,amafa,ndiye,mukamat,kudzakhala,nkhondo,dziwani,kudzakhala,kuphana,basi,
@johnnyirenda5848
@johnnyirenda5848 20 күн бұрын
Chimachine Chichita kutchera kwa Ife amalawi or KU I'm foreiners Device yitilamula? Zobweretsa mafunso opanda mayankho. Kodi Chipani chasandusa Malawi Kukhala lake? Kuohunzira ndiyekuti kuti tiziuzidwa za kusiyakwa device ndiye kuyima kulembetsa what is it Amalawi mituyathu yayima tanba kuyendera zisulo kumatilamula? Zosamveka pilizi chonde
@MartinNice-z9n
@MartinNice-z9n 22 күн бұрын
ND akuba agaluwa akunama kwambiri dziwavuta
@WilliamNhlane-fd9hi
@WilliamNhlane-fd9hi 20 күн бұрын
Inuyo a mec ndi NRB mubweresa nkhondo ku Malawi , sitikumufuna smartimatic we need manual process of voting, results of that machine you can see what happens in Mozambique. You have to respect the will of citizens ignorant people
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 23 күн бұрын
Mbamva izi
@MosesNyasulu-c3x
@MosesNyasulu-c3x 23 күн бұрын
Mcp yizapambana chifukwa cha ifeyo za mashine sitikulankhulapo chilichose kuti tisayagwilise tchito nthawi yikupita
@JulietNyondo
@JulietNyondo 23 күн бұрын
Kmatu apa masmart Anu awo muchose ndithu takana amalawi Ife musatipusise pls so nthawi ya kamuzu ino ndi democracy pano 1992 kunali zoospa kwambiri ndiye sibwino kuti ana athu azavutike
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 23 күн бұрын
NRB ya mcp
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 23 күн бұрын
km,mukamati,padzayenda,zikwanje,,mukunama,inuyo,nde,mudzave,kuwawa,kwambili,osava,kuwawa,ndi,tipekisi,uja,,anzanu,sadachite,mantha,,ndi,chi,mashini,chatipekisi,,,,,,anadikila,kuponya,voti,nanga,inuyo,phuma,bwanji,nanuso,mudikile,kaye,voti,mungafe,ndi,bp,
@MikeSangano-u8m
@MikeSangano-u8m 23 күн бұрын
Nrb mec ,these are mcp ndondocha
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 23 күн бұрын
otsutsa,kusapilila,kwanji,kumeneku,ndiye,kut,mcp,mukuiopa,kwambili,eti
@BrightZionga
@BrightZionga 23 күн бұрын
Kkkkkk iwe tapita ku school ya kwacha manyazi mulibe kodi😮😮
@IvyMkhura
@IvyMkhura 22 күн бұрын
Tidzaonana, mcp no chance again
@TimexKaufa
@TimexKaufa 23 күн бұрын
Zabodza muduladulabwanji😂😂😂😂😂😂
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 23 күн бұрын
anzanga,olemba,makomets,musamati,akadzawina,chakwela,kuzavuta,ndiyeno,mukufuna,adzawine,nindani,km,ngati,mukumudziwa,owina,musakavote,,chifukwa,zikuonetsa,kt,palibe,npikisano,
@Felie-p7l
@Felie-p7l 23 күн бұрын
Musatipusitse agalu inu
@ErickCPatrick
@ErickCPatrick 23 күн бұрын
a,dpp,akadzava,kt,mcp,yawina,kudzavuta,nawoso,a,,mcp,akadzava,kt,dpp,yawina,kudzavuta,chifukwa,aliyese,alindi,anthu,amene,amakonda,zipanizi,
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 23 күн бұрын
Baba MCP a malawi sakuyifuna
@BrightZionga
@BrightZionga 23 күн бұрын
​@@PrinceThom-pe6iekkkkkk tamuuzeni uyu akayambe ya kwacha
@MaryShumba-ob4to
@MaryShumba-ob4to 13 күн бұрын
Basi ya Mozambique ija izabwera kuno mukuwaona kupusa a malawi
MULANDU WA TAMIA JA __27 January 2025
16:22
HOT 265
Рет қаралды 9 М.
Kaliati kuyankhulapo Zabodza La Michael Usi
6:51
Sam Malvitha
Рет қаралды 61 М.