BOMA LAKHUMUDWA NDI MAU OMWE ALANKHULA A PETER MUTHALIKA KUNJAMBA MVERANI NOKHA |

  Рет қаралды 10,526

DZIWE TV

DZIWE TV

18 күн бұрын

Пікірлер: 137
@hadgeyahyaa8574
@hadgeyahyaa8574 16 күн бұрын
Kunkuyu ndiwe mbudzi nanu osapita mukayakhule zanubwanji machende😅😅😅😅😅😅😅
@AndrewChimwaza-rf7hw
@AndrewChimwaza-rf7hw 16 күн бұрын
APM alankhula zambiri monga kukwera mitengo yazinthu,kusowa kwa fertilizer, sugar,komaso forex,bwanji osayankha zimenezo ndikumayankha zobera mavote .zakupweteka popeza akotulukila maplan any eti.
@cadohjabu5565
@cadohjabu5565 16 күн бұрын
akudzichedwetsatu awa
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e 16 күн бұрын
Kumkuyu akulira ndiye akhaulatu cakwera wakoyo chidziwa iye ndikukonza maubale koma kukonza boma lake sadziwa ulibe nzeru kumkuyu asatanic inu
@LoveHere-ki8ck
@LoveHere-ki8ck 16 күн бұрын
DPP ikalankhula wina aliyese amatsekuka nayo mmimba, ndiye tikamati DPP ndi machine tikunama? 😂😂😂😂
@shuraimuwamama2349
@shuraimuwamama2349 16 күн бұрын
Katangale analipo koma samafika ponyatsa pomwe pafikkapa, anthu akumudzi amanjoya fetereza amafikira mmokwanira pano anthu akudya kamodzi komwe aakukatcha😂 mgundakamodzzi zamanyazi
@AlisenMatola
@AlisenMatola 15 күн бұрын
Pot amalawi ena apangisa kale ma I'd akumozambiq kut akavote kumeneko mu October,anthu amenewo amalowa bwanji mdziko muno kod chimenechi sichikhala chipeleganyu?
@user-xn3lq1hj1r
@user-xn3lq1hj1r 16 күн бұрын
Ndakuso kotsera nkulinga utamva mawu ndiye apita patali ndipo alankhulidea mopanda kudzungulira straight and directly to the point. APM my vote✔️
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 16 күн бұрын
Ndipo ayankhula mchichewa ❤
@HawardKalipande
@HawardKalipande 17 күн бұрын
Simunati apaka Inu bola mwaziwonera komanso kudzimvela iweyo kumkuyu ndi mzakoyo mwapanga chian??munya simunati APM yemweyo
@dimukenneth6580
@dimukenneth6580 16 күн бұрын
2. 2 2 2 22 222 2w22222 2 22. Ss
@ThoccoBondo-mx7vt
@ThoccoBondo-mx7vt 15 күн бұрын
Kkkkkkkk mwayamba kunjemeratu ndye simunatitu Mr mkumkuyu😂😂😂😂
@usumanidaudi
@usumanidaudi 16 күн бұрын
Inu pamafunika kuku pweteka kuba apm samaba km m boma ra chakwera ndirimene rikuba kwambiri
@Yamikie-yamikie
@Yamikie-yamikie 16 күн бұрын
Mneneri wa boma kmalankhula ngat wachipani😅😅😅😅 Zilikotu ziliko😂
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r 16 күн бұрын
Abc ndiyachakera simungatiuxe xopusaxo , koman apm sakunam
@PatrickNjolomole-vb7jf
@PatrickNjolomole-vb7jf 16 күн бұрын
Vinyo wa kumkuyu akutha 2025
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w 16 күн бұрын
Kunkuyu sangalankhule zolondola ayi, chilungamo ndichoti APM abwerere mu boma basi, anthu akuvutika mu Malawi kusiyana ndi ulamuliro wa DPP.
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r 16 күн бұрын
Chison chachan athu okuba in and mbc panopa yavunda coz mcp
@thokoJames-gp8mk
@thokoJames-gp8mk 15 күн бұрын
😂😂😂😂😂 Ikwagwa mvula muchuluka zoliralira mwayambatu kulira akunkuyu , mulira simunati apa zangoyamba 😂😂😂😂😂
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 16 күн бұрын
Apm🔥🔥
@spargomw
@spargomw 14 күн бұрын
Demet, Dpp woyeeee
@josephmillion9894
@josephmillion9894 16 күн бұрын
Aboma mwachangu a apeter pamene anthu akudandaula kukwera Kwa zinthu koma palibe chimene akuyankhulapo.Chachiziwikile kuti aboma akufuna kulimbana ndi asogoleri azipani zina m'malo mogwira ntchito yosamalira amalawi.
@JoyMphika
@JoyMphika 16 күн бұрын
Ayamba kare kunjenjemera
@KanjebweAlie
@KanjebweAlie 16 күн бұрын
Mkhukhuyo mbuzi 3:48 3:50
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g 16 күн бұрын
Mu ulamuliro wa chakwera katangale wakwera 99%,, nepotism kulemba ana Ake ntchito APm sanalembepo mwana wake ntchito,,chakwera walemba achibale ntchito wochuluka not APm,, Chakwera wagwetsa dziko
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e 16 күн бұрын
Sanasokoneze inuyo a MCP ndiye mbudzi mukuona ngati anthu sakuziwa ma plan anu muzakhaula DPP ikulowa muzilo gedza kumeneko
@KanjebweAlie
@KanjebweAlie 16 күн бұрын
5:26
@rashidadan2533
@rashidadan2533 16 күн бұрын
MCP ikufuna kubela má vote , ndizoona Mr APM sakunama ndipo ineyo ndi mboni mukafuna umboni mundipeza And even MCP itazabela ma vote sangazawine ndipo asamalote zozawina.
@HafizahHarack-bn3bf
@HafizahHarack-bn3bf 16 күн бұрын
Akhumudwa nzenzeni sanata😂😂😂 Dpp more fire
@user-ir8md7uq1j
@user-ir8md7uq1j 16 күн бұрын
Iweyo kunkuyu wasowa chonena iwe mukutuluka anthu sakuvoteran inu ndianthu okuba kwambili anthu boma lanu akuvutika kwambili tivotera APM
@shakilasaid705
@shakilasaid705 15 күн бұрын
A Minster palibe cha mzeru mukuyankhulapo apa
@ephraimphalawala4720
@ephraimphalawala4720 16 күн бұрын
Aliyense amateteza mchere wake...ndiye chatsala kkkk
@LucySandram-mo6uq
@LucySandram-mo6uq 15 күн бұрын
Ayamba kaye kutsegula m,mimba heee!!!! Muona pole chaka chake ndichino mulira inu mwangoyamba kaya ndangodutsaaaaa
@user-fm8ed7eo3i
@user-fm8ed7eo3i 17 күн бұрын
I weee ndi zoona inu ndi mamva kwambiri, mungodyelatu tionana pa tsikulo
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 16 күн бұрын
Mbc ndi ya boma singakambe zoipa kuopa kuchosedwa ntchito
@niassastudios8939
@niassastudios8939 14 күн бұрын
Taona stae ya Mozambique italowa mMalawi ndi makina awo nkumachita kalembela ma umboni tili nawo ndipo tikudziwa kuti Malawi ichita chimodzi modzi
@HolickLemajomo
@HolickLemajomo 16 күн бұрын
Akumkuyu musayankhure zopusa peter mutharika akuyankhula zoona kuti zaka ziwiri azasintha dziko lino inu mutisendera chani anthu oipa inu mwatitopesa muzikayalura chire
@AustinChiyembekezo-cx4mz
@AustinChiyembekezo-cx4mz 16 күн бұрын
Mkukuyu ndichisilu kwambili .....inde mukufuna kubela
@sheikhjaffarwhyte2688
@sheikhjaffarwhyte2688 16 күн бұрын
Vinyo watha akatere😂🤣
@user-xu9rh1lm8o
@user-xu9rh1lm8o 16 күн бұрын
Munya muona akutulukilani tikumana 2025 pamenepopo ndipang'ono chabe mutsegulabe mimba
@KawisaCharles
@KawisaCharles 13 күн бұрын
Palibe mbabva yomwe imafika ndikunena kuti ndine mbabva pokha pokha umboni ulipo mcp singabwere poyera mkunena kuti ibera chisankho koma ndizoona zake zoti akufuna abere ndithu
@OwenYobe
@OwenYobe 16 күн бұрын
Munyabe 2025 Apm my vote
@ntombifuthikarabo5964
@ntombifuthikarabo5964 16 күн бұрын
Amen🙏🙏🙏🙏
@usumanidaudi
@usumanidaudi 16 күн бұрын
Kukuyu ndiwe chisiru bwanji chifukwa chani ku Lilongwe akurembesa ana azaka 12
@patrickscott9086
@patrickscott9086 16 күн бұрын
Eti akulembesad ndipo andiwuza angapo anakalembesa pa Kakule school ku chinsapo kuno
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q 16 күн бұрын
Ine kuzionela ndekha, ndekuyakhula zachitosi chabakha kuikila a MCP kumbuyo, mene akuvekela sakumuziwa m'ndani, DPP motoooo
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q 16 күн бұрын
Kunkuyu palibe angayankhule zanzelu zokhuza dziko, azuzulekaye MCP kutimwina tiyebme kumvela
@patrickscott9086
@patrickscott9086 16 күн бұрын
Kunoko ku chinsapo ku Kakule primary school akulembesa nd ana azaka 12 omwe mmmmm kma boma ili. Akulemba ndi mzika za Mozambique zomwe. Ndye Nick chakwela wakapangisa ma ID kunja ozabela zisankho kma
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 16 күн бұрын
Nkunkuyu ndiwe chisilu ndi chakwela wakoyo tazingobani
@mcdonaldgerard9707
@mcdonaldgerard9707 14 күн бұрын
Zimene walankhura muthalika kwamunthu wanzelu zake palibe cholakwika ayi, koma kuti maloto achumba amakhala ofoira ndiye zimene akunena chakwera yo!!!!!
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x 17 күн бұрын
Zitsilu inu galu wanu chakwerayo mmesa ndi wankulu wampingo
@user-mj2te7vl6p
@user-mj2te7vl6p 17 күн бұрын
Y only that sentence
@BysonMakalani
@BysonMakalani 13 күн бұрын
Nyekhwe
@HassanJameskananjie
@HassanJameskananjie 16 күн бұрын
Aganiza bwino bwino mmene mukubela anyapapi inu munya next year
@alfrednazombe
@alfrednazombe 15 күн бұрын
Tili kwaeni kom zikutheka salary kulandilisa apolisi 5 komnso kuwalipilila magesi madzi ndi rent kkkkk mcp out kunkuyu tazingophuza long life pills bs unyanya kugagadaa kkkk
@laymanchirwa8026
@laymanchirwa8026 16 күн бұрын
Kunkuyu nthongo lako
@user-nn7sv5yb8h
@user-nn7sv5yb8h 14 күн бұрын
Ndichifukwa chiani mukunamiza a Malawi mopusa chotere ngati amalawi ndi opusa
@jamusnamwino-br2iz
@jamusnamwino-br2iz 16 күн бұрын
simunati mulila akhukuyu koma akunama palibe chimene mungalankhule chazelu
@SandraBanda-hd1li
@SandraBanda-hd1li 17 күн бұрын
Panyo....panu.. ndi.. aboma... ndi. Chakwera... wanu yo... mwayaluka... ndi, Kuba... Kwanuko
@MisheckNtanbalika
@MisheckNtanbalika 15 күн бұрын
Eeee Kom Sana name jt mufuna mubele muchoke bas zopusa zanuzo mukasak kopangila agalu inu iwe ukulakhul we ukulakhul izi fukwa chandler komas kuopa imfa
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 16 күн бұрын
Aaaa iwe mcp
@user-nk5mj5ws8v
@user-nk5mj5ws8v 17 күн бұрын
kodi yiweyo moses kukhuyu koma umaganidza bwino bwino kapena ukuyenda achakwela asamadziwe dzili kunjaku
@user-wx1jt5fd2j
@user-wx1jt5fd2j 15 күн бұрын
ADPp analinso ndi zobvuta zawo koma zanu zanyanya chizaone ndi chipande poomora siinunso lero mwanena kuti azipani zonse aiwale kuti muzachoka m, boma kuthandauza kuti palipo mwaponda
@fastbanda3630
@fastbanda3630 16 күн бұрын
Kkkk munyatu inu
@LukaNangole
@LukaNangole 16 күн бұрын
A dadi osadanda anbuye alinanu akumenyelani nkhondo kuti muombole a malawi
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 15 күн бұрын
Umuuze chakwera akangwere chilungamo kupweta agalu inu
@ThoccoBondo-mx7vt
@ThoccoBondo-mx7vt 15 күн бұрын
Kusowa zoyankhula basi mubeletu ndalamadzo 2025 wina azaziguguda pamtima
@ThokohKalonga-je9rx
@ThokohKalonga-je9rx 16 күн бұрын
Palibe chomwe mungakaneso abulutu inu, adanena chilungamo.
@user-ce6hy6tp7e
@user-ce6hy6tp7e 16 күн бұрын
Kunkuyu ndi chakwera wakoyo kagwereni uko ndpo amene akutibera ifeyo amalawi ndi chakwera ndpo chakwera ndi mbava watilanga ifeyo osati pang,ono
@user-ql8nf2vb8s
@user-ql8nf2vb8s 17 күн бұрын
Zamanyi eti akunkuyu chakutichako usankhe wekha
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 16 күн бұрын
Nkukuyu pano mukuva kukoma chifukwa muli mboma mudzava kuwawa mukatuluka mboma just wait
@user-ml4bl2ll2g
@user-ml4bl2ll2g 16 күн бұрын
Kungoti chilungamo chimawawa kwambiri musakane a MCP ,,mcp ikuluza ,,,chakwera zaka 4 wapanga chani?kuba 99%, umphawi panopa wakwera pamalawi chifukwa chakwera walephera kuyendetsa dziko
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 16 күн бұрын
Iwe kumkuyo mmaso mwako mbava yotheratu ..Koma usayiware pamene ulipo panali azako anachokaposo ndizosiirana azo
@carenchikwe268
@carenchikwe268 16 күн бұрын
Mwayamba Ku njenjemeratu🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@YonahBanda-kp9rm
@YonahBanda-kp9rm 14 күн бұрын
Inu mwapanga chani kupatula kugawana ndalama za a Malawi a Mcp
@jennyx6914
@jennyx6914 17 күн бұрын
mtima wawawa amcp pooma chinantindi chawanthu ndiye uku nkulira a mcp iwo chimene angachite nkuosngitsa msonkhano wawo basi
@user-pl2lj6mh1z
@user-pl2lj6mh1z 15 күн бұрын
Agalu. Inu muzilila kwambili akukuyu munya
@user-ev6bi7jr7g
@user-ev6bi7jr7g 16 күн бұрын
Dzisakuwaweni m'mamunyonzatu Koma iye amangomvetsera lero nayenso wayankhula kamodzi kokha mwatsegula m'mimba
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py 16 күн бұрын
Akumva pain mkukuyuyo uziona usambamo Uli wamuna zakuonekera. DDP ikulowaso m,boma 2025 mcp out
@DennisDonework
@DennisDonework 16 күн бұрын
Kunkuyu. Mavuzi okalambawo ndimatenda ulinawowo osamva makhwalawo
@HaroonMaundala-lg5lg
@HaroonMaundala-lg5lg 16 күн бұрын
Mwayamba kale kulilatu a mkaka. Mumayelekedwa kwambili a mkaka. Machende anu mwava
@user-el8to1te3l
@user-el8to1te3l 14 күн бұрын
Ndiye iweyo vuto lako ndi chan galu iwe
@KanjebweAlie
@KanjebweAlie 16 күн бұрын
Nkhukuyu ndi mbuzi iwe mungatiuze chani
@user-sq5dt3bc4u
@user-sq5dt3bc4u 16 күн бұрын
Mundilakwisa
@AustinChiyembekezo-cx4mz
@AustinChiyembekezo-cx4mz 16 күн бұрын
Ndipo inenso
@user-un9jw6kx3u
@user-un9jw6kx3u 16 күн бұрын
Bola Dpp inu nde mwaonjeza kwambili Kuba
@MoureenGalilea
@MoureenGalilea 16 күн бұрын
Km kunenazoona awa yakolokota pathako eeee faziii imeneijaaa Dpp eeee zinangoona kuvuta km yabaya ndithu iwoowo amanena kangat akapita ku mcp kwaoko tsono kungowanena kamodzi akhumudwa kale😂😂😂😂
@user-hx6ly3cl8m
@user-hx6ly3cl8m 16 күн бұрын
Komano APM sakunama chilichose chakwela
@wilisonbornface4282
@wilisonbornface4282 16 күн бұрын
Chilugamo chimawawa agalu inu mungatiuze Chan zobera mavote zinamveka kale iyeyo wagodusamo bs
@user-xv5pr3ji6w
@user-xv5pr3ji6w 16 күн бұрын
Kunkuyu chisiru cha munthu ngatiniwe za ziii
@user-po6ir6eh4z
@user-po6ir6eh4z 16 күн бұрын
Chisiru iwe nkukuyu ndi mbuzi zizakozo anthu akuba inu
@PatrickNjolomole-vb7jf
@PatrickNjolomole-vb7jf 16 күн бұрын
Kumkuyu kkkkkkkkkkkkkkk ukuziwa kuti mcherewa ukuthaaaa 2025
@usumanidaudi
@usumanidaudi 16 күн бұрын
Inu punga ma tumba 6 mungathandize kuripirira ana ku sukuru mukagurisa mupeza ka ndarama kochepa maro moti monene kt zindu zakuvutani
@ChimwemweMagombobanda
@ChimwemweMagombobanda 17 күн бұрын
Kinkuyu mutu wako sukugwira mwayamba kale kunjenjemera
@WilsonLimited-fh1mz
@WilsonLimited-fh1mz 17 күн бұрын
Mbc manyi a Tv
@ChicoBanda-kq7py
@ChicoBanda-kq7py 16 күн бұрын
Kukuyu ndiwegalu ambuye akuyendele
@victorauwana7258
@victorauwana7258 16 күн бұрын
Hahaha 😂 manyazi bwanji a mcp
@lymonmanda-cd8ol
@lymonmanda-cd8ol 16 күн бұрын
Koma katangale walero wanyanya
@user-yt2op5rl2q
@user-yt2op5rl2q 16 күн бұрын
Akunkuyu ndiopusa awamukufunad kubera
@YusuffuDaud-cs7yu
@YusuffuDaud-cs7yu 17 күн бұрын
Mbava inu mcp
@InnocentMmanga
@InnocentMmanga 16 күн бұрын
Mwachita makola
@DanielJoe-jf1or
@DanielJoe-jf1or 16 күн бұрын
Nduna yopanda zeru mbava mwaivatu
@IsaacMusa-py2jm
@IsaacMusa-py2jm 15 күн бұрын
Kapolo wadziko iwe,,
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 16 күн бұрын
Atonse alliance munabela mavote mu 2020
@user-ke4dk2io6q
@user-ke4dk2io6q 15 күн бұрын
Pa mtumbo panu a mcp
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 15 күн бұрын
Mkukuyu mutu sukugwira
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 16 күн бұрын
Iwe kumkuyu mboloyako
Izindaba zesiZulu @19H00 | 29 May 2024
23:09
SABC Izindaba
Рет қаралды 13 М.
2024 Elections | EFF leader Julius Malema casts his vote
9:24
Bro be careful where you drop the ball  #learnfromkhaby  #comedy
00:19
Khaby. Lame
Рет қаралды 37 МЛН
Eccentric clown jack #short #angel #clown
00:33
Super Beauty team
Рет қаралды 15 МЛН
it takes two to tango 💃🏻🕺🏻
00:18
Zach King
Рет қаралды 27 МЛН
uNgizwe ephawula eyokugqishwa R15 Million ebuzwa uGeh
1:12:09
King Zoso TV
Рет қаралды 6 М.
Nelson Chamisa Gives SADC  Deadline , Or He Will Be The Answer..
4:53
A Police Ndi A Army Ntchito Yanu Siyoopsyeza A Malawi - Bon Kalindo
14:09
Amazwi akhuluywe President Zuma evota ngakubo
17:07
King Zoso TV
Рет қаралды 54 М.
ODUU Afaan Oromo Hatattaaman Amma Nu Gahe May 30, 2024
20:14
Tumsa Media
Рет қаралды 1 М.
Bro be careful where you drop the ball  #learnfromkhaby  #comedy
00:19
Khaby. Lame
Рет қаралды 37 МЛН