BON KALINDO KUFOTOKOZA ZOMWE WAFUFUZA-15 September 2024

  Рет қаралды 8,419

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 46
@RajabShahida
@RajabShahida 3 күн бұрын
Achakwera sinsogoleri ndisatana ameuja kodi tikuwopa chani makamaku kumuchosa pampando pajapo panali mugwilizano ndi malemu chilima ndiponso chilima 2022 adanena kuti ngati mugwilizano akufuna uthepo anene tipitenso pachisankho Chifukwa panali mugwilizano wazipani.zoona kugulitsa munda olima uli ndi ana mayi malawi 😭😭😭😭😭😭 tilire bwanji yooooo
@funnynyirendafunny7888
@funnynyirendafunny7888 3 күн бұрын
Strong msg ndiwakubadi ndi mlomo wake ngati wambuke osuta mbiya
@MaxwellMangamba
@MaxwellMangamba 3 күн бұрын
Yokhayi yogulitsa Likoma District mmmm aganizeponso bwino siziona ayi.Kumene kuja ndi kwawo Kwa amalawi anzathu
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i 3 күн бұрын
Strong 💪 message Mr president bon kalindo will trust you your number one DC 😀 👍
@GiftNdeleman-xr2xu
@GiftNdeleman-xr2xu 3 күн бұрын
Kwinaku nditukwana sopano 😏 ñdatopa nae chakwera ine
@JohnWame-u3l
@JohnWame-u3l 3 күн бұрын
Amene sakunvera zakeizo kutidziwitsa nde ukuyesetsa,koma,Amalawiena Alikumudzi sakudziwa chinachilichonsetu
@MaryTchapo-py4hh
@MaryTchapo-py4hh 3 күн бұрын
Ine ndiwaku nsanje komweko si sitima ya mafuta amangonama
@johnkambala692
@johnkambala692 3 күн бұрын
A Kalindo ndi m'mene akupusitsidwa ndi tindalama from opposition parties. God is on our side, 2025 boma.
@GiftNdeleman-xr2xu
@GiftNdeleman-xr2xu 3 күн бұрын
u're blinded but u don't know
@TecksonKaima-dr6er
@TecksonKaima-dr6er 3 күн бұрын
Chakwera ndi wa misala komanso mmutu mwake therere lokhalokha
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 3 күн бұрын
Chakwera ndigalu pamozi ndi mcp yose makape saziwa kuyendesa dziko amayesa joke 😅
@FanizoKawindula
@FanizoKawindula 3 күн бұрын
Usanamize anthu iwe ku Malawi kuno anthu sanalemereko
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 3 күн бұрын
Amalawi Nonse Munafa Koma Simudziwa No wonder mukubeledwa likoma Island osapangapo kanthu.
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t 3 күн бұрын
Tikutumula mukapenim afe sitingavotele
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 3 күн бұрын
Alomwe nenani zoona osati maboza maka galuyi kalindo ndiwe chisilu
@ElizabethMaononga
@ElizabethMaononga 3 күн бұрын
Munthu samakuyankhani manyazi bwa
@ZephinutMtande
@ZephinutMtande 3 күн бұрын
Iweyo ndiwe mbuzi ya munthu ukaona ku Malawi zinthu zikuyenda
@raymondmikondo2102
@raymondmikondo2102 3 күн бұрын
Mutu opindikawo wamva mxiiiiew zimaendamo mmutumo koma?
@MaryTchapo-py4hh
@MaryTchapo-py4hh 3 күн бұрын
Zitsiru nonse amene mukumuitanira chakwera makape
@abelkalulu2904
@abelkalulu2904 3 күн бұрын
Njala ilipo cifukwa ca cilala osanama apa
@ZephinutMtande
@ZephinutMtande 3 күн бұрын
Chosecho achibale akuvutika kugona ndi njara kapolo iwe
@elvisnjoka8428
@elvisnjoka8428 3 күн бұрын
@@ZephinutMtande muwauze abale anuwo azigwila ntchito Ali ndi manja
@amiduclement2142
@amiduclement2142 3 күн бұрын
Munthu ukakhala ukudana naye umayesetsa kut tsiku lililonse udzpeza zofooka zake, boma lapita Lija linalibe zofooka?
@ChristopherManase-s1f
@ChristopherManase-s1f 3 күн бұрын
Kkkkkk walila cadet kufuna boma
@PotipharEphraim
@PotipharEphraim 3 күн бұрын
Chakwera awinaso ❤❤
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 3 күн бұрын
Mmmmm plz save us that nonsense
@alexgama9037
@alexgama9037 3 күн бұрын
True talk
@GiftMwenisongole
@GiftMwenisongole 3 күн бұрын
Koma chkwerayuu wandikwana kwambir
@Jayleezbond
@Jayleezbond 3 күн бұрын
Mukamva ndafa mudzimu wandipha bas 😂😂😂😂
@elvisnjoka8428
@elvisnjoka8428 3 күн бұрын
Akalindo ndinu achitsiru inu sindinunso omenyela ufulu anthu mumanamiza anthu zambiri....anthu ongofuna zikuyendeleni inu
@symoldicky
@symoldicky 3 күн бұрын
Inuyoso nde chitsilu chothelatu cuz ukat kumenyela ufulu kupose apa? iyeyu akunenaz zokomela kunyumba kwake or nzika zamalawi
@ChristopherManase-s1f
@ChristopherManase-s1f 3 күн бұрын
Chifukwa chiyani kodi alomwe inu. Eeeee koma anthu asanje ngati inu sindinaone
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 3 күн бұрын
Koma zilipo. Chaka chino
@elvisnjoka8428
@elvisnjoka8428 3 күн бұрын
@@symoldicky Wangokula mutu iwe galu....anthu omenyela ufulu samakhala ngati amenewa mxieew
@user-ii9ch7oz8n
@user-ii9ch7oz8n 3 күн бұрын
Kalindo palibe chazeru
@AustinNangwale
@AustinNangwale 3 күн бұрын
Uyu atipha ndithu palibe chomwe chikuyenda😂😂
@xinalungu9616
@xinalungu9616 3 күн бұрын
Kodi paja *MANIFESTO YA BON KALINDO ndi KUDANDAULA?
@PotipharEphraim
@PotipharEphraim 3 күн бұрын
😂😂😂 campaign imemeyo
@dalitson3558
@dalitson3558 3 күн бұрын
A opposition ndimakape kwambiri tikuvutika chifukwa cha agalu amenewa, angoti vendee!! Agalu osusawa
@felixsaidi6715
@felixsaidi6715 3 күн бұрын
Wachambaa iwe. Anthu amazuzuzika like this 2014 kufika 2020?
@dalitson3558
@dalitson3558 3 күн бұрын
@@felixsaidi6715 machende ako galu iwe , mcp ikufuna kubela zisankho nanga osusawa akupangapo chani stop these nonsense tactics from mcp? What kind of human being are you? The fact is our opposition is weak
@DinnesChitsulo
@DinnesChitsulo 3 күн бұрын
Chitsilu iwe
@MaryTchapo-py4hh
@MaryTchapo-py4hh 3 күн бұрын
Guys amene mukuitanira chakwera tiuzeni chabwino chomwe akuchita kapena achita?
@tasmania527
@tasmania527 3 күн бұрын
Why is it that all these noise makers are from the south? Is it that these people are jealous or they're bad people by nature? Ife kudabwa ndithu chifukwa zanyanya. From Mangochi to Machinga and to Mulanje, Phalombe and Thyolo, it's all elements of tianthu towukira, tamwano, totukwana, taphokoso, tosawopa Mulungu, tonyoza president. Should we say they're the most capable and intelligent people? It is surprising to note that APM during his time, he messed up several things including Albino killings and lack of reliable electricity etc. and these so-called Omenyela ufulu were dead silent without any condemnation of the regime, but now a Chewa is in power, we hear so many disgusting messages of hatred from the same people. Is it that they don't want either someone from the central or north to be their leader? I am baffled by the way the likes of kalindo, Ntanyiwa, Game Changer, and others express their dislike for Chakwera as if APM, Bingu, Bakili or Joyce Banda brought sanity and economic liberation to Malawi. In fact, problems faced by Malawians today emanate from the careless leadership of Muluzi, Bingu, and APM. Please do not divide Malawi because you will be the worst losers if that happens. I am not a Chewa, but I get offended if someone disrespects the president and throws insults at him. We never insulted APM and others before despite their shortfalls. Bon kalindo, you need to stop this rubbish of producing audios that disseminate hatred and propaganda because you lack substance and are not intelligent after all. You are such a bitter person that needs to chill. There'll be no achievement in all this.
@DysonTummiesSajiwa
@DysonTummiesSajiwa 3 күн бұрын
Iweyo ukhala pamenepo mpaka 2030 boma sitikusintha ndipo udzakhumudwa nthawiyo
@LovemoreSambuke
@LovemoreSambuke 3 күн бұрын
Ukatero wakhuta ndalama za ku capital hill
APULE ANYAMUKASO LERO- NKHANI
19:36
HOT 265
Рет қаралды 3,8 М.
Самое неинтересное видео
00:32
Miracle
Рет қаралды 2,6 МЛН
Minecraft Creeper Family is back! #minecraft #funny #memes
00:26
Whoa
01:00
Justin Flom
Рет қаралды 61 МЛН
Angry Sigma Dog 🤣🤣 Aayush #momson #memes #funny #comedy
00:16
ASquare Crew
Рет қаралды 50 МЛН
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH PATRICIA KALIATI
58:51
Zodiak Malawi
Рет қаралды 21 М.
BON KALINDO LERO PA 18 September 2024🙌🙌🙌
15:19
HOT 265
Рет қаралды 12 М.
FREDO MASINTHA
12:07
Fredokiss
Рет қаралды 28 М.
Seed Security: An Interview with President Bingu wa Mutharika
3:13
Vice President Chilima's visit to the SVTP (Chichewa Interview)
1:47
Shire Valley Transformation Programme
Рет қаралды 69 М.
TIKUDYA CHITEDZE!
12:26
Rodwell Lumbe
Рет қаралды 26 М.
Самое неинтересное видео
00:32
Miracle
Рет қаралды 2,6 МЛН