TIKUDYA CHITEDZE!

  Рет қаралды 30,243

Rodwell Lumbe

Rodwell Lumbe

Күн бұрын

Пікірлер: 248
@Giftmweruza
@Giftmweruza Ай бұрын
There's a time when all these will never been recalled, God is watching and will intervene shortly...... whatever God said about the last days events, has to pass. Our prayers should be to Him to deliver us out of these and grant us an opportunity to inherit his kingdom.
@Ennlesssodoma
@Ennlesssodoma Ай бұрын
Amen
@lastonmasoatenganji-bs5gf
@lastonmasoatenganji-bs5gf Ай бұрын
Lord, remember your people. You are the last hope we have✝️🛐
@rashidadan2533
@rashidadan2533 Ай бұрын
Mukadzavotela mcp 2025 , muzadya madothi , this situation had never happen in malawi , my first time to hearing this
@Hoticejazz
@Hoticejazz Ай бұрын
2001 we had this situation
@FelixGerman-gf3ps
@FelixGerman-gf3ps Ай бұрын
Komandipo
@ShakiraArridie
@ShakiraArridie Ай бұрын
Pitas time anatiuzaa kt tidzidya zitete
@rashidadan2533
@rashidadan2533 Ай бұрын
@@ShakiraArridie zitete not chitedze ,
@MavutoKamuonjola
@MavutoKamuonjola Ай бұрын
Anthu tinaiwala msanga, APM 2016 adalankhula mwakemwake kuti amene ali ndi njala azidya zitete/ziwala ndi mbewa. Nadiya msatinamize kuti uku nkuyamba. Aaaaaaaaah!
@RossanaMitha-tl9in
@RossanaMitha-tl9in Ай бұрын
Chibadwile changa,,Wani kumva anthu akudya chitedze.. Ambuye mulowelelepo..🙆
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w Ай бұрын
Ndipo kungovetelaso chakwela dziko la Malawi lidzakhala Manda okha okha ndithu
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np Ай бұрын
Zomvetsatu chisoni kwambili pamene achimwendo akumapanga matama poyankhura kut MCP yomweyo,moyo wanga umamva kuwawa kwambili, tiyeni tipange sonkhasonkha abale wanga amene tilinako plz
@Twayaibrahim
@Twayaibrahim Ай бұрын
2001 kunaliso njala bt dz iz too much mmmh Allah atitetezere
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w Ай бұрын
@@Twayaibrahim inaliko inde koma sanadwepo chiteze chifukwa tiimakagona kwa adimac koma timakagula chimanga komaso ndrama imapezeka nanga zimenezi ndi chani mmm. Mulungu yekha basi
@JonerdandhamuzMisokwe
@JonerdandhamuzMisokwe Ай бұрын
Ndipo alowerere ndizonvesa chisoni 😢😢😢
@kelvinchola739
@kelvinchola739 Ай бұрын
Bakili Muluzi TV imafotokoza molondola za mavuti amenewa , koma ena akufufuza munthuyu kuti amgwile ndi wa bodza. Ine ndikonda Bakili Muluzi TV imafotokoza nkhani zenizeni basi
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
Allah mwathandize anthu amenewa powapasa ma riziki pls pls Allah 😭😭😭😭😭😭
@JonerdandhamuzMisokwe
@JonerdandhamuzMisokwe Ай бұрын
Ambuye atithandinze kuno ku Malawi 😢😢😢😢😢
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe Ай бұрын
Kwamene tili nako kuthekera komapeza chakudya nkumadya nkumkhuta tiyeni tizigwada pansi nkumuyamika ambuye azibale athu akuvutika😭
@FatimaRehemah-gi4mp
@FatimaRehemah-gi4mp Ай бұрын
Allahumma inni as'aluka bi-annaka Anta Allah, la ilaha illa Anta, Ar-Rahman Ar-Rahim, alladhi la yahluthu …😢😢
@JamesSaiti-h1l
@JamesSaiti-h1l Ай бұрын
Mkoyamba kumva ine mmmm ambuye achitireni chifundo😢😢
@silvesterbanda-r2t
@silvesterbanda-r2t Ай бұрын
Nkhani yomvetsa chisoni kwambiri. Politics aside, Abale athuwa akufunikira thandizo la nsanga. Thanks and may Almighty God in heaven bless you Rodwel for this evidence based story shared.
@AtupeleMtogolo
@AtupeleMtogolo Ай бұрын
Ambuye atichitile chifundo njala yaonjeza mudziko lathu😭😭
@mirriamwilliam-nq9wg
@mirriamwilliam-nq9wg Ай бұрын
Ambuye achitireni chifundo anthu anu alikufa ndi njala,,, Ena akutaya zakudya zikagona,, Ena akudya chitedze,, akumbukireni ambuye
@MaryBanda-n3h
@MaryBanda-n3h Ай бұрын
Amen
@caremalawi3139
@caremalawi3139 Ай бұрын
Amen
@AshimayeGama
@AshimayeGama Ай бұрын
Wina ndiye angotenga ndalama Kuma pita ku China 🇨🇳 Italy 🇮🇹 Germany 🇩🇪 Zimbabwe 🇿🇼 komaso ku Mozambique 🇲🇿 athuake amane Ana vota Akufa ninjala mulungu amu khululukile chakwela
@ZikhonaPantshwa-qs6jn
@ZikhonaPantshwa-qs6jn Ай бұрын
Aaah mmm😢😢 nkhani Yom esa chisoni kwambili
@FelixKada
@FelixKada Ай бұрын
😢😢😢😢 zosayenda kwambiri 🙏🏾 Yehova atithangatire, 😢😢😢😢
@AckduFackson
@AckduFackson Ай бұрын
Mulungu tichotselen mulili mwagwetsa Ku dziko lathu lamalawi muchifunilo chanu😢😢😢😢😢
@InessJere
@InessJere Ай бұрын
Kuziwiliya kulonde vaulele muona ngati boma lingakulimiyani va zii 😂😂😂
@GanizaniKamvazaana
@GanizaniKamvazaana Ай бұрын
Athu akudya chitedze koma a president kumapita kwa America kykakwera njinga ayi zikomo
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w Ай бұрын
@@GanizaniKamvazaana plesdent wake utiyo mbuzi yamuthu ngati imenei
@bestonjumah3835
@bestonjumah3835 Ай бұрын
Anapita liti ku America kukakwera njinga? Kumakhara ndi info yokwanira musanalembe. Tikuyenera kupemphera chifukwa azathuwa anakumana ndi ngonzi ngati Kusefukira kwa madzi komaso ng'amba. Mulungu atichitire chifundo.
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i Ай бұрын
Mr president chikangawa manyadzi bwanji anthu akudya chiteze kuno but still you need ridership go away mr president pls Apm is coming soon to be president of this country 😀 🙏 adad God bless Apm pls 🙏
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo Ай бұрын
Malawi akupita kuti😢😢😢😢
@KenJambo
@KenJambo Ай бұрын
Eee zosakhala bwino ayi!!!
@PaulMunukwa
@PaulMunukwa Ай бұрын
AMBUYE mdaliseni mnyamatauy Rodwell
@PeterCHAGUNDA
@PeterCHAGUNDA Ай бұрын
This is so insane, apapa zafikapa kuposanso mayiko muli nkhondo,koma mr president ganizirani anthu mziko lathu,where is Malawi 🇲🇼 going,this is never happen even before
@EdwardGeorgeKasabola
@EdwardGeorgeKasabola Ай бұрын
Brother Rodwell Mulungu akudalise pantchito imene mukuyigwila, Chifukwa anthu amene ali m'bomawo saziwa kuwayendela anthu awo chimene aziwa ndikuba ndalama za boma ndikukakwela njinga ku German basi
@SleepyAnteater-bh5zo
@SleepyAnteater-bh5zo Ай бұрын
Ndipo mulungu amupatse moyo wautali Rodwell
@StellaChalera
@StellaChalera Ай бұрын
Rodwell mulungu akupatse moyo wautali ntima umeneu usausiye zikomo
@ThokoMsonkho-hy4uc
@ThokoMsonkho-hy4uc Ай бұрын
Ndilibe mawu May God intervene
@CosmasChimdikira
@CosmasChimdikira Ай бұрын
Eeish mmmh koma zomvetsa chisomo izi Mulungu akumbukire Malawi
@cosmasnkanda8193
@cosmasnkanda8193 Ай бұрын
Lord have mercy on our dear land Malawi
@shamsdeenuthmanmsikita1712
@shamsdeenuthmanmsikita1712 Ай бұрын
Ndiye muziti chakwela woyeee
@MkandawileLloyd
@MkandawileLloyd Ай бұрын
wina aziti chakwere yomweyo uziwe ndiwe garu
@thomluciouss7360
@thomluciouss7360 Ай бұрын
Kkk akudya zomwe anavotela malawi kusava
@miketholiwa1762
@miketholiwa1762 Ай бұрын
Zomvetsa chisoni kuti dziko likungoonerera anthu akuzunzika ndi njala. Admarc ili kuti imene mmati muikonza ija? Mwatilephera Malawi.
@zondanitzulumusicfly.5202
@zondanitzulumusicfly.5202 Ай бұрын
Nyimbo iyii Ni ya chitedze
@BrianNowa
@BrianNowa Ай бұрын
May God almighty bless you sir Rowell and your Team, the president and his government must watch this, akamayenda kupita kunja mbari inayi mkumalimbanilana mipando yomwe sangakhalepo mkumadzilamulira okha koma pafunika kuwasamalira anthu Maka akumidzi komwe zinthu zafika povuta, a president ngati alibe nthawi yoona mmene anthu akuvutikira koposa kudzikozekeretsa mthumba mwawo kuti awineso, mmene Malawi wafikira zikungofunika tokha tokha kuthandizana not kudikira boma kuti lithandizepo coz mmalo moti athamange ndi thandizo ayamba kaye alowetsapo zandale uku anthu akufa ndi njala Njala ndi yoopsya ndipo ndi yowawa and imachotsa umunthu, Let's unity and help each other, zinthu sizili bwino dziko lathu
@FrancisEnock-e7n
@FrancisEnock-e7n Ай бұрын
Mmmmmm zonvesa chison ambuye achitepo kanthuu
@JimmyMulewa
@JimmyMulewa Ай бұрын
Koma chakwera president akudya zamafuta anthu Ake akuvutika ndithokhoze anthu akwathu kuchikwawa amuswera ma galimoto Ake lero
@GloriaTobias-pn7rn
@GloriaTobias-pn7rn Ай бұрын
Eish ambuye atikhudze ndi dzanja lake ,mpaka chitedze abale
@InnocentKapeya-m1g
@InnocentKapeya-m1g Ай бұрын
You deserve to be Mp some where in this part of Malawi, thumbs up
@robenmatchilinga604
@robenmatchilinga604 Ай бұрын
Ambuye khunzani Malawi
@BatsonMitangaMbewe
@BatsonMitangaMbewe Ай бұрын
speechless only God knows...tipempheko even opposition party lets join hands anthuwa athandizike
@JohnWame-u3l
@JohnWame-u3l Ай бұрын
God bless our my fellow Malawians,plz,,,,
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l Ай бұрын
Mr Mulungu apitilize kukudalisani pazabwino zimene mumachitazi
@EstherManda-ex3bc
@EstherManda-ex3bc Ай бұрын
Mmmmmm zokhudza Koma 😭
@emilymasiye2674
@emilymasiye2674 Ай бұрын
I'm speechless 😢😢 God have mercy upon your children 😭😭🙏
@asamzymw571
@asamzymw571 Ай бұрын
Or ntavota kutulo singadzavotere chakwela ine,, munthu kuononga ma billion kupita Ku china so wabwera Malo moendera kuchitedze nkumapeta kukaona ng'omve zoona?😢😢
@HendersonMorson
@HendersonMorson Ай бұрын
Wina nde azit ziko likuyenda bwino Ambuye akuyendele😂😂😂😂
@ComfortSabe
@ComfortSabe Ай бұрын
Taonani anthu mene adzutikila koma chikangawa sakuona ayi,,mulungu achitepo kanthu
@WasiliMuhammad-r6u
@WasiliMuhammad-r6u Ай бұрын
Manganya ndi chakwera Osayankhula kali konse apa koma akuti akuyembekela ku kuti anthu avote ndichome iwo akuziwa
@FidesChandama
@FidesChandama Ай бұрын
Malawi wathu mwezi uno kudya chitedze mvula sidagwe zachisoni kwambiri chikangawa akukaona ng'ombe anthu akuvutika
@AishaTawakali
@AishaTawakali Ай бұрын
SubhanAllah!! May Allah make it easy for them. This is really sad
@GeorgeSoko-k3t
@GeorgeSoko-k3t Ай бұрын
Wina Ali busy kukayendela ng'ombe Koma zili zake kale 😢
@JustinLipipa
@JustinLipipa Ай бұрын
Aaaaaaaa Sikangawa atipha, kukayendera ng'ombe m'malo moyendela wanthu.
@GoodsonsambanThapulen-vb8sg
@GoodsonsambanThapulen-vb8sg Ай бұрын
My good😢 God bless us
@KondwaniLungu-x5l
@KondwaniLungu-x5l Ай бұрын
Wina ndie si mmene akuendela maulendo akunja , moti samamva kuti anthu akuvutika nzikomuno
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie Ай бұрын
Akulu akulu koma mukundiuza kuti kuchokera 1964 pomwe tidalandila ufulu wozilamulira koma ANTHU akugona nyumba zoyika zisaka pa windo😮😮😮koma Malawi ndi dziko KAPENA kotaya zinyalala
@NoahKalima
@NoahKalima Ай бұрын
Kupeza kusiyana ,mukakhala pabwino ziyendani kuti muziwe KUT zikomo kulinji
@Ayichamatack
@Ayichamatack Ай бұрын
Rowero murungu azikudarisa mukukwanisa kukaona anthu amene akusowa thandizo pomwe Ena pamene akukaona ng,ombe kusanje zovesa chisoni
@MaryJefry
@MaryJefry Ай бұрын
Ambuye mulowerelepo mpaka chiteze abele inu sindinanvepo ine
@victorauwana7258
@victorauwana7258 Ай бұрын
Kodi mesa mcp mukumayiuza kuti boma ndilomweli?
@UnicekapachikaHanzwell-zz8te
@UnicekapachikaHanzwell-zz8te Ай бұрын
God bless our country everything is control from God 💞 In your will trust 🙏
@YusufGafa-s3j
@YusufGafa-s3j Ай бұрын
Ndi mulungu ekha angatipulumutse ku Malawi kuno kudzela mwa anthu achifundo athandize anthu awa
@Dawoodjabali
@Dawoodjabali Ай бұрын
Andale ndionvesa chisoni please Malawian tisamangowona ndale athu akamayakhula, see this timangonva kuti kunali 19 49 akalenu zinali chonchi kapena ?
@giftkayome3568
@giftkayome3568 Ай бұрын
Ndipomwe wina akuyendetsa njinga ku Germany anthu akufa ndi njala
@KateChantelle
@KateChantelle Ай бұрын
Tiyeni amalawi anzanga tiyambe ulimi wachinangwa this might help alot we must not depend on chimanga
@JimmyMaster-l1x
@JimmyMaster-l1x Ай бұрын
Galu wina ulendo kokawona ng'ombe anthu akufa ndi njalaaaaa Mboma ndilomweli Mukunatu gayz
@GeraldThobowa-ny7ng
@GeraldThobowa-ny7ng Ай бұрын
What is the title of the song in the background?
@cliftonchikhwasa6489
@cliftonchikhwasa6489 Ай бұрын
People like you by Morgan heritage
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 Ай бұрын
Ambuye alowerere anthu akuvutika awa💔💔💔
@MadalitsoBokosi-j3u
@MadalitsoBokosi-j3u Ай бұрын
Eshiiiii ndidapulumukira phunga 2001 koma ambuye awakhuze nyengo yowawitsa ngati imeneyi
@BRIDGETMagwira
@BRIDGETMagwira Ай бұрын
A Rodwell ine chomwe ndikufuna ndi contact yanu kuti mwina titapempha mwa anthu thandizo tingakupezwni bwanji izi ndi zokhuza kuno ku south Africa.
@MosesDicostar
@MosesDicostar Ай бұрын
Mulungu dalisani Malawi
@JacquereenPereira
@JacquereenPereira Ай бұрын
Athu akuvutika kugona zisakasa tsogoleli wadziko akungo njoya kuendela ngo'mbe athu aku chitedze chocho akufuna mavoti kwa athuwa shame on you chikangawa
@EthelDiston
@EthelDiston Ай бұрын
Kusamva a Malawi munyanya mukatero muzivoteranso MCP
@MenasKaliati
@MenasKaliati Ай бұрын
God may protect us please
@JohnWame-u3l
@JohnWame-u3l Ай бұрын
Ena opandanzeru akuti BOMA ndilomweri,kupandanzerunkuyankhulatu,kuchikamwa😡
@LonjezoPhiri-d3b
@LonjezoPhiri-d3b Ай бұрын
Yona atathawa ntchto ya Mulungu,anazuzitsa onse anali mchingalawa,uyuso atizuzitsa ndithu
@hopembendela
@hopembendela Ай бұрын
Koma mulungu asalekelele malawi please anthu matupi ngati kudwala koma kuli kusowa chakudya muthupi
@Chikwawa
@Chikwawa Ай бұрын
Koma dziko limeneli mtsogoleri alipo?
@Mohammed-sk1fy
@Mohammed-sk1fy Ай бұрын
Zosayenda ndthu amwene eeeehh
@PraiseMasinga
@PraiseMasinga Ай бұрын
Ndalira pakana anthu kudya chiteze ambuye mulowelelepo mmmmmmmm
@AlfajarAlfajar-s3o
@AlfajarAlfajar-s3o Ай бұрын
Ndiye wina aziti boma ndilomweli MCP osazayivotelaso
@caremalawi3139
@caremalawi3139 Ай бұрын
AMBUYE MUTICHITIRE CHIFUNDO😢😢😢
@AtupeleChitenje
@AtupeleChitenje Ай бұрын
Koma mulungu awaone athuwa please
@giftmakoyo1441
@giftmakoyo1441 Ай бұрын
pulesedent ali busy kuyendera makola ango'ombe zaweni shame on chikangawa
@wallezysmooth4169
@wallezysmooth4169 Ай бұрын
Boma ripite malo ngat amenewa akagawe chakudya kuti anthu apulumuke kunjara komaso kwathandiza ndrama yogaisira chimanga chonwe angagawire nthawi ya Boma tsopano kuphatikizapo anthu akufuna kwabwino kuti akafikire anthu onse ambari imeneyo nkwathandiza chakudya komaso ndrama
@auspiciousmaloya
@auspiciousmaloya Ай бұрын
Wina kumati boma ndilomweri uku akukayabwidwa chitedze kuti adye yet akumipandowo akudya madzila anthu ndife zinsilu
@AustinBai-rg2cu
@AustinBai-rg2cu Ай бұрын
😭😭😭😭😔😔😔My country Malawi
@ivymakiyi
@ivymakiyi Ай бұрын
Kulibe madzi mmadambo?
@kennethkaunda3636
@kennethkaunda3636 Ай бұрын
Pamene chakwera ndi mkazake busy ndi mandege wa kunja
@fannyzimba149
@fannyzimba149 Ай бұрын
Chakwera Chikangawa ,kamajekete, Jezebel Belezebulu mukuti bwanji apa?koma kumangoyenda kutha ndalama mmalo mopulumutsa miyoyo yawanthu mulungu akukhutdzeni ndikukukanthani
@JoaquimElidioChiwisse
@JoaquimElidioChiwisse Ай бұрын
Osamangoti tikuvutika lima kunja Kuno anthu ndiye akuvurikadi ambuye akhuzeni Ana anu kulibe kwina kothawila komakwainu basi
@YusufGafa-s3j
@YusufGafa-s3j Ай бұрын
Zomvesa chisoni kwambiri 🙆🙆🙆🙆🙆🙆
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete Ай бұрын
Zokudya katatu zija how far Lazaro waumphawi manyaka enieni basi
@cym4052
@cym4052 Ай бұрын
Za maudzu kuno Ku Mangochi Ku Mselema Kwa Group village mtola anthu akudya zimenezo akumagona nayo njala ..... Last year kunalibe mvula...
@felixmbama3999
@felixmbama3999 Ай бұрын
Zosayenda mulungu chitani nawo anthuwa
@MetrinaChikwawe
@MetrinaChikwawe Ай бұрын
Muzilima oasamadalila zopatsidwa musiyeni chakwera chitedzeso chimakoma
@Numerinjateni
@Numerinjateni Ай бұрын
Boma ndilomweli km tizasintha chipani cholamulandi president
@comfortfungulani
@comfortfungulani Ай бұрын
Bwana ngati nkotheka mudziyika English Subtitle mma Videos ofunika thandizowa ntchitoyi ndiyayikulu
@MarianoRaulPhir
@MarianoRaulPhir Ай бұрын
Ena nkumati njala kulimbe
@Margaret-t7m
@Margaret-t7m Ай бұрын
Eish ndamva chisoni 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@ChifundoNinje
@ChifundoNinje Ай бұрын
Mmmm zovesa chisoni
@WilfredGunya1
@WilfredGunya1 Ай бұрын
Izizi tegopepha kwa athu ari kutherekera kupatura andarewa pot dziko rino gt tuzuzika ndathu andarewa
@WinesYusufu
@WinesYusufu Ай бұрын
Zitsiru zaathu muzaona muthawi yovota azavotelaso zitsiru
JETU vs 7 GUYS (POP THE BALLOON BLIND DATE )
39:00
Madness Entertainment
Рет қаралды 136 М.
風船をキャッチしろ!🎈 Balloon catch Challenges
00:57
はじめしゃちょー(hajime)
Рет қаралды 33 МЛН
World’s strongest WOMAN vs regular GIRLS
00:56
A4
Рет қаралды 22 МЛН
Family Love #funny #sigma
00:16
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 38 МЛН
Каха и лужа  #непосредственнокаха
00:15
Akumagwira maganyu olima nkumalipidwa ufa
10:08
Rodwell Lumbe
Рет қаралды 13 М.
Maria wa zaka 15 amalera azibale ake
16:11
Rodwell Lumbe
Рет қаралды 26 М.
Ogulitsa Ziwalo Xa Anthu  Agwida Ku Thyolo.
1:27:49
Malawi Lovers 🇲🇼
Рет қаралды 229 М.
phuzitsi wina amene anamwalila, waonekera Kwa achibe wake
30:56
Balanço semanal CK & Govate
Рет қаралды 15 М.
Mwana akanzi aite bhuru remudanga naBaba vake (6 Nov 24) repost
52:55
Bhozhongora (Topic)
Рет қаралды 7 М.
風船をキャッチしろ!🎈 Balloon catch Challenges
00:57
はじめしゃちょー(hajime)
Рет қаралды 33 МЛН