BON KALINDO KUYANKHULA ZA CONVENTION YA PP🙌🙌🙌🔥🔥

  Рет қаралды 10,817

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 28
@stuartsangaloti8461
@stuartsangaloti8461 9 күн бұрын
If Marry Chilima is to stand as UTM president I do see Dr Joyce Banda supporting her I do see 90 percent of candidates supporting her I do foresee a landslide and the rise of a new dawn. Vote Marry Chilima...... Ma Bishop please approach this woman please she's our last hope.
@edsonwolemba3011
@edsonwolemba3011 9 күн бұрын
Cashgate leadership
@AllanaChiphazi
@AllanaChiphazi 9 күн бұрын
😮A Joyce Banda ayiwala cashgate hahaha
@MsondaBanda
@MsondaBanda 8 күн бұрын
Chaboza ichi
@billymhoni9527
@billymhoni9527 8 күн бұрын
Mai mary is the Key for UTM malawi...
@MuhireDominic-rw4vf
@MuhireDominic-rw4vf 8 күн бұрын
That woman bolaninso m c p 😂
@MisheckAselo
@MisheckAselo 8 күн бұрын
Kkkkkk zoona Mr DC kungong'alura 🎉🎉🎉
@RaphiqueYusuf
@RaphiqueYusuf 8 күн бұрын
Koma Bon Kalindo ndikuyamikireni mumatsatiradi,zowonadi mayiyu walankhula mopereka chiyembekezo kwa anthu osawuka.
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza 9 күн бұрын
Bring moreee!!! ❤
@DickisonyusufChiwalo2
@DickisonyusufChiwalo2 9 күн бұрын
Pls joyce banga send bus south Africa we are seafaring here boma lakuno likutigwila ndikumatibvutititsa chonde tumizani mabasi aboma pumani boma pls pls
@fortunekamdumli-xy5zn
@fortunekamdumli-xy5zn 8 күн бұрын
Kamala Harris sangawine
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 9 күн бұрын
Kalindo is a confusionist. He can't tell you the truth. He hates the current leadership bcause he was not given minesteeial post. Kagwere uko ndi dpp yakooyo
@AhamaduKareem-x5y
@AhamaduKareem-x5y 9 күн бұрын
Zoona bwana
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 9 күн бұрын
Komatu ndi Mai Joyce Banda yemweyo amachemelera chakwera
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 8 күн бұрын
Tiyeni tipeze munthu yemwe sanalamulileko, mmalawi,onse awa,ndi okuba
@georgeraphael8198
@georgeraphael8198 8 күн бұрын
Cashgate,kugulisa ndege mai emwe anaononga dziko la Malawi kwa nthawi yochepa bola Chikangawa emweyu than Joyce Banda😂😂
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 8 күн бұрын
Koma iwe ndi Nyani WA MUNTHU.
@hamissimdoka9665
@hamissimdoka9665 8 күн бұрын
Kulepherako sikuti alephera onse iyeyo Joyce Banda sikuti anali mu tonse alliance momo. Ndiye lero akubwebweta chani misala eti
@AndrewChirombo
@AndrewChirombo 9 күн бұрын
Mai amenewa simunthu wabwino akunama amenewa ndi nthila kuwili saziwa chimene akufuna
@Blessings-b7h
@Blessings-b7h 9 күн бұрын
You're right ndi mmai oipa kwambiri.
@georgeraphael8198
@georgeraphael8198 8 күн бұрын
@@AndrewChirombo mai wakuba wakupha
@SteveZimba-e8s
@SteveZimba-e8s 8 күн бұрын
Koma born karindo uku ukunena zoona ku utm ofunika kusogolera ndi Mary chilima chifukwa chilima sadasogolele dziko ndipo chipanichi chikhoza kumangidwa bwino imvani inu utm msamutaye Mary chilima ndi key wanu
@SlindiryLoveness
@SlindiryLoveness 8 күн бұрын
Iweso mutuwako sikuyenda bwino satana iwe bwanji uzingolimbana ndi dpp yakoyo zazii zimene ukuyankhura
@DeviLinya
@DeviLinya 9 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤❤
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 9 күн бұрын
Bola asdzalowensenso cashgate,,,codzadziwa mcipande poomola
@chadreckchibwithala1493
@chadreckchibwithala1493 9 күн бұрын
u don't know ndale nayi banda ali ndi mcp u must know that. adpp munya akalindo ali busy pa ganyu wawo
@ganizanistephano-gi5lr
@ganizanistephano-gi5lr 8 күн бұрын
Share fone number ya Bon Kalindo pls
@MonicaChimangira
@MonicaChimangira 8 күн бұрын
Galu iwe
WILL IT BURST?
00:31
Natan por Aí
Рет қаралды 48 МЛН
Brawl Stars Edit😈📕
00:15
Kan Andrey
Рет қаралды 43 МЛН
Kenny Kunene's take on the GNU's performance thus far
19:08
SABC News
Рет қаралды 95 М.
Newspapers | 16 September 2024
8:24
SABC News
Рет қаралды 6 М.
BON KALINDO ANKAKHALA KU CHIKANGAWA-17 September 2024
17:21
WILL IT BURST?
00:31
Natan por Aí
Рет қаралды 48 МЛН