BON KALINDO LERO PA 21 DECEMBER KUNG’ALURA MOSAOPA AKUTI IYE ANAFA KALE

  Рет қаралды 36,293

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 118
@HildaLimbusha
@HildaLimbusha 7 күн бұрын
Don't blame Chilima,Laindon,Timothy n others mpuno sabotage,nobody knew what was to come
@SamsonChitezi-o6g
@SamsonChitezi-o6g 8 күн бұрын
Mphavu yachuluka chakwera uchisiru ukaguriseso dambwe kwanu garu
@BerthaMATUMBO
@BerthaMATUMBO 8 күн бұрын
Go on Boni kalindo mumayitimilira
@RichardJuly-s7f
@RichardJuly-s7f 7 күн бұрын
Aaaah malawi😰😰😰😰😰😰
@ProgloKazembe2-eu7hn
@ProgloKazembe2-eu7hn 8 күн бұрын
Nkhani ya Nyanjayi Bwana APM mukanalowelelapo mwina mkuwathandiza aphwanuwa kuobola Nyanma yathu Pliz...
@jaafarstenala1166
@jaafarstenala1166 8 күн бұрын
Uyu kwasala atigulisa tonse bas
@Anney-w1j
@Anney-w1j 8 күн бұрын
Akamaliza kugulisa nyanja kenako agulisa dziko mr chikangawa bola angofa
@BazukaChikungaM23
@BazukaChikungaM23 9 күн бұрын
DC akasongo awa atiphweteka Koma tingapange njira iti Kut akasongo awa atisiye chifukwa Ife stimatha kupha❤ One love Koma Kasongo atiphweteka
@LucyBakali
@LucyBakali 9 күн бұрын
Kodi is
@LucyBakali
@LucyBakali 9 күн бұрын
Kodi iwe chakwera wa suta. Chamba wationj 11:04 11:20 11:50
@DiversonMotah
@DiversonMotah 9 күн бұрын
Inetu nnafusa kuti kodi chakwerayu ndi mmalawiiiii????
@DiversonMotah
@DiversonMotah 9 күн бұрын
Uyutu mungoona kumusiya aimaliza Malawi
@DiversonMotah
@DiversonMotah 9 күн бұрын
Uyu ngongodutsaa akatha kugulisa aziita kwao
@GodfreyKamphiripiri
@GodfreyKamphiripiri 9 күн бұрын
The DC woyeeeeeee ❤❤❤❤❤❤Fireeeeeeeeee Fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee
@hamiltonsolomon3756
@hamiltonsolomon3756 9 күн бұрын
The DC 👌..Umakwana 👌 ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@BlessingsMatiki-g2p
@BlessingsMatiki-g2p 8 күн бұрын
Ubwele
@MarthaBango-s3y
@MarthaBango-s3y 8 күн бұрын
Tanzania ikuchita kudziwa bwino kut palibe tingachite,akudziwa chitetezo chanthu mene chilili kosaka ndeka anakhala akuwaitana,mapephapepha awa ationela kudambwe akudziwa tilibe chilichonse olo nkhondoyo sitingathe kumenyana nao💔💔
@MikeChimombo-n6w
@MikeChimombo-n6w 7 күн бұрын
Chikangawa watipweteka
@BORNFACESIMBOTA
@BORNFACESIMBOTA 7 күн бұрын
Kma zoona bs nyanja yapitad 🤔🤔🤔
@dicksonmwale8617
@dicksonmwale8617 9 күн бұрын
Zosayenda izi,Mangochi, Salima,Khotakota,khatabay,Mzuzu pofunika wanthu achitepo kanthu.Nyanja agulitsa bwanji munthu wakutali ndinyanja.Wosasiwa mpang'ono ponse ubwino wake.
@DianaKaluwa
@DianaKaluwa 8 күн бұрын
Nyanja yapita guys 😢😢😢
@FloridaMakwinja-eq2ek
@FloridaMakwinja-eq2ek 9 күн бұрын
Kodi ayima bwanji 2nd Term pomww anasayina gwilizano wa 5 yrs ndi Chilima Iye manyazi alibe poyimansopo😊
@JacquereenPereira
@JacquereenPereira 9 күн бұрын
Kwacha ndi iyi ikungo gwa daire katatu patsiku ikugwamamawa masana madzulo Achekwela anabwela kudzangosokoneza dzikoli
@JosephEphraim-j9x
@JosephEphraim-j9x 7 күн бұрын
Akazi atatu akumuzunguza mutu uyu
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 9 күн бұрын
Tadzimvera chisoni.......dziko ....la ....malawi ranthu lanukha ..... kwambili...Mcp Anthu oipa heavy .......yaposa zipani zonse😢😢😢😢😢😢😢💔
@lilianprince661
@lilianprince661 9 күн бұрын
Amalawi feeee penapake ndife opepela kwambiri munthu tikumuona akuononga ziko lathu chovuta ndichani tose tizuke ndikumuchosapo monga mene munampanga peter muthalika
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 9 күн бұрын
Mene apangra ku South Korea amuchosa km kuno kupepetuludwa koma
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya 8 күн бұрын
Ndiponso
@BORNFACESIMBOTA
@BORNFACESIMBOTA 7 күн бұрын
Ndipo zikukanika pati kma?
@KarimuSaidi-c3z
@KarimuSaidi-c3z 8 күн бұрын
Chakwela kuti zimuchitile bwino kpena uti zizamuchitile ubwino akazagoluza azagofa, infa yokha ndiyomwe ikhoza kumupulumusa
@OsmanGift-f4p
@OsmanGift-f4p 8 күн бұрын
Koma mpakana kugulisa manja😮😮😮😮 kwatani muthu ameneyu
@EdwardMathuwa
@EdwardMathuwa 9 күн бұрын
Koma apapa Malawi wafikapo we made a very big mistake kuika ng'ona party mu government
@Samson-ve5rs
@Samson-ve5rs 8 күн бұрын
Zili Mitu phwii Ngati Za nzeru Koma abetsa nyanja, Tanzania kungodzambatuka pamene paja ndikutenga nyanja
@ShabanMajor
@ShabanMajor 8 күн бұрын
A Nyo i want my money 😂😂. Mr kasongo bolan akhale president ine ndikwatire mitala please winiko 😅😅😅😅.
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c 8 күн бұрын
😢😭😭😭😭mpaka kugulitsa nyanja zandionjeza kwambiri chakwera munthu oipa kwambiri amalawi tiyeni tikwiye tipite paseu wationjeza kwambiri chakwera
@BridgetMazuko
@BridgetMazuko 8 күн бұрын
Mizimu ya anthu 9 yawazunguza kwambir make akupanga zosayenera pena pake kumawavesesa anthuwoa anapha anthu ambiri
@alickkachepa3801
@alickkachepa3801 9 күн бұрын
Bushit chakwera my foot for selling Malawi lake 😣😣😣
@MustafaAliMakwinja
@MustafaAliMakwinja 8 күн бұрын
Tatiphudzitseni nkhani yanyanjayi. Tinamva kuti pali lamulo loti ngati nyanja ili pakati pamaiko awiri ndiye kuti onsewo amayenera kukhala ndi gawo mbali yawo. Kodi pamenepa tagulitsa nyanja kapena kuti chigamulo chaperekdwa ndi oweruza?
@NelsonMataka-d1w
@NelsonMataka-d1w 8 күн бұрын
Kungotangwanika ndi zopanda ntchito. Busy kuzikundikira.
@YounusWabullah
@YounusWabullah 9 күн бұрын
😭😭😭😭😭 eeee ayitaaa km umene ndi mtundu wanji wa anthu km achina chikangawa wa
@NolaniHoyi-tv3nq
@NolaniHoyi-tv3nq 8 күн бұрын
Mr Dc😊
@ObvinessKBanda
@ObvinessKBanda 8 күн бұрын
Mbali imodzi ya nyanja yagulitsidwa chifukwa A Chakwera akufuna mafuta azichokera ku Tanzania ndiye apanga deal yogulitsa mbali imodzi ya nyanja
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya 8 күн бұрын
Magulu ogulitsa katundu wamnyumba kkkk
@Nelsonmatenda
@Nelsonmatenda 9 күн бұрын
Kalindo sakulakwisa ai ndipo iye polowa utm + mcp ankawona ngati chakwera being abusa atithandiza & kalindo anatuluka mu tonse atawona kuti mcp ndi manyaka ..A kalindo pitilizani potimenyela nkhondo osaukafe
@TheraAufi-q3n
@TheraAufi-q3n 9 күн бұрын
Nyanja zoona 😭😭😭😭
@TineKaliati
@TineKaliati 8 күн бұрын
Why atsogoleri a Malawi
@FelixJumby
@FelixJumby 8 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 THE DC mwana ooopwa 😂😂😂😂 timaku yadilani ambuye azikudalisani ankolo anga
@GestardKamanga-r7w
@GestardKamanga-r7w 8 күн бұрын
Achakwera atigulisa mmmm tilibe musogileli ku malawi
@PatrickDiness
@PatrickDiness 9 күн бұрын
Chi Dc chikati afit inuyo!anthu asatanic inuu!!anthu akumadzi inuyoo😂😂😂
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya 8 күн бұрын
Akati Dzikoli silachaamanu😂😂😂😂
@Alex-d2h
@Alex-d2h 9 күн бұрын
THE DC 🔥🔥🔥
@lilianprince661
@lilianprince661 9 күн бұрын
Pano ndiizo part of nyanja yapita ndipo zikolose pompano likhala mumanja mwa america kozekani
@ChifundoJeffrey
@ChifundoJeffrey 9 күн бұрын
Koma namayenda mpaka kugulitsa Nyanja zomvetsa chisoni 😢😢😢😢
@annievitumbikonkhoswe770
@annievitumbikonkhoswe770 9 күн бұрын
Okalindo, mukuyankhula zomvekako sometimes, koma mufuna anthu adzavotere ndani,, bwanji osapanga chipani chanu tidzakuvotereni inuyo kukhala president?? Nanga campaign yo mukumenyera ndaniyo??? Ndani angalikhonzeso dziko la Malawi???
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 8 күн бұрын
Mazising'anga amene mumachiza nthenda yamisala konzani mankhwala muwadyetse onse amene akuti boma ndilomweli yense amene akuti chakwela aimanso 2025 azimwa mankhwala ochiza misala
@ManesKamtambo
@ManesKamtambo 9 күн бұрын
Mmm yapita Ku Tanzania,zikuti bwanji Kodi amnzanganu,AAA chakwer must be serious
@FrancinaMalika-kw6pt
@FrancinaMalika-kw6pt 9 күн бұрын
Ubwino wake Kalindo anavomereza kuti zinalakwika ndipo anazindikira changu ndikubwerera msanga
@HassanBabujr
@HassanBabujr 9 күн бұрын
The DC ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@David-z9o4m
@David-z9o4m 9 күн бұрын
Yona analidi mtumiki wa mulungu ndthu chifukwa atakana ntchito ya mulungu pamapeto pake anabwelela kwa mulungu osat Ziwanda ndkuziona leroz za MCP
@GiftBanda-s6c
@GiftBanda-s6c 9 күн бұрын
Koma nditukwanaaaa
@JamesBrown-gx8my
@JamesBrown-gx8my 9 күн бұрын
Bingu adawauza kuti ndikuphulitsani sadaneneso mfweeee!!!
@ChanceGondwe
@ChanceGondwe 9 күн бұрын
Koma Chakwera azanyongedwa ndithu. Kodi watenga dzikoli ngat ndi lake eti?
@JoefreyGongoni
@JoefreyGongoni 9 күн бұрын
Kodi mthundu wanyau siathu , ngati amanya kukhu yosaphika kusonyeza kulimba mtima kupha athu
@TheraAufi-q3n
@TheraAufi-q3n 9 күн бұрын
Km ndi lake Malawi yomwe mulungu amulange mwana wahule amenities
@KarimuSaidi-c3z
@KarimuSaidi-c3z 8 күн бұрын
Koma mwati mwansoka atatu wabwladi ndikuwina chizachitike ndi chani
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 8 күн бұрын
Later fight each 🤔🤔🤔🤔
@AndrewKanyemba-zu5mg
@AndrewKanyemba-zu5mg 8 күн бұрын
So sad 😭😭
@MaureenNgoma-p7l
@MaureenNgoma-p7l 9 күн бұрын
President wa anthu osauka ngati ifeyo
@trickermussa472
@trickermussa472 9 күн бұрын
Asilikali anthu analephela kusaka ka ndege ka chilima angakwanise kumenyana ndi asilikali aku tanzania
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 9 күн бұрын
Achina chikangwa mcp machimo
@StevenTembo-mb7rm
@StevenTembo-mb7rm 9 күн бұрын
Where is the minister of homeland security and the inspector general of police
@IsaacBwanali-m8c
@IsaacBwanali-m8c 9 күн бұрын
Busy with monitoring the opposition
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya 8 күн бұрын
Kuti angatani,oti onse ndi amodzi?
@AfraidzembaMalume
@AfraidzembaMalume 9 күн бұрын
Ndimakunyadilani malumemumatisengula maso
@HusseinMoffatt-mi1fl
@HusseinMoffatt-mi1fl 9 күн бұрын
Tilibeso president zikolino awa ndimanyaka namapwalauyu sangatithandizeyi
@JoefreyGongoni
@JoefreyGongoni 9 күн бұрын
MCp it's an evil forever , God have mercy on Chakwera and his evilnesses , shame on Yu Chakwera and your evil deeds
@AlickRichard
@AlickRichard 8 күн бұрын
Nyanja yapita bas anatiziwa kut tilibe kalikose kot tingazichite défend pangondo
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 9 күн бұрын
Kalindo mundiperek moni kwa Timothy Ntambo komaso Gift Thirapenzi
@PhilipoGoji
@PhilipoGoji 9 күн бұрын
Chakwera simunthu koma satana
@PaulRice-n1f
@PaulRice-n1f 9 күн бұрын
Koma guys chakwera Abwela kudza lamula dziko kapena kudza sakaza dziko Ulamùliro wamtundu waja uwu
@PromiseJere-m2j
@PromiseJere-m2j 9 күн бұрын
I feel sorry for malawi 😢😢
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 9 күн бұрын
Aaaa agulisa ATSATI ALANDA AYI ANGOGILATSA MALAWI YOSE NANGA TATSALA PATI PATI UCHISILU WA CHAKWELA KUKONDA NDALAMA CHILIMA ANATISILA MAVUTO AMALAWI AAAA DZISILU ZA MCP AKUCHEDWA NDIKUMATI BOMA NDILOMWELI UKU DZIKO LIKUTHA A MCP AGALU KWABASI
@tracybennie7783
@tracybennie7783 8 күн бұрын
Áyi. Zikomo
@ElizaKumwenda
@ElizaKumwenda 9 күн бұрын
Ndipo chimunthu chimenechi amangokhala ngati alibe mutu bwanji
@PeterKampiraBanda
@PeterKampiraBanda 9 күн бұрын
Tamuwuzen chakwera atumizeko anyamata azikwanje,
@InnocentZebra-ho4th
@InnocentZebra-ho4th 9 күн бұрын
Koma guys !!! Tigulisidwa tonse😢
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i 9 күн бұрын
The DC
@VioretMandolo
@VioretMandolo 9 күн бұрын
Zosayenda
@WilliousNyirongo
@WilliousNyirongo 9 күн бұрын
Uzimvere chisoni kaye kenako utiuze bwinò waiwala kut wapangisa zosenzi ndiweyo,sitinayiwaletu
@MissyThobve
@MissyThobve 9 күн бұрын
The Dc
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 9 күн бұрын
Amalawi ndi ife anthu omvetsa chisoni
@ShamzySteve
@ShamzySteve 9 күн бұрын
Koma charakwe ndiopusa kwabasi manja mwake
@paulinechitenjere846
@paulinechitenjere846 9 күн бұрын
Em
@ClementZintula-wi4tz
@ClementZintula-wi4tz 9 күн бұрын
Koma guys
@VincentKamwendo-e9t
@VincentKamwendo-e9t 9 күн бұрын
Kalindo and your friends you contributed also to these problems,, today you are appealing to us that we should boot out this govt,, you should also be at front rather than your voice
@ChrispineMuzungu-l8h
@ChrispineMuzungu-l8h 9 күн бұрын
Inu let's not stop blaming this man but find a better way
@BesterTheu
@BesterTheu 9 күн бұрын
A​@@ChrispineMuzungu-l8h awo nde mau😮
@IsaacBwanali-m8c
@IsaacBwanali-m8c 9 күн бұрын
When did Kalindo become part of selling L Malawi?
@kingsleymsampha2260
@kingsleymsampha2260 9 күн бұрын
Kalindo sanavote yekha kuti Chakwera awine. Ineso I voted but I regret my vote.
@LucyKamoto-li9ob
@LucyKamoto-li9ob 9 күн бұрын
It is not Bon Kalindo
@JamesRaphael-k7c
@JamesRaphael-k7c 9 күн бұрын
That's being awitchcraft not aleader.
@MoyendaChileka
@MoyendaChileka 9 күн бұрын
😂😂😂
@PiassDayit
@PiassDayit 9 күн бұрын
Mako chakwela mutu siwukugwila
@hawardgonde-zd4od
@hawardgonde-zd4od 9 күн бұрын
Kalindo, chilima,mtambo . Munatilakwira
@ChrispineMuzungu-l8h
@ChrispineMuzungu-l8h 9 күн бұрын
Mmalawi muno mulibe anthu bc Aaaa mpaka our lake mw kugulisidwa aaaa km amalawi
@WilsonMbendela
@WilsonMbendela 9 күн бұрын
Tithawila kuti abale
@JamilahEmmanuel
@JamilahEmmanuel 9 күн бұрын
Kmtu lero sitinalandile moni tangofikila pa kolasi🤣🤣
@salmankhanofficiel.5018
@salmankhanofficiel.5018 9 күн бұрын
Ati eee ee eee koma inu zoona nyanja 😂😂😊
@HenriKhenyeza
@HenriKhenyeza 9 күн бұрын
😢😢
BON KALINDO LERO PA 30 DECEMBER MPAKA KUFIKA POYANKHURA IZI?
18:14
99.9% IMPOSSIBLE
00:24
STORROR
Рет қаралды 31 МЛН
Cheerleader Transformation That Left Everyone Speechless! #shorts
00:27
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 16 МЛН
LIVE: UBC LEERO NE MARION NAKITENE | DECEMBER 30, 2024
UBC Television Uganda
Рет қаралды 379
From poverty to progress: 1 year of cash impact | GiveDirectly
3:49
99.9% IMPOSSIBLE
00:24
STORROR
Рет қаралды 31 МЛН