The DC Boooon Kalindo mukamati makape mukuwalekeza komano muziti ife a Malawi ndife amasikini ma street kids ndiye ifeyo president mwanthu ndi ochitisa manyazi kwambiri tipemphere Kwa Mulungu kuti president amene akutenga boma pa 16 September 2025 azatikonzere mavuto osanenekawa
@ChisomoYosefe8 күн бұрын
exactly
@ChrispineMuzungu-l8h8 күн бұрын
First comment I come in peace the DC 🎉🎉🎉
@chirwaellace10937 күн бұрын
Keep it up vitu
@GabrielKbanda7 күн бұрын
Olaruwa,,,,,,,VA mcp this is my Malawi amene amagwira mbendera ya Malawi SAOPA TIDZAFERA MBENDERA IYI
@akilaentertainment19937 күн бұрын
Timakutsatani daily I hope tsiku lina malawi azakhala okomela tonse
@JamesPhilimon-h2w7 күн бұрын
Inetso l appreciate Vitumbiko Mumba for everything he is doing
@user-hh8eu8dr4u8 күн бұрын
We lucky to have you brother, you stand on justice, you fight for the people
@SmeldoBlack7 күн бұрын
Mwana oophwya kwambiri 😂😂😂😂😂
@WilliamNhlane-fd9hi7 күн бұрын
Good job Minister vitumbiko mumba
@NellieChikuse7 күн бұрын
Ambuye bwerani mudzaweruze dzikoli😢
@GraceShaibu-i9d4 күн бұрын
Makape a MCP 😂😂😂😂😂
@MathewsMakalan-l6v8 күн бұрын
The dc mwana oipa kwambili auzeni anthu awa osava aphaso wao yemwe kuntyolo anthu opanda chisoni awa auze born kalindo the dc
Chikangawa akukatenga balance ya nyanja..kodi munthu angakulande nyanja ndikumapita konko🤔🤔
@ElediyaWatch7 күн бұрын
Ulemu wanu the DC
@Bbbbwesgtcjoug7 күн бұрын
Bola Inu olemeranu simupempha koma kunyoza mwezi ukatha kulandila bola mimatha man koma lapani msanga yesu amakukondani ndale sitidya ndipo ndale mulibemo chipulumutso sorry 😅😅😅
Of course ndi zabwino zomwe akupanga V_Mumba,, koma tiganizilenso anthu omwe akuchotsedwa ntchito chifukwa cha kutsekedwa kwa ma Company,, Zisankho zayandikira tiona ma busy,,, MCP yapanikizika.
@BenitoCazota-q6u8 күн бұрын
Kodi ndalama zopitila ku Tanzania ko chakwera wazitenga kuti pakuti ku malawi kuno dollars kulibe?
Ai tiona kumene kupite Malawi chifukwa tafika potopa nazo
@ShamimuBisani8 күн бұрын
Let me laugh in Swahil any way Kalindo our freedom fighter
@Nelsonmatenda8 күн бұрын
Kalindo mumatiyankhulila osaukafe ..mcp no more in 2025: anthu oipa zedi
@BysonPhiri-gu4io8 күн бұрын
The DC 😅 mwana oopsa kwambili
@MathewsThugho8 күн бұрын
Winana wachita kumanga nyumba ku airwing ngati nyumba zaziphuzisi koma zilinyumba zake kom kumalawi
@judithStuwart8 күн бұрын
Anthu aku mpoto ndi anzeru or simmawasankha kukhala president
@LetshaChirwa7 күн бұрын
Kkkk km yaaa kukhalila kupepha bambo wamutundu wanji
@MissCaddy-yh7wd7 күн бұрын
I really hate the mayor of Lilongwe, a very fake woman nde okonda ndalama. Anthu ambiri amawadandaula both okuda ndi amwenye omwe, sindinaoneko munthu wadyera ngati mzimai amene uja. Eish!!!!
@morgankaponda39457 күн бұрын
Nonsense! Ma pensioners akuvutika mu boma la congress. No gratuities. Akungofuna kubera ma company basi.
@ChingotopeJailos8 күн бұрын
Ine ndimafuna ndimve Yama ARVs ndye mwat tramp wait bwanji
@tungwaprecious8 күн бұрын
BAKILI MULUZI TV
@bridgetmajor36467 күн бұрын
Akufuna anthu timwalire......chifukwa cha ulamuliro opusa wa Chakwera
@RichardAlick-o8k8 күн бұрын
The DC
@BlessingsMuhaliwa7 күн бұрын
5 years popanda chochitika
@augustinechibbalazi88978 күн бұрын
What benefit acrues we , Malawians if our political and religious leaders are viliacos and cupidity diehards ???
@StigaraAfick-o2x8 күн бұрын
bon ku mcp kulibe wazeru kupatikiza ndi chakwela emweyo wazeru aliko ndi nduna ya zatchjto vitombiko basi
@greemynkhoma88867 күн бұрын
Akalindo tinatopa nao ndikape weni weni uyu
@ChikoMasapula8 күн бұрын
Chatsala Ku state House ndi chigololo😂😂😂 EEE zoopsa