BON KALINDO LERO PA 4 SEPTEMBER WATI SAKUOPA KUFA NDIPO LERO ANENA CHILUNGAMO OPANDA KUOPA MUNTHU

  Рет қаралды 41,588

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 119
@ChristopherChapeta
@ChristopherChapeta 11 күн бұрын
Born kalindo ndi activiits okwanila keep it up more fire
@augustMag
@augustMag 11 күн бұрын
Mr Bon Kalindo kuikunena zoona president Chakwera palibe chimene akuchita mdziko muno la Malawi lafika powawa popweteka Ambuye atimenyere nkhondoyi 2025 achoke vote yanthu Amalawi imuchose munthu osaganizira aphawi tchito kugawa ndalama Kwa anthu akwao kukasiya the DC Boooon Kalindo president wa aphawi ku Malawi the voice of Malawi 🔥🔥❤❤❤❤
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 11 күн бұрын
Muuzeni born kalindoyo kah adzaimire pa mpando wau president mudzamuvotere kut adzakuomboleni mavuto omwe muli nawowo tione ngat iyeyo adzakwanitse kulamurira anthu
@spargomw
@spargomw 11 күн бұрын
M'mene adafera Chilima muja, imfa yowawa, yovetsa chisoni, kufa ngat chitsiru, kukafera ku Nkhalango, kufa ngat chiweto😭😭😭😭 ndiye akubanja akhoza kulora kut m'modzi wa iwo azipangabe za NDALE, ngat uli UMPHAWI ndibwino akhale nawo koma iwowo alirebe Maliro am'bale wawo amene adaphedwa ngat Garu😭😭😭😭😭
@DamianoYohane
@DamianoYohane 11 күн бұрын
Zofuna a Malawi president yu akuyenera asabwelereso ku ku Malawi kuno
@AronLuka-ue5hl
@AronLuka-ue5hl 11 күн бұрын
Akulu akulu Mr Kalindo akunena zoona zokhazokha ganizani bwino pakhani imeneyi
@StephanoMaganizo
@StephanoMaganizo 11 күн бұрын
Ndipo nkhaniyi is honest
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 11 күн бұрын
Ndikanakhala ine mayi osiyidwayo ndikanapanga zoti president ndi gulu lake akanandidziwanso. Amalawi ndi opepera kwambiri kufasa kwa mtundu wanji? Uzimu chani?
@NancyBanda-g2j
@NancyBanda-g2j 11 күн бұрын
Atha kuphedwa Mary ndie akuopa KUsia ana paumasiye src
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa 11 күн бұрын
Okufa saopa kuola
@dysonmasiye5736
@dysonmasiye5736 10 күн бұрын
Ndikanakonda mai Chilima abwere poyera kuti akapikisana nawo ku convention. Koma ndithokoze kuti nthawi zonse mmawauza anthu zofunika koma makutu awo ndi ogontha.... Kunena zoona atangoti maiwo akapikisana nawo ndipo atha kuwina koopsa cos alibe mbiri zoipa ai and alinako kuthekera kupotitsa patsogolo dziko lino
@ishmaelsiffah9900
@ishmaelsiffah9900 11 күн бұрын
Generation yathu ndiyomvetsa chisoni,mwina ndikusawerenga history,taonani achina Kamuzu,kwame Nkuruma,Nyerere,Mandela anamenyela ufulu wao alindizaka zochepa, remember 16 June ku South Africa inali ya achinyamata,ine ndimaona ngati achina Kamuzu anamenyera ufulu pothana ndi atsamunda,zimene zija zinatheka atsamunda amkatiphinja aja anathana nao,lero ikutiphinja ndi corruption ndimaona ngati tikanadzuka ndikuwauza atsogoleriwa kuti enough is enough katangale watizunza mokwanira watikwana kuyambira pano palibe apangenso zakatangale zakezo tithana naye tokha
@ElizabethDziko-wp8kc
@ElizabethDziko-wp8kc 11 күн бұрын
😊
@rhodamaunge-uq5dz
@rhodamaunge-uq5dz 11 күн бұрын
Tiyenera kuchitapo kathu
@MalonzoMazombwe
@MalonzoMazombwe 11 күн бұрын
Kamuzu sanamenyere ufulu kuchotsa atsamunda ayi,, Chilembwe ndiemwe anamenyera ufulu omwe tikuuononga lerowu,, kamuzu anali mtsamunda sanali mmalawi ayi, chabe kuti kalero makolo athu analibe nthawi yotsutsa izi poopa kufa.. Samora waku Mozambique amathamangitsa atsamunda ndipo kamuzu amkadana nazo, apa mpomwe ungadziwire kuti sanali mmalawi.
@LoveNgona
@LoveNgona 11 күн бұрын
Yea u r right ❤
@MayamikoPangani
@MayamikoPangani 11 күн бұрын
Iwe ndi number 1 zafika powawa kwambiri ❤😢
@user-un8yq1gg2i
@user-un8yq1gg2i 11 күн бұрын
Ineyo manganya uja ndimkamuyesa munthu wanzeru koma ayi ndithu, angozungulira m'dziko muno kumawononga misonkho pomwe eni misonkhowo akuzunzika kobasi
@giftkayome3568
@giftkayome3568 11 күн бұрын
You have spoken the truth Mr Kalindo 💪
@LehmanManere
@LehmanManere 11 күн бұрын
Tichose mawu oti Malawi is a God fearing National.
@khumbombale496
@khumbombale496 11 күн бұрын
Abale !! Pajatu timati (wamisala anawona nkhondo) Kumamuvera chisoni mayi SKC
@MikeArthur-jd2ij
@MikeArthur-jd2ij 11 күн бұрын
The DC 🔥🔥 Mwana oopsa kwambir
@RodwellPhinifolo-v9e
@RodwellPhinifolo-v9e 11 күн бұрын
2 point Mr president wanthu osauka key ndi Mary chilima anthu 4 amenewo akhale pa emergency meeting di
@user-sc7ih4op3l
@user-sc7ih4op3l 11 күн бұрын
Akuchita kuona kuti mamuna wake waphedwa pompo nde muzikati naye apange za ndale? Mmaudxiwa ululu wa ifa inu?
@ChipiliroSpencer
@ChipiliroSpencer 11 күн бұрын
Kodi ndiye chakwelayi akusungilidwilanji kuti azipitilizabe kulamulila zikoli pomwe akuononga chonchi athu osamuchosa bwanji
@FlaviusJoseph-x6s
@FlaviusJoseph-x6s 11 күн бұрын
It's true, Mary can do better
@MafavukeJere
@MafavukeJere 11 күн бұрын
More fire❤❤❤ the dc
@georgekesten3975
@georgekesten3975 11 күн бұрын
Ndikuva kukoma povela audio imeneyi.... wamisala anayiwona nkhondo
@justinmalala-e4o
@justinmalala-e4o 11 күн бұрын
Kodi mmalawi muno tiziikana mma udindo chifukwa cha chisoni? Aliyense akuziwa kuti UTM si chipani koma movement, ndipo movement singakhale ya kubanja kwamunthu. Komanso Mary Chilima sananenepo kuti ali interested ndi za ndale. Don't force her, azachite kupanga chiganizo mwiniwake. Kukhala mkazi wa munthu wa ndale sizitanthauza kuti nawe ndiwandale
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa 11 күн бұрын
😂😂😂😂 awanso
@ThomasMlowoka
@ThomasMlowoka 11 күн бұрын
More fire 🔥🔥🔥 The DC 💪💪
@CaptainNyenga
@CaptainNyenga 11 күн бұрын
I get you DC😢 merry chilima should stand as UTM candidate
@PaulineKamwana
@PaulineKamwana 11 күн бұрын
Ndipo ndiifedi opepera kobasi tizizimuka tonse titatha cx zafikapa Mmmmm 🙌
@FaheemChipojola
@FaheemChipojola 11 күн бұрын
Apa zafikapa kungopita kusiteti house kuchotsa zake zomwe wazisiya popita ku chaina zo dziko likhale mwanja mwa ansilikali mpaka patsiku livota bas
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa 11 күн бұрын
Chokani apa mmangoyankhula tiyeni kunseu ntooo osatuluka
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa 11 күн бұрын
Asilikali ake ati? Oliza mikonono ndi masana omwa? Fools
@Martinmkapangakapanga
@Martinmkapangakapanga 11 күн бұрын
iwe born kalindo ine ndinanena kale kuti pamalilo achilima anthu ena ankayakhula mwa mphamvu koma pano kuli ziii atangoyika malilo dziko lamalawi lovesa chisoni
@MarkShuva-jq8iz
@MarkShuva-jq8iz 11 күн бұрын
Phindu la chilima yomwe tikuziwa ife ndi campain yomwe anamuika pachulu Chakwera,
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 11 күн бұрын
Ineo chibadwileni changa sidawone chisilu cha presdent ngati ichi ndichifukwa ndikuti tilibe presdent
@SafariBvumbwe
@SafariBvumbwe 11 күн бұрын
Ndipo a usi aja mmmmm mulungu akuwawona
@WinfordGondwe
@WinfordGondwe 11 күн бұрын
That's true Kalindo.mayi Chilima atengeko mbali ndi yogwira kwam6
@christinaguliguli
@christinaguliguli 9 күн бұрын
Kodi ndiposo mademo mmakapempha kaye kwa DC kuti chani amenewo si ma demo omwe tikufuna ife inu mukuona ngati angalore akudya ndalama zochokera konko? Tiyeni tichite mademo osaleletseka atiphe atiphe ineso zikundiwawa kosalekeza usiku ndikagona ndikungoganiza zaupandu,mundisamaletu mwamva anyani inu
@HevenChiwaya
@HevenChiwaya 11 күн бұрын
Mr Kalindo inuyotu muyesese kuti muwapulumuse aMalawi chifukwa ndiinu nomwe munapangisa kuti a Malawi azikumana ndi mavuto omwe akukumana nawo lelolino popanga ma demo ndi Chakwela wanuyu...
@user-gp2zp2dj1w
@user-gp2zp2dj1w 11 күн бұрын
Chakwera chitsiru Cha president
@JamesBhiwhymilanzi
@JamesBhiwhymilanzi 10 күн бұрын
It's nice ❤
@BrightNamoko
@BrightNamoko 11 күн бұрын
Kkkkk Nkhan nd way forward Tiuzen titan
@ChisomoPachanya
@ChisomoPachanya 11 күн бұрын
Tamuudzeniso DC kuti kuno ku South Africa amalawi ambili ali ma prison kumangidwa kamba ka mapepala please amalawi ambili akuvutika kwambili ma prison akuno atipemphele ma transport
@MACKDBandah
@MACKDBandah 11 күн бұрын
Amalawi azanga chonde mokupephani ndimafuna number ya Mr president Bon kalindo chonde tanditumiziren chonde kose komwe muliko amane ali ndi number ya a president anthuwa Mr bon kalindo ndithandizeni mopepha chonde
@BeatriceLilemba-ww6cb
@BeatriceLilemba-ww6cb 11 күн бұрын
The DC my vote🔥
@LucyEndmond
@LucyEndmond 11 күн бұрын
More fire 🔥🔥🔥🔥🔥 the. DC👂👂👂👂
@maryphiri2409
@maryphiri2409 11 күн бұрын
Bodza lokha lokha ilo musamumvelele palibe iye cimene angakuchitileni zaboza
@johnkatapeh7182
@johnkatapeh7182 11 күн бұрын
❤❤❤ the DC
@alicechinyama4155
@alicechinyama4155 11 күн бұрын
Pajatu African national parks ili mmanja MWA mdzukulu wa kwini kubmangalande
@HalimaMtewa
@HalimaMtewa 11 күн бұрын
The DC more fire agalu amenewa akutizudza kwambiri
@EstherChimalizeni
@EstherChimalizeni 11 күн бұрын
Ing'alule fada
@DavidMsokera
@DavidMsokera 11 күн бұрын
Khani ya infa ya chilima ambiri mulungu odziwa za kumwamba ndi pansi akatiweluza chifukwa chokwelezera kusavana pakati pathu, chifukwa iye ndi amene alimwini chilungamo
@DavidKajawa
@DavidKajawa 11 күн бұрын
More fire baba kalindo
@MalitaKapesi
@MalitaKapesi 11 күн бұрын
Abale tatiyeni tipange zoti chakwela asabweleso ku China kwake wapitako aaaaa tatopa naye uyu
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 11 күн бұрын
Ku malawi kulibe presdent
@FixLogik-sd4bz
@FixLogik-sd4bz 11 күн бұрын
Zoonad kalindo umakwana ukunena zoonad,koma marry ndalesangayikwanitse
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 11 күн бұрын
Good messages the DDDDDDDDDCCCCCCCCCCCC bon kalindo 🇲🇼
@KosmasMunthali
@KosmasMunthali 11 күн бұрын
Tichotse ng'ona gyz😂❤❤❤❤❤❤❤❤❤😂😂❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@rhodamaunge-uq5dz
@rhodamaunge-uq5dz 11 күн бұрын
Mcp angoizimisa isazapezekeso mmalawi A mary pamoz ndi akubanja tithandi zeni
@NormanMwale-g1i
@NormanMwale-g1i 11 күн бұрын
More fire Bon!!
@DavidMsokera
@DavidMsokera 11 күн бұрын
Mh, infa ya chilima yapezetsa anthu zokamba, koma amalawi adzayankha zosezi kudzera mu voti yao, ndipo nkhani imenei mh yakwana guys, and only God knows
@ConlardNkhoma
@ConlardNkhoma 11 күн бұрын
Mkufuna kt akhale nkazi wanu? Kkkkkk
@sulleahmnyimbili1362
@sulleahmnyimbili1362 11 күн бұрын
Mmmmm koma the way mmene anafera Chilima I don't think angapange zandale izi
@aarondickson70
@aarondickson70 11 күн бұрын
Bon talk about the truth of tea pluckers who are employed in two weeks contact, can they send their children to school with the cash of two weeks contract ?
@Danp-q4n
@Danp-q4n 11 күн бұрын
Big up a dc
@ShrenkieNgoni
@ShrenkieNgoni 11 күн бұрын
Mary chilima 💙
@PartsonMdeza
@PartsonMdeza 11 күн бұрын
akut muchira 😂😂😂
@VanessaHale-v7x
@VanessaHale-v7x 11 күн бұрын
Zowona bwana
@yotamumahomed1313
@yotamumahomed1313 11 күн бұрын
inenso ndikudabwat kut Mary chilima akupangapo chan pa imfa ya chilima
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa 11 күн бұрын
Ali duuu
@GladesMhango
@GladesMhango 11 күн бұрын
Zoonadi the DC
@danielfaylosi2661
@danielfaylosi2661 11 күн бұрын
komatu kufa samaferana bwana DC olo inu simugafere akazanu atamwalira
@GeoffreyMaulana-rh5rx
@GeoffreyMaulana-rh5rx 11 күн бұрын
Achinyamata alelo ndiokomedwa ndindalama comrade palibepo amaonazasogololaziko lelosatana akulamulilaziko
@ShrenkieNgoni
@ShrenkieNgoni 11 күн бұрын
@mary chilima ❤
@ConlardNkhoma
@ConlardNkhoma 11 күн бұрын
Paja amati maso apatali amaongola mtengo. Inu mngayendetse?
@user-mm9ox2pz7p
@user-mm9ox2pz7p 11 күн бұрын
Zoonadi komaso vuto mulibe mbali mukati atuluke ku utm lero mwaukira olo mary abwere azaimire inu nomwe muzayakhulaso za ndalezi zovuta tigosiya mulungu akhale mulungu
@LindaZuze
@LindaZuze 10 күн бұрын
Koma dziko la2 ndilomvesa cison
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 11 күн бұрын
Monga mmene anthu adagwirizirana kupanga " Tonse alliance " kuti athane ndi ulamuriro wa ntundu umodzi uja , panonso , chonde gwirizanani monga mwakunena kwa a Kalindo kuti Boma lakuphali lichoke kuti anthu amenewa adzidzaimbidwa milandu Ali kunja kwa boma . Mtendere weniweni tidzaupeza liti a Malawi ?
@StainThika
@StainThika 11 күн бұрын
Koma chakwela watidzunza amalawi kodi iyeyu zikutivuta pat kumuchosapo uyu wamankhwala uyutu
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 11 күн бұрын
Tili ndi kaliati mesa❤❤
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa 11 күн бұрын
Hiiiiii Mpaka Kaliati? Hahahaha
@InnocentBanda-g6i
@InnocentBanda-g6i 11 күн бұрын
@MussahMundisiye-re4sn
@MussahMundisiye-re4sn 11 күн бұрын
😢😢😢ndipo aise aaaa 😮
@JoshuaNgugimsiska
@JoshuaNgugimsiska 11 күн бұрын
Imwe muli wanalume mukuyowoya unenesko
@JusticeNyirenda
@JusticeNyirenda 11 күн бұрын
Ndipo unenesko nad
@blessingsgeoffrey9414
@blessingsgeoffrey9414 11 күн бұрын
Kma ya Mary chilima yokhayo aaa bodza sunduona utsogoleri mwa Mary guys
@Kelvin-hj5qv
@Kelvin-hj5qv 11 күн бұрын
🎉🎉🎉❤
@sulleahmnyimbili1362
@sulleahmnyimbili1362 11 күн бұрын
Generation yomvesadi chisoni
@MkusaMalota
@MkusaMalota 11 күн бұрын
Mcp sikuchoka
@DysonTummiesSajiwa
@DysonTummiesSajiwa 11 күн бұрын
Mufuna muveke munthu u president chifukwa chachisoni inu mudapengadi et
@CathrineBizza
@CathrineBizza 11 күн бұрын
Ng,alulizasion fada
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 11 күн бұрын
Anthu okubaa inu
@DavidKanyemba-n2s
@DavidKanyemba-n2s 11 күн бұрын
The DC Moto buuu
@LM-gz5pk
@LM-gz5pk 11 күн бұрын
Nama drama 🤣🤣🤣🤣 i qoute
@LACKSONDMASIYE
@LACKSONDMASIYE 11 күн бұрын
Kmt ngt ndikulota mmm
@innocentkhwamba856
@innocentkhwamba856 11 күн бұрын
Wakuru yanuyija
@ChristopherChimbalanga-ez5he
@ChristopherChimbalanga-ez5he 11 күн бұрын
The DC
@GoodsonJim
@GoodsonJim 11 күн бұрын
Sizitipindulira izi
@OwenNyambose
@OwenNyambose 11 күн бұрын
Kalindo
@VanessaHale-v7x
@VanessaHale-v7x 11 күн бұрын
😢😢😢😢😢
@MenasKaliati
@MenasKaliati 11 күн бұрын
Uyu anadza
@DanNzima
@DanNzima 11 күн бұрын
The Dc
@ChristopherBwanali-i6b
@ChristopherBwanali-i6b 11 күн бұрын
Generation z singavotere chikangawa
@DavidColings
@DavidColings 11 күн бұрын
Ndipo
@Danp-q4n
@Danp-q4n 11 күн бұрын
Guys kalindo ampase moyo wautali
@user-gp2zp2dj1w
@user-gp2zp2dj1w 11 күн бұрын
Chakwera mboli yake
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 11 күн бұрын
Kampeni yomwe mukupanga a Born kalindo aaaa 😂😂😂 useless. Chidani chani ndi anthu MCP i think sichikutinkhudza, ndie musamatulangitse kut ifeso tikhale opusa chifukwa chofuna kukhutitsa mimba zanu wanva
@solomonkandiero6357
@solomonkandiero6357 11 күн бұрын
Palibe chomwe ukudziwa khala chete
@Aaron-w9x
@Aaron-w9x 11 күн бұрын
Deal it
@LindaKaombe
@LindaKaombe 11 күн бұрын
Yes akubanja please tapapata
Or is Harriet Quinn good? #cosplay#joker #Harriet Quinn
00:20
佐助与鸣人
Рет қаралды 53 МЛН