BON KALINDO LERO PA LUNTHA TV WAYAKHULA MOSAOPA KUTI CHAKWERA NGATI WAPANGA CHANZERU NDIKUBA NDALAMA

  Рет қаралды 68,651

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 243
@joegibsonzulu2599
@joegibsonzulu2599 10 күн бұрын
A day is never complete for me if I do not listen to what the DC has to say. I always look forward to hear his talking points, views, suggestions and general advice.
@HappinessKapombeza-ut9mo
@HappinessKapombeza-ut9mo 10 күн бұрын
That is really truth.....BIG UP BRAZA....!!!!
@sollomavenda8283
@sollomavenda8283 9 күн бұрын
Yoh right brother
@user-yt8lv6cq3k
@user-yt8lv6cq3k 10 күн бұрын
Mufune musafunee born kalindo asakhara president believe me this is our future president if you like it or not born kalindo is going to be president one day 🤞🏽🤞🏽🤞🏽
@alexandermeke6994
@alexandermeke6994 10 күн бұрын
Mbuzi ya anthu opusa ndi opanda mzeru nzanu ndi ameneyi
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 10 күн бұрын
Or atakhala mbuzi its better than crocodile yemwe akungodziwa kupha anthu kuba komanso kuononga
@Okalekale
@Okalekale 9 күн бұрын
Kkkk,Koma Malawi analowadi mphepo,Uyuyu akhale president zoona?,anthu anzeru zawo ophunziranso ali kuti,Malawi si pamajigatu?.Komanso awa ndi antchito a Peter Muthalika.Ikadzawina DPP adzapatsidwa udindo m'boma
@alexandermeke6994
@alexandermeke6994 9 күн бұрын
@@Okalekale misala imeneyi chamba chili thooooooooooo
@Memoryphiri-rm2gl
@Memoryphiri-rm2gl 10 күн бұрын
The real freedom fighter
@Drmuhammadchiwona
@Drmuhammadchiwona 10 күн бұрын
Komatu mr plezident mukunenepa sopano we malawias we love you plezident
@alexandermeke6994
@alexandermeke6994 10 күн бұрын
President wa ma bodza ngati abambo ake satana plus APM wopha malubino😅😅😅😅
@AlexGomani-ss5nj
@AlexGomani-ss5nj 10 күн бұрын
You are the true fighter mr DC!! your our Samson here in Malawi,. May God continue protecting you until we have rescued from this crockdile's mouth...
@user-pz4py6ew6z
@user-pz4py6ew6z 10 күн бұрын
Watching from SA the freedom fighter Indeed ❤❤❤ mulungu akutetezeni boss
@yasiniKalonga
@yasiniKalonga 5 күн бұрын
Kunenepa plus kutchena big up Mr president ❤❤
@JohnJacko-j4l
@JohnJacko-j4l 7 күн бұрын
Chilungamo ndichopweteka Kalindo keep fire burning 🔥 Malawi akufunika anthu ngati Kalindo
@donnyirenda2620
@donnyirenda2620 7 күн бұрын
THE DC, I REALLY LIKE THE GUY 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@chrisboyce2
@chrisboyce2 10 күн бұрын
Akuti Kodi Mr Kalindo mungayipatse ma percentage angati MCP mu Zaka 4 yakhalayi ( Kalindo says 0 out of 10 😂😂😂) Mwana Olimba mtima Kalindo🔥💪
@alexandermeke6994
@alexandermeke6994 10 күн бұрын
Ndiyo nsanjeyo or pa cement akuuzani kuti fumbi
@SheenahMwalabu-iz3pr
@SheenahMwalabu-iz3pr 10 күн бұрын
Muli uthenga mwa kalindo, kupanda kumvera the DC sindingagone 😅 chilungamo chabwanji ichichi. Kod amamvera achakwera wo? Ndipo nde 0 pa 200 wachita pazaka 4. Chilimatu amatiwawa ndipo kaya wnanu mmamva bwanji? 😢 RIP Saulos Chilima 😢
@user-re8es1ib7l
@user-re8es1ib7l 10 күн бұрын
Boni kalindo the Dc mwana owopsaaa kwambr 💪💪💪💪💪
@MangaDamiano
@MangaDamiano 10 күн бұрын
Kupandatu anthu Ngati Bon kalindo okubawa sitinakawaziwa ndibwenzi tikuungoti boma ndilomweli
@WilsonMagongwa
@WilsonMagongwa 6 күн бұрын
Kalindo always stands on truth if leaders listened the country could be developed
@MikeSamuel-i5i
@MikeSamuel-i5i 10 күн бұрын
God be with you bwana DC you always be side of poor people longing to live
@imraanJafal
@imraanJafal 10 күн бұрын
❤❤❤❤ My support to you Mr boon kalindo the DC president wathu
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 10 күн бұрын
Long live Mr pangolin the DC❤❤❤❤❤
@GroupFortyfour
@GroupFortyfour 9 күн бұрын
Big man everything you says I agree with you 🎉🎉🎉🎉🎉🎉 Pitilizani big 🎉🎉🎉🎉
@giftelesoni
@giftelesoni 7 күн бұрын
The real freedom fighter Mr DC you need face Malema the strong men
@RaffickAllie
@RaffickAllie 10 күн бұрын
Kkkkk my president wandipedza akuti chakwera amavala plastic shoes leather
@ChifundohMitulo-bg2lv
@ChifundohMitulo-bg2lv 10 күн бұрын
Out of 10 nd zero tisachedwepo pamenepo😂
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus 10 күн бұрын
Wa mcp sasowa...mfiti iwe
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 10 күн бұрын
😂😂😂😂😂booon kalindo akuti zero pa ten
@YohanePaul
@YohanePaul 10 күн бұрын
Ati pamenepo tisachedwepo😂😂😂😂
@ADAMSONGONDWE
@ADAMSONGONDWE 9 күн бұрын
We love you here from mpoto Mr Dc
@WesleyKalimwayi
@WesleyKalimwayi 10 күн бұрын
Kkkkkk zoonadi chikangawa anali ovetsa chisoni kalindo sakunama ndipo sadzanamapo
@EmanuelPaul-io2hk
@EmanuelPaul-io2hk 10 күн бұрын
Am agree kt report anatulutsali ndi lopanda pake and pamwamba pakuti it's istupit ine mkuti ndizamanyi ndibwino akangokhala chete chabe,a pule kumwambaku ku Mulungu yemwe dzina lake ndi YEHOVA analenga diso lanulo sangalephere kukuonani.
@RhodneyBwa3
@RhodneyBwa3 8 күн бұрын
BON KALINDO NDI MUNTHU WABWINO KWAMBIRI KEEP IT UP MY PRESIDENT
@JohnfosterNkusengwa
@JohnfosterNkusengwa 8 күн бұрын
We need people like mr b kalindo in this country ❤❤ l really like the way this guy is doing and l wish if we can choose mr kalindo as a president in our country All the way from cape Town pa boma ❤❤❤❤❤❤
@JuniorchokaniKhanene-f8e
@JuniorchokaniKhanene-f8e 8 күн бұрын
DC is best chiyembekezo chathu
@user-ul1fb4yn5o
@user-ul1fb4yn5o 10 күн бұрын
Pangolin wathu olo aboma amadziwa ❤❤ machine opangira zida za ufulu
@FrankwelNkhoma
@FrankwelNkhoma 8 күн бұрын
God may bless you a good activist
@user-zg6mn8qr4m
@user-zg6mn8qr4m 9 күн бұрын
The DC president Wathu Wathu ❤❤
@GiftDumba
@GiftDumba 10 күн бұрын
Umakwana bon iwe ndi bakili muluzi komaso mutanyiwa mukuyenela kutetezedwa
@AbdulrazaqHussain
@AbdulrazaqHussain 9 күн бұрын
Remember one thing, leaders born leaders, not made, it's a gift, chakwela doesn't have it,let's face the fact
@user-dq1zf7hf1l
@user-dq1zf7hf1l 2 күн бұрын
Ulemu wanu a Mr president, inuyo msadzafe ayi mmatiyimila
@CHRISTOPHERCHINYONGONYA
@CHRISTOPHERCHINYONGONYA 8 күн бұрын
Born kalindo akufinikila anthu angapo timupatse support ndikumanga umodzi molimba kuti tisithe Malawi wathu
@robietadeyo9205
@robietadeyo9205 7 күн бұрын
Kalindo the top notch
@MusaManati-ho4zf
@MusaManati-ho4zf 10 күн бұрын
Timamvananu kukoma mapwiya apwiya...........muulupali.❤❤❤❤
@LaquissoneMoises
@LaquissoneMoises 10 күн бұрын
Palimbe angabweze galimoto iwe ndiyowamba
@WilfredMathews-yl6ij
@WilfredMathews-yl6ij 9 күн бұрын
Only one man standing love u Mr president onest speaking
@BhekiLithuli
@BhekiLithuli 8 күн бұрын
The DC MWANA Woooopsa kwambiriiiii 🔥🔥💯
@GriffenSakuwa-h6t
@GriffenSakuwa-h6t 8 күн бұрын
Atasalemo Chakwera ndi Nkazi wakedi😂😂😂😂😂
@ConfusedCupcakes-ke8ql
@ConfusedCupcakes-ke8ql 10 күн бұрын
Boni Kalindo "DC" watching from Nkhotakota
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 10 күн бұрын
Chilungamo pamtete . Congress yabisala pachipande .
@lysonmalizan2587
@lysonmalizan2587 4 күн бұрын
our. freedom fighter
@AchimkokoChigonambango
@AchimkokoChigonambango 9 күн бұрын
Osaopa, Osatopa, Osafooka ABiyeni Adawaphela dala, Awona matsoka akathithi Ayemusipi
@JosephPhiri-v3b
@JosephPhiri-v3b 6 сағат бұрын
Tsiku la lero fees ya Ku secondary school kuchokera pa 7500 mpaka 40,000 school free
@user-cd4df3vg4y
@user-cd4df3vg4y 10 күн бұрын
Uyuyu ndi kamuna 😅
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl 9 күн бұрын
Our president boooorn kalindo 🔥 sazatheka
@YusufuKaifa-r2y
@YusufuKaifa-r2y 9 күн бұрын
I'm proud on you Mr president of born to suffer of Malawian people's
@LottiAffati
@LottiAffati 7 күн бұрын
bigman tsopano bwana kalindo the dc mumatiimirira biggy
@HassaniKhenge
@HassaniKhenge 10 күн бұрын
Mr DC timenyereni khondo kuipulumutsa Malawi
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 10 күн бұрын
0 pa 10 😂😂😂 anali wovesa chison chakwera ndi nkazi wache 😂😂😂😂😂chikangawa woyooooo😂😂😂
@FREZERMICHAELBANDA
@FREZERMICHAELBANDA 9 күн бұрын
Bon Kalindo following from Zambia
@GibohKatema
@GibohKatema 8 күн бұрын
Fire bwanaa
@AbdulrazaqHussain
@AbdulrazaqHussain 9 күн бұрын
If we know the difference between politics and economics, we will enjoy as a country, our politicians they mix the two together, that's why we are in this situation
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza 10 күн бұрын
The DC mumayima pa chilungamo inu ❤❤❤❤ Good bless you true story
@AngolanChinga
@AngolanChinga 10 күн бұрын
Munthu wamkulu ameneyo the DC
@Okalekale
@Okalekale 9 күн бұрын
Iwe usatinamizepo apa iwe Kalindo,zolinga za gulu lanuli ndi zolinga za amene amakupangani sponsor,amakupangani sponsor ndi ndani?
@GeraldMustafa
@GeraldMustafa 10 күн бұрын
🤣🤣🤣 Dzaka 10 pa u president koma ziliko the DC!!!!!!!
@SamukLungu-zg7fl
@SamukLungu-zg7fl 10 күн бұрын
Kuyankhura kwa zeru kumeneko
@AbdulrazaqHussain
@AbdulrazaqHussain 9 күн бұрын
All in all, the DC is right, politicians think politics is a self riches garden
@IshmaelMkwanda
@IshmaelMkwanda 9 күн бұрын
Kuyankha mwandiiiiii DC ❤
@pauljosephmakaula6835
@pauljosephmakaula6835 10 күн бұрын
Munthu wa nzeru zachibadwidwe
@Andrew-mr5kp
@Andrew-mr5kp 10 күн бұрын
The nyonyolido mwana wakwathu umakwana
@Abdulla-y9t
@Abdulla-y9t 10 күн бұрын
God bless the DC
@paulinekayuni1621
@paulinekayuni1621 10 күн бұрын
Ndipo zodabwitsa ndege inyamuka bwanji opanda zipangizo ngati zimenezo President amayenera kufusa responsible people zimene akufusa Kalindo
@MrThomas-j9d
@MrThomas-j9d 9 күн бұрын
More 🔥 fire Mr BK ngaluleni Ameneyo
@CassimWasotso
@CassimWasotso 10 күн бұрын
😂😂😂😂😂 DC mumandiwaza
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 10 күн бұрын
The DC pangoline our representatives and freedom fighter ❤❤❤
@HendersonDziwa
@HendersonDziwa 10 күн бұрын
Aborn ambuye akutetezelen kwambili mumati imilila
@user-nd7hy6st4j
@user-nd7hy6st4j 9 күн бұрын
A Kalindo andikumbutsa nzathu wina wake apolice anamugwira atangofika kumene kuno ku South Africa anatuluka kundende after 2 months anakabwera qanenepa anthu osamamudziwanso kkkkk pano amangoti mukunena uja ananenepera ku ndende uja? Kkkkk😂😂😂😂
@WillmotChiuimia-vr6ou
@WillmotChiuimia-vr6ou 9 күн бұрын
Yes Mr DC bon kalindo❤❤❤❤
@GreatConqueror-xx3vi
@GreatConqueror-xx3vi 7 күн бұрын
Mwayankhura bwino ndipo zanzeru kwambiri
@gkay-striker
@gkay-striker 9 күн бұрын
The only thing I love about this guy chimayankhura without fear keep telling them the fact
@PempheroMoleni
@PempheroMoleni 10 күн бұрын
Ameni born kalindo mulungu atimenyela nkhon 🙏🙏🙏🙏
@CharlesSelemani40000
@CharlesSelemani40000 8 күн бұрын
akulu bola musadzasithetu kukhala ngati mtambo uja.Enafe timakunyadirani ndithu muli ndi fundo za bwino.
@MercyMfune-dc3rq
@MercyMfune-dc3rq 10 күн бұрын
Watching from S.A.
@user-jd9yz5hp7y
@user-jd9yz5hp7y 10 күн бұрын
The one and only the Dc💪🏼💪🏼💪🏼
@MsondaBanda
@MsondaBanda 10 күн бұрын
Kkkkk Simbi zikulu
@ThomasStephan-tg6ng
@ThomasStephan-tg6ng 10 күн бұрын
the DC umakwana
@GodfreyMzembe-b3n
@GodfreyMzembe-b3n 10 күн бұрын
Kodi bwana kalindo sumungayimireko u president
@alexandermeke6994
@alexandermeke6994 10 күн бұрын
Aaaaa a alibe mzeru awa chamba chili thooooooooooo 😅😅
@user-iw6cz5ft2l
@user-iw6cz5ft2l 10 күн бұрын
machine opangira machine amzake more 🔥🔥🔥
@AmonNgoma-c4h
@AmonNgoma-c4h 10 күн бұрын
Mutiyimile mr Born Kalindo as "PREZIDENTI",2025 .coz nzanuyu mmmm😢
@user-mv1wg2qd6i
@user-mv1wg2qd6i 9 күн бұрын
Kaswiri kwambili DC
@user-yj8ez7dd3o
@user-yj8ez7dd3o 9 күн бұрын
Mbala iyi wachita kunenena ekha kut akufuna kuthandizila zipani zina ndiwa bodza uyu akumatinamiza kwambir,ungadyese anthu osauka chisiru iwee nyapapi iyi ndi mtambo sakusiyana zao ndi zimozi
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 9 күн бұрын
MCP inapha chilima ndianthu ena Aja basi palibeso umboni wina tikuufuna apa
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 10 күн бұрын
Host yu amadziwa ntchito 👍👍👍
@MistonBaton
@MistonBaton 6 сағат бұрын
DDDDCCCC CHILOMBO MWANA WOBADWA MIYEZI 9 Osapita kumagetsi ayi
@johnbullyohanittokasikizim7127
@johnbullyohanittokasikizim7127 5 күн бұрын
Zilooo out of 10😂😂😂😂😂😂
@user-lw4hw9ce4w
@user-lw4hw9ce4w 10 күн бұрын
Our great activist the DC
@BashielSalade
@BashielSalade 10 күн бұрын
Osadandaula bwana mumangidwanso
@user-lb5gt4uv3s
@user-lb5gt4uv3s 10 күн бұрын
The Dccc mwana oopsa kwambiri
@GroupFortyfour
@GroupFortyfour 9 күн бұрын
Koma Aprezident anenepatu 😂😂😂
@AustinBanda-r8i
@AustinBanda-r8i 9 күн бұрын
Wise man dc
@MoyarChiumia
@MoyarChiumia 9 күн бұрын
Bon kalindo ndimunthu akumagonetsani tulo inu
@bernardchagomerana4221
@bernardchagomerana4221 8 күн бұрын
😂😂😂 atatsala chakwera ndinkazache
@user-os7qt6lw2c
@user-os7qt6lw2c 9 күн бұрын
This guy is making sense ndithu...
@philchinyanganya2047
@philchinyanganya2047 8 күн бұрын
0/10 is not a fair judgement. Attacking the president as a person does not help anyone including anthu ngati ife who will vote not for a political party but capable leadership with sound developmental policies. Abale we need not be misled by people who are promising us heaven so that they can get in on our ticket then to further their political growth . This is home to all of us . These drama issues will not build a nation.
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 9 күн бұрын
Chikangawa lipoti limeneli ukawuze abambo ako iwe ndichisilu kwambiri ukutitenga ngati Amalawife makape eti? Uchoke gwape iwe 2025 A.P.M boma osati iwe,gyz ku Malawi kuno kulibe pulezidenti ichi ndi chisilu timuchotse
@SoftwareSolutioz
@SoftwareSolutioz 10 күн бұрын
Big DC
Buchaman atabukidde Bobi Wine,yamba aba FIREBASE
1:12:32
Kasuku Live
Рет қаралды 7 М.
Touching Act of Kindness Brings Hope to the Homeless #shorts
00:18
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 18 МЛН
Fake watermelon by Secret Vlog
00:16
Secret Vlog
Рет қаралды 15 МЛН
这三姐弟太会藏了!#小丑#天使#路飞#家庭#搞笑
00:24
家庭搞笑日记
Рет қаралды 123 МЛН
GTA 5 vs GTA San Andreas Doctors🥼🚑
00:57
Xzit Thamer
Рет қаралды 30 МЛН
Action News anchor Brian Taff's full interview with VP Kamala Harris
11:20
6abc Philadelphia
Рет қаралды 1,2 МЛН
Politics and Big Tech | Bloomberg Surveillance | September 10, 2024
2:50:46
Bloomberg Podcasts
Рет қаралды 3,2 М.
KOPEMPHA NGONGOLE - Episode 169
12:37
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 34 М.
Touching Act of Kindness Brings Hope to the Homeless #shorts
00:18
Fabiosa Best Lifehacks
Рет қаралды 18 МЛН