Kuganiza uku mkopanda uzimu ndi umunthu komanso vumbuluso. if you doubt the source of money, why not pray to my God to reveal it to you oe personally visit this man and share your concerns with him. Mukatero palibe vuto. Musangokhala anthu opemphera koma amtima osagawa. The Bible says it was given to you freely and you should freely give...Mathews 10:7-8
@PetersonChipangula2 ай бұрын
Indeed a man of God may the spirit you have continue zoterezi zimasowa ma number anu Abusa tiasowa
@HumphreysBanda-e7g2 ай бұрын
Wamasiku otsiriza ine za ma prophet ndiye ayi yesu anati anthu adzadza mu dzina Langa masiku otsiriza ndiye ndi zimenezi guz khulupiriran mulungu not 🤞
@Littlefair72 ай бұрын
Ndipo Hebrews 1:2 akunena momveka bwino kuti za maprophet zinathera ku old testament komanso Luke 16:16 akutiuza kuti Yohane anali mneneri omaliza, uyuyu ndi ofunika makofi.
@MaryBanda-n3h2 ай бұрын
Nukuuzani Za anthu osawerenga izo khalani Maso anthu a Mulungu please
@shakiraameen80012 ай бұрын
Zoona
@BakaliPhili-es3xjАй бұрын
I'm behind of you
@MphatsoKanswalaАй бұрын
Koma mulungu simunthu amene Ali ndi chikhulupilil mwambuye madaliso samu sowa
@EdwardZuze-r7wАй бұрын
Owelenga khala maso, Yesu ananeneratu za atumiki mu nthawi yotsiriza,
@JonathanNsiyanyalo-c2m2 ай бұрын
I do agree with this man, it is biblical, if you read the beginning of the gospel apostles through the decoans were distributing daily necessities to the poor and the needy
@Bilirahealthycentre2 ай бұрын
Man of God thandizeni mapemphero ine ndakumvetsani,ndimamva ululu daily mbali imodzi ya nthiti zanga ndakhala ndi kujambulitsa kangapo koma no solution, ndilibe ndalama yodzafikira kumeneko plz
@lowkey_drey2 ай бұрын
Samalani mangalowe,muziwanda
@ShadreckMwijaАй бұрын
Amwenye amakhulupirira kungawa zachifundu koma amalemera ndiye Muthu okunda akathandiza itunduwake wamalawi muli sisabuye miliri bas muphuzire kuk
Malawi people please be careful with this things we lost lost mind why kind of this people still coming to our country we can see our self is joking with God 😢😢😢😢
@smithh.njirayafa58472 ай бұрын
Powerful Man of God.
@BeatriceNkhoswe2 ай бұрын
Ndamene akuthetsa anthu kukasungu kudzera mu ngozi zosiyana siyana Please anthu osalandila ndalamazo muthetsa Ana anu
@EmmanuelMassa-j7o2 ай бұрын
Fact ❤
@shakiraameen80012 ай бұрын
Inu ndiye mwalankhula
@Priscilla-f9n2 ай бұрын
Kkkkkkkkk,apo waganizadi
@paulvimbamvula95082 ай бұрын
Kaya ndi umphawi kaya....amalawi pliz...DC wa pa Kasungu take heed musamalole izi.....maina achizungu eti Church ku gawa ndalama
@EdwardZuze-r7wАй бұрын
KKK koma guys
@dixonbzuze8192Ай бұрын
Abusa mubweleko kuno ku South Africa mudzagaweko ma Rand❤❤❤
@ChimzySting27 күн бұрын
Butao ntambalika,machinga nsanama Ineed scholarship plus.ihave followed u on u tube
@ShadreckMwijaАй бұрын
Kuchita zachifundo muzaona zizayamba kukuyenderani Nanu simuzavesesa akukuchulani maina achilendo monga sataneci komaso uchita ma business onyasa ndipamene muzakhulupirire kuti amalawi ndi Atomasi Didimo amen ambuye akundaliseni
@EdwardZuze-r7wАй бұрын
Koma ntolankhani uyu ndi dolo, ndipo akuluwa si zauzimu ayi, Yakobo 5 yemwe akunenayo, akunena momveka bwino kuti ngati alipo wina wa inu adwala, adziitanile akulu a mpingo ndipo amupempherere atamuzooza ndi mafuta, osati akagule, ndipo odwalayo adzchilitsidwa komanso adzakhululukidwa
@CharityMhone-uk9ym2 ай бұрын
Iiiii kamwana ka chikangawa ndi bushiri aka chilichonse kunamizila mau amulungu😮😮😮 ndalma zomwe akugawazo amazitenga kt mmene akuonekela mo
@Bilirahealthycentre2 ай бұрын
Ine ndikuonamo chauzu indeed,zilibwino man of God pitilizani kutitumikira komanso kutithandiza ovutikafe
@lowkey_drey2 ай бұрын
Umphawi udzakuphani
@SalomeKadenkhu-p1eАй бұрын
Paja masiku otsiliza anthu adzakhala okonda ndalama satana wayamba kugawa ndalama take care for that man
@SmarshChikwanah2 ай бұрын
Zanja lopereka silisowa thus the man of God and his family are still blessed by the JEHOVA GOD ...May God continue extend your territory allover the world
@EmmanuelMassa-j7o2 ай бұрын
😂😂😂😂😂 umudziwe yesu iwey
@GanduBondu2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂take care yourself don't try trust money u wanna regret one day 😢
@MaryBanda-n3h2 ай бұрын
Yesu akachitira chinthu munthu samalengeza ankalengeza yekha munthuyo 😢😢😢😢😢😢 za satana izi
@charlesnankumba99912 ай бұрын
Ambuye akudalitseni kwambiri Prophet Gift Byton. Mulimbe mtima kwambiri chifukwa ngakhale anthu ena kwathu kuno sakulandirani ngati prophet wa Mulungu, sizitanthauza kuti inuyo sindinudi mneneri wa Mulungu. Ine ndine mmodzi mwa okhulupilira amene ndikhala ndikuthoza Mulungu chifukwa cha mayitanidwe anu komanso utumiki wanu.
@davidsnkhomah2688Ай бұрын
I think am looking at a real man of God, the first person ( Prophet) which can be trusted in Malawi, because as far as l see we don't have a trusted one in Malawi as far as prophets are concerned.
@CatherineDesire2 ай бұрын
Mmmh mmmmh mmmh mmmh people man of God ,who which one?
@LeniaBanda-r9tАй бұрын
Anthu amulungu please chenjerani please please
@PassionNgosiАй бұрын
This is powerful
@SammyLijuni2 ай бұрын
I'm very interested with this man of God
@ChristinaBanda-em4tzАй бұрын
Amen man of God
@BbbbvcccJftgff2 ай бұрын
Ambuye akusungeni ndi moyo wautari a prophet gift Byron.
@anthonysawa20392 ай бұрын
Who sell the anointing oil and water in the bible......the descendants of TB Joshua
@CatherineDesire2 ай бұрын
Mlungu wake uti ogawa ndrama which is material thing yho people of God
@anniezovu26202 ай бұрын
Mmmmm a2 akupanga zoopsa chenjerani 😊
@MayamikoHaroldАй бұрын
Ifeso tidalitseni man of God
@CharityChatipwa2 ай бұрын
Praise the Lord !
@wonderkapichira69292 ай бұрын
Ndalama dzimene akupelekazo patsogolo muzabweza magadzi , Chenjerani a Malawi
@JohnmalikoMalikoАй бұрын
Amen prophet gift byton
@KalongaWhyАй бұрын
Yaa pajatu nthawi yatha basi anayankhura anthu azalemelela Zina Langa Ali mulungu azaweluza zilemelani paziko
@HarveynsonthiNsonthi-u4nАй бұрын
Sign's of tym Jesus is coming soon
@SmarshChikwanah2 ай бұрын
I wish titakumana nafe mutitchure inayake 😊
@pettersen27172 ай бұрын
Keep helping the needy man of God
@PaulMkweza2 ай бұрын
Ndagwira bwimo point yokamba kuti, ntchito ya Mulungu si yaulele koma ndi ya mtengo odura
@gamajose39912 ай бұрын
Zidyani bwino ndalamazo muona zotsaritra😢😢😢
@PenjanNkhoma2 ай бұрын
Bless me with 200 k man of God
@yasiniKalongaАй бұрын
Original prophet was only jesus zinadzi zitipweteketsa ndithu 😢
@AREFRIEDNELSON2 ай бұрын
😂😂😂😂 athu ku malawi Iiiiiiiii ayi kumango Khulupilira chilichonse kuagawa ndalama zimenezo ndi ndalama ndithu koma
Masiku otsiliza anthu akukonda kukolora asanalime malire ake nkumachulukitsa ngozi ndi zodabwitsa nkumachotsa mioyo ya anthu
@AlfredChikadewaАй бұрын
Man of god
@KalongaWhyАй бұрын
Amen zachan zaufitizo
@WarriorKB-u3k2 ай бұрын
Bizinesi ndiyongobisalira iwe azako ndi chikangawa ine zamapolofetizi ai mwanga ndi yesu osati inu okupha
@GiftChalunda-ss9qu2 ай бұрын
Aprophet ,a name anga chaka chobadwa chimodz 1993 ine mwezi wa June then mukuti inu July school taphunzilaso kofanana pa ndanga thawi imeneyo a heard anali anjele ine ndinali ndikukhala Kwa amfumu a mpira
@JoyceLiwonde2 ай бұрын
Ukuzitenga kuti ndalama daddy 😮
@GroupFortyfour2 ай бұрын
This Guy is original..he is not yet underworld..and so Young
@LinleyBolamungu2 ай бұрын
How do you know , do you have evidence?
@GroupFortyfour2 ай бұрын
@@LinleyBolamungu brother you know,,the start is always beautiful.But as time goes by things get fishy 🥺🥺🥺🥺..but anyway thanks for your question it means that we are in the same page..we follow what's happening.👍👍👍
@SharifuMasimbo2 ай бұрын
I need to meet with you prophet.
@MercyChirwa-x5n2 ай бұрын
Amen uwume mtengowo
@MercyNkhoma-b6h2 ай бұрын
Mmmm koma tilowa satanic chifukwa cha umphawi ndithu.