BON KALINDO NDIYE KUTI SAMAOPA? NANGA ZOMWE WAYANKHULA LERO PA 16 AUGUST ZI TIZITI ALIBE MANTHA?

  Рет қаралды 67,664

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 138
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 2 ай бұрын
❤❤ the DC president wa anthu osawuka 💪✊
@ThokoMbewe-k5x
@ThokoMbewe-k5x 2 ай бұрын
j
@LessonBester
@LessonBester 2 ай бұрын
Bon Kalindoo The DCCCCCCCCCC mwana oopsa kwambriiii
@MichaelPhiri-jn7bb
@MichaelPhiri-jn7bb 2 ай бұрын
😊
@sylvesteralfred8355
@sylvesteralfred8355 2 ай бұрын
Bon Kalindo simunthu wamba this guy is hero palibe kanthu kuti fans ina imamunyoza but he's true son of the soil yemwe amalifunira zabwino dziko lake
@MosesFanuel-k3u
@MosesFanuel-k3u 2 ай бұрын
Get well soon the DC
@KellsDesderious
@KellsDesderious 2 ай бұрын
Machine the Dc ❤
@jackiendlovu9564
@jackiendlovu9564 2 ай бұрын
Get well soon the DC Mr Bon Kalindoooooooo
@DonexKatuli
@DonexKatuli 2 ай бұрын
Powerful speech
@shaibuidriss2741
@shaibuidriss2741 2 ай бұрын
Kalindo deserve to be called President wa anthu osauka🙏
@HamiltonRaphael-q2d
@HamiltonRaphael-q2d 2 ай бұрын
koma chakwera olo atafa palibe angadandaule afe galu ameneyi 😢😢
@ChisomoBisani
@ChisomoBisani 2 ай бұрын
Ndipo live
@AllanJentala-g6h
@AllanJentala-g6h 2 ай бұрын
Kunali Mr Mtambo nawoso anayamba chonchi koma chomwe tingadziwe ndichakut onsewa ndi andale chabe akungofuna kutiphimba mmaso.
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g 2 ай бұрын
Dc❤❤
@Phiricostina
@Phiricostina 2 ай бұрын
Zoona angangaa enu Ake Boma ndife ndipo tiziziwaso zose zochitika mbomamo osat zoophwyezazo ayi🤷
@marryphili5419
@marryphili5419 2 ай бұрын
Mulungu ndi wamphamvu ndithu tiyembekezera phiri limeneri Kuti ligwe mwina mapiri enawo angapume
@ndalamaandrew
@ndalamaandrew 2 ай бұрын
Ndipo wayankhula mosanyengelera
@EmmanuelMinyanga-gm4hv
@EmmanuelMinyanga-gm4hv 2 ай бұрын
Loud and clear
@SamsonMalefula-j4b
@SamsonMalefula-j4b 2 ай бұрын
Mwana woophya kwambiri the Dc
@chrisboyce2
@chrisboyce2 2 ай бұрын
Bon Elias Kalindo president oyamba wa anthu Osaukafe Kuno ku Malawi🔥🔥
@TyconSululuwa
@TyconSululuwa 2 ай бұрын
The Dc Bon kalindoooooo. Auzeni kuti nthawi yathera
@DKMWALE-ew3lp
@DKMWALE-ew3lp 2 ай бұрын
Get well soon
@MillieMalakam
@MillieMalakam 2 ай бұрын
Bon kalindo God ahead u
@Yusuf-j6c
@Yusuf-j6c 2 ай бұрын
I love you ❤️ Mr Dc
@WestonGawaza
@WestonGawaza 2 ай бұрын
Saport kalindo ndikuonaziko likulira kuli ifa zosaikana Borne kalindo amaona patali kwambiri
@SungananiBalaka-z4s
@SungananiBalaka-z4s 2 ай бұрын
Dan Lu ameneyo akudwalayo walupha oyimba azake
@MafavukeJere
@MafavukeJere 2 ай бұрын
Møre fire❤❤❤
@jezalakaphuka7325
@jezalakaphuka7325 2 ай бұрын
Booooooon Kalindoooooooooo the DC mwana owooooopsya kwambiri
@LastonTheniford
@LastonTheniford 2 ай бұрын
Get well soon the D C
@TecksonKaima-dr6er
@TecksonKaima-dr6er 2 ай бұрын
Fireeeeeeeee
@BittonRashid
@BittonRashid 2 ай бұрын
Yes bon kalido aimilileni makolo adyeletu masiku awasalilawao.
@KinziWindassoni
@KinziWindassoni 2 ай бұрын
The born kalindo the dc
@GladesMhango
@GladesMhango 2 ай бұрын
President wathu wathu wa Anthu osaukafe🔥🔥
@cassimyusuf6683
@cassimyusuf6683 2 ай бұрын
Ena omwe mukuziwa tiwuzeniko kuti phiri limeneli ndindani
@AlickChiphwanya
@AlickChiphwanya 2 ай бұрын
Chifiti ukugwa ndiwe chambacho chitha😢🎉😂😂😅🎉nkhope ngati galu
@Amgwagwa
@Amgwagwa 2 ай бұрын
@AnnaPhiri-b8t
@AnnaPhiri-b8t 2 ай бұрын
Adziwe zoti wamphamvu ndi Mulungu yekha chifukwa palinyengo zina ngakhale chuma chako sichingazakupulumutseni
@ThokoLungu-tq6pw
@ThokoLungu-tq6pw 2 ай бұрын
Amen 😢
@AUTONYMOUS-YARD-SOUND-ENTITY
@AUTONYMOUS-YARD-SOUND-ENTITY 2 ай бұрын
Makosana munakapanga focus zanu zja izi mungopa devalue kanthu kanuka za ziii asiyeni machanel andale azipanga zandale izi mulowa nazo pasi izi zofoila izi😂
@ShorayChimera
@ShorayChimera 2 ай бұрын
🎉
@PreciousChlima
@PreciousChlima 2 ай бұрын
The DC mwana woooopsa kwambiri
@CatherineDesire
@CatherineDesire 2 ай бұрын
Phiri la Dr Chikamgawa?👉iwe Bonnie 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤸🤸🤸🤸🤸🙋salute sir🙄🤸🤸🤸🤸🤸🤸🤝
@mercychirwa2147
@mercychirwa2147 2 ай бұрын
Boring government... They must get out of power
@MuhiyeBright
@MuhiyeBright 2 ай бұрын
Zoona bon kalindo more fire
@ThokoLungu-tq6pw
@ThokoLungu-tq6pw 2 ай бұрын
Mulungu wathu saodzela, ulemu wanu the dc
@MalonzoMazombwe
@MalonzoMazombwe 2 ай бұрын
Phiri ligwa nthawi yanji pls!! Tikuona kuchedwa mwina enafe mkupanga party... Phili iwe tagwa amalawi tipume.
@MartinsilverChirwa-fv9wn
@MartinsilverChirwa-fv9wn 2 ай бұрын
❤❤
@PhilbertoChaimah
@PhilbertoChaimah 2 ай бұрын
Inenso ndikuvomereza kuti lingwe kumene😂😂😂😂
@yotamumahomed1313
@yotamumahomed1313 2 ай бұрын
Sikale enafa tinatopa kale any mistake tili ready
@JamesMisoya
@JamesMisoya 2 ай бұрын
More. Faya, osasiya
@jonaslabisonnthyola8036
@jonaslabisonnthyola8036 2 ай бұрын
Machine kung'alula osaoa freedom of expression launched 1996 Chakwera stop arresting people
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 2 ай бұрын
😢
@JamesNyalubwe
@JamesNyalubwe 2 ай бұрын
Uyu eee
@TaweniChavulaKamwendo
@TaweniChavulaKamwendo 2 ай бұрын
Mmm 🤔🤔🤔🤔
@tanishadias
@tanishadias 2 ай бұрын
😂😂😂 my president the DC ❤
@TrizaGeorge-q8w
@TrizaGeorge-q8w 2 ай бұрын
Asiyeni abe momwe angabele kaya amaliza ndrama zose koma mulungu si Lazaro chomwe tikupepha mulungu atichotsele boma limeneli chifukwa siliva ndi golide ndi zake zaye yehova akaba zose mulungu azabwezeletsa kuposa zomwe abazo chomwe tikufuna ife ndi m, tendele mudziko lathu
@WillmotChiuimia-vr6ou
@WillmotChiuimia-vr6ou 2 ай бұрын
Yaa ndizowona zakee ndithu
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 ай бұрын
From 1964 ku malawi sikunakhalepo president wanzelu kaya mulungu dzikoli analipanga bwanji 😢
@Creslevison-vj2sl
@Creslevison-vj2sl 2 ай бұрын
Suli m'Malawi iwe and suyamikai waonekeratu
@temwekamlenje4358
@temwekamlenje4358 2 ай бұрын
-KUBA TSANKHO, KUPHA, FAMILY YONSE M"MBOMA . ENDLESS LIST. NDALE ZONYASA ZA KUMALAWI NGATII DZINA LAKE LOMWE NYASA LAND
@ELLENZAPS
@ELLENZAPS 2 ай бұрын
Inuyo bwana simukuyenera kudwara oyenera kudwara komaso kufa ndi chakwera mfiti
@omarbindula
@omarbindula 2 ай бұрын
Mmm koma yah ziliko
@emmanuelpiffano259
@emmanuelpiffano259 2 ай бұрын
Or JOSEPH NKASA adayimba kale kuti mudziwauza anawa MBIRI yadziko lawo Adanena ndithu zankhanza 😂😂😂😂😂
@EmmanuelMpalagule
@EmmanuelMpalagule 2 ай бұрын
Tasunga video kudikila kut phili limeneli ligwe ndipo tizaitulutsanxo video imeney phili lo likazagwa
@InnockishmaelAnafi
@InnockishmaelAnafi 2 ай бұрын
Respect 🙏 🫡 the dc
@ThomasMwandila-tn7cf
@ThomasMwandila-tn7cf 2 ай бұрын
Wayamba mantha wonkhwima amadwara,osamatumbwa kumwamba kuri murungu akukuwonani
@NizigiyimanaChantal-c2p
@NizigiyimanaChantal-c2p 2 ай бұрын
@@ThomasMwandila-tn7cf choka idiyonyo m,dima umadana mkuunika vaziii vilibe na salt
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 2 ай бұрын
Mo fire winiko umatimilira osadanda tilitonse
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 2 ай бұрын
Winnico mcp ikazachoka usazankhare ndimpando wamba wayesesa
@ChrispinEdward
@ChrispinEdward 2 ай бұрын
Koma thyolo yokhayo ndi mukapanga chibwana tiyambinsa khondo yomwe mukufunayo mufunse mai joice banda mwa goliat.
@ReginaMulipa
@ReginaMulipa 2 ай бұрын
Kalindo tamasuka ukutikuluwikatu chachitikaso ndichani 😂😂
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 2 ай бұрын
One day,,,,,ena adzanong'onezadi Bondo ndithu
@LINELYBISANI
@LINELYBISANI 2 ай бұрын
Kodi akupatsidwa ma 50
@yotamumahomed1313
@yotamumahomed1313 2 ай бұрын
Sikale ay ndipompano tiphana
@LimbanMedson
@LimbanMedson 2 ай бұрын
DC mukutiimililadi ife pitirizani zimenezi
@DRIPMIND-q3n
@DRIPMIND-q3n 2 ай бұрын
Eeeh kwavuta
@VictorJaphet-z5l
@VictorJaphet-z5l 2 ай бұрын
Kodi akalindo mumati mumaimirila athu athu akendiakuti tiuzeni teve pano
@VincentVin-v1p
@VincentVin-v1p 2 ай бұрын
What is the main, go to the point
@ZuzeMbalame
@ZuzeMbalame 2 ай бұрын
Boma ili munkati tilivotere ndi inu nomwe.Ulendo uno mukutisankhiranso okuti timusankhe?Bola musazapwereketsenso aMalawi kachikena.
@ziwani3682
@ziwani3682 2 ай бұрын
The DC president wathu wathu wa ife amphawi
@AlickChiphwanya
@AlickChiphwanya 2 ай бұрын
Chifiti ukugwa ndiwe chambacho chitha
@mphatsogondwe1836
@mphatsogondwe1836 2 ай бұрын
Ayi tikudikira ife tione phiri lokugwa
@PetarKenedi
@PetarKenedi 2 ай бұрын
Phili ligweee💔
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 2 ай бұрын
M.C.P sikubwerela palibe chichita iwo D.P.P ikubwerela boma tidzidya nsima mamawa,masana,manzulo osati M.C.P ndichipani cha satanic
@JacquelineKanjedza
@JacquelineKanjedza 2 ай бұрын
Mcp ikuwinatube ndithu ndipo mwanena kale kuti ikubera
@Creslevison-vj2sl
@Creslevison-vj2sl 2 ай бұрын
Inu tsekani chabe kuchikamwako ,awinise ndamako,iya
@CharlesBanda-pm2oe
@CharlesBanda-pm2oe 2 ай бұрын
Ndiachitsiru ichi wotsatira chitsiru amakhalanso chitsiru
@PatriciaMbewe-xn7ke
@PatriciaMbewe-xn7ke 2 ай бұрын
Bola likhale phiri limene ndikuliganiziralo Malawi apume uyu😊
@SuzgoMkandawire-ss4kh
@SuzgoMkandawire-ss4kh 2 ай бұрын
Ineso ndikuganizira phiri Lina lake
@MaxwellSamuelChikapa
@MaxwellSamuelChikapa 2 ай бұрын
Umphawi sizinthu
@AnthonySadick-u1b
@AnthonySadick-u1b 2 ай бұрын
zofuna amavotera dala mcp
@BlessingsNkhata-q7h
@BlessingsNkhata-q7h 2 ай бұрын
👍👍👍👍👍💕💕💕💕💕🙏🙏
@SalahKamanga
@SalahKamanga 2 ай бұрын
Koma kalindo .eeee mavulutso awa anayamba ndinthu.anthu ambili anenelelapo.ambuye ndemwini wazonse
@ChikumbutsoDzukwa
@ChikumbutsoDzukwa 2 ай бұрын
The DC 😅😂
@PgodfreyBanderouss
@PgodfreyBanderouss 2 ай бұрын
Mangochi anabwera dzulo pansika wa chiponde apolice amangotiopseza mmalo odyera,omwera anamanga anthu ochuluka
@moureenmolesi
@moureenmolesi 2 ай бұрын
ife tikudikira kuti zitero ndithu
@bonfacestoro
@bonfacestoro 17 күн бұрын
......
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 2 ай бұрын
Wakufa saziwika chifuwa chomwecho ukhoza kufa ndiwe chisilu galu fiti chindele
@NizigiyimanaChantal-c2p
@NizigiyimanaChantal-c2p 2 ай бұрын
Ayambira ndimayo ibwa I we atase fiti muleka mwatsala pangono
@charleskayamba-s7c
@charleskayamba-s7c 2 ай бұрын
galu iwe panyapsko kalindo
@ChrisyMbewe
@ChrisyMbewe 2 ай бұрын
Awandi.akatundu.wawa.kuchikwedza uko
@YusufGafa-s3j
@YusufGafa-s3j 2 ай бұрын
Bola ligwe mwachangu Phiri limeneli kkkkkkk
@yusufbakali
@yusufbakali 2 ай бұрын
😂❤
@MussaAndreQuenessi
@MussaAndreQuenessi 2 ай бұрын
Auze mau the dc
@fredwchipatala
@fredwchipatala 2 ай бұрын
Koma uyu
@FloraBanda-w7t
@FloraBanda-w7t 2 ай бұрын
😂😂😂just hit the head of the nail
@MartinMajola
@MartinMajola 2 ай бұрын
Chakwela mbuzi
@azunguauskay4903
@azunguauskay4903 2 ай бұрын
Afe ndithuuu
@OffenLebinala-k9b
@OffenLebinala-k9b 2 ай бұрын
Dangerous child booooooooorn kalindooo!
@ZuzeMbalame
@ZuzeMbalame 2 ай бұрын
Phiri lokugwa lidzadziwika lokha 2025
@LINELYBISANI
@LINELYBISANI 2 ай бұрын
Akutimanga mmasambatu
Kluster Duo #настольныеигры #boardgames #игры #games #настолки #настольные_игры
00:47
Não sabe esconder Comida
00:20
DUDU e CAROL
Рет қаралды 51 МЛН
Миллионер | 2 - серия
16:04
Million Show
Рет қаралды 1,8 МЛН
Jomo wamukana Bon Kalindo
4:20
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 73 М.
TIKUFERANJI 25 MAY 2019
29:39
Edson Gunsalu
Рет қаралды 554 М.
Kluster Duo #настольныеигры #boardgames #игры #games #настолки #настольные_игры
00:47