Koma chonde chonde a comrade Bon Kalindo munakwanitsatu kuwachosa ADAD nakha chikuvuta ndi chani? Kuchosa chikangwayi abale tawuwuze. A comrade Mtambo. A comrade. A ntanyiwa, A comrade Namiwa wa Bakili Muluzi tv. anthu tu ndiwokozek kuyende pamsewu, omwe ali mademo bas chakwera azipita kwawo, bas we love you comrade Bon Kalindo❤❤
@MarthaGama-q1oСағат бұрын
Ndipo inuyo bwana DC ndinu 1 chifukwa mumayankhula mosawopa komanso zimakhala zowona more fire 🔥🔥
@PillianiMekelani23 минут бұрын
👏🏽👏🏽👏🏽👏🏽zonadi sakamele ameyo
@IbrahimSumayila45 минут бұрын
❤❤❤❤ the bc√ Tiyeni tigwilanemanja pobwezeletsaufuluwathu ndifeanaamasiye kambakayimfa ya chilima koma tisadziyang'anilepansi MADEMO!!!! alipo √ ~
@IbrahimSumayila52 минут бұрын
❤❤❤❤ fire fire the bc MADEMO achitike!!! Please Malawi a pulumuke Taluzamiyoyoyazibaleochuluka cozy of Mcp please tiyenitigwilanemanja amalawi chilikwazako mawachilikwayo
@IbrahimSumayila25 минут бұрын
❤❤❤❤ osadankhawa tipulumutsa dzikolindilathu amalawi and will never dzikolanga anthukuzuzibwa inendilimomuno ndizamenyelaufuludzikolanga
@MattinGold-l9wСағат бұрын
Ma transport kukwela mafuta kulibe zakudya kudula boma limeneli LA chakwela munthu oyipa kwambili
@EllenGomani-i4f2 сағат бұрын
SSS nyooo your no 1❤❤❤🎉
@lilianprince66127 минут бұрын
The DC ipase 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@EsterManiyaСағат бұрын
Tazitiyeni pansewu apa tarekani MA audio cz action speaks louder than words let's go to the streat
@stanleykundembo7765Сағат бұрын
Tatopa ndi ma audio pamene dziko likumira ife tikuwona tsogolerani anthu tipite pa nseu.
@YasenYasen-q9g2 сағат бұрын
Dc ❤❤❤❤❤timakunya dlani bwana
@MiddayDelezaСағат бұрын
Chakwera ndi president woyipa pa dziko lonse la pansi Awuzeni the DC olo atagula anthu koma Mcp 2025 pack and go kodi nde kuti m'mene zililimu achakwera akufunanso mbvoti?
@GiftNgwira-e8lСағат бұрын
Bon kalindo moto buuuuuu tikudikira mademo mbuzi chakwera watipha kale
@OwenYusuf-t9kСағат бұрын
DC tilinanu limozi paka woohoo
@HenrySanudi42 минут бұрын
Mumakwana the d c
@JeanBanda-zy6wu58 минут бұрын
Ndipo ndiye ma vote azawelengedwe manual tiwawone kuti apanga zotani ndi ma I'd anyamula a anthuwo akuvundilani mmanja hedeee 😂😂😂😂😂
@TottiesJackie4 минут бұрын
Your not alone MR DC
@HAJIUBAYIDABLACK-q7n40 минут бұрын
The DC wathu mulungu azikutetezani nthawi zonse
@SaidiMbawa-st6bjСағат бұрын
Kwa America 🇺🇸 sikumalawi dziko iriyose iri ndizochita zake
@TriplejMalawi-cx1vj12 минут бұрын
😂😂
@sylvesteralfred83557 минут бұрын
DC apa ndiye mwakhadzulatu Opposition yomwe timafuna ndiimeneyi jakapu sopano mademo anyoooh aja awandikila no Smartmatic, no Mec Chair ndi wapampando wa Mec
Mukanadziwa kuti ndi nthawi yanji tikukhalayi simukananena za kusankhidwa kwa Trump,ndipo ndizisitanilanatu ndi kuno ku malawi amene mulungu afune kuti amupatsa udindowo mufzamuwona chaka cha mawa bapangani za umbuli wanuwu 😅😅😅😅😅