No video

CHAKWERA KILLED CHILIMA | KHAD PROVED

  Рет қаралды 35,766

Malawi Youtube

Malawi Youtube

Күн бұрын

Пікірлер: 63
@raytavares2256
@raytavares2256 2 ай бұрын
Shalom Shalom mlongo wanga greetings to you from London UK. Ndimati tiyeni tigwirizane monga a Malawi tisonkhetse makobidi a president wathu wa anthu osawuka kuti president wathu 'yo wamubera ndarama anthu a Kadukha ndi mfitizo zichite manyazi ammene amutengera ndarama zonse za mtsogoleri wathu mwana wochokera mudothi our orator and the only potus so that asabvutike ndiku- samalira banja lake ndipo so nkhani ya transport akamayendera anzathu osawuka mmidzi akuyendera ma orphans, ma widows and widowers and onse wochokera from unpriveledged backgrounds and discriminated including anthu wodwala matenda a misala ndiponso kuthandiza anthu amene anammangidwa wopanda zifukwa zeni zeni kapena amene ayiwalidwa kuposa mkaidi😂 wakupha anthu koma adamangilidwa kuba bread kapena kuba nkhuku ndi tomatoes chifukwa cha njala korma ayiwaludwa ndi system yoti mafairo adasowa kale kale and papita zaka kuposa 8 years sentence chifukwa choba chocolate or tray ya madzira. Tiyeni tisonkhetse kangachepe kuthandiza munthu wachisoni akufunira mtundu wa chibale aliyense kuti akhale voice for the reasons for all the voiceless. Ambuye akudalitseni pokamba chilungamo.
@MadalenaJoaoMasseco
@MadalenaJoaoMasseco 2 ай бұрын
Ine ndili ku Moçambique Koma zomwe zinachitika ku Malawi ndizowawa kwambiri mntima umandiwawa ngati ndi m'bale wanga .a Malawi chitanikoni kanthu .sizingatheke munthu akhala akumuzengetsa milandu kenako ndikudzati basi mulandu boma lathetsa ,panepadja kunali kumphimba mmanso ndikuti akudziwa kale Kuti timupha pompano.
@AchinaKellz
@AchinaKellz 2 ай бұрын
yes guy's pa 10 go komko
@ChikondiBanda-ce8tk
@ChikondiBanda-ce8tk 2 ай бұрын
Many African people are watching us Malawians. What we will do next. If we can just let it go like that, we will be considered the weakest people.
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 2 ай бұрын
Iwe Chakwera uwona zachitika ku Kenya 🇰🇪 usamale,anthu ako ukulowetsa mudziko mwathu usiyiletu dziko silako siwe mulungu galu iwe uchoke sitikukufuna takutopera
@GodfreyWhayo-hh1dm
@GodfreyWhayo-hh1dm 2 ай бұрын
Mwati muyankhula muchichewa koma mukuphatikiza dziyankhulidwe dzina .
@AchinaKellz
@AchinaKellz 2 ай бұрын
Timanga olo angofelatu mwaulemu Nancy, gotani hara mumangiretu mabanja apa mufa ndende ikudilira inu,there is no one who can vote for blood
@ukanie
@ukanie 2 ай бұрын
Ine ndikuti ngati Chimwendo banda anati ndenge inazaza it means there where pipo inside which occupied the remaining seat which where invisible to the pipo inside the plane but Banda new about it.
@ukanie
@ukanie 2 ай бұрын
And those invisible pipo where the pipo Who eliminate Chilima.
@JohnKayinga
@JohnKayinga 2 ай бұрын
Wandikumbusadi MCP ndi Israel kuyambira kale amagwilizana I remember nthawi ya kamuzu Banda tinali ndi malawi young pioneer amathandizidwa ndi ma Israel pa ma training awo komaso zida za nkhondo
@modestamhango611
@modestamhango611 2 ай бұрын
Zoona mwanenazi. Nthawi ya operation bwezani a MYP adapezeka ndi zida zomwe a MDF analibe.
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 2 ай бұрын
Eeeish Malawi wathu,Yehova ekha atigwilire nkhondo
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 ай бұрын
😂😂 kodi chakwera unabadwila kuchipatala kapena pasi pamtengo chifukwa dzi anthu dzobadwila pasi pamtengo sidzikhala ndi nzilu monga iwe chakwera 😂😂
@HamiltonwaNamuwah
@HamiltonwaNamuwah 2 ай бұрын
Zikudwabwitsa chifukwa Ndege inagwera pafupi ndi midzi and guard wa pa chitawa anawona zonse ndipo anamutseka pakamwa. Koma chilunga its a plot cha Boma la Chakwela ndi chipani chake cha MCP. Komano ili ndi dziko ndipo limazungulira.
@HamiltonwaNamuwah
@HamiltonwaNamuwah 2 ай бұрын
Mchifukwa chake amawalozela ku malo olakwika kuti azikasakako ndege, chonsecho akudziwa komwe kuli Ndege. Komatu Mulungu alipo wa moyo ndiye ayi ndithu ili ndi dziko
@user-du9qs4tb6u
@user-du9qs4tb6u 2 ай бұрын
Chakwela ndiwe munthu oyipa mulungu sakukhululukila ndipo udzafa ngati galu mulungu amaona 😢😢😢😢😢
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 2 ай бұрын
Zosayenda big zoona zake ndithu, I hate mcp from long time
@Billy-sr1ol
@Billy-sr1ol Ай бұрын
Have u ever sat down and think kuti ndegeyi ndi ya 1988? Do u think malawi can maintain ndege bwinobwino up to standard??? Land-rover ya police 2 years old munaionako how it looks? Think about that
@DannielOnions-fy3dc
@DannielOnions-fy3dc 2 ай бұрын
Nice one thanks brother keep 👍 it up please
@MatthewsGideon
@MatthewsGideon 2 ай бұрын
😮😮onily ja knows
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 2 ай бұрын
Apha wañthuwa Ndi a MCP tonse taziwa,a fisi amenewa koma Ndiye awononga Malawi wathu.sakuziwa zoti amalawi ada penha, ndipo ambiri tiri kunja koma Kuti konzera Maliro ifeyo kunja Kuno nkumatiririsa, But this people,nnnhhm.ele tenq ter quidado nos somos pessoa vamos resolver isso agora, não há problema vamos fazer greve, até eles saíram
@MaxwellMbesa
@MaxwellMbesa 2 ай бұрын
Anthu oipa kwambili awa nthawi yawo yatha sikale ziwateata zoipa achitazo
@KhebranConnections
@KhebranConnections 2 ай бұрын
Office of the vp called for the plane not the rubbish u are talking....and chilima sanali pa protocol yoimila president
@malawi_youtube
@malawi_youtube 2 ай бұрын
I'm not the one talking contact khadi
@wittinessnkhokwe
@wittinessnkhokwe 2 ай бұрын
Machende Ako mwa obadwila ku uhule iwe
@MikeKapondah
@MikeKapondah 2 ай бұрын
​@@wittinessnkhokwei nd mbuz eti ndwe modz wawo mwapha vp, kma mnyera2. Nyapanu nd lazalasi wanuyo mnyera.
@KhebranConnections
@KhebranConnections 2 ай бұрын
@@MikeKapondah Hahaha I jst laugh out ....ine zotukwana ai am smart if u have ma facts olo mfundo u welcome...koma poti dpp munazaza manyi mmutu mwanu bas mukalephela mfundo u resort kutukwana
@user-re7fo3be2z
@user-re7fo3be2z 2 ай бұрын
Komano adali pachani
@alexsumani6823
@alexsumani6823 2 ай бұрын
😢😢
@BlessingsKalonga
@BlessingsKalonga 2 ай бұрын
Akanamwalira Chakwera bwezi tikuti waphedwa ndi Chilima may his soul rest in peace zokamba kuchuluka ena akuyakhura kuti ndi amuyaya
@AchinaKellz
@AchinaKellz 2 ай бұрын
Khanga zaona anthu awa adzuzika ndalama zikhala chete
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j 2 ай бұрын
Ndipo kwambiri tu mmm
@user-dp7bc7yy6s
@user-dp7bc7yy6s 2 ай бұрын
Amwene mukamanga ma voice anuwa nxt hr muziyetsetsa kubweza volume wailesi wanuwo
@user-du9qs4tb6u
@user-du9qs4tb6u 2 ай бұрын
Boma lakupha osanyengelela
@RichardMofya-so5hk
@RichardMofya-so5hk 2 ай бұрын
Puti chakwela on fire
@Billy-sr1ol
@Billy-sr1ol Ай бұрын
Mboli yako iwe ndege sinaombe Phili chek the photos properly that plane was landing they tried to land it coz they thot its a ground check nkukuluzi umene inalemba frm point of impact mungolankhula zosazidziwa bwanji. Ndege ikagwa ngati mwala imathelatu the fuselage gets destroyed alot if the fuselage its not destroyed kwambiri it simply means that it came down with less speed kapena titi it was controlled although there was alot of challenges. Mukati anaing'Amba wat do u mean ? Anaingamba ndi chani.
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 2 ай бұрын
Kodi nanga anthu ena 8 wo imfa yawo inali yotani? Anali atatengera kuti pamenepo sipakumakambidwa bwanji?
@robertkabade5011
@robertkabade5011 2 ай бұрын
Yehova mwini wake ateteze malawi wathu
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 2 ай бұрын
Ndi mfiti ya president Chakwera okupha
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 2 ай бұрын
Malawi wa lero
@BMDMasulani
@BMDMasulani 2 ай бұрын
Raf anali ndinzeru kwambiri adamupanga chipongwe kwambiri raf sangamwe zomwe amanazi chakwera ndi chitsilu
@mathewsosman7313
@mathewsosman7313 2 ай бұрын
Amen
@ChimwemweZgambo
@ChimwemweZgambo 2 ай бұрын
Mvula ikagwa zoliralira kuchuluka😢
@user-lg2ws2ki3d
@user-lg2ws2ki3d 2 ай бұрын
Poti sunayike khope Yako that's why nakutsakula fork 1:34
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 2 ай бұрын
Mudzipha anzanu ngati nkhuku choncho muzadziona Mulungu alipo kunja kuno
@RamseyWasi
@RamseyWasi 2 ай бұрын
Tiyeni tiingobwerera kwathu ku Eden
@ruthkundwe7448
@ruthkundwe7448 2 ай бұрын
Paja moses sanakalowe nao mukenani
@andyomar1618
@andyomar1618 2 ай бұрын
This is fact guys chakwera ndiwakupha
@KhebranConnections
@KhebranConnections 2 ай бұрын
Where is the evidence . ?
@AchinaKellz
@AchinaKellz 2 ай бұрын
Talk talk bro
@BlessingsKalonga
@BlessingsKalonga 2 ай бұрын
Nde face ukuzipangaso edit aaaaa
@Billy-sr1ol
@Billy-sr1ol Ай бұрын
Inu nde ndimangoona ngsti ndinu a salvage mumanama koopsa u don't have information or knowledge about things
@MasegoModukanele-xg2hj
@MasegoModukanele-xg2hj 2 ай бұрын
Mukanenela komweko
@user-hg2cw1om1p
@user-hg2cw1om1p 2 ай бұрын
U umakwana brother
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 2 ай бұрын
Wakupha kumene uyu
@LukaThawe
@LukaThawe 2 ай бұрын
Iwe ndiwe ndani choyamba uzitiuza dzina lako mapwala àko galu iwe palibe chimene ukunena mbuzi yamunthu
@LukaThawe
@LukaThawe 2 ай бұрын
Mulomo wakuwo Mumbai Ngati ukumwa manyi
@ElizaSichinga-gn9je
@ElizaSichinga-gn9je 2 ай бұрын
Shupit,wasowa zochita eti,apeze athu ena owanamiza
@Billy-sr1ol
@Billy-sr1ol Ай бұрын
Ine i can not buy ur nonsense u just dont know wat ur saying
@BLADSONBOSTON
@BLADSONBOSTON 2 ай бұрын
Tava ndeno titani
@MalonieBanda
@MalonieBanda 2 ай бұрын
Zazii
У ГОРДЕЯ ПОЖАР в ОФИСЕ!
01:01
Дима Гордей
Рет қаралды 5 МЛН
МЕБЕЛЬ ВЫДАСТ СОТРУДНИКАМ ПОЛИЦИИ ТАБЕЛЬНУЮ МЕБЕЛЬ
00:20
Now it’s my turn ! 😂🥹 @danilisboom  #tiktok #elsarca
00:20
Elsa Arca
Рет қаралды 12 МЛН
A Michael Usi Inu Si A UTM - Lyton Mangochi
23:13
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 34 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 250 М.
HOT CURRENT KUNG'ALULA MOSAONA NKHOPE 1 September 2024
55:12
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 116 М.
У ГОРДЕЯ ПОЖАР в ОФИСЕ!
01:01
Дима Гордей
Рет қаралды 5 МЛН