Chakwera V Mutharika: 2025 Kuli Gule - Redson Munlo

  Рет қаралды 10,190

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

Күн бұрын

Пікірлер: 304
@ChrispineJonathan
@ChrispineJonathan 2 ай бұрын
Kuvotela chakwel ndichimodzimodzi kutseka kobibila mkumabibila kukamwa amuthalika my vote
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 2 ай бұрын
Ndie akutukwana kwake kumeneku nkumati inuyo mungadzalamulire kopanda tsankho? Alomwe inu!!
@garnetphiri
@garnetphiri 2 ай бұрын
Kkk ok kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkokkkkkkkkkkkkkkkkkk ok kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkokkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkokkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
@AgnesMatola
@AgnesMatola 2 ай бұрын
Mbava za MCP izi
@AgnesMatola
@AgnesMatola 2 ай бұрын
Mwawononga dziko A galu inu 😢
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 2 ай бұрын
@@isaacchiwaula731pamtumbo pako iwe ndiChakwera wakoyo chitsiru iwe
@JonathanMsiska
@JonathanMsiska 2 ай бұрын
Saulos Chilima ndiamene azawinise Peter Mutharika mawu anga sapita pachabe.
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 ай бұрын
Mesa chakwera ndamene Ali muboma chifukwa chan chilima yemweyo munamupha agalu inu
@Blessings-b7h
@Blessings-b7h 2 ай бұрын
Zoonadi kuti muthalika ndi Chakwera ndizosiyana chifukwa choti Chakwera ndi wakupha.
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 2 ай бұрын
Zoonadi ndi wakupha
@amosnyirenda-pl1ss
@amosnyirenda-pl1ss 2 ай бұрын
anapha bombo ako kape iwe mzazvutika nayo dpp yanuyo
@BrightZionga
@BrightZionga 2 ай бұрын
​@@amosnyirenda-pl1ssadapha chilima
@ellennchambalinja484
@ellennchambalinja484 2 ай бұрын
Chilima rest in peace my dear
@DanNzima
@DanNzima 2 ай бұрын
APM my vote
@JoshuaMbewe-ff5mk
@JoshuaMbewe-ff5mk 2 ай бұрын
Iwe Redson mapwala ako a bambo ako mayi ako a village anu ndi mudzi wakwanu onse machende anu
@StevenGama-i2n
@StevenGama-i2n 2 ай бұрын
Pepani amwene chitsiru chili ndi mwini
@PollyLysonLutepo
@PollyLysonLutepo 2 ай бұрын
Popeza kuti makutu amamva chilichonse. Ndicho chifukwa timamva nkhani za m'nulo. Ine kuti ndidziwe kuipa kwa chakwera ndi mcp ndi m'nulo ndi ben longwe. Pachifukwa ichi ndikuti dzikomo a m'nulo. Ndalama yagwiladi ntchito pa anthu awiliwa..
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 2 ай бұрын
Poti anakupasa money,yang'ana ma comment a wanthu ngati mcp izawine kuposela kubera
@MercyNkhoma-b6h
@MercyNkhoma-b6h 2 ай бұрын
Koma a Munlo afikapo, umphawi wakukhadzulani achimwene. Mavuto amamupeperetsa munthu.
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 2 ай бұрын
Eyaa uphawi sizinthu ndaonera munulo
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 2 ай бұрын
Muthu kulephela ivini kutsekela nsokhano wake wa conversation ndeno angakhale president wadziko,,,kulifunila dziko la Malawi ubwino aii guys khalani Sirius plz
@ChifundoJohn-w3t
@ChifundoJohn-w3t 2 ай бұрын
Machende ako plus mbolo yako yosadulayo wamva usalimbane ndi DPP wamva ife tinakutuluka kale kale ndipotu sitimakusowa gwape
@JuniorJone-v1g
@JuniorJone-v1g 2 ай бұрын
amutharika my vote 🇲🇼🇲🇼
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 ай бұрын
Iweyo ndwe kape olo atapanda kugona km ndi wakhupha peter ndamene tikumufuna ife atiphure pamoto akuphawo sitikuwafuna anamupha chilima anthu oyipa iwe munulo machende ako wamva
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 2 ай бұрын
Kodi mumafusilaji kuti chakwela ndi apm iwe redson uzagovotela chakwela koma ine wanga ndi madala APM
@UseniMailosi
@UseniMailosi 2 ай бұрын
Ife tinavotera chakwela koma pono sindingakufotere
@ChrispineJonathan
@ChrispineJonathan 2 ай бұрын
Utafe ndiwe palibeso Cha zelu ukulankhula kapena iwe
@JACKSONHULUWA-j2n
@JACKSONHULUWA-j2n 2 ай бұрын
Kape iwe anaukugula ndalama zingati? Kape
@MaxwellMbesa
@MaxwellMbesa 2 ай бұрын
Sitikuvotera zaka koma kuthekera kwa munthu iweyo khara ndi mcp chikangawayo
@michaeltchuwatchuwa5699
@michaeltchuwatchuwa5699 2 ай бұрын
You are very mad person my vote is going to dpp
@DanielDoctor-t3p
@DanielDoctor-t3p 2 ай бұрын
Iweyo nzeru ulibe nkhani ndiyoti Anthu atopa ndi mr chikangawa mukamalankhula muziganiza wava iweyo garu
@Drmuhammadchiwona
@Drmuhammadchiwona 2 ай бұрын
Gwape uyu
@eddiesilika618
@eddiesilika618 2 ай бұрын
Thawi zina ndibwino kukhala tchete ngati ulibechonena chazelu,chakuti chako buzi,ingodikila uwone angagwele Lazalo wakoyo
@AdamNapwanga-ff2wm
@AdamNapwanga-ff2wm 2 ай бұрын
Gwape weni weni za ziiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii8iiiii chule
@JusticeKawilira
@JusticeKawilira 2 ай бұрын
Zoti MCP idzawina mukunamizana ku MCP komweko tapitani kumidziko mukamve maganizo a Malawi akumudzi APM my vote
@WonganiKatchale
@WonganiKatchale 2 ай бұрын
Auzeni akuzinamiza
@SuzgoMkandawire-ss4kh
@SuzgoMkandawire-ss4kh 2 ай бұрын
Chikangawa party
@AbdulmalikAmanu
@AbdulmalikAmanu 2 ай бұрын
Yes is better kuvotela Peter muthalika ndikuvotera chikangawa bola Peter ntchivukwa chikangawa ndimunthu wakupa anamupa mzake chilima kuyiwalira kuti anamuwinisa bola Peter ngakalekuti ali wa mkulu is no problem
@joegibsonzulu2599
@joegibsonzulu2599 2 ай бұрын
Munlo singing for his supper. Ndale zaku Bagamoyo adakonza.Maluzi amamusintha munthu.
@ThomasStephan-tg6ng
@ThomasStephan-tg6ng 2 ай бұрын
Iwe pachende pamako pamozi ndi chipaniakowo ndi chakwera wakoyo😊
@pauljosephmakaula6835
@pauljosephmakaula6835 2 ай бұрын
Mudzadzimuka Mutharika asakuyima kutabwera mnyamata wa Economics...
@PlanzaWisiki-cv2fs
@PlanzaWisiki-cv2fs 2 ай бұрын
Mapwala ako amunulo
@BilalihmacksonBilalih
@BilalihmacksonBilalih 2 ай бұрын
Mbwelera izi
@LehmanManere
@LehmanManere 2 ай бұрын
Line up doesn't matter all we want is change and good governance
@hagayichiluwe
@hagayichiluwe 2 ай бұрын
Munthu wazeru dziko lonse lapansi 🔥🔥🔥🔥🔥🔥💯
@SuzgoMkandawire-ss4kh
@SuzgoMkandawire-ss4kh 2 ай бұрын
Chikangawa party ndi yanzeru?
@MussaZakeyu
@MussaZakeyu 2 ай бұрын
Ndilibe mawu ambili km wekha uone ma comet okhawa ndi mavoti kale 😂 ndiye uzikati chakwela awina 😂😂
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe 2 ай бұрын
Mwina mudzachite kuberatu koma paulere ndakaika,APM my vote
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 ай бұрын
Amunilonso ndinu achitsiru mwasowa zokamba basi kulimbana ndi Dpp munya muwona mwayiwala kuti mumatulutsa ma audio anu womutukwana razalo, lero ndalama zafika pa inde Inde la 40 lidzakwana pangatalike Maka dpp woyeeeeee ❤❤❤❤❤❤❤ angasapote Mcp ndi mbuli wa mbuli zonse, chifukwa ngakhale mwana akudziwa kuti Mcp ndi chipani chokhetsa mwazi
@MaryNgwira-s5z
@MaryNgwira-s5z 2 ай бұрын
Dpp my vote
@victorauwana7258
@victorauwana7258 2 ай бұрын
Mungozitukwanisa munlo
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 2 ай бұрын
Umuze Chakwerayo akuyembekeza Ku ndende,ukuseka chapa Kati cha Mako,umuze Chakwerayo lipoti lachikangawa lituluke, Amalawi akufuna Wanthu amzeru achikondi Osati Okupha koma iweyo Panyero pa Mako
@EdnahShantell
@EdnahShantell 2 ай бұрын
Litembeleledwe thako la mzimayi anakankha chimutu chakocho ubongo wake osakanizana ndi mamina Dpp my vote
@LenardWillard96
@LenardWillard96 2 ай бұрын
The game is president muthalika he's ahero in Malawi Government for sure.MCP Government they know nothing more especially president.That's why muthalika's family we call them ngwazi.
@McDonaldbeketeNkhata-n4l
@McDonaldbeketeNkhata-n4l 2 ай бұрын
Mzanga iwe akutuma Chakwera kadya ndalama izo akupasa koma mawa uzalira
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 2 ай бұрын
Kuvotela Peter Mutharika zili ngati muthu amene sakuona matso kapena tinene kuti wakhungu,,,,,taonani manja a Peter Mutharika akulephela olo kugwila bwino pepala basi muthu kumu ponyela vote zoona zimenezo,,,ngakhale zitavuta motani sindingavotele DPP.
@Georgemphamba-to1ik
@Georgemphamba-to1ik 2 ай бұрын
Che mmunlo mukuzinamiza nokha. Kodi ndi ndani amend Amati, Tamita mumsika wa Limbe ukanene kwacha kwacha ngati sugendedwa. Anthu adzasankha Poona mfundo ndi pa ground pali bwanji . iyi sinkhondo yomenyana ndi manja kuti ifuna mphamvu za thupi ayi. Usapeperetse a Malawi akuziwa omuvotera. Inuyo simungauze anthu chochita. Zidyani ndalamazo zikatha muzatipeza
@macleodphiri3759
@macleodphiri3759 2 ай бұрын
Even if you elected angels, your party MCP is an island.
@alfredhanleck9043
@alfredhanleck9043 2 ай бұрын
Mapazi ako iwe munlo, si iwe wemwe umkat pano sungapite munsika wa Lizulu ndikut kwachaaa ! Suyankhidwa
@rashidadan2533
@rashidadan2533 2 ай бұрын
Musavutike ndi mtima , MCP palibenso kubwelela m'boma . Redson munlo alibe mzelu zotiuza amalawi
@SmarshChikwanah
@SmarshChikwanah 2 ай бұрын
Achisiru inu
@VincentKamwendo-e9t
@VincentKamwendo-e9t 2 ай бұрын
Peter my vote
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 ай бұрын
Chakwera umkamutukwana za mkabudula ndi ben longwe wako uja lero mwakoma chakera woyee tione ngati anthu sakutibula mu msika achitsiru inu.
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 2 ай бұрын
Mutukwana mutopa kkkkkk koma bola mwanvera audio-yo 😅😅😅😅😅😂😂😂😂
@BenBanda-q9j
@BenBanda-q9j 2 ай бұрын
Mutharika akumufuna a Malawi ambiri chifukwa chakwera ukumufuna wekha ndiye umuvotere chakwerayo wekha
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 2 ай бұрын
DPP ayiiiii plz a Malawi,,mudzakulukuta manoooo
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 2 ай бұрын
Mankhwala akumwa a Redson munlo sangafike zaka za APM, Mayankhulidwe ake chinafa kale ichi
@FungulanReuben
@FungulanReuben 2 ай бұрын
Maphala Ako iwe, chikangawa sangawine, zingodyani ndalama zamishoko ya Malawi
@FosterChakanga
@FosterChakanga 2 ай бұрын
Pa chisale yaopa mbuzi iyi😂😂😂😂😂ndipo ukamati mpikisano kodi ukuona ngati ndiothamanga???😅😅😅Umbuli ndi matenda sure!!!
@ChristophrMaiko
@ChristophrMaiko 2 ай бұрын
Koma ameneyi ali ndi azibaleako ku malawiko chifukwa anakati azimuzuzula pazomwe akuyankhulazi vuto azingozitukanisa komanso azibaleakewo pamozi ndi ana ake samapasidwa ulemu mr mulo zisiyeni izi taonani mmene mwatukwanilidwa mmmmm ai ndithu
@MandalaChaona
@MandalaChaona 2 ай бұрын
Anyamata a Zikwanje tsopano 😂😂😂😂😂 Msundwe Chabe 😂😂😂😂 zithani mawu Koma mudziwe Kuti Odzawina ndi kutenga Boma Mulungu wamusankha kale poyang'anira ndi mbiri zake Wosapha, Wopanda tsankho, Wachikondi, Wosaba, Wodzichepesa .
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 2 ай бұрын
Koma Munlo makadeti akutukwana koopsya 🤣🤣🤣 wandiseketsa bwanji 🤣🤣
@JamesRoben-dy7bx
@JamesRoben-dy7bx 2 ай бұрын
Muthalika ndi chakwela sangafanane zoon muthalika alibe mbili yokuba kupha kuba nkhadza alibe muthalika koma chikangawawa mmm waonjeza kuba kupha khadza mmm ai chakwela mm out in Jesus name
@MericksonAbello
@MericksonAbello 2 ай бұрын
Chakwera ndiwoipa kwambiri okudya Matewera
@KennedyChikapa-v1p
@KennedyChikapa-v1p 2 ай бұрын
Vote yanga Peter basi
@MathewsChitsulo
@MathewsChitsulo 2 ай бұрын
Akulu Inu ndi wopusa kwambiri mulibe nzelu akukutumani ndi atsilu pitani mukayambileso. Mbudzi ukuyinenayo chakwela alive ndi mzeru zomwe ungayelekedze ndi anthu ena? Ndichifukwachake akungopha athu amene akuoneka anzelu
@DanielChisaka-tg1il
@DanielChisaka-tg1il 2 ай бұрын
Iwe redson Kaya ukufuna chakwela akupaseni ndalama zina wauponda DPP ikuwina ndipo uzathawa Malawi iwe chifukwa cha manyazi
@MustaphaChimangeni
@MustaphaChimangeni 2 ай бұрын
Kodi munkati suite iliyonse amavala chakwela mulinayo ndetiziti mukupikisana😂😂😂komanso umalimbikila kutindiwe ophunzila koma bwanji still umaonekakuti ndiwembuli komanso savage munthu osowa zochita I believe even akadzi ako amachita nawe manyazi
@AndersonChiponola
@AndersonChiponola 2 ай бұрын
Redson Mutu wako sumayenda bwino kagone ngati wankhuta mbewa
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 2 ай бұрын
Komaso Munro ukamalankhula umaonekeratu kuti fundo ulibe ..uli busy kudzilumaluma koma fundo zako mwana wen wen ..udindo sakupatsani olo mutelo 😂😂😂
@UmaliIshmael
@UmaliIshmael 2 ай бұрын
Achakwera akupanga chani lwe munlo
@anusahjenala1063
@anusahjenala1063 2 ай бұрын
My vote is munthalika
@ebenezerkamanga6016
@ebenezerkamanga6016 2 ай бұрын
Ndi chifukwa munamupha kuona ngat mutenga ma vote awo unya ovota ndife si iwe ndi kabwira wakoyo
@FrankMwachande
@FrankMwachande 2 ай бұрын
Kodi ndindani iyeyu tandigaireni photo Yake ndimuziwe galuyu
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe 2 ай бұрын
Kodi mesa a munlo amati anasiya kuyankhulira a Malawi? Ndiye akuyankhula zichani apapa
@JamesRoben-dy7bx
@JamesRoben-dy7bx 2 ай бұрын
Fuso ndilakut akufuna chakwela kut atan walephela wagwesa kwacha wapha athu oziwa ndiye akufuna atan plz chakwela sazawinaso olo half
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 2 ай бұрын
Awudzeni mwina akhodza kunva,,,,ngati sakunva asiyeni akwele yakubwa tayala,,,, ubwino wake kaya afune kaya asafune chakwela akupitilidza kulamulila malawi,,, uthenga ndi umenewo.
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 2 ай бұрын
Iwe amene amakuvela ndizitsiru pamtumbo pako munlo
@IvyMkhura
@IvyMkhura 2 ай бұрын
Ukuti line up ya mcp ilibwino, azavote ndi achina Jessie Kabwira akowo? Ovotati ndi amphawi amene ali mmidzi, amene akuzunzika ndi njala mmidzimu. Mbuzi yopanda mzeru iwe.
@LawrenceMalinda
@LawrenceMalinda 2 ай бұрын
Iwe ndi mphake wa chikangawa machende ako ndithu iweyo ndi bambo Ako achikangawa mudzalakalaka kulowa pansi pa nthaka palibe angadzavotele MCP ndipo mudzakhawula ndithu mudziwudzana ndi nzako Ben Longwe wakoyo anthu oputsa ngati inuyo dzipumi ngati akwiri .
@StephanoMaganizo
@StephanoMaganizo 2 ай бұрын
Umbuli umenewo kuphuzira sindiye kuti ndiwe wanzeru zedi nkhani ndi thinking mbuzi iwee
@EvanMchere-qf8fs
@EvanMchere-qf8fs 2 ай бұрын
Chakwera ndi Munthalika ndizosiyana kumene chifukwa chakwera ndi mubusa or ndi church chomwe chinamumvuta kuyendetsa peter tu paja anali president tinaona kale ntchito zake inuyo ngati ali a mcp ndi zanu vote yamunthu imakhala mu mtima mukungomvutika ndikulakhula a mcp munadzipanga dekapeni nokha pomupha chilima,
@wisdomchilanga723
@wisdomchilanga723 2 ай бұрын
Koma DPP chilowereni muboma ma vice sanaphedwepo ndimumozi yemwe. Koma MCP kwawo ndikupha,Kuba, maboza,kaduka,Njala, Corona, sankho koma mwalipha dziko ndinu you will never wine
@GiftChitsulo
@GiftChitsulo 2 ай бұрын
Iwe ASE ndikukulonjeza ngati suganiza bwino kuchipani chako cha MCP Cho sungawineso kwanuko pa mp
@KnowledgecGodwin-xo4pw
@KnowledgecGodwin-xo4pw 2 ай бұрын
Tangonenani kuti ndalama zatha akupaseni zina Achisiru anxanuwo, amasikini inu.
@Littlefair7
@Littlefair7 2 ай бұрын
Aaaaa iyayi, mfundo zandale zisakhale zopanga attack age yamunthu, uku ndikuyankhula kwa ubulutu, ndale mwayamba liti inu? MCP mesa mwalowera dyera iwe ndi mzako ben Longwe.
@wahosonsoso
@wahosonsoso 2 ай бұрын
💙💙💙💙💙 my vote
@MaryNgwira-s5z
@MaryNgwira-s5z 2 ай бұрын
Patseni number yayemwe akuyankhulayo
@JessicaManda-zm1ug
@JessicaManda-zm1ug 2 ай бұрын
Chakwera must go
@SteveBishopPhiri
@SteveBishopPhiri 2 ай бұрын
Awa nda chitsilu tiyankhulitsa molakwika ndinu opanda mzelu bambo mumat sinu wandale izi ndichan palibe chamzelu mwakambapo apa mudziwe kt Mulungu saika.munthu chifukwa chamamphumziro kpena kudziwika taonapo ife Mulungu akugwilitsa ntchto anthu opanda mbili kt ukulu wake uwonekele misachedwe ndimaphunziro km yamban mwayang'ana zomwe kumwamba kukufunila dziko.lamalawi kt lidutse
@ellennchambalinja484
@ellennchambalinja484 2 ай бұрын
Chilima rest in peace 😢
@KondwaniNguleti-x1q
@KondwaniNguleti-x1q 2 ай бұрын
Iwe Munlo panyapako palibe chomwe ukudziwa
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 2 ай бұрын
Olo kumwa katchatsoyo ku votela DPP basi muthu kukhala pa line yovota uku votela DPP
@HumphreyKachepa
@HumphreyKachepa 2 ай бұрын
Kodi Mesa iwe umati wasiya zolankhula ifetu sitiyiwala komanso sife opusa
@EmmanuelSambani
@EmmanuelSambani 2 ай бұрын
Ndimaona ngati uyakhula za nzeru koma popeza maloto salesana
@SuzgoMkandawire-ss4kh
@SuzgoMkandawire-ss4kh 2 ай бұрын
Redson machende ako pamoz ndi chikangawa party
@PatrickChifunilo
@PatrickChifunilo 2 ай бұрын
Zosatheka Mwalemba M'madzi
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 2 ай бұрын
Iwe mumlo udzingodya ndalama akupatsazo,,APM akadzawina tisadzakuone uli khwekhwere kisendera konko
@eliaskhofielias8152
@eliaskhofielias8152 2 ай бұрын
😂😂😂 MCP ndinu ana kwambili amunulo even mutachita kuichemelera bwanji mcp mugwera nayo kuphompho limodzi 2025.tidzakukokani zolendelerazo nxt year mutaluza.kukopa anthu sizocheza mcp ndiana kwambili ndi line up ya DPP ndiyokungana.
@EmmyYafete
@EmmyYafete 2 ай бұрын
iweyo ndiwechitsilu sunganiza,mbuzi iwe, munthalika boma 2025
@GracianSomola
@GracianSomola 2 ай бұрын
Nde ndani angazavotere Chakwera 😂😂😂😂😂
@IsmailTambula
@IsmailTambula 2 ай бұрын
Ulibe kuganiza mulo chikwa ngat ndawi ya mutalika timagula chimanga 7 yachakwela 50'000 zikutsiyana kwambir ndiye aliyese akufuna kugula dzindu mochipa komaso chakwela pemene anazitembelela yeka powasiya anthu 9 kichikangawa paka mawa kwiyo waanthu ulipamenepaja kuluza kulipo muzingozipasa minyama komaso munthu amene amatukwanidwa amawa ukapemba chele komweko ndipo mutalika ukamamutukwana mukumupasa mwayi omwina ndipo mulungu mwin kusoza ozikweza ngat inu
@ChristophrMaiko
@ChristophrMaiko 2 ай бұрын
Ndipp iyeyi akamabwela poyela chonchi nkumalankhula izi alibe manyazi ngati wasowa chochita bwanji osapita azikasisita maliseche ankazache bwanji ? chifukwa akuoneka kuti alibe chochita galu ameneyi
@MathiasVictorBanda
@MathiasVictorBanda 2 ай бұрын
DPP oro itakhara osapanga kampeni ndiyowina kare,anthu akudzwa ndipo akuona okha mmene Dziko likuyendera
ZAULULIKA MCP YAPHA MUNTHU WAKE YEMWE - UYU NDIYEMWE WAULURA ZONSE
5:04
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 48 М.
Elza love to eat chiken🍗⚡ #dog #pets
00:17
ElzaDog
Рет қаралды 12 МЛН
Sigma baby, you've conquered soap! 😲😮‍💨 LeoNata family #shorts
00:37
General Election 2024: What's in store for education?
1:00:06
The Sutton Trust
Рет қаралды 2,1 М.
MCP Ikuwina Zisankho Mu 2025 - Redson Munlo
19:53
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 4,4 М.
NKHANI ZA LERO__CHIPANI CHA UDF 29 October 2024
18:54
HOT 265
Рет қаралды 7 М.
Elza love to eat chiken🍗⚡ #dog #pets
00:17
ElzaDog
Рет қаралды 12 МЛН