I will vote next year because of chikangawa accident witnessed by my naked eyes,rest well my handsome VP SKC
@user-uk3bz1hr5tАй бұрын
Ndpo inenso
@paulphiri-fz9meАй бұрын
❤ love you bro
@PempheroMoleniАй бұрын
Muli NDI ufiti
@chisonimponda363Ай бұрын
Vote vote basi
@user-ol7xv3ws6gАй бұрын
Same as me. Ndinkaseka agogo anga akamandiuza zomwe amakumana nazo nthawi ya mcp koma pano sizokuti ndukunva koma kuuona
@EdenEreneoАй бұрын
Tsoka kwaiye anatengako mbali pa ifa imeneyi sazaona mdalitso Amen 🙏
@BlessingsMassiАй бұрын
Amen
@YamikaniMwale-bo7cvАй бұрын
Powerful message,,,we silute you,,,, keep on doing this please
@GeraldmkwewuАй бұрын
Amen amen amve Mr chikangawa fiti
@UsenLashidАй бұрын
Mawu amphavu kulakhula mosaopa munthu koma kowopa mulungu
@user-pv9uk6sc3wАй бұрын
Mmmmmmm, koma a Bishop inu mwamaliza zonse, ndipo kumene aliko mutu waima Chakwera ndi boma lake la MCP. Tili pa mbuyo panu Bishop, osafowoka, osatopa .❤❤❤❤
@MaxwellChiwaya-tv7knАй бұрын
Ine mpakana lero sindikumvetsabe kuti Biyeni anamwalira mmmmmmmmm only God knows
@esthermalixani2244Ай бұрын
Zoonad
@user-xm1ic3nr9wАй бұрын
Tiyen tipitilize kuyatsa ma kandulo iziwapweteka daily mpaka kampen wao azakhare opanda mphamvu Amen🙏
@josephinekatupi6919Ай бұрын
Zoonadi❤
@JoyceChaimaАй бұрын
Ambuye Mulungu odziwa kuweluza.... aweruze ndithu. MZIMU WA CHILIMA usowetse mtendere aliyense amene anatengako gawo pa infa imeneyi😢😢😢
@EllahChikwatuАй бұрын
Amen 😭😭😭😭😭
@josephinekatupi6919Ай бұрын
Amen and Amen🙏
@HappyAnt-uz5je13 күн бұрын
No mtendere mpaka adzafa
@Hellenistic109Ай бұрын
Thank You very much Bishop for the Wise Preaching,I Salute You..😢😢😢
@chinomwephiri1183Ай бұрын
Amen, and powerful SKC, may your soul rest in peace
@GraceZumazumaАй бұрын
Powerful massage father,mwatiyankhulira ndipo chakwera am sure wamva ndipo akudziwa kuti next year zake zada or atatani ndi manganya wakeyo mfiti zokupha zimenezi zikapume
@user-oc9vl9xz8eАй бұрын
Mathembelelo akhale pamutu pa onse amene anakhudzidwa ndi imfa ya a Chilima ndi anthu 9 mwadzi wawo ukhesedwe pamitu pawo omwe anapanga izi Mudzina la Jehovah's...Amen..
@MirriamChakanzaАй бұрын
Powerful message, wakuva wamva. Amen 🙏
@EstherChibwana-lp3gxАй бұрын
Abig message to malawians I salute u bishop
@user-eh1mg3ww6dАй бұрын
Ndipotu zoonadi ambuye kudziwike kuti kuli mulungu pa ifa ya athu amenewa ikhale panutu Pao ndipo china chake chichitike ndithu ❤❤
@HashimNyirendaАй бұрын
Uthengawu nde ndiwankaka ndi uchi
@DavieKennedy-g2pАй бұрын
Nkaka ndi uchi wabwino 😂😂😂
@modestamhango7737Ай бұрын
😂😂😂😂😂
@jjhollyland4918Ай бұрын
We need this everyday. Men of God come out and preach the truth 🙏
@JafaliAkimu-ll1bfАй бұрын
chakwera wazimvera yekha ma umboni apose apo chakwera ndiwe chigawenga ndithu
@user-hq2io8nk7sАй бұрын
Very very powerful , may God continue giving you fearless speeches for Malawians to know the truth of God.
@LuskaMosesАй бұрын
Ambuye yesu akudakitseni Fathar😢😢😢choonadi chimamasura
@Creslevison-vj2slАй бұрын
Aaaa yes bishop watokota chilungamo uyu eshiii i lv the way he cud articulate the whole story fearlessly amidst mr chikangawa eshiii
@SildaKatunduАй бұрын
Uthenga of the year ,2024
@MaryAaron-nn8ecАй бұрын
😂😂😂😂Amen pastor and thank u for reminding us that we don't have a president 😂😂😂😂
@EstherDebweАй бұрын
Iiiih koma abale😂👐
@NeemaMatewereАй бұрын
Powerful gospel,imfa yowawa ngati ya Yesu Christu,ngati yaa Martini Aku Uganda,ngati yaa Postoli Mtima woyera WA Yesu,mutichire chisoni,a Martini Aku Uganda mutipemphelerw Ife,woyera ose akumwamba mutipemphelere ife. Kuyankhula kulalika zomveka .Amen
@gracemkandawire8769Ай бұрын
Achita bwino kulankhula ku tchalichi,,atidyenawo akwiya kuteleku,,koma ali mbuu,,
@user-er7ub4ug7yАй бұрын
God bless you bishop the power of message
@misoMoyoАй бұрын
Munthu wa mlungu wayankhula mosaopa nae ndi okhumudwa ndi IFA ya bambo Biyeni
@Hellenistic109Ай бұрын
Bravo Bishop Bravo tell them..They should know that people are watching..RIP SKC 😭😭😭💔
@DONNEXKhama-bk1gyАй бұрын
Amen. Pastor uthenga wamveka uyu opanda chilema
@user-gd2kl1fx1qАй бұрын
Once catholic always a catholic and our tears for our vp skc will never end until justice prevail
@WisdomPupweeMwalilinoАй бұрын
Our God will do it and make us move forward with grace.
@user-db5wf7pd7iАй бұрын
Uthenga usu ngati Chakwera sanawunve pls mutumizileni awunve. Tony Momadi. Johannesburg, RSA.
@ifristathope1131Ай бұрын
Amen bishop🙏🏿 chatsika blood on his hands. God gonna answer our tears. Osaopa osatopa n osafooka we need better Malawi for all not za sikusinjazi
@stevenfrancism3638Ай бұрын
mzina la Dada nalamwana Nala mzimu utuwa . Amen.
@petroszgambo9949Ай бұрын
Still can't believe our Biyeni is really gone forever 😢
Nenaso kuti chakwela ndi fit wakupha anthu MCP ndi anthu oipa kwambili
@BwanaGDАй бұрын
Chibaluwa chawelengedwa kupita kwa babo chikangawa zivele mtoloooooo kuchikagawakooooo
@user-ck7eb7tb7vАй бұрын
The Catholics are very powerful 🔥🔥🔥🔥
@user-wq8ul6tu5tАй бұрын
Powerful massage
@mussamapira801Ай бұрын
Mwamvatu a chakwera ngakhale mukubisa umboni anthu akutopelani poti chilungamo nchowawa kuyamba kumanga koma mwa Allah mwini chisoni ndichifundo Ali nafe Ameen mwa Allah