Пікірлер
@GeorgeTewesa-v4r
@GeorgeTewesa-v4r 4 сағат бұрын
Mau mau mau chilungamo
@JasonMailos
@JasonMailos 4 сағат бұрын
Atibuleni osanyengelelq
@BlestoneJonas
@BlestoneJonas 6 сағат бұрын
Comrade awa musawadabwe anakhululukidwa mulandu sangapange zanzeru olo
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 8 сағат бұрын
Yes azimenyedwa makapewo....what kind of construction is that?
@Chikwawa
@Chikwawa 9 сағат бұрын
Iweyo ukuwapereka anthu aku Machinga kwa anthu oipa. Alibe chifundo kuti anthu akuvutika njala mpaka kumadya chitedze.
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 9 сағат бұрын
This is True 😢😢
@BillyChisale-cs1zj
@BillyChisale-cs1zj 12 сағат бұрын
Ndi ufura wa alliance (+1) Aitanidwakare pitani inu aMCP
@BillyChisale-cs1zj
@BillyChisale-cs1zj 12 сағат бұрын
Mesa anenakare basika
@ConradccjSokoSoko
@ConradccjSokoSoko 13 сағат бұрын
Chitetse, kapena njalayo mwaiwona pano, DPP anapha ndi BINGU.
@eliasgondwe
@eliasgondwe 13 сағат бұрын
Mwasowatu zochita otsutsa, sikunotu uku kkkk
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo 14 сағат бұрын
Kkkkkkkkkk
@MphatsoLuka-gn3lr
@MphatsoLuka-gn3lr 15 сағат бұрын
Ziko lapasi ukathawa mulungu siziyenda akufuse yona
@MartinKapito
@MartinKapito 17 сағат бұрын
Nice song
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata 19 сағат бұрын
Yaphweka ndrama ya misonkho ya a Malawi pangani m'mene mungathere
@ElatonGwaza-k4h
@ElatonGwaza-k4h Күн бұрын
Koma Malawi akupita kuti kumangozira ngati nyumba
@johnkatapeh7182
@johnkatapeh7182 Күн бұрын
Chikangawa no more
@hamiltonsolomon3756
@hamiltonsolomon3756 Күн бұрын
Kkkkkkkkk
@UseniMailosi
@UseniMailosi Күн бұрын
M 300 000 yapita pamenepo
@GeorgeMboma-e7j
@GeorgeMboma-e7j Күн бұрын
Kkkkkkk😅😅
@Halima-i4x
@Halima-i4x Күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂
@MercymithieMithie
@MercymithieMithie Күн бұрын
Akt akuika tala😂😂😂😂😂😂😂😂😅😅😅😅😅😅
@rashidadan2533
@rashidadan2533 Күн бұрын
Amalawi kupusa mpaka kumazila mseu mukuona
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata 19 сағат бұрын
Ndipo Ife anatilodzayo ayi dzikomo
@AndreaNgulube
@AndreaNgulube Күн бұрын
Kunalembedwa aliyese alindi makweloake nanga aja anapwedwa kumuzuzu sanali athu 20 aja inu adpp
@rasheedjohn6956
@rasheedjohn6956 Күн бұрын
Atupule simunthu olakwa iyayi. amatiuza amalawi koma kumsava
@Joel-o3k
@Joel-o3k Күн бұрын
Kulibe boma kumalawi ndi za drummer bs zikupanga atsogoleri . Kugula oyimba ndi anthu a maudindo otchuka mu zipani zina bac Chakwera alibe umuntthu wa umunthu satanic yamulowa kwambiri
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Күн бұрын
Bola pamenepo kmabe takhumudwa.nane
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune Күн бұрын
Achita bwino nawoso tidzaatsiya osatengako nduna ku UDF kkkkkkk
@RiteRoderick
@RiteRoderick Күн бұрын
Apapa Chikangawa yaonano kuti kunoko palibeyi akuifuna ataah 😂😂😂
@RiteRoderick
@RiteRoderick Күн бұрын
Apapa kulephera kwa MCP NDI Chakwera kwaonekera kudziko😂😂😂😂😂
@Amirkhan-nn6pz
@Amirkhan-nn6pz Күн бұрын
No one is good in this world 🌎
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Күн бұрын
Beautiful song
@MussahDaud-w8o
@MussahDaud-w8o Күн бұрын
Mayi wadyera ameneyo wapanga bwino kutula udindo mbuzi
@hourlyview4226
@hourlyview4226 Күн бұрын
Kodi inu mumati conversation😅
@MariamJaffali
@MariamJaffali Күн бұрын
Apa ndiye bolano 🔥🔥🔥🔥🔥💪💪💪💪💪💪💪
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy Күн бұрын
God song
@Imrandaniel683
@Imrandaniel683 Күн бұрын
Ndipo bola akanafa atupele osati skc😢😢
@MrMagombo
@MrMagombo Күн бұрын
Bwana Atu. Bwino mukapitiliza kusemphana ndi ma sapota muchitha chipani. Anthu akwanu akudya chitedze inu mukupita kwa A Congress kkkkkkkk Ndale yosamveka bwana.
@RaphealKwelani
@RaphealKwelani Күн бұрын
Ase mumakwana uli bho
@ArnoldKhandeya
@ArnoldKhandeya Күн бұрын
a udf mukula mopusa , masewera mumachitawotu chipanicho chidzatheratu
@sabinaphili
@sabinaphili Күн бұрын
antanyiwa mwadzuka bwanji mwasowatu Pauline pamakoma chifukwa cha inu
@rashidadan2533
@rashidadan2533 Күн бұрын
Muitane zipani zinazo kupatula mcp , chipani chamagazi , chokupha komanso chokuba
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Күн бұрын
Aisha mambo panyini pamakenso hule ya Ku mangochi
@IgnatiousFote
@IgnatiousFote Күн бұрын
chakwela azafa imfa yowawa kwmbr
@MosesDzonzi-em5px
@MosesDzonzi-em5px Күн бұрын
UDF ndi Chipani cha kubanja zolamulira dziko la Malawi yiwalani komaso MCP 50% plus 1 idzatheka payokha MCP kuyipeza
@NICODEMUSMWAMBULA
@NICODEMUSMWAMBULA Күн бұрын
Apapokha mwaikwapula wakuva wanva😅😅
@AboudujanahMawulidi
@AboudujanahMawulidi Күн бұрын
Amambo moti sakudziwa kuti MCP ikuwapangila nkhaza amalawi??? Iyeyo alikutiko e cluding Aslam akugaza, coz chakwela akulimbikitsa nkhondo ku Gaza kuti isathe ndiye oteloyo akabwele ku msongano wa udf?? amambo mukuphenga kwambiri
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani Күн бұрын
@@AboudujanahMawulidi za ku Gazaz siyani nkhani zafika poipa dzulo atiphera wamkulunso wina America Mulungu sadzaikhulukira or
@AdamPetro-v2q
@AdamPetro-v2q 2 күн бұрын
Nanga umakula mtima bwanji???
@Fatima-f5c
@Fatima-f5c 2 күн бұрын
Ayisha patumbo pakoo wava maliseche osathunawo😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@JaneBanda-ht4ve
@JaneBanda-ht4ve 2 күн бұрын
UDF Kodi mutakhala osatchula MCP simungamve bwino? Kodi a MCP anakupemphani kuti abwere ku convention yanu? Kodi simudziwa kuti MCP inapangisa convention yawo ndipo sinaitane chipani china chilichonse? Ndale izi nde ziti❓❔ Mukufuna chani kwenikweni ❓❓
@RiteRoderick
@RiteRoderick Күн бұрын
Chifukwa ndi chipani chokupha cha afiti chowadyesa anthu chiteze chomwenso chikudzuza anthu kuno Ku Malawi in short MCP ndi anyani okhaokha
@JasonMailos
@JasonMailos Күн бұрын
UDF mukuti mukumyendela maganizo atiwo kwenikwani kapena nose kumeneko ndi azimai please musakhale anthu ochititsa manyadzi
@JusticeNyirenda
@JusticeNyirenda Күн бұрын
Ndipo live 😅 😅 ​@@RiteRoderick
@JaneBanda-ht4ve
@JaneBanda-ht4ve Күн бұрын
@@RiteRoderick mmmmh achimwene, musataye Mulungu wanu chifukwa cha ndale chonde
@RhodrickSapala
@RhodrickSapala 2 күн бұрын
Kodi waimba ndindani? Koma mau akufanana ndi anjiru fumulani