chifukwa chomwe anthu amamudera Dan Lu

  Рет қаралды 60,807

Sam Malvitha

Sam Malvitha

Күн бұрын

Пікірлер: 225
@sammalvitha
@sammalvitha 2 ай бұрын
Dan lu, amadedwa kwambili ndi anthu amene sankafuna kut DPP ikhale pa mpando ... Popedza kut ambili amene sankafuna DPP anali anyamata ... Dan lu pokhala mnyamata anadana ndi anthu ambuli maka achinyama .... Dan lu ndioimba wabwino amene sankayenera kusikidwa ... . Zikanakhala kut dan lu ... Ankasapota UTM bwenz zisanachite affect music career yake ... Sindikut career ya Dan inaonongedwa ndi DPP ai koma kut panali kusiyana ndithu ... .. I come in peace
@tariroJinya
@tariroJinya 2 ай бұрын
Palibe amene amamuda Dan lu
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 ай бұрын
answer Dan lufan amaimbila chipani choti anthu ambili kuchokwela pasi pa mitima yawo chipanicho amadadanacho mmodzi mwaiwo ndi ineyo basi khani yamala
@AeeshurQuenjie
@AeeshurQuenjie Ай бұрын
Dan lu u r still my fav artist osadandaula kut ukudedwa ndi anthu worry when God abandon you coz I biliv God loves you more
@eusterkalungu
@eusterkalungu Ай бұрын
I like you Dan since I was 5 years yuh are my best musician
@hannahsitimandau9107
@hannahsitimandau9107 2 ай бұрын
Amamuchitira nsanje nyimbo zake ndi zobeba
@FloridaOssy19
@FloridaOssy19 2 ай бұрын
Zoonadi ❤❤
@ShamimuWilliame
@ShamimuWilliame Ай бұрын
My vote brother Dan lu Amamuda shifukwa shachilungamo amayimba saumboni dzoka dzoka love you Dan lu God bless you 🙏 amen
@emmanuelkennedy6389
@emmanuelkennedy6389 Ай бұрын
Khani nayi amakonda kuyimba nyimbo zoraura atasiya kuyimba nyimbo zaraurazi kubwerera chuni chake chakare zose zitha kubwerera chumake umatha kuyimba iweyo ndiwe number one osagonja ili ndi luso lomwe anakupasa mulungu pitiliza
@MtolaMbalaso
@MtolaMbalaso 2 ай бұрын
Amadele,chifukwa chakuti,Dan luu, amata, OK tangowona nyimbo dzimene anathulusa dzachipanidzo winandan angamakwe, palibe kumalawi kuno km Dan,yemwewo
@MussaMbota
@MussaMbota 2 ай бұрын
Man dan luu ndimwana wabwino kwambili amadana nayeyo angokhala ansanje
@EuniseMasuku
@EuniseMasuku 2 ай бұрын
Dan lu tandiponyeleko kanyimbo ka sanje ndiye mandigwilane imandimvesa🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@MaupoMhango
@MaupoMhango 2 ай бұрын
Koma enafe Dan lu sitikumuda ayi. Komaso nyimbo zake zimatisangalasa koopya akamati kuyamba nyimbo zake nkumati Malawian music Dan lu❤❤❤❤❤❤
@FloridaOssy19
@FloridaOssy19 2 ай бұрын
Ine ndimamukonda Dan lu ndip ndazamukondabe mpaka kale ❤❤❤
@BunayaSalanje
@BunayaSalanje 2 ай бұрын
ine ndimakhonda kwambili ❤kupoza winaaliyese oyimba ku malawi ko 🇲🇼 achalume wachiyao wangalusa brother
@AdeelMusaah
@AdeelMusaah Ай бұрын
I love u Dan no matter how people hate u I will be there for u 😥😥
@DeodataKachapira
@DeodataKachapira Ай бұрын
Mnyamatuyu amaimba bwino asavutike ndi anthu all days are not Sundays. Komanso akati mpikisano ndi umenewo. Ajetuwo alibe nthawi, go ahead vuto achinyamata ambiri ngakhale aziimba zoimbidwazo samamva
@DoresChisale
@DoresChisale 2 ай бұрын
Ine nde ndmakonda mpaka Pano ndpo nyimbo zake ndmazikondaso Maka Maka ija ya Tulani pasi udindo ija eeee anapha 😊😊
@MaryBanda-n3h
@MaryBanda-n3h 2 ай бұрын
Ine Maka ija yoti winaso ai eee ndimaikonda
@blessingkamanga1781
@blessingkamanga1781 2 ай бұрын
I don't know that people hate Dan Lu myself I love him.
@ishmaelbrighton9885
@ishmaelbrighton9885 2 ай бұрын
Mumamuda ndiinu asamu mungatiwuze kuti amadedwa bwanji chifukwa ife sitimava athu akukamba zomunyoza mwangosowa zokamba akulu
@ApsChap
@ApsChap 2 ай бұрын
Sam Malvitha has a problem with Dan Lu
@MaryBanda-n3h
@MaryBanda-n3h 2 ай бұрын
Ndipo ine kuyamba Kumva zoti Dan amadedwa mmmm
@GraciousBayard
@GraciousBayard 2 ай бұрын
Kaoneni KZbin views ya nyimbo zake mupeza kuti Sam akukamba zoona muziitsata music paliponse not m'ma benning centre koma pa social media
@rainJCMw
@rainJCMw 2 ай бұрын
Umangomuda ndiwe ine simamuona vuto ayi
@ChristopherKawilam
@ChristopherKawilam 2 ай бұрын
Ndat boza Ada Sam uyu Ali ndi sanje kwambilil
@AgnesMwale
@AgnesMwale 2 ай бұрын
Mungoti chili chose chili ndi season... Nanga rashly wakhala zii apa???
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 ай бұрын
Dan luuuu amamuda chifukwa ndi munthu ozindkira kunena zoona dpp ndi boma labwno alibe zambiri ngat mcp chipan chamagazi manja nde Dan luuu ndi nyamata oganiza bho❤
@sharifujoe7633
@sharifujoe7633 2 ай бұрын
All most amakhala oyimba amnzizawo ife kwatu kuyamikira any one amapanga bwino pa music industry
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 2 ай бұрын
Dan Lu amaswa koopsa athu amachita .naye nsanje ali ngt mfumu payekha ... nyimbo zake Za chipan anaswa
@YoungScott-p7e
@YoungScott-p7e 2 ай бұрын
How about malemu Lucius Banda poti nayeso wakhala akuimba nyimbo zandale
@HypeGallery-ur9xd
@HypeGallery-ur9xd 2 ай бұрын
Umamuda ndi inuyo ife timamukonda😊❤
@ApsChap
@ApsChap 2 ай бұрын
Sam Malvitha tikusika akapitiriza kuda Dan Lu
@GraciousBayard
@GraciousBayard 2 ай бұрын
Umboni ndi KZbin views ya nyimbo zake
@GraciousBayard
@GraciousBayard 2 ай бұрын
​@@ApsChapSam mavitha akukamba chilungamo ngati simusata music ndi bwino kukhala chete
@BonomaliIman
@BonomaliIman 2 ай бұрын
Ngati dziko la malawi emwe anayimba nyimbo zabwi nzachipani ndi Dan lu bs nde tingamudele nji ife ma citizens iwe umamuda siife ayi
@KelvinChitwanga
@KelvinChitwanga 2 ай бұрын
Umamuda ndiweyo nde ukanati ndichifukwa chan munthu amamuda dan lu osat anthu! Wamva iwe
@JacksonNamalumbe
@JacksonNamalumbe 2 ай бұрын
Alipo wakutuma kuti uziyakhula zopusazi ? Ife ukuziwa mene timakondela Dan Lu ( lozani zanu ife tiwone)❤
@SandikondaIsaac
@SandikondaIsaac 2 ай бұрын
Ilove danlufani and his music
@JusticeFriday-q1j
@JusticeFriday-q1j 2 ай бұрын
Muthu sakondedwaandi athu ose kom kwaenafe tiribe naye murandu amatisangarasq kuno
@MoosaSame
@MoosaSame 2 ай бұрын
Ur first person to say that bro no one hates Dan lu
@LailoguntherElick
@LailoguntherElick Ай бұрын
Amamuda kaya chifukwachan nanensosinziwa koma Dan lu ali fantastic 2 mach
@RhodwellLevison
@RhodwellLevison 2 ай бұрын
Kufotokoza kukuvutani akulu mmene mwayambila Diamond Diamond simukutopa? 😂😂
@CuthbertMughogho-u1b
@CuthbertMughogho-u1b 2 ай бұрын
Uja anaimba yoti tiyende pamodzi ndi mtima umodzi timayikonda mpaka lero. Kuna koipa kuimba nyimbo ya Peter panthawi yoti dzithu zikubvuta iye kumanjoya. Iyeyo amasapota Muthu amene amaszunza anthu ndipo anthu amamuda Peter amapanga mademo kusamfuna Peter munthalika.
@GraceMaida
@GraceMaida 2 ай бұрын
Done ndimfana oti amatha ndiye timuda bwanji iweyo ndiye usamamuwonela kukondwa koma Done ndimbambande moooo fire Done we love you so much ❤❤❤❤❤❤
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo 2 ай бұрын
Ndimfana wabho ndilibe naye bvuto
@CASSIMDinala-z7e
@CASSIMDinala-z7e 2 ай бұрын
Amatha nfanayu broskie
@shukurajaaffarie-cr2nm
@shukurajaaffarie-cr2nm 2 ай бұрын
Umamuda ndi iweyo osati ifeyo iwe sudziwa kut Dan ndi mu yao ? Ndie sundiwaso kut mchewa ndiwa sankho?
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune 2 ай бұрын
Woyamba kusankha ndiyeyo. Bwanji anzake onse tsakudadwa. Apo nkatsa sangadedwe chifukwa sakusankha mbari mwaonatso nokha
@StevenLikukuta
@StevenLikukuta Ай бұрын
Dan Lu anakwera chipani cha anthu oipa osayamika komanso ozikonda. Vuto ndi limeneri. Muziwe kuti DPP inayamba bwanji nanga zonse zomwe zinachitika kwa anthu omwe anaononga chuma chawo nthawi yawo kuti bingu akhale pammpando zinawawa bwanji nanga abwenzi awo. Ndiye wina akaimbire nyimbo anthu awa avina? Amavina ndi kusekerera ndi omwewo a DPP chosatila chake Dan Lu ali mmazi. Olo nyimbo zake kukubwera kuno anthu adzasiya kumvera azamvere ndi okhawo akuwatamandawo
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 2 ай бұрын
Ineyo ndimamukonda dan lu ❤❤❤ APM uja osazamuphwekesa
@Ghama-k4i
@Ghama-k4i 2 ай бұрын
I don't know if there are people who hate dan lu coz us we love him
@IshumeilHaroon
@IshumeilHaroon 2 ай бұрын
Dan lu is the best
@RICHARDMAGWIRA
@RICHARDMAGWIRA Ай бұрын
Iwe nawe Muthu sakondedwa ndi onse osangonena kt umamuda iwe bwanji
@PreviousStanley
@PreviousStanley 2 ай бұрын
Guys Moyo ndichoncho munthu amankhala ndi anthu omukonda komaso odana naye sizingantheke kukondedwa ndi anthu onse olo utankhala wabwino
@IssaLazack-ij1gf
@IssaLazack-ij1gf 2 ай бұрын
Amaphangila jerazi amayimba momveka bwino Dani yoo❤❤❤
@SayiBotoman
@SayiBotoman 2 ай бұрын
Ada awawa amakamba chilungamo komnso kuima pa chilungamo so pajatu amalawi amadana ndichilungamo amakonda boza bas
@HappyBotha
@HappyBotha 2 ай бұрын
Dan luu ndimunyamata oyimba bwino,,,that's y amamuda
@hanffyamizy2706
@hanffyamizy2706 2 ай бұрын
Unayamba wapitako ku sho yake ngat
@GraciousBayard
@GraciousBayard 2 ай бұрын
Umboni ndi KZbin views ya nyimbo zake
@Hassanianusa-go9wv
@Hassanianusa-go9wv 2 ай бұрын
Aaaa iwe choka kape iwe
@falliotphiri688
@falliotphiri688 2 ай бұрын
Dan Lufani Ali ndi Magazi a Blue, ndipo palibe oyimba amene Ali wa DPP. Kuposa Dan. Choncho amene amadana naye ndi adaninso a DPP
@Chiwaya-v6h
@Chiwaya-v6h 2 ай бұрын
lne ndimakonda Dan lu ndip ndazamukondabe mpaka khale😊😊😊
@AliNtolera
@AliNtolera 2 ай бұрын
Malawi amadana ndichilungamo komanso jealous chifukwa Dan lu amatha komanso ndiokongola samaoneka ngati mbuli za kumalawi
@DavieLosani
@DavieLosani 2 ай бұрын
It's my first time kunva kuti Dan Lu amadedwa
@andrewchirwa2193
@andrewchirwa2193 2 ай бұрын
Dan Lu ndiwoyimba wakulu so sakuyenela kuyamika andale aziyimba nyimbo zake woyimba akwathu ndale zikuwabwezelesambuyo🤷
@SmilingBurger-qm4oh
@SmilingBurger-qm4oh 2 ай бұрын
Dan lu amasapota andale amene anyamata akudana nao koma chosecho iye amayimba nyimbo zachinyamata mwachitsazo ulamulilovwa DPP umadana ndiachinyata ambiri koma iye akhayimba zochemelera chipanicho ndichifukwa ambiri adangomutulaka
@SamsonNyoma
@SamsonNyoma 2 ай бұрын
Amamuda coz ol yandareyo Imakhala hit
@YusufDyton
@YusufDyton 2 ай бұрын
Ngani ndiyakuti dan lu amawada anthu chifukwa choti ndi muyawoo ukaunika ku malawi ndi zikho losalana mituthu kuli monga D20, Dan lu,Bandera,ndi ayaoo ena km zakhondedwa ndi anthu akumalawi ayi
@DavieLosani
@DavieLosani 2 ай бұрын
Iweyo udzinvela kwambili nyimbo ya Dan ,msanje.
@stevietungama9775
@stevietungama9775 2 ай бұрын
Amamudela Zina ameneyo bwanji nkasa samadedwa
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 Ай бұрын
Oimba ena sadedwa ndi anthu chifukwa alibe mbali ya chipan pomwe Dan lu akuwonesela kuti ndiwa dpp
@tamandanimaliro7519
@tamandanimaliro7519 2 ай бұрын
Umafotokoza zosaveka iwe ungosiya bola bakili tv
@JoevsJohn-fg6wz
@JoevsJohn-fg6wz 2 ай бұрын
Mmwe Ali Tongo sam malvitha mkulimana nazibambotu mwasene gakwiona,mufune Muthu Wina osati Dan Lu mungoyalukapo apa
@InnocentMaganga-gd6kn
@InnocentMaganga-gd6kn 2 ай бұрын
Anthu amamuda chfkw nd oimba amene anaimba za ndale ndkupindula nawo pamene oimba ena onse mwanenewo palibe chomwe anapindula kuposa Dan lu😢😢😂😂
@SamboRuphan
@SamboRuphan 2 ай бұрын
Anyamata anyemba yemba (saymon and Kendall bwanji amayimba ya MCP,,,ndiye kuti mwangoeonapo Dan lu yekha 😂😂😂 zanu izo wakwiya akakolope nyanja😅
@owenmaseya6936
@owenmaseya6936 2 ай бұрын
Ndinu zitsiru kwambiri zifukwazo nde mwanena?
@ChikondiSabe
@ChikondiSabe 2 ай бұрын
Amamuda chifukwa Dan lu ndi number one sangafane nawo, sanje ndiyowe yakula basi
@TheresaKuluwemba
@TheresaKuluwemba 2 ай бұрын
Inetu ndye I love him kwambiri enawo ndizawonso!
@MikeAlabi-w2g
@MikeAlabi-w2g 2 ай бұрын
Iweyo Sam nddi amene umamuda Dan lu osati anthu enawo enafe timamukonda kwambiri ndiye siya uchitsilu wakowo
@muhammadisaid3968
@muhammadisaid3968 2 ай бұрын
Komaso oyimba ambiri monga Billy , Banda bwanji samawaba , ndiye kuti anthuwo ndidzsilu
@MosesPinto
@MosesPinto 2 ай бұрын
Anthu amachita mantha ndi dpp nde kuwawidwa ntima kwake mchifukwa amadana ndi dan lu
@MussaMalon
@MussaMalon 2 ай бұрын
Kwayineyo dan lu ndi super power osamutuluka.
@EmmanuelGasiten-fo5dr
@EmmanuelGasiten-fo5dr 2 ай бұрын
Ukakhala pa top, umakhala topic. Ndiye nkhani yaketu
@IvyMkhura
@IvyMkhura 2 ай бұрын
Amamuda Dan Lu ndiweyo, ife amatiwaza ndi kwambiri, amatha kuimba heavy
@SelemaniFred-rg9tt
@SelemaniFred-rg9tt 2 ай бұрын
Ine ndiye amandiwaza Dan lulu mnyamata wa kwathu kumangochi !!!! Kwa amene amamuda Dani Lulu ndiye kt amamuposa pachilichonse osamalimbana ndi ana osamba monga aku Mangochi ana olimbikira
@SmartMasauli
@SmartMasauli 2 ай бұрын
Ife timafila Dan Lu🔥🔥🔥
@OsmanRatbu
@OsmanRatbu 2 ай бұрын
Yathu ija amalawi munthu zikamamuyendera sitisangarara imakura nd sanje dan lu amatha man ndpo kwambliiiso
@LaynaAdam
@LaynaAdam 2 ай бұрын
Akulu inuyo mukumana amene amamuda ali ndi zifukwa zawo osati chifukwa choti anaimbira dpp nkasa waimbira zipani zingati
@AsimaAndiwochi
@AsimaAndiwochi 2 ай бұрын
Ine ndimamukonda dan ru
@CannyMpehla-d1s
@CannyMpehla-d1s 2 ай бұрын
vuto ndiuphawi kumalawi amamuda coz the man how is handsome komaso kuchimake kwa khutsa
@lacksonmanyewu3615
@lacksonmanyewu3615 2 ай бұрын
Zoti Dan lu anthu amamuda ndi bodza lankunkhunidza
@InnocentChauwa
@InnocentChauwa 2 ай бұрын
Tachoka naye patali Koma zomudazo mukuziwa ndinu kapena anakuuzani yekha
@MillyKachepa
@MillyKachepa 2 ай бұрын
Anthu akamakuda akuona zabwno za iwe kumangoyamika osamazitengera amakhala akukubersa madalitso ako
@JoevsJohn-fg6wz
@JoevsJohn-fg6wz 2 ай бұрын
Athu amaziwa Kut iweyo umamuda Dan Lu ndikuziwa munamufananidza ndi Dala wanu uja jetu iwe ndikaphe
@MatridaChikaphonya
@MatridaChikaphonya 2 ай бұрын
Mtengo womwe ulindidzipatso ndumene umagendedwa don't worry Dan luu
@billymhoni9527
@billymhoni9527 2 ай бұрын
Zimene zikuooneseni kuti ambirife sitikuikonda DPP.
@AlexBanda-p1k
@AlexBanda-p1k 2 ай бұрын
Ine danieli Joe kuno kwangabu Dani lu amafuna mtendele ngati mene adadi Ali wamtendele
@MalitaKapesi
@MalitaKapesi 2 ай бұрын
Nkhani yakula ndinjilu imene imavuta kwa ena mwa amalawi fe
@BenardMuhammad
@BenardMuhammad 2 ай бұрын
Penapaket osamachukira pa munthu osamanamiza anthu apa
@RamusiCassmu-m1x
@RamusiCassmu-m1x 2 ай бұрын
Vuto loti amadana ndi ndalama Dan lu ndindalama zimenezo akunama pitilizani bro
@AquimodinisbilioteBiliote
@AquimodinisbilioteBiliote 2 ай бұрын
Dan lu ndi big,ochita zabwino amachuluka ndi adani even jesu christu ankachita bwino koma yuda adangulisa kwa adani mpaka kuchosa moyo wake.
@KennedyMitochi-nz8fp
@KennedyMitochi-nz8fp 2 ай бұрын
Dan lu amadedwa chifukwa amaima pachilungamo pajatu chilungamo chimawawa Dan lu kumenya kugwesa
@PatrickJemus-x7s
@PatrickJemus-x7s 2 ай бұрын
Anthu amama nd jars chabe ban lu amayimba bho komaso amaziwa kumvara bwino
@dalisoulphiri3094
@dalisoulphiri3094 2 ай бұрын
Mungofuna attention for your KZbin channel akulu,,, kafukufuku munampangayo munampanga kuti? Ndipo munamupanga kwa anthu angati?
@AdamsIssa-p3j
@AdamsIssa-p3j 2 ай бұрын
Vuto ndiloti anali pa payroll ya boma pa chifukwa chongoimba nyimbo za dpp
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata 2 ай бұрын
Omudawo ali ndi zawo zomudera kkk
@DIMZYRECORDS
@DIMZYRECORDS 2 ай бұрын
Amavita boza sanachite kuwawoda achina psquare
@alexsumani6823
@alexsumani6823 2 ай бұрын
Sometimes manners play a role, period
@jackaustin966
@jackaustin966 2 ай бұрын
Mmmmm choka iwe DAN LU amamuda ndani?
@serakillo8668
@serakillo8668 Ай бұрын
Apa waonetsa kusankhazikika manganizo dan chifukwa tamutuluk
@Alexkalonga-t9s
@Alexkalonga-t9s 2 ай бұрын
Iyi wapala mavita
@ApsChap
@ApsChap 2 ай бұрын
Malvitha wadabwisa bwanji kms akuzisusa yekha
@JibuzahDrag
@JibuzahDrag 2 ай бұрын
Aaah mavita panyapako wava..galu iwee
@yotamumahomed1313
@yotamumahomed1313 2 ай бұрын
Chomwe ndimadziwa ndichot moyo was aliyense uli mmaja mwa mulungu bas that's all
Chakwera Wakhazikisa Kafukufuku Wina ... Anthu Adabwa
8:59
Sam Malvitha
Рет қаралды 1,5 М.
didn't manage to catch the ball #tiktok
00:19
Анастасия Тарасова
Рет қаралды 35 МЛН
Seja Gentil com os Pequenos Animais 😿
00:20
Los Wagners
Рет қаралды 60 МЛН
This dad wins Halloween! 🎃💀
01:00
Justin Flom
Рет қаралды 27 МЛН
Kutha Kwa Rashley.. Kunali Kochita Kukonzedwa.. Pedzan Chifukwa Chake
11:28
CRUISE 5 WITH JETU
34:03
Zodiak Malawi
Рет қаралды 367 М.
JUDICIARY OPEN DAY 2024 LIVE CHE MANDOTA PERFORMANCE
14:19
CHE MANDOTA COMEDIES
Рет қаралды 82 М.
Zathapo! ... Izi Ndi Zomwe Ankabisa!
4:13
Sam Malvitha
Рет қаралды 12 М.
Achinyamata Akwiya Nae Dan Lu
8:07
Sam Malvitha
Рет қаралды 19 М.
Patricia Kaliati wamangidwa pa mlandu wa treason
9:15
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 89 М.
didn't manage to catch the ball #tiktok
00:19
Анастасия Тарасова
Рет қаралды 35 МЛН