Chilima vs The Rest - Samuel Lwara

  Рет қаралды 6,119

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

Ай бұрын

Today on Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara continues campaigning for the Vice President Saulos Klaus Chilima, whilst evaluating the leaders of other political parties on suitability for the Malawian Presidency.
Lero pa Nyasa VoiceBox, Samuel Lwara akupitiliza kuchita kampeni ya wachiwiri kwa Purezidenti Saulos Klaus Chilima, pomwe akuwunika atsogoleri azipani zina zandale kuti akuyenera kukhala Purezidenti wa Malawi.
#malawi

Пікірлер: 47
@fractionkadzuwa2116
@fractionkadzuwa2116 Ай бұрын
It's true that this man Lwara show his side, chifukwa akupanga campaign wa vice president to be president, anganene bwanji zabwino za, zipani zina, komana i remembered very well kuti a vice president anali minister of economic and planing for a year anasintha chani? Komanso inu a UTM mudziwe kuti you don't have Stactures on the ground, plus mmene a vice president wo apangira perform mmmm zizavutabe anthu anakhumudwa naye amendyo
@HurryBeston
@HurryBeston Ай бұрын
That's good analysis only kuti anthufe kumvessesa zinthu kumativuta, go Mr Lwara go its up to us to take it or leave it
@allanngumuya-ql2cw
@allanngumuya-ql2cw Ай бұрын
This Lwara man is just honest, he just hit the nail on the head, only those who don’t have the truth in their mind can hate him. He has analize each party and its leader in a very clear and sober way. That’s the way to go man. I love it. This is. Your best Audio ever. Thank you and God bless Malawi.
@FrankSubili-fv2sf
@FrankSubili-fv2sf Ай бұрын
This man is good at analysing politicians
@user-zf7lh1py7u
@user-zf7lh1py7u Ай бұрын
Mr Lwara is probably right. Chilima could be the best candidate for 2025. He has my vote. I have always supported his agenda and manifesto. But Chilima needs to clear his name in the courts. In addition there is a constitutional issue regarding his eligibility which needs to be clarified. If he is eligible to stand I would encourage him to collaborate and forge a formidable coalition with other youthful leaders such as Kamuzu Chibambo, Enock Chihana, Atupele Muluzi, Mnnesa etc. They would need to strengthen grassroot structures. Chilima has a formidable campaign strategy as well as a marketable manifesto. And he is charismatic. He knows the art of moving crowds. The Chilima led team needs to approach and strategise their campaign from a three pronged approach: a) Rural masses: these constitute 85% of the population. The campaign should be responsive to the needs of the rural folk. b) Youth: Malawi has a youthful population of about 80%. The campaign must speak to the needs of these youth c) Gender: women constitute about 52% of the population. Need to attract the women vote. Probably need to pick a woman running mate to make the ticket more attractive. Free advice to the Mr Lwara and team
@LeviChakwira
@LeviChakwira Ай бұрын
Keep it up brother , we love the vice president
@AmosBandula-up4yb
@AmosBandula-up4yb Ай бұрын
That's true skc ndikatundu koma amalawi ena sakuziwa
@NathanielNthala
@NathanielNthala Ай бұрын
Very good analysis.
@JorgeSacuate
@JorgeSacuate Ай бұрын
Amalawi Simuchedwa kuyiwala. uyutso akudya bazi lero lá Chilima. Akufuna kusokoneza athu mitu. Chilima siuja akati tizidya katatu. Chilima siuja ananyamula thumba la chimanga pa phewa. Nanga galu akuwayi akufunabe ife tizikhala ku bangamoyo? Choka NDI bazi lakolo kagwere uko iwe chakwera Chilima. Ife tavota kale ana a DAD
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Ай бұрын
Ase ife chilima chakwela achoke, atione za udf atupe
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y Ай бұрын
Good Message
@user-qp8kh2hj9o
@user-qp8kh2hj9o Ай бұрын
Ine mmene ndikuonera Mr Rwara wayankhulazo bwino koma kuti munthu ndi munthu palibe chomwe akunamiza anthu tiyeni tiphunzire kumva ko zinthu zoyankhula munthu wina chifukwa anthu anjiru ngati inu omwe chilichonse mukuti ndi cha bodza hmm Malawi azakhala chonchi mpaka kalekale komanso mmene ndikudziwira mau abwino ndi on ena kuti aliyense ali ndi zoofoka zake nkhani iyi ndiyona atsogoleri onse a Malawi ino palibe yemwe mungandiuze kuti ndi wabwino in fact wabwino ndi Mulungu nde mukufuna kuti munthu aziyankhula kuti chani zomwe mungayankhepo mwa ulemu??? Olo ngati akunamiza anthu know that amene mukufunayo si onse omwe akufumufuna aliyense ali ndi zokonda zake sitingakhale ndi zokonda ofanana never tiyeni tiphunzire kulemekeza anthu ena zikomo
@user-zf7lh1py7u
@user-zf7lh1py7u Ай бұрын
UTM has to establish and strengthen structures on the ground. And they should start campaign in earnest. Time is not on their side. UTM should also begin to work on strategic alliance.
@user-rd4ft9nd8t
@user-rd4ft9nd8t Ай бұрын
Amwene tiyeni tipemphere mulungu atipase tsogoleri
@user-vm7iz6oz6r
@user-vm7iz6oz6r Ай бұрын
Musazuziike zoyakhura za mcp pan ife tinawatuluka and athuwa coz sitidya boza ife koma zintchito zathu
@temwamfunejere
@temwamfunejere Ай бұрын
SKC Vote
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 Ай бұрын
Apm❤
@macmsiska2937
@macmsiska2937 Ай бұрын
Exactly especially afford mmmmmmm
@isaaczuze
@isaaczuze Ай бұрын
Mr lwara mwayankhula chilungamo kwambili
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi Ай бұрын
Luwalayo ndiwopenga
@franciscoduartie5762
@franciscoduartie5762 Ай бұрын
I personally love Enock chihana apart from Chilima ,Chihana has fact.
@Rananet360
@Rananet360 Ай бұрын
very true
@jamesgama5489
@jamesgama5489 Ай бұрын
Analysis yabwino kwambiri koma musamayiwale chimodzi ndale zaku malawi zimayendera zigawo. Let me give an example pa central region mchewa simungamusunthe za mcp. Lomwe DPP, yao UDF, tumbuka AFORD, ngoni for UTM
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem Ай бұрын
Zopusa zmenezo ngat mukudya baz zikapwisan uko ndichilima wanuyo
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete Ай бұрын
Unenekuti amatha kunama chilimayo
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Ай бұрын
Ngati achilima anatinamiza kuti tidzidya katatu. Nde lero tikudya katatu ko? Bvuto amalawi fe timayiwala
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Ай бұрын
Zoonadi zake
@frankbanda7333
@frankbanda7333 Ай бұрын
Aaaa poyamba unayankhula za nzeru koma mu vn iyi wapala iyi ndi mbuzi ya munthu chilima mbava yeniyeni
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Ай бұрын
Olo dpp bola
@frankbanda7333
@frankbanda7333 Ай бұрын
Iyi nayo ndi mbuzi jkkkk
@MaryTchapo-py4hh
@MaryTchapo-py4hh Ай бұрын
Onseo ndiolephera chilima ndi chakwerayo
@MaryTchapo-py4hh
@MaryTchapo-py4hh Ай бұрын
Chilima ndi amene wasaukitsa dziko. Ndihule pa ndale
@richardManemba
@richardManemba Ай бұрын
Iwe kod wakita chani atupe atupe nde KUT chan chamba eti
@user-ti2ct8ts8d
@user-ti2ct8ts8d Ай бұрын
Vuto malamulo sakulola aise,chilima 2terms yakwana basi no more .alibe nthito chilima
@user-uw3sp6rq8m
@user-uw3sp6rq8m Ай бұрын
Iwe ndioipa ndi chilima wakoyo amalawi isadora kuvoteraso chilima ichi ndi chitsilu chikulankhulachi Chilima ayi
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 Ай бұрын
Eeeeee koma amalawi katangale uja asiya chilimayu kod ndiye atiuze kaye kt sadzabasotu
@LovelyBlini-cu3iu
@LovelyBlini-cu3iu Ай бұрын
Tifele maboza eti
@MaryTchapo-py4hh
@MaryTchapo-py4hh Ай бұрын
Sitikufuna munthu iziwa kuyakhula kma oyendetsa bwino dziko. Iwenso sukutha kuyankhula
@jamesgama5489
@jamesgama5489 Ай бұрын
Chilima too much utambwali tamuyesa kale 10 years is enough akapume. Chilima alibenso stronghold
@greychizaka4088
@greychizaka4088 Ай бұрын
Vote SKC
@edwinchimbuto
@edwinchimbuto Ай бұрын
Zopusa izi.. chilima wakhalla vice kangati. Ndale zopusazo ayi mitisaukisa..ife tifele kuyankhula
@EvancesimonAdam
@EvancesimonAdam Ай бұрын
That is your views musanamidzepo anthu apa
@phirimacdonald8638
@phirimacdonald8638 Ай бұрын
Nthawi ino siyomva za chilima aise nthawi yake inatha analembedwa nganyu ndi chakwela kumanyamula fertilizer pa phewa kut asika,Kodi mwasowa chochita pa radio yi mulibe maprogram oti muchite othaniza ziko koma kuyikapo mbuzi yamunthuyi?
@EagerChicken-qj6xu
@EagerChicken-qj6xu Ай бұрын
Zoona inenso vote yanga ndi chilima yemweyo.
@user-nu8oo6oc4j
@user-nu8oo6oc4j Ай бұрын
Kagwere uko iwe ndichilima wakoyo
Ma Passport Akuchita Kuyanika Pa Dzuwa Kuti Ituluke  - Bon Kalindo
14:41
The Confession of Charles Ben Longwe (Part 1)
33:13
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 2,4 М.
КАК СПРЯТАТЬ КОНФЕТЫ
00:59
123 GO! Shorts Russian
Рет қаралды 2,7 МЛН
Did you find it?! 🤔✨✍️ #funnyart
00:11
Artistomg
Рет қаралды 120 МЛН
Como ela fez isso? 😲
00:12
Los Wagners
Рет қаралды 25 МЛН
A Malawi Lyton Mangochi Musamukhulupilileso - Bon Kalindo
19:43
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 12 М.
Skeffa Chimoto Apresident new Audio Official
8:35
Yathu Music Official
Рет қаралды 99 М.
Confessions of Charles Ben Longwe (Part 2)
33:07
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 773
یک نگاه - گفت‌وگو با عباس میلانی
29:46
Mtsogoleri Oyenela Ndi Chilima Basi - Samuel Lwara
21:57
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 13 М.
APM Sanaluze Zisankho Mu 2019 Ndi Mu 2020 - Innocent Mutholo
22:47
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 10 М.
КАК СПРЯТАТЬ КОНФЕТЫ
00:59
123 GO! Shorts Russian
Рет қаралды 2,7 МЛН