CHIPANI CHA UTM CHALIMBA MTIMA.ZILI KU MASINTHA GROUND.

  Рет қаралды 41,161

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 80
@JosephHill-fy1bb
@JosephHill-fy1bb 3 ай бұрын
Mama Kaliat,, Dr chilima aja munkawakondadi kuchoka pansi pamtima.... The movement is massive now.. 🔥🔥🔥
@CrescentShaba
@CrescentShaba 3 ай бұрын
Akweni mwaonesa kuti ndinu mwamuna wamasomphenyadi. Ndinkakukaikirani koma pano mwandigwira mtima , you are strong lady.
@OpheenMbukwa
@OpheenMbukwa 3 ай бұрын
SKC spirit is in us forever more
@lastonmasoatenganji-bs5gf
@lastonmasoatenganji-bs5gf 3 ай бұрын
I can feel the presence of SKC spirit all over and every where.
@JemesMalawa
@JemesMalawa 3 ай бұрын
Plz my god protect all peoples they need to keep better our 🇲🇼 🇲🇼 🇲🇼 🇲🇼 🇲🇼
@LuskaMoses
@LuskaMoses 3 ай бұрын
God is good 🙏
@MoHaTri-g5u
@MoHaTri-g5u 3 ай бұрын
A UTM osamusiya DENNIS MAHATA mfana uja akhoza kusintha ndale. Viva UTM.
@MacadamsNdhlovu
@MacadamsNdhlovu 3 ай бұрын
Achinyamata siolimbana nawo ....UTM 2025 yadutsa basi..... tiyeni tisafooke ndale zisintha mmalawi muno. UTM motooooooo!!!!!!
@EDGARMPIKAMEZO
@EDGARMPIKAMEZO 3 ай бұрын
Long live SKC ! Long Live UTM 🔥🔥🔥🔥
@ThomasKaundama
@ThomasKaundama 3 ай бұрын
Mulungu kumwambako timenyereni nkhondo patokha sitingathe
@MarvinPeason
@MarvinPeason 3 ай бұрын
#thevoicethough......pangolin owez remembered💯
@MwawiMinga
@MwawiMinga 3 ай бұрын
Well done utm God bless utm
@ernestphiri5507
@ernestphiri5507 3 ай бұрын
UTM is more powerful now may you keep this spirit to 2025 wooo
@RaphaelKweve
@RaphaelKweve 3 ай бұрын
Masintha yayaka moto this is UTM that I know,,, Osaopa,, Osafiooka❤
@ChrisBanda-f5d
@ChrisBanda-f5d 2 ай бұрын
Tiyeni tisafooke kaya atifinya atifinye
@JosephEmmanuel-nv5td
@JosephEmmanuel-nv5td 3 ай бұрын
Look sharp 🎉🎉🎉🎉🎉
@peterkapalamula
@peterkapalamula 3 ай бұрын
More fireeee..utm moto kuti buuuuuu
@HeriqueJulias
@HeriqueJulias 2 ай бұрын
Osaopa
@emanuelbanda9448
@emanuelbanda9448 3 ай бұрын
I like it
@martingams5613
@martingams5613 3 ай бұрын
The vision must continue 🔥🔥🔥🔥🔥
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 3 ай бұрын
Utm kupanga zomwe SKC analephera kuchita....this is beautiful
@owenmulemba5347
@owenmulemba5347 3 ай бұрын
Plz don't insult the spirit of the son of the soil skc plz plz
@ChifundoChiwanda-ru3pg
@ChifundoChiwanda-ru3pg 3 ай бұрын
SKC is an idea,SKC ndi ineyo, SKC ndi inuyo! Osaopa💪osatopa💪osafooka!!!!!!!!!!!!!!
@DanielMjasten
@DanielMjasten 2 ай бұрын
Tili limodzi ndi skc
@douglaskayira8362
@douglaskayira8362 3 ай бұрын
Pangolin Patricia kaliat
@GladMarawaMsowoya
@GladMarawaMsowoya 3 ай бұрын
Well done utm mwachita bwino kwambiri ndakunyadilani 🔥🔥
@henryphiri6100
@henryphiri6100 3 ай бұрын
Kaliati,Kamtukule,ndi Calista munamukonda ndi mtima wonse.Kaliati special woman.
@PhillipSemu-z9h
@PhillipSemu-z9h 3 ай бұрын
UTM Sizocheza 2025 moto kuti buuu munya.
@SafariBvumbwe
@SafariBvumbwe 3 ай бұрын
Chilima kumene uliko wona ana ako awa pena zilingati unachita kuwanthawa ndinthu
@AminAbbasi-xc4qk
@AminAbbasi-xc4qk 3 ай бұрын
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉✊✊✊✊
@GoldenHuzaifa
@GoldenHuzaifa 3 ай бұрын
Long life skc afana oganiza bho
@giftmasenti5732
@giftmasenti5732 3 ай бұрын
Ku UTM kuli anthu anzeru 💪
@mabvutophiri6650
@mabvutophiri6650 3 ай бұрын
Mulungu akusogoleleni muzawina 2025
@WilsonChinzenga
@WilsonChinzenga 3 ай бұрын
🔥🔥🔥
@raphaelbanda875
@raphaelbanda875 3 ай бұрын
Pls utm musatsogoze dyera ..let's join hands and fight we have sympathy vote....
@MarvinPeason
@MarvinPeason 3 ай бұрын
I support it
@JamesKadango-qs3ej
@JamesKadango-qs3ej 3 ай бұрын
Respect fax for SKC
@ElizahMadi
@ElizahMadi 3 ай бұрын
Malawi wakoma ,uyu akhale m Busa ,akulongola bwino
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 3 ай бұрын
Ng'ona zajiwah.., no chance
@lukemapepa9530
@lukemapepa9530 3 ай бұрын
Fearless party
@PatrickMailos
@PatrickMailos 3 ай бұрын
Koma chakwera MMM iwe ulape ndithu mokwa ni😢😢😢
@EmercianahKasiku-en6hl
@EmercianahKasiku-en6hl 3 ай бұрын
Chikwati chatha ndi Manganya asatipusitse
@emanuelbanda9448
@emanuelbanda9448 3 ай бұрын
AMBUYE AKUSOGOLELENI
@BrianZenengeya
@BrianZenengeya 3 ай бұрын
2025 boma
@EmercianahKasiku-en6hl
@EmercianahKasiku-en6hl 3 ай бұрын
Chipani cha pamolo ponse UTM ndi idea munya muona BOMA timachotsa kupititsa kwina osaopa osafooka more 🔥
@YNOTGEORGE8
@YNOTGEORGE8 3 ай бұрын
Ng'ono zili madzi
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 3 ай бұрын
Pyoooooo
@TasleemahOsman
@TasleemahOsman 3 ай бұрын
Mphamvu zokhazokha za SKC ❤
@IanAllstal
@IanAllstal 3 ай бұрын
Ndizafela mbendela iyiiih 🇲🇼🇲🇼🇲🇼
@Lexkasonkanji
@Lexkasonkanji 3 ай бұрын
😢😢😢😢 ambuye
@AlexManuelMisomali-sv1vn
@AlexManuelMisomali-sv1vn 3 ай бұрын
😂😂😂😂 m'gwilidzano watha ?
@SolomonMbewe
@SolomonMbewe 3 ай бұрын
Welcome to DPP....Tisagone kwambiri coz MCP siikugawa kamba
@PearsonYonah
@PearsonYonah 3 ай бұрын
Mulungu akwezeke UTM MOTO!!!!!!!!!!!!!
@JonesChilonga
@JonesChilonga 3 ай бұрын
Kuvota ndi ufulu wathu sipafunika kuti munthu akhale ndi Cha unzika kuti akavote, please don't take Malawians for granted, don't block people from voting
@GloriaKaduya
@GloriaKaduya 3 ай бұрын
Kwambiri asatitengere ku dodo ngati ndife maliro anjoka ai it's our rights to vote
@josephinemisomali6840
@josephinemisomali6840 3 ай бұрын
SKC it’s idea osaopa osatopa Osafooka
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 3 ай бұрын
Zoona ❤
@MwawiMinga
@MwawiMinga 3 ай бұрын
Madolo mwaganiza bwino kusiya mgwirizano
@JamesChiphazi
@JamesChiphazi 3 ай бұрын
Iwe ndi chakwela wakoyo nose pa
@Mahmoodwargison-op2gm
@Mahmoodwargison-op2gm 3 ай бұрын
Nthawi ya campaigning tiziza panga masana ndiusiku omwe
@peterkinsLekera
@peterkinsLekera 3 ай бұрын
Lilongweyi adachita kutenga malole akwina kapena lilongwe yekha
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 3 ай бұрын
Aaaaaa iwe ulibe ulesi kuzilowera kutenga malore ku mcp ko aaaaaaukuona ngati mizimu imeneyi igona owooooo ikusowesani mtenderetu
@MaxwellSakwata-wb8ep
@MaxwellSakwata-wb8ep 3 ай бұрын
UTM for ever
@MuhaSaibu
@MuhaSaibu 3 ай бұрын
Masitha yayaka moto
@FelistasNkasalaMakumbo
@FelistasNkasalaMakumbo 3 ай бұрын
Dennis mlowa mmalo wa Chilima
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 3 ай бұрын
Koma utm madrama tikuonelani kumene mukathele ife pheeeeee ndi chakwela wathuyu 2025boma kale
@AishaChibwana-b8o
@AishaChibwana-b8o 3 ай бұрын
Aaaa kagwere ndi Chakwera wakoyo iwe mwana Wa anjoka iwe nde ukakhala kuti mfiti
@FanuelMaponda
@FanuelMaponda 3 ай бұрын
Uziwona nd nyau zakozo
@SafariBvumbwe
@SafariBvumbwe 3 ай бұрын
UTM yikhodza kupanga kamupeni siku limodzi ndkulowa mboma
@chrissyyendayenda4650
@chrissyyendayenda4650 3 ай бұрын
Skc my vote ❤
@MadalitsoBokosi-j3u
@MadalitsoBokosi-j3u 3 ай бұрын
Olo thawi ya yesu ayuda adazindikira kt yesu anali pulumutsi atamupha kale .... Ndiye azindikira kt skc anali pulumutsi wathu ndipo amakondedwa komaso ntendere alibe okuphao
@FysonKaliba
@FysonKaliba 3 ай бұрын
Chipan cha UTM mcha anthu amadrama bas
@ChimwemweMnthali-l5n
@ChimwemweMnthali-l5n 3 ай бұрын
Yakubayani anthu akamachoka chilipo ndithu chifukwa akumachoka,bwanji anabwera kwanu.
@LomezyWhite-vq9bv
@LomezyWhite-vq9bv 3 ай бұрын
Chipani cha achinyamata tisafooke mpaka mpaka⚒️
@EdsonKampango-y7d
@EdsonKampango-y7d 3 ай бұрын
Kaya zako izoooooo
@MarthaJafali
@MarthaJafali 3 ай бұрын
Zkulila mbava
@IyahMohyoh
@IyahMohyoh 3 ай бұрын
Udzanyangoliza fumbi mphepete mwa nsewu
COMRADE NTANYIWA PA LIMPOMPO FM  - KALINDO AMAFUNA KUPHEDWA
20:13
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 43 М.
Osman Kalyoncu Sonu Üzücü Saddest Videos Dream Engine 275 #shorts
00:29
A SULEMAN ndi ACHISALE KUYANKHULANA MOSAOPA
21:24
HOT 265
Рет қаралды 14 М.
DACHA Webinar Series: Lunchtime Webinar 2
1:30:48
ARCEoE
Рет қаралды 12 М.
HOT CURRENT__ ANJAWALA AWANG'ALULA MWA NYOO!!
15:54
HOT 265
Рет қаралды 7 М.