Eish ndimadandulatu kuti chachitika nchiyani kwa mr Ntanyiwa?...
@GoodluckVithumbiko8 күн бұрын
ndipo tinakusowani amr ndakusowani ziii musatere ineyo ndikakhara kopanda kuva mawu anu sindikuva bwino zikomo ambuye amuyendere achira murungu akuba mapemphero athu amen
@ErnestChansa8 күн бұрын
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥moto buuuuuuuu mr tanyuwa
@LilianKachala-yz2xf8 күн бұрын
Afuna kupha wanthu ndithu.Trump has with drawn statement Ndiye agulitse Chifukwa Chani?
@nabphiri26278 күн бұрын
Nonse muli pano amene muli ndi connection ndi Ntanyiwa, please aneneponso za ku immigration pakuti ku o ku Mzuzu kaya kapenanso kwinako, passport ya K 50,000 ija anthu akumapereka ma K120,000. Kodi zikutero Kodi? Ndipo munthu ukafuna ya express mmalo mwa K 130,000 akumalipiritsa K190,000. Koma akamalemba GR amalemba pa mtengo otsika uja, koma Malawi akupita kuti. Koma bomali lingafufuze zimenezi?
@ChristopherJohn-z5z8 күн бұрын
Ndimayesa kuti mwina aku nyonganit ndimadabwat ziii
@FrancisKaliwo8 күн бұрын
Boma LA makape Ili lathapo tiye nawo Comred Ntanyiwa