COMRADE NTANYIWA KU CHIKANGAWA KUNALI ANTHU OCHULUKA OMWE A CHILIMA ANAWAONA SAKANAPULUMUKA

  Рет қаралды 10,885

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 28
@MalawiTrendsTV
@MalawiTrendsTV 2 күн бұрын
Part 2 ili kumapeto tionele mpaka kumeneko. Kwa amene sitinayipeze pangani click link iyi kuti muyionele: kzbin.info/www/bejne/o6DYXmdtoZWMiKcsi=iBOn9VqdiSvgv6oK Mafuno abwino kwa nonse
@brightkamwaza9177
@brightkamwaza9177 Күн бұрын
@JeffreyKambwemba-zs7wy
@JeffreyKambwemba-zs7wy 2 күн бұрын
First comment COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM ❤❤❤
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em Күн бұрын
Ur the best Mr Ntanyiwa thus why we love u,God protect him where ever u are
@MandalaChaona
@MandalaChaona Күн бұрын
Chakwera Munthu Woyipa Koma anali M'BUSA, Ku mpingoko tu anapuma ndipo Ampingo amangoti Zikomo Amalawi mwatichosera chiphinjo mu Nyumba ya Mulungu yi🤣🤣. Chakwera unaphera njiru Mtima wakaduka kufuna Kuti upitirize kulamulira Munthu wokupha iwe. Ukhalepotu pa mpandopo mpaka 2040 tili Pano kuonera. Mphyodza Magazi ndi mikodzo iwe Chakwera mwana wa Njoka. Stay safe ✊ Comrade MTANYIWA Stay blessed 🙏 Comrade MTANYIWA
@Jessica-tc7rf
@Jessica-tc7rf Күн бұрын
❤❤❤
@PatrishaMwale
@PatrishaMwale 2 күн бұрын
Rimpopo f m ❤❤❤
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon Күн бұрын
😅😅😅 COMLADE TAMALIZANI AUDIO YO AMATI CHANI CHILIMA KKKK
@BoscoKalua
@BoscoKalua Күн бұрын
Kamlepo is highly respected in LAKESHORE n the NORTH as the whole
@JosephHill-fy1bb
@JosephHill-fy1bb Күн бұрын
🔥🔥🔥
@ajasikalonga3210
@ajasikalonga3210 Күн бұрын
Kodi a Msomda ali moyobe,ndimesa ndi rip 😂😂😂
@Christopherchapeta-q2j
@Christopherchapeta-q2j Күн бұрын
Amtanyiwa muzangosowa or chimachine chawocho chikunama inu ndiwakulu moto kuti buuu or mutati mupikisane athu awiri inu ndi Chakwera inu mukhoza kubabdula
@JeffreyKambwemba-zs7wy
@JeffreyKambwemba-zs7wy 2 күн бұрын
MALAWI TRENDS page❤❤❤
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika Күн бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@YusufMaulidi-b2c
@YusufMaulidi-b2c Күн бұрын
A mayiwa tiwatuluke palibe chanzeru chimene angatiuze Satanism inalowa mmutu asatipepelese
@TimeAbilu
@TimeAbilu Күн бұрын
Always 100 % mtanyiwa news
@RosinaPatel
@RosinaPatel Күн бұрын
Comrade tiuzeni ndithu tidziwe zobisika
@ashrafcoastance2665
@ashrafcoastance2665 2 күн бұрын
🔥
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza Күн бұрын
Mai Joyce banda ndi a mcp
@SadrackTseka
@SadrackTseka Күн бұрын
Tonse tikudziwa kt Skc adaphedwa ndi chakwera km mmmmm ndaled ndi nkhondo eeeeeesh ukayamba kuganiza mutu umawawa ambuye akhale nafe
@CleverChiumia
@CleverChiumia Күн бұрын
A Chimwendo adanena kale kuti atsogoleri azipani adachoka ku Tonse koma anthu ena a mzipanizo akugwirabe ntchito ndi MCP
@Ruthgomonda
@Ruthgomonda Күн бұрын
Amayi ndekuti alimbali ya boma sichina koma njela sadachoke Ali momwemo mulungu simunthu atimenyela nkhondo
@KennedyMvula-js7uk
@KennedyMvula-js7uk Күн бұрын
Kodi nchito yogawa chimanga ndimayesa ndi ya DODMA?
@kennedybanda
@kennedybanda Күн бұрын
Paja ng'ona yikakupana mwendo sumachita matukutuku nde zomwe akuchita Joice Banda.
@ThoccoChimbali-h6g
@ThoccoChimbali-h6g Күн бұрын
Ken msonda mnyamata onyenga mbuzi
@EnnetJimu
@EnnetJimu 2 күн бұрын
😂😂😂
@MarySinjirani
@MarySinjirani Күн бұрын
Joyce ndi oyipa koma akufuna aziti pusitsa aziwe kuti za cashgate sitina yiwaletu ana lephera kuteteza chuma cha dzikoli wayiwala chitsiru mayi ameyu ndipo ndi osokoneza
@Christopherchapeta-q2j
@Christopherchapeta-q2j Күн бұрын
Ken Nsonda timangotu rets in peace amen
Taariikhdii Tataarka Qaybtii 2aad Sh Mustafe
1:08:55
Sheekh Mustafe Official Channel
Рет қаралды 288 М.
УНО Реверс в Амонг Ас : игра на выбывание
0:19
Фани Хани
Рет қаралды 1,3 МЛН
GIANT Gummy Worm #shorts
0:42
Mr DegrEE
Рет қаралды 152 МЛН
$1 vs $500,000 Plane Ticket!
12:20
MrBeast
Рет қаралды 122 МЛН
Impeachment complaint vs. VP Sara Duterte, inaprubahan na ng Kamara
10:41
UNTV News and Rescue
Рет қаралды 250 М.
Wayneenta Nabi Maxamed ﷺ - Sh Mustafe xaaji ismaaciil
1:03:14
Sheekh Mustafe Official Channel
Рет қаралды 2,2 МЛН
BON KALINDO 05 FEBRUARY 2025 KUNG’ALURA PA WEDNESDAY
16:33
Malawi Trends TV
Рет қаралды 5 М.
Prophet Uyu Walosera Zoopsa Pa Zisankho Zikubwerazi ... Tanvani
27:34