Comrade Ntanyiwa Pa Limpopo FM "Gangata Amusamutsira Ku Nkhotakota"

  Рет қаралды 32,875

Malawi Extra

Malawi Extra

Күн бұрын

Пікірлер: 92
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 13 күн бұрын
Comrade ndizomwe ndimanenazo kuti wa police ameneo awotchedwe cifukwa dzikuonesa kuti a malawife tafasa kwambiri ndichifukwa mcp ikutitola kwambiri nde wa polisi ameneyi timufufuze, timpeze, timugwile, timuotche palibe zodikila police cifukwa mmalawi muno mulibe police.Comrade timakunyadilani mcp yatitola koma apapa sitisiyana kuphana, kuphana ngatinso ili nkhondo iyambila pompa.Tikamati cikangawa ndi opepela ndizimenezi kumanga nsewu kwa eni dziko lake palibe ciliconse wacita 0%.timadziwa kuti malipoti onse a ndege ngabodza coona cidziwika posacedwapa, comrade smart matic muyifinye mpaka ife sitikuyifuna, Anabelo,nsambo onsewa agwidwe pakhosi💙💙💙💙💙💙💙💙kumwamba kwavomelezanso
@JoyceMoyo-mp3de
@JoyceMoyo-mp3de 13 күн бұрын
Good point stupid police with Lazarus
@AlexGomani-ss5nj
@AlexGomani-ss5nj 14 күн бұрын
Comrade Ntanyiwa ndimakunyadira may almighty Father grant you more favour and long life until izizi zidzachoke tidzakuone live!! Live!!
@osmanmdala-uh7xw
@osmanmdala-uh7xw 13 күн бұрын
Allah ateteze Gangata. Mayi Said may you get better soon. Pemphero lathu: ambuye tichotsereni boma la Chakwera ndi mcp
@LawrencePhiri-sf6nl
@LawrencePhiri-sf6nl 13 күн бұрын
Mtanyiwa ndiwe wabodza kwambiri Gangata Ali ku Lilongwe
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 14 күн бұрын
Ndipo zafikapa was police ogwilitsidwa tchito ndi boma lolamulali chonde guys ,tisanyengelele was police tiphee osati kumenya ayi kupha ndipo anyamata olimba mtima ndipezeni pa in box yanga tigwile tchito ndi a police ogwilitsidwa tchito ,ndiomwe akutuma zautsiluwa tithane nawo asatipusitse ife mene tikuvutikila panomu zikusiyana chani ndi nkhondo
@FrancesPeter-xw3vb
@FrancesPeter-xw3vb 14 күн бұрын
Zosezo ndi Jezebeli watuma apolice kuti aombere munthu
@JusticeMahira
@JusticeMahira 14 күн бұрын
Kwabasi tikuzuzika ndi mcp zinthu sizikuenda guys
@VioletSinthulo
@VioletSinthulo 14 күн бұрын
Koma chilungamo chioneke waombelayo amangidwe olo aphedwe galu ameneyu pathako pa make
@FreddieKanyerere-u2z
@FreddieKanyerere-u2z 13 күн бұрын
Comrade boma likubwerali muzathandizile kusankha maudindo Monga Ku police and army kutengela ma phuziro.
@mozesjackson6328
@mozesjackson6328 13 күн бұрын
Zonsenzi zikuchitikazi just bcoz Biyen kulibe congres bwezi leloli titayedzeka mwana uja anali opeleka ma busy that's y sanamvele chisoni koma ok tiona
@michaelcohen2372
@michaelcohen2372 13 күн бұрын
Deputy commander ndi dolo heavy, not politically influenced or shaken, well educated and a real soldier
@MukileNkhana
@MukileNkhana 13 күн бұрын
More fire Ntanyiwa, vuulani a Malawi pamoto please
@HennockMpumulo
@HennockMpumulo 14 күн бұрын
Gog may u protect gangata
@paulyohane3197
@paulyohane3197 13 күн бұрын
I’m love you my brother
@GetrudeBanda-sd1yf
@GetrudeBanda-sd1yf 14 күн бұрын
May God protect Gangata
@MartinNice-z9n
@MartinNice-z9n 13 күн бұрын
Lord 🙏 bress you mtanyiwa,bon kalindo,end bakili TV
@JimmyMhone-b5p
@JimmyMhone-b5p 14 күн бұрын
Richard chimwendo ndiwonyasa ngakhale anyani ndiwokongola kuposa Richard chimwendo
@lolinichitute
@lolinichitute 12 күн бұрын
😂😂😂😂
@MorrocianNdunya-f1t
@MorrocianNdunya-f1t 13 күн бұрын
Any time judgement will come upon him,we are Malawians and no fear gun, police becareful
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune 13 күн бұрын
Ndipo sitikusinthadi mpaka 2030 woooooo
@ABRAHAMFRIGHTON
@ABRAHAMFRIGHTON 13 күн бұрын
Good job ntanyiwa
@AlicePondani
@AlicePondani 14 күн бұрын
Rest well biyeni, i know mzomwe munkafuna mu dziko muno sidzimenedzi ayi,,,,,God bless ntanyiwa
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune 13 күн бұрын
Ok malamuro Ali mmanja mwanu boss
@RoseChimbwefu
@RoseChimbwefu 13 күн бұрын
Kkkkkk ntanyiwa wazivera wenkha chitumbuka apo umakwana
@UmaliMakidadi
@UmaliMakidadi 13 күн бұрын
Zabwino zonse Atanyiwa musawasiye mpaka akhaule agalu amene tiwachotse basi
@BlessingsKamwendo-z9g
@BlessingsKamwendo-z9g 13 күн бұрын
Tili konko mafuta olo pa Black market tipeza
@SonnexTembo-v3w
@SonnexTembo-v3w 12 күн бұрын
Agalu amenewo atiwojeza kwambiri km zikapitililabe adzangotipha tonse chifuka ife nde sikuowa kufa tilimbananawo mpaka afitiwa achoke ndithu.
@MulaMasawu-g7o
@MulaMasawu-g7o 13 күн бұрын
Mumatha bro
@TwalibiDougrousdyton
@TwalibiDougrousdyton 13 күн бұрын
Ntanyiwa ulemu wanu mulungu azikudalitsan ndithu
@MercyChiwaya-um6us
@MercyChiwaya-um6us 12 күн бұрын
koma ndiye kutola kutola asabzabwanji zimenezi koma
@MartinNice-z9n
@MartinNice-z9n 13 күн бұрын
Dzikoli anthu asukusura panopa because of ntanyiwa, Bon kalindo, kmso bakili TV
@MilcahChirwa
@MilcahChirwa 12 күн бұрын
Ndipo a chakwela ndabambo ochitisa manyazii
@HabiboZimba
@HabiboZimba 14 күн бұрын
❤❤❤
@REXCHARLESKAJAWO
@REXCHARLESKAJAWO 8 күн бұрын
Cholinga chawo ndichani Kodi amenewa
@paulyohane3197
@paulyohane3197 13 күн бұрын
Kkkkkk😂😂😂😂❤❤❤
@UmaliUkuje
@UmaliUkuje 13 күн бұрын
Mtanyuwaaa!!!!
@KingsleyWilliams-y1x
@KingsleyWilliams-y1x 14 күн бұрын
Akuti mcp yaonjezela Masiku amwezi uno wa january 😂😂
@McdonaldSairo
@McdonaldSairo 13 күн бұрын
Kkkkkkkk kwaola
@ShiraKasekaNyirenda
@ShiraKasekaNyirenda 13 күн бұрын
Malawi wathu wabwino akupita kuti abale 😭😭😭
@marychavula698
@marychavula698 13 күн бұрын
Bravo
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune 13 күн бұрын
Mmataniko ku police? Otsaophyedza nyani iwe Nafetso sitingakuope
@JohnKufetula
@JohnKufetula 13 күн бұрын
Mcp idzstha ngati makatan
@SamsonKantukule
@SamsonKantukule 13 күн бұрын
Go on Ntanyiwa tililimodzi
@OssmanAbubaker-v7t
@OssmanAbubaker-v7t 13 күн бұрын
Smartmatic akawerengera kudambwe
@ManuelKanyangala
@ManuelKanyangala 13 күн бұрын
Man to man sangatikhwapule kumeneko 😂😂😂😂
@GamahCharles
@GamahCharles 13 күн бұрын
Mukhonzeke a MCP nduna zonse ndi ena onse amene mukukukhudzidwa ndi nkhani za uchifamba ndi nkhani ya zosololasola ndalama za a Malawi. pambuyo pa chisankho motsogoleledwa ndi chakwera nonse miyoyo yanu ikathera kundende mphamvu nzobwerekedwa izo simuli pamenepo kwa muyaya ai
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 14 күн бұрын
Kodi a police anthu a silikali anthu ndinu a mcp??? Komatu zinthu zisintha ndipo musakayikire bomali likusitha 2025 ino ndiye police ya kulilongwe ikukhala ngati ndi ya mnyumba mwa chakwera.
@Piase-i8q
@Piase-i8q 14 күн бұрын
More🔥🔥🔥
@MrArif-tc2cu
@MrArif-tc2cu 14 күн бұрын
We don't want killer party ( MCP) fotseki
@MarkElia-i7q
@MarkElia-i7q 13 күн бұрын
Koma nzimay wachitumbukay akuipasa moto 😂😂😂😂
@CeciliaMunthari
@CeciliaMunthari 13 күн бұрын
Mumatiyimira mulungu azikutsogorelani muzonse eee mumatimvetsa ku koma
@ZekebKwendenayo
@ZekebKwendenayo 13 күн бұрын
Koma nde akhaulatu yomweyo ntanyiwa
@ShadreckJevasi
@ShadreckJevasi 13 күн бұрын
Go deeper cmrade nthawi yakwana kuti chobisika chivundukulidwe as the bible says
@SostenPiyo
@SostenPiyo 13 күн бұрын
God is able
@JemimahPaligolo-dj2uz
@JemimahPaligolo-dj2uz 13 күн бұрын
Yomweyo comrade
@InnocentTwalick
@InnocentTwalick 13 күн бұрын
Koma ukundisimikizila kuti smartmatic basi anamisala muchilele chamtenza
@AdamuKasimu-x5o
@AdamuKasimu-x5o 14 күн бұрын
Pajatu wafuti amamutawa wamwala amalawi tisaope tiyen tidzuke
@ReginaMzunga
@ReginaMzunga 14 күн бұрын
Mutibwanji apa
@johnmapira3151
@johnmapira3151 13 күн бұрын
Mbambande lipopo
@AlliSikweya
@AlliSikweya 13 күн бұрын
Pitilizani kut malawi aziwezoonandi
@KonSalieHara-w2j
@KonSalieHara-w2j 11 күн бұрын
MR C T fana woganizaboh motto kuti booo
@InnocentTwalick
@InnocentTwalick 13 күн бұрын
Comerade lelo wapsamtima wabwela ndimoto wapolice ameneyu akupita basi
@JeniferKananji
@JeniferKananji 13 күн бұрын
Mayo Malawi uja wasanduka mukapolo wakalavula gaga . Abale tangomuchosani chakwela watikwana
@GloriaKamwendo-w2h
@GloriaKamwendo-w2h 13 күн бұрын
Mumakwana bwana Mtanyiwa,wa police ameneyo aphedwe ndithu
@AchinaKellz
@AchinaKellz 14 күн бұрын
Aphiri zowonadi andale amayang'ana pagulu kuti chitsiru ndi chiti choti tikachisakha chizativera. Mbuzi
@KhirChisale
@KhirChisale 14 күн бұрын
Koma ineyo guys ndikuona kuti azipani zotsutsa akanagona coz izizi zikufunika atitsogolele kuti anthu awa tithane nawo agaluwa coz dziko sila Chakwera kapena mcp ai. Azipani zotsutsa ndikukudandaulani titsogoleleni ife asaona akuyelikofe.
@CharlesMotloung-w3n
@CharlesMotloung-w3n 14 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@OsamaOsama-u8m
@OsamaOsama-u8m 13 күн бұрын
M mawa saliwona wa polisi ameneyo tipeleke chisazo kwa kwa apolisi ena ose
@SymonMbuto
@SymonMbuto 13 күн бұрын
bana wawene ntanyiwa🤣🤣🤣
@BerthaKasambala-y5k
@BerthaKasambala-y5k 14 күн бұрын
Mmaro mongo turusa brack box ari busy kumanga anthu km president ameneyu ine mawu ndiribe sure
@Malume2024
@Malume2024 13 күн бұрын
Katundu koma comred mcp tikutitu ikunama zitsilu kwambiri
@GiftTonnexMawila
@GiftTonnexMawila 14 күн бұрын
Mtanyiwa machine athu iweyo
@SellinaSanena
@SellinaSanena 13 күн бұрын
Kumeneko nso Dpp ilipo
@MemoryMteketi
@MemoryMteketi 13 күн бұрын
Kkkkkkkkkkk koma mpaka Alibe MCE chibwatiko chamnthu
@JemimahPaligolo-dj2uz
@JemimahPaligolo-dj2uz 13 күн бұрын
Alibe msce😂
@GiftTonnexMawila
@GiftTonnexMawila 14 күн бұрын
2025 machende achakwela ndi phiri pamtumbo pamayako chakwera
@JusticeMahira
@JusticeMahira 14 күн бұрын
Mcp sitikuifuna ife tatopanao anatinamiza kuti feteleza tizangula 4999 mafuta azakhala ochipa pano mafuta tikugula 9500 pa litr aaaaaachimanga pano tikugula 70000 thumba limozi sinaone ine paziko la malawi aaaaa mcp sizalamulaso padziko lapasi mulungu atichitile chifundo tikuzuzika amalawi
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 13 күн бұрын
Ndipo chimwendo, may the good Lord punish him
@MakinahMaidah
@MakinahMaidah 14 күн бұрын
Wa police ameneyo akaziwika amve kuwawa
@SmartRuthGarteni
@SmartRuthGarteni 14 күн бұрын
Tibweza bas
@FelixSumani-n7c
@FelixSumani-n7c 13 күн бұрын
We love you ntanyiwa
@MagretChirambo
@MagretChirambo 13 күн бұрын
Pp
@MasautsoLameck
@MasautsoLameck 14 күн бұрын
Gang ka 4 ntanyiwa
@LukaUsen
@LukaUsen 13 күн бұрын
Wawa
@DavieChikumba-kl5tt
@DavieChikumba-kl5tt 13 күн бұрын
Ndale sindimapanga koma chomwe ndimadziwa kugwa mmanja mwa Yehova ndikoopsa kwambiri Palibe chomwe chimaenda,sindikudabwa nawo A president achakwera.
coco在求救? #小丑 #天使 #shorts
00:29
好人小丑
Рет қаралды 120 МЛН
How to treat Acne💉
00:31
ISSEI / いっせい
Рет қаралды 108 МЛН
WELCOME TO TODAYS SERVICE
1:33:15
MVAMA CCAP NKHOMA SYNOD (Rev. Yassin Gammah)
Рет қаралды 591
coco在求救? #小丑 #天使 #shorts
00:29
好人小丑
Рет қаралды 120 МЛН