Kulakwa. Nanga mzimai wa mimba walakwa chaninso nanga mdziko lovutika kale ili eeee....God Have Mercy...
@ChristinaMdeza7 күн бұрын
Zoona zake chakwera eee munthu woyipa kwambiri a chilima kuyika mpando wa .u president ndiku mupha, nso eee zovesa chisoni. Kwambiri Kom poti mau amati. Kulanga, kwa Yehova. azamulanga, ndithu chikwera ndi nduna zake Ambuye akuze malile anu a comrade ntanyiwa ❤
@OwenZimba-b4s7 күн бұрын
Zoona report akagawane iye nkazi wake ndi ana ake ndimbuzi chakwela
@JustinMakoka7 күн бұрын
Zativuta ndife bas zikoli
@robsonmapeto19114 күн бұрын
Koma ameneyu nsima akudya nilowa muchifu chakecho? Njoka yeniyeni