Boma ngati liri ndi nzeru lisandutse msikawu shopping mall, awamangire anthuwa ma shop olongosoka ndi owoneka bwino, shopping mall ayipezere malo ena. Zimamvetsa chisoni ma vendor akupsa ndi dzuwa mmisewu koma amwenye ali ndi ufulu ndipo salola munthu kupanga malonda pakhonde la shop koma mukapita ku new york mukapenda ma vendor mma khonde a ma shop. Amalawi ndife ogona ndithu. Even ku Johannesburg boma linayika ma bench a ma vendor ndikuwapatsa malamulo.
@EDGARMPIKAMEZO3 күн бұрын
Ine ndiri ndi maganizo Osiyana. A malawi tisiyanitse ufulu ndi chitukuko Cha dziko. Naperi it's part of urban, msika wa pa kamba sugwilizana ndi Area imene ija. Shopping mall ndi filling station ndi chitukuko chapamwamba. Pa kamba pamapindulira zidakwa, ma Hule ndi akuba. Kodi ma restaurant ake ati? Azimasakawo? Please a malawi tikamati Mizinda yathu itukuke ingatukuke bwanji?
@@adamusaidih8570 anzeru ndinu komano ndingokupemphani muziyenda. Mu township simumakhala ma restaurant azisaka. Opanda mzeru ndi iwe ukufuna kumayala makala mu mkati mwa mzinda. Kumasuntha ndi dziko amwene.
@EDGARMPIKAMEZO3 күн бұрын
@@zayedmitawa8345 point ikhale yoti palibe njira yonveka bwino pa za relocation kapena compensation. Koma Malo Aja patha kuchitika Cha mzeru kuposa mmene palili panomo
@lastonmasoatenganji-bs5gf3 күн бұрын
Abale athuwa sakudana ndi chitukuko, koma dandaulo limveke. Nthawi ili yachabe. Apatseni 5 years notice kudzanso alternatives.
@Crysis252 күн бұрын
@@lastonmasoatenganji-bs5gf 😅😅😅malo ndi a khonsolo not awo..chikuvutani kumvetsetsa ndi chan kod?? . Umunthu ukatichulukila sittitukukapo apa
@martinkhozombah2 күн бұрын
🎉Kudesa town ndizimasaka zanuzo, iyaaaa. BCC gulisan malowo
@EDGARMPIKAMEZO3 күн бұрын
Pa kamba patafika shopping mall, ma modern restaurants ndi filling station. Patha kupezeka mwai wa mbiri wa ntchito kwa a Malawi ambiri kuposa omwe akupeza phindu pano. Maganizo anga
Maganizo a shopping mall ndi abwino koma pali vuto mpoti BCC siikutsindika zomanga shopping mall komanso siikufuna kukambilana ndiochita malonda munsikao.
@AlexNjovu-j4z15 сағат бұрын
Think about poor people
@EDGARMPIKAMEZO14 сағат бұрын
@AlexNjovu-j4z come out of that mentality. Those poor will get employed. We should not put it that some are poor, rather all of us we deserve better living. All we need is to force our government to set proper measures on business policies between locals and foreigners. We need not to pay equal tax on equal business with foreigners.
Msika is under district council not government. School ijaso pena imathandiza kudziwa omudandaulila.
@JamesKalasa-s6s22 сағат бұрын
Blantyre ikufunika ma building abwino,chokani kasakeni kwina malo amange zooneka
@AlexNjovu-j4z15 сағат бұрын
Kodi mukuti amphawife titani?tilowerekuti?
@MikeSangano-b6x3 күн бұрын
The most important thing in life is human welfare. Mukati achoke ma vendor Mali atagulutsidwa it means sangabwererenso pamenepo coz pagulitsidwa. Amalawi tiyeni tidzikondana tokhatokha,Moyo pano walimba, ntchito kulembedwa sizikutheka pomwe katundu akukwera mtengo daily salary yomweija. Munthu uli ndi family penanso kumasamala makolo,achibale plus amasiye,ndiyeno akuthamangise pa malo a business zitha bwanji? Chitukuko cha filling station sichingasamale banja lako komanso zosowa zamunthu. Ngati kuli kotero,amange kaye msika wabwino woti mavenda apa Kamba asamukiremo pomwe akuyamba kumanga zama filling station zawozi. Boma lonyasa ngati ili sindinalionepo chibwadwireni. 2025 ilimukhonde,muzawafuna mukuwanzunzawa.God is watching you!!
@RaymondKaumba3 күн бұрын
Accept development
@cvali26533 күн бұрын
To be honest ,nsika uwuwu sumapanga ndalama ndipo kuikapo shopping mall and filling station zithandiza kwambiri,this area anthu omwe amabwera apa ndiozadya ndikumwa mowa
@zayedmitawa83453 күн бұрын
Kodi shopping mall ndi filling station zimathandiza ndani? Msikau ulipo mpaka pano chifukwa umathandiza anthu ozungulira. Council ya Blantyre yagulitsa malowa pa zifukwa zina. Chitukuko siukambila kuseri
@chancyblack63843 күн бұрын
Ayi tikufuna chitukuko amangebas akupasani pena
@Crysis253 күн бұрын
Thats wat we call development...pena timakakamila zopanda tsogolo
@zayedmitawa83453 күн бұрын
Development sabisa.Kuwafotokozera anthu momveka bwino zimachepetsa mikwiyo. Zikuoneka kuti malowa agulitsidwa pa zifukwa Zina osati kumanga shopping mall.
@Crysis252 күн бұрын
@zayed munakamva zomwe ceo wa bt anayankhila b4 kutiyankha
@AngellahKaukonde-z7l3 күн бұрын
Ndipo asachoke nsika umene uja umathandiza Maka ukakhala ku chipatala kuja
@SamuelKhumbiwa3 күн бұрын
Khani iyi ndiyosekesa kalata yopanda siginecha so why?ndichifkwa chani sanasayinile umeneo ndiye utambwali,Blantyre city ilipo chifukwa Cha wanthu ,popanda wanthu city kulibe,Inu acity musamalakhule kt Malo ndi anu ,munawatenga kt?
@chesterdimba02093 күн бұрын
The govt should be non profit business allow its citizens to conduct business
@Maxielyies3 күн бұрын
Ma senior a Blantyre city council ndi makape akatero apeza mwenye kuti amugulitse
Khani yomanga mnsika pliz ndiyofunuka,ma new models akufunika kt mzinda .ndi ma toun zizioneka bwino.kma pakufunika ndondomeko kt anthu ali mmenemu apasidwe Malo ena ,kupanda kutero simunthana nawo chifkwa ndi m'badwa ndi mzika zamalo ao.nthaka ya amalawi ndiya wo kma ulemu ndi ndondomeko zikhalepo.
@SalatiKiddie3 күн бұрын
Osatopa osawopa osafoeoka
@chippakaribafox28653 күн бұрын
MCP kubesa mavoti....
@Littlefair73 күн бұрын
Amwenye ali ndi malo opangira malonda mwa ufulu, ayini ake adziko akupsa ndi dzuwa mmbali mwa misewu, amalawi ndife ogona.
Inde chokani pabwere town pachuluka afiti kwa kamba kkkk achokepo basi
@YusufuKaifa-r2y3 күн бұрын
Osachoka akamange kwawo kwa zimayi awo zachibwana
@RaheemNgoma-pk1ev3 күн бұрын
Osachoka ndipo osaopa
@zayedmitawa83453 күн бұрын
Koma Council posakhala transparent pa nkhani ngati iyi nchiani? Ngatidi akufuna kumanga shopping mall mwai umapelekedwa Kwa nzika kukhala ndi mashop awo mkatimo ndipo iyi ndi nkhani yabwino. Koma ngati kuli kupha Kwa nsikawu at least apange relocate ma vendors apititse kwina kudzera mkufotokozerana. Apa a council plus Boma akubisala mawa adzayambe kugwiritsa ntchito a police kuthamangitsa anthu ndi teargas. Mchifukwa ninji boma la Malawi silikhala ndi chidwi ndi nzika zake.Mzika zimaesetsa kuzipezera zokha zochita zomwe Boma limapindula nazo misonkho koma boma lomwero likafuna chinthu pa anthuwa limagwiritsa ntchito mphanvu osati kukambilana. This nonsense must stop. Wakawaka in Lilongwe, you're next!!!!
@ENOKMAKONDI2 күн бұрын
This action is encouraging kuti anthu azilowa ndi Malonda nkati mwa town apezeka kuti akukagulisa Malonda pa nandos kandodo etc kenako a city azitengaso galimoto kumakalanda Malonda omweyo kumakadya makwawo are you trying to kill poor malawians
Koma tiyeni tlikinde dziko akamanga shopping Mall paonekabwino tauni idzisintha matemba tidzikagulabe kuseli kwa shopping Mall,, pano pa queens hospital padadzadza ma hawker palibenso amapita kwa kamba kukagula zinthu
@zayedmitawa83453 күн бұрын
Sakufuna kumanga shopping mall nchake anthuwa akuti sachoka. Malowa Council yagulitsa pazifukwa zina. Council iyenera ipeze malo kwina ikaike anthuwa
@RencoMandah-vd2yp3 күн бұрын
Osamangakaye wenela bus deport bwanji instead kumalimbana ndi misika yamuma location
@valentinokaundama79023 күн бұрын
Koma if its redevelopment and malowo si amunthu, i dont see any problem, we need standard things, enawo akhoza kukayala panyumba pawo, or apeze pena akayambise okha
@KampilaAllie3 күн бұрын
Funso mkumati kuyambila litiro kuona malowo ndi akulu ? This government its too much corruption ndeno akagulitsa malowo what is your benefit you will get ?
@MikeKameta3 күн бұрын
Komatu
@EDGARMPIKAMEZO3 күн бұрын
Abale a Malawi anzanga ngati timafuna dziko lathu kutukuka ngati Maiko ena, tidzakwanitsa bwanji kutero ngati pano tikukana shopping mall mu urban? Kaya akumanga ndi a Mwenye kaya ndani koma tidziwe kuti zikumangidwa mu dziko lathu, ndipo olembedwa ntchito pamenepo ndi abale athunso
@ChikaNation-g8j3 күн бұрын
Kuchoka ndizotheka kma situation ku Malawi sikuli bho powachotsa pamafunika ndondomeko yoyenela at least kuwapititsa malo ena
@EDGARMPIKAMEZO3 күн бұрын
@@ChikaNation-g8j ndizoona
@ShamimuBisani3 күн бұрын
Ma comment onse iweyo wabaya osat nzeru zozaza soda mutu@@ChikaNation-g8j
@ChrisyMbeweКүн бұрын
Ndipo.musachokedi.khaza.bas
@KampilaAllie3 күн бұрын
Chilungamo ndichofunika kuwaudza anthu mcp why your doing this to Malawians