KOMA SILVESTER NAMIWA MPAKA KUYANKHURA CHONCHI LERO? AKUTI SAKUOPA AKUNGOFUNA CHILUNGAMO CHIDZIWIKE

  Рет қаралды 33,740

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 78
@BoscoKalua
@BoscoKalua Ай бұрын
I commend your action please help the marginalized people BRAVO bravo bravo NAMIWA
@jogechawa6192
@jogechawa6192 Ай бұрын
Namiwa I salute you ma chinese ayenjeza
@CosmusZula
@CosmusZula Ай бұрын
Thats what the human rights freedom fighters should be We salute the human rights activists
@PeterMakaika
@PeterMakaika Ай бұрын
Koma Namiwa powerful massage ❤️ ❤️ ❤️
@IssahAluba
@IssahAluba Ай бұрын
good information 🙏🙏
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje Ай бұрын
Welcome mr namiwa
@MemoryMteketi
@MemoryMteketi Ай бұрын
Powerful Mr Namiwa
@BlessingsMakalani
@BlessingsMakalani Ай бұрын
💯Mr Namiwa Mumakwana koma pena Musamasowe kwambiri
@PatumaCassim
@PatumaCassim Ай бұрын
Iiiiii 😂😂😂nde ma demo enawo azatheka apolice sazakhara busy kuwaperekeza apule ku nsokhano???😂😂😂😂
@MakawaPartrick
@MakawaPartrick Ай бұрын
Mr namiwa osaopa osafooka osaopa tili nanu bwana atiphele limobzi
@lovemorengwira
@lovemorengwira Ай бұрын
💪💪💪💪💪💪💪💪namiwa your the best
@rashidsaid2232
@rashidsaid2232 Ай бұрын
Thanks mr Namiwa 👍
@JudithKamwendo-fb3me
@JudithKamwendo-fb3me Ай бұрын
Ulemu wa Mr Namiwa ndipo Inu mutiyimilira Malawi wathu akanapezeka ena atatu mukhale 4 aaa dzikoli chibwana chikuchitikachi kulibe koma painu nokha mukukwa 4 timakunyadukani
@Pangolinimw
@Pangolinimw Ай бұрын
Welcome ❤❤❤❤
@ChrisScott-f8r
@ChrisScott-f8r Ай бұрын
MCP yagwilitsa penalty kukanengo
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i Ай бұрын
Nde sunadzisate Anamiwa tsiku limenelija ndi amene anali patsogolo ndi a kabambe koma atsogoleri ena osusa sanapiteko.Mademo enawo acitika popanda comvuta cifukwa pali njira zatengedwa.We are waitting wll be there big up 2 u mr namiwa mumatiyimilira.
@tisuhmakhwah7085
@tisuhmakhwah7085 Ай бұрын
Tisamangoyankhula tiyeni tizipanga zinthuz pa ground ndine okwiya kwambiri ndi mcp
@RightwellZumbwe
@RightwellZumbwe Ай бұрын
🔥🔥🔥🧐🧐 anamiwa achakwela akukuyang,anilani diso limozi
@MavutoFodya-p1u
@MavutoFodya-p1u Ай бұрын
Well come Mr namiwaa
@victormbewe7462
@victormbewe7462 Ай бұрын
I like your channel, but if possible can you please try to fix vuto loima-ima ngati cd please 🙏
@JeremiahKapundu-j1p
@JeremiahKapundu-j1p Ай бұрын
Kom anamiwa mmaitha hevy
@Samuel-c1j1t
@Samuel-c1j1t Ай бұрын
A namiwa tsekani pakamwa ndinu wa mantha mumakonda kuthawa ma demo😂😂😂😂😂
@PempheroAlli-v8y
@PempheroAlli-v8y Ай бұрын
Mawu Mr namiwa Lazaro watikwana tiyen a Malawi pa nsewu
@EnifarSeleman
@EnifarSeleman Ай бұрын
Mai yolamu inuyo khope ija yayipa ndi mtima omwe kani
@GeofreyRhonard
@GeofreyRhonard Ай бұрын
Mademo ameneo bola asadzalephereso chifukwa mmmm zikuopsa tsopano nd ulamuliro ulipou koma kale zidari easy kupang mademo
@SylessD.Dzungu
@SylessD.Dzungu Ай бұрын
Mr Namiwa, ntchito zina zimene mwayankhulazo zimene aku China abwelera kuno, ife a Malawi titha kugwira
@JohnBandawe
@JohnBandawe Ай бұрын
Kod za ndege zilipat
@MadalitsoAbambo
@MadalitsoAbambo Ай бұрын
Zayamba kumenyana zigawenga zachikwanje zija ku ngwenya ndiye mkulu wa police akuti anawamanga😂😂😂 muyalukatu mayi inuu
@Clyne_Phiri_265
@Clyne_Phiri_265 Ай бұрын
Makosana Team, Please work on improving the quality of your titles when posting content on your platform. Aim to maintain a professional standard.
@WilisonWilliam-d9j
@WilisonWilliam-d9j Ай бұрын
Uyu alingt born kalindo tanyiwa samaopa
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift Ай бұрын
Mulandire urem
@kasambegrace
@kasambegrace Ай бұрын
Mayi uja angakhale ndi mtima wabwino ndimmene akuwonekeramuja aaaaa or bible amaliziwa , ndikuligwira nkumawelenga aaaa
@PiassDayit
@PiassDayit Ай бұрын
Koma M'mene ndi kuwoneramu ziko lamalawi sitizalandidwa ndi machan misewu tikupasidwayi kod mundu angachoke kwake kuzabwela kwanu kundizi kuthandiza pophanda chopeaza khandu ndimene akuchitila machan 🤔🤔🤔🤔🤔
@JoefreyGongoni
@JoefreyGongoni Ай бұрын
Ine team iyi ndinasiya kuikhulupirira , mademo angalepheleke zoona athu wanzeru ngati inu mulimuno mumamalawi
@williamSaka-ep1qz
@williamSaka-ep1qz Ай бұрын
Zoonad bwana Namiwa
@HarryMsyamboza
@HarryMsyamboza Ай бұрын
Munthu amayankhula poyambayo ananveka motsika kwambili kaya ndi mwachikonzedwe kaya
@blackcobra-b2y
@blackcobra-b2y Ай бұрын
Galu iwe,iwe ndiwe wa chilungamo?
@BillyBentryMunthali
@BillyBentryMunthali Ай бұрын
Lero namiwa ayankhulako zanzeru, apa ndikuponyera ulemu osat zandale
@samdiverson9733
@samdiverson9733 Ай бұрын
Machine machine namiwa
@Christopherchapeta-q2j
@Christopherchapeta-q2j Ай бұрын
Pano tikafuna kupanga campain xa opposition tizingopita ku ma demo ndiye a mcp azibwera ndi zikwanje akatero aziipitsa mbiri yawo
@SamKaposa-i5c
@SamKaposa-i5c Ай бұрын
😂😂😂Good move
@SylessD.Dzungu
@SylessD.Dzungu Ай бұрын
Komanso sitikudziwa kuti munthu atachitiridwa nkhanza, angakupedzeni kapena kulumikizana nanu bwanji ?
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin Ай бұрын
Mupange mademoiselle anyone Komaso mudzikapezekako kumademoko
@joegibsonzulu2599
@joegibsonzulu2599 Ай бұрын
Sentence yoyambayo mukuti bwanji?
@AjidahZmachemba
@AjidahZmachemba Ай бұрын
Anthu obwera akumasuka mdziko lino kwambiri
@Samuel-c1j1t
@Samuel-c1j1t Ай бұрын
Wamantha uyu adathawa commision of enquiry😂😂😂😂
@emmanuelalbertbotolo
@emmanuelalbertbotolo Ай бұрын
Choti udziwa anakana chinyengo osati anatawa ai
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 Ай бұрын
Anthu saziwa kusiya ....nisa...kusiya kupanga commission of enquiry.......kuti uyu you samafuna chinyengo chaka anasiya kupanga nawo... eyetu Amalawi Adzanga
@faithmwale2902
@faithmwale2902 Ай бұрын
Anthu akuzunzika mwa ma china nd amwenye mu..
@PiassDayit
@PiassDayit Ай бұрын
munazilekela dala relo ndi simeneso chisazo Ku South Africa mumavaso Kut mafolena Kutila jobo
@ZakeyoPhiri-s6n
@ZakeyoPhiri-s6n Ай бұрын
Kodi inu muli kotsutsa paja
@HannaMkhalipi
@HannaMkhalipi Ай бұрын
Namiwa umatiyimilira
@GRACEFESTORN
@GRACEFESTORN Ай бұрын
Tatopa ndi ulamuliro wa MCP Donnex Gondwe
@PatrickFicklem
@PatrickFicklem Ай бұрын
kkkkkkk ndiyeno iweyo namiwa ndi mai yolamu ali ndi mphavu ndi ndani? kkkk
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie Ай бұрын
Koma iwe ndinamachende yeti .iwe nyau yosadulidwa mbolo yeti? Kodi kupanda ife athu hule wakoyo yolamuyo bwenzi Ali mkulu WA police?
@PatrickFicklem
@PatrickFicklem Ай бұрын
@PrinceThom-pe6ie pansana pako, ine chiwanda chako chotukwanacho ayi!!!!!! aliyense akuyankhula zimene akufuna usandinyasepo apa sidakupemphe kuti upange comment
@mabvutomichaelpanagona1949
@mabvutomichaelpanagona1949 Ай бұрын
Mkulu wa polisi ndi oyipa mtima ndipo sindikukhulupirira kuti ali ndiana.ameneyu akufananaso ndi anabelo mtalimanja kuipa mtima kwawo.
@EnockMvula
@EnockMvula Ай бұрын
mkunama inu anamiwa munadwa bazi inu tasiya kukunkhurupirirani anamiwa zaziii
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 Ай бұрын
Ulemu wanu
@Aubiekenneth
@Aubiekenneth Ай бұрын
Iwe namiwa utithera bundle wanva makutu amako
@YamikanChirwa
@YamikanChirwa Ай бұрын
😂
@GeorgeSathula
@GeorgeSathula Ай бұрын
Komadi ife amalawi timapheredwa ufulu tipite mayiko ena timanyozedwa moopsa tikhare kumuzi Chimozi mozi kodingati anapanga ubare ndiye azitiphaso achayeneake ziko koma apolice nanu muzaona muzibweresa maumboni aboza mupitilize chinyengo
@AlicksonMakata
@AlicksonMakata Ай бұрын
Koma amalawi osaiwalira khasu chifukwa mukapita kumademo nthawi yolima iima ndiye pamawa osadzanena kuli boma labweretsa njala zimu waulesi umachokera kwa Satana.
@RaphaelThawi
@RaphaelThawi Ай бұрын
Mukunenadi zoona a police awa ndiadyera kwambili amateteza anthu obwera
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 Ай бұрын
Mukayendela za chakwela wanuyo muchedwa
@LetshaChirwa
@LetshaChirwa Ай бұрын
Ulemu bwana namiwa pitilizan kutiimila ife mau athu sangamveke ife akumudzi
@AwidsMaseko
@AwidsMaseko Ай бұрын
Utsogoleri nkubwira utsi uja eti?
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani Ай бұрын
Usogoleri ungakome bwanji mphamvu zingachuluke bwanji koma znse zimatha mkulu wapolis aphunzire kukhal bwino ndi anthu table will turn any tym komas aliyense masiku ake ndi owerengeka aliyensese ayesese kut ikadzamafika nthawi yokufa kwake akonze moyo wake osadzafa munthu akukudandaula tikhale ndi umunthu
@JulioChiwalo-t4f
@JulioChiwalo-t4f Ай бұрын
Mayi yolamu akunama kuti anamanga zigawenga za chikwanje
@PatienceMphuche
@PatienceMphuche Ай бұрын
Nkhani yakuchikwawa ndiyomvesa chisoni chilungamo chionekepo apa
@PatrickFicklem
@PatrickFicklem Ай бұрын
kodi iweyo umatumidwa ndi a opposition?
@ChisomoMandawala
@ChisomoMandawala Ай бұрын
Pansana pako m'mene zililimu paliso zotumidwa apa?
@PatrickFicklem
@PatrickFicklem Ай бұрын
@ChisomoMandawala u too pansana pako
@SandraChibaka
@SandraChibaka Ай бұрын
Chisana chopidicho galu wa munthu palizotumidwa apa galu wamuna..pusi iwe
@PatrickFicklem
@PatrickFicklem Ай бұрын
@@SandraChibaka ngati zakuwawa zako izo, ndiwe galu kwabasi🤣
@tasmania527
@tasmania527 Ай бұрын
Kamunthu kena kobowa ndikameneka, ka mutu ngati nguli. Nkhope yokhala yolutsa nthawi zonse. Vuto ndi loti tianthu ngati timeneti timapasidwa space ngati kuti tili relevant pamene ndi tima mouthpiece ta chipani cha DPP. Democracy ya ku Malawi njautsiru yapanga promote tizitserekwete.
@PatrickFicklem
@PatrickFicklem Ай бұрын
uyu ndichifukwa chake anyamata anamutulutsila zikwanji coz amapanga ngati iyeyi ndiwe wamphavu kwambiri, kudelera kukupweteketsa iwe kaya ndi ganyu kupangira dpp ndi enawo zikuvuta
@SteveNkhambule
@SteveNkhambule Ай бұрын
Nde mwati maina ama Chinese ndindani???
IL'HAN - Qalqam | Official Music Video
03:17
Ilhan Ihsanov
Рет қаралды 700 М.
Quando eu quero Sushi (sem desperdiçar) 🍣
00:26
Los Wagners
Рет қаралды 15 МЛН
人是不能做到吗?#火影忍者 #家人  #佐助
00:20
火影忍者一家
Рет қаралды 20 МЛН
BON KALINDO LERO PA 27 JANUARY
17:02
Makosana
Рет қаралды 22 М.
Hon Suleman Vs Mr Sambo: Interview Ndi Chimwemwe Magazi
54:59
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 38 М.
One-on-one with Jacob Zuma
55:52
Newzroom Afrika
Рет қаралды 1,5 МЛН
IL'HAN - Qalqam | Official Music Video
03:17
Ilhan Ihsanov
Рет қаралды 700 М.