Gotani kunjenjemera kuti bwana wake akukhaulitsidwa ndi mafunso
@JohnmjigoMalindaКүн бұрын
Ndipo zoonad mayi ameneyi ndioyipa kwambiri
@WarriorKB-l3i2 күн бұрын
Aaah cikangawayi ndi mbuzi ya munthu palibe cogwila chifu chilichonse wanena. Mbwelela zokhazokha wathawa kuyankha mfunso ya njala simwaona? Ndicifukwa timanena kuti mmalawi muno mulibe presdent.Cifukwa tsogoleri adzikhala ndimayankho. Uyuyu ofunika athamangitsidweko ku state house adzipita ku kasiya akapitilize ubusa wa nyau cisilu cimeneci kwambiri palibe cicita iye & cikhalila iye ku state house ine sindicidziwa cifukwa kumene kuja mkokhala presdent, nanga mmalawi muno tili ndi pule?
@charlesmasauko4651Күн бұрын
Chikangawa woyeeee
@JohnmjigoMalindaКүн бұрын
Mayi uyu speakeryi usamale kwambiri soon u will be introuble ukumuteteza chakwera
@NtambalikaКүн бұрын
Njala ikalowa nyumba bamboo amayesesa kuthamanga thamanga kut zithu zisithe Koma bambo uyu chakeranyu sakutithandiza akupanga khaza kwamblili