Thanks Mr Bon Kalindo the DC for opening our eyes every day,,, Zomwe Umayankhula zimachitika ndipo ma umboni alipo.
@WanangwaMfune18 күн бұрын
Mulungu ngati angavere iwe ndiyeno chamba ndichabwino kwambiri 😂😂😂😂
@JamesALLi-m8i18 күн бұрын
The DC bon kalindo ulemu wanu big be strong 💪 mr president bon 💪
@LukaThomas-o6e17 күн бұрын
Ambuye !!ambuye !! Ivani kulira kwathu
@viennasamuel297618 күн бұрын
Amene ali ndi maso auzimu akuvomeleza zomwe akunena munthuyu,otsutsa izi ali kumidima komweko.
@bridgetmajor364618 күн бұрын
The dc moto kuti Buuuuuuuu🔥🔥🔥🔥
@razackibrahim588018 күн бұрын
The dc moto kuti buuuuuu 🔥🔥🔥🔥❤️❤️❤️
@FaithMatitha18 күн бұрын
Zikomo chifukwa cha mvumbulutso mulungu atimulutsa mene watipulumutsila kwa chido yesaya 54 is 17
@RobertLuka-wy9cl18 күн бұрын
Mvula ibwera mulungu akuona mavuto amalawi 😭😭😭😭😭😭😭pls Allah bless malawian😭😭😭😭
@ANTHONYCHANZA-q6k18 күн бұрын
Pa mvula pokhapo kudzakhala njala malo akuti akuti bible linatero. Amene amawerenga aweramuke. Zinazo zikunenedwazo ndapitilirapo
@AwidsMaseko18 күн бұрын
A kalindo pena mumakamba zomveka koma apa pokha ayi ndithu simudaganize bwino Inu si Mulungu. Mukungovutika ndi kupeka nkhani zabodza izi zidalembedwa kale mbaibulo
@liz942518 күн бұрын
What he has said is true, mcp is evil they are doing whatever they can to continue ruling Malawi. Not all 🌧️, namondwe are from God , some are man made to control people, even the earthquake are made made as well , they are creating disaster as the platform to bring help to Malawians so that we can clap for them ! If this is deep for you it doesn’t mean it’s false to some of us we have fully understand this
@aaronmhone71418 күн бұрын
Keep the Fire Sir....
@SamsonChitezi-o6g18 күн бұрын
Ndizowona bon ambuye akudatise
@HarlodLemwe18 күн бұрын
iwe Born kalindo ngat upezapo nthandizo lako usamasewele amalawi wava ukamat ndiwe president wa anthu osauka chonsechi ndalama ukuika mmatumba mwako panyapako wako
❤Aboni kalido inuso ndi Inu osokoneza penapake musamakhale ngati mukuuza ana mudzimudziwa mulugu mulugu aliyekha sauzidwa
@aaronmhone71418 күн бұрын
Right now Azitumiki Amulungu ndinu ndi onse Amene akulankhulira mulungu pakuulula machimo obitsika omwe dziko ndi azitsogoreri ache a Chita... Azibutsa enaonse Amene angoti Chete osalankhulapo ndikudzudzula za infa ya achilima ndi Ena komanso katangale akanidwa ndi mulungu... They are rejected... 2025 there is hell to pay for the wicked.. GOD IS BEGINNING JUDGEMENTS...
@LawrenceBelson18 күн бұрын
Kodi nde kuti inuyo ndinu zitsulo zoti simuzafa eti mulungu wathu ndi wadongosolo sangalore zimenezo yesu ndiye bwezi lenileni
@PanjibenfreyMakwakwa-e4y17 күн бұрын
God is watching
@ChamvekaAdamu18 күн бұрын
Ya allah bless the our country in Malawi please Allah we need u peace
@KennethMugabe-i1g18 күн бұрын
Yes yes you are truly mwana oopsa kwambiri coz you don't want nonsense
@JonathanGondwe-wt8mu18 күн бұрын
Good job the DC
@bridgetmajor364618 күн бұрын
Koma mwana ameneyu .......chikusangarasa.......ndi chani....Macfalen......Abare..😢😢😢😢😢😢😢 koma.... Ambuye.....Atithandize munyengo yowawisayi
Inu si Mulungu mwamva mawa palibe amadziwa za mawa
@SimonChuungula18 күн бұрын
Big love always ❤
@WarriorKB-l3i18 күн бұрын
Mkukuyu iweo ndicisilu munthu, Nkhani ya lipoti la ndege sitisiya kulankhula kufikila titawona black box icho nde udziwe bishop akunena zoona lipoti limeneli ndi manyaka.Ndizona bushiri ndi azache a mcp ndiomwe akulenga mavuto onsewa akucitika mmalawi muno sizocokela kwa mulungu zinthu.Ndicifukwa timanena kuti tili dzikoli lili mmanja mwa satanic.
@mosesmatola540718 күн бұрын
Zitsilu zokhazokha ndizomwe ungazipange brainwash osati munthu oti mutu wake amaugwilitsa ntchito ekhayi,Mvula ikugwilizana bwanji ndi boma
@ElinatBanda-h7h18 күн бұрын
Pavula pokhapo ndie wanama siwe Mulungu ndiwe galu chipani chikumtundu ife takana
@viennasamuel297618 күн бұрын
Tamalowani ma group anthu amene akupemphera muuzimu ndi mu choonadi mukhulupilira.mudzimve muuzimu ndipo mundivomeleza
@IqrahSikweya-wm5mn18 күн бұрын
Mvula imagwa chifukwa cha Mulungu not munthu, mzosatheka kut Mvula isagwe chifukwa cha Munthu, kamban zinazo koma osati yamvula, Kod mesa ndi Bon kalindo yemweyu ndamene anabweretsa makape amenewa m'boma akuti sokosa ife osati daily tizingomva zachamba
@AlfredYona18 күн бұрын
Mtumiki Twaibu said same thing 3 months ago, Lord have a Mercy on Malawi 😢
@thomasthomson-rn5ch18 күн бұрын
God is there watching
@CharlieChirwa18 күн бұрын
MCP ndiyakupha
@scotnkhoma18 күн бұрын
Nde mwati akulepheletsa nvura ndi chakwera? Nanga ku zambia ndi chakweraso? A kalindo za mvura musiyileni Mulungu musaphatikize ndi za ndale plz.